Mkulu wina wa zaka 35 zakubadwa ku Lilongwe walamulidwa kukakhala ku ndende ndikukagwila ntchito ya kalavula gaga kwa zaka 21 kamba kopezeka olakwa pa mlandu wogwililira mwana wa zaka khumi. Malingana ndi mneneri wa apolisi… ...
Articles By Ben Bongololo
Njonda zitatu zomwe zidanjatidwa pa mlandu okuba katundu zitavala ngati gulewamkulu kwa Chaima m'boma la Kasungu azipeza zolakwa pa mlandu wakuba ndipo azilamula kukagwira ntchito ya kalavula gaga kwa zaka 12. Nkhani yonse ikuti njondazi … ...
Apolisi m'dziko lino anjata a Shirieesh Betgiri yemwe ndi mkulu wapampando wakale wa kampani ya Salima Sugar kamba kokhudzidwa pa mlandu wakatangale wa ndalama zoposa K50 billion A Peter Kalaya omwe ndi mneneri wa apolisi… ...
Anthu atatu amwalira pamene anthu ena asanu ndi m'modzi avulala pa ngozi yomwe yachitika dzulo madzulo m'boma la Nkhotakota Yemwe ndi mneneri wa apolisi m’bomali a Sub-Inspector Andrew Kamanga ati galimoto ya mtundu wa Sienta… ...
Nthambi yoona zanyengo ndi kusintha kwa nyengo m’dziko lino lachenjeza a Malawi maka akuchigawo chakum'mwera ponena kuti lero pa 14 December 2023, mvula yamphamvu ikhale ikugwa. Malingana ndi uthenga omwe watulutsa ndi mneneli wa nthambiyi,… ...
A Ken Msonda omwe ndi membala wa komitiyi yaikulu ya chipani cha DPP apepesa kwa mtsogoleri wa chipanichi a Peter Mutharika pa zomwe iwo akhala akuchita ndipo pano ati akufuna a Mutharika atengenso mpando wa… ...
Apolisi m'boma la Zomba amanga njonda ina kamba kopezeka ndi ma simukadi a lamya okwana 99 omwe njondayi imafuna kuti ilowetse mundende ya Zomba. Malingana ndi mneneri wa apolisi m’bomali, mkuluyi yemwe dzina lake ndi… ...