UNICEF has demonstrated their commitment to improving healthcare access by generously donating 18 motorcycles to the Blantyre District Health Office (DHO) to help improve the delivery of vaccines in the district’s remote areas. These 18… ...
Articles By Archangel Nzangaya
Thupi la katswiri pa mayimbidwe, Lucius Banda, likuyembekezeka kufika m’dziko muno lero masanawa kuchokera m'dziko la South Africa komwe wamwalilira, ndipo pali chiyembekezo kuti lilowa m’manda Lachinayi sabata ino. Izi ndi malingana ndi mwana wa… ...
Sukulu zomwe sizaboma zalangizidwa kuti ziyesetse kuti ndalama za nkhani nkhani zomwe ophunzira amapeleka ngati fizi zidzioneka phindu lake pokhozetsa bwino pa mayeso a boma, ponena kuti makolo amakhala atadutsa m'zikhomo kuti apeze ndalamazo. Izi… ...
The former ruling Democratic Progressive Party (DPP) will hold its long-awaited elective convention General Assembly next month. According to a press statement signed by the Presidential and Party Spokesperson Shadric Namalomba, the elective Indaba is… ...
Inkosi Kwataine ya m’boma la Ntcheu yadandaula kuti anthu opeleka chiyembekezo ochokera m’bomali amafa mosadziwika bwino ndipo ati ndiodabwa kuti anthu akuuzidwa kuti asunge bata pamene imfa ya yemwe anali wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko… ...
Malawian celebrities are mourning alongside musician Wonderful Kapenga, known as Waxy Kay, following the passing of his father, Bishop Charles Kapenga, on Sunday. Bishop Kapenga, who founded and led the Believers Assembly International Church, passed… ...
Patadutsa pafupifupi miyezi inayi (4) chimwalilireni, thupi la katswiri pa nkhani ya zisudzo m'dziko la Nigeria a John Okafor omwe amadziwika kwambiri ndi dzina loti Mr Ibu, layikidwa m’manda tsopano. Thupi la Mr Ibu omwe… ...