Boma la Malawi lalengeza kuti kuyambira lolemba pa 22 February, masukulu onse atsekulidwa. Izi ndi malingana ndi nduna ya zaumoyo a Khumhize Kandodo Chiponda omweso ndi m’modzi mwa akuluakulu a komiti ya mtsogoleri wa dziko… ...