UDF
2025 kuli gule! Zisankho zapatatu zitionetsa kathu! Yemwe anati mwana mbu, make mbu analinga atapsola diso ku chipani cha United Democratic Front (UDF). Inu, ali ndi mwana agwilitse. Atupele Muluzi yemwe m’chaka cha 2022 adatula… ...
Noel Chikoleka
Woyimba Noel Chikoleka yemwe adayimba nyimbo ya “Makofi” ndipo amadziwika kwambiri ndi dzina loti Phyzix, watsutsa mphekesera zoti iye adamenya woyimba nzake Pop Young chifukwa chokakamiza nkazi yemwe adapita naye kokayimba kuti amulore chibwezi. Potsatira… ...