Twenty-two buses carrying Malawian returnees are expected to arrive in the country through Mwanza Border today, Saturday, February 20th, 2021. This is according to Mwanza border public relations officer Inspector Pasqually Zulu who said 1539… ...
Articles By Archangel Nzangaya
Pomwe boma lalengeza kuti lolemba likubwelari sukulu zonse mdziko muno zitsekulidwe, bungwe la aphunzitsi la Teachers Union of Malawi (TUM) lati aphunzitsi onse apitilirabe kukhala pa tchuthi ngati boma silimva pempho lawo pandalama zaukaziotche. Malingana… ...
Boma la Malawi lalengeza kuti kuyambira lolemba pa 22 February, masukulu onse atsekulidwa. Izi ndi malingana ndi nduna ya zaumoyo a Khumhize Kandodo Chiponda omweso ndi m’modzi mwa akuluakulu a komiti ya mtsogoleri wa dziko… ...
Malawian concerned students have organized city after city demonstrations starting next week over prolonged school closure due to the COVID-19 pandemic. According to a statement made available to Malawi24, the group through its national chairperson… ...
Apolisi mumzinda wa Lilongwe anjata wachiwiri kwa mkulu wanthambi yowona za ngozi zogwa mwadzidzi a Fyawupi Mwafongo kaamba ka ndalama za mlili wa covid-19. Nkhaniyi ikutsatila kafukufuku yemwe akuchitika zitadziwika kuti ndalama zomwe zimayenera kugwira… ...
Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera achotsa paudindo mkulu wa nthambi yowona za ngozi zogwa mwadzidzi komanso wapampando wa komiti yamtsogoleri wadziko pantchito yothana ndi mlili wa Covid-19 kaamba kakusakazidwa kwa ndalama za Covid-19.… ...
Opposition Democratic Progressive Party (DPP) Spokesperson on Legal Affairs Bright Msaka has told president Lazarus Chakwera to refrain from trying to gag the Malawi Human Rights Commission and Anti-Corruption Bureau (ACB). Msaka was responding to… ...