M’modzi mwa anthu omwe akhala akutsogolera a Malawi ku ziwonetsero zomwe zakhala zikuchitika mdziko muno posachedwapa, a Bon Kalindo, alengeza kuti ayimitsa kaye ziwonetsero zonse zomwe anakonza kuti zichitike. A Kalindo omwe amadziwika ndi dzina… ...
Articles By Archangel Nzangaya
,Phungu wa chipani cha MCP kum’mwera kwa boma la Ntchisi, a Ulemu Chilapondwa, apepesa pa zomwe anayankhula dzulo kuti anthu akumudzi sadandaula za kukwera mtengo kwa mafuta ophikira. A Chilapondwa apepesa lero mu nyumba ya… ...
Mpondamatiki Thom Mpinganjira tsopano akupuma mpweya wabwino bwalo la milandu la apilu litalamula kuti atuluke ku ndende pa belo. A Mpinganjira analamulidwa kukakhala ku ndende kwa zaka zisanu ndi zinayi (9) kaamba kowaganizira kuti ankafuna… ...
Imodzi mwa makampani ogulitsa zipangizo zomangira m'dziko muno ya Macsteel, yapeleka mphoto ya K1.2 miliyoni kwa bambo wina yemwe wayigwilira ntchito kampaniyi kwa zaka zokwana 40. Malingana ndi akuluakulu akampaniyi, bambo Biston Mtemankhawa ndiomwe alandira… ...
Anthu m'dziko muno akudzudzula mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera pabodza lankunkhuniza lomwe wayankhula kuti boma la Tonse lapanga ntchito zoposa 900,000. Potsekulira nyumba ya malamulo Lachinayi mumzinda wa Lilongwe a Chakwera anatutumutsa anthu… ...
The Malawi Government through the Ministry of Education has distributed over 1.2 million new Science and Mathematics textbooks to secondary schools across the country. This is according to minister of education Agnes NyaLonje who was… ...
Police in Dedza have arrested a 49-year-old carpenter for stealing 25 toilet doors worth over K1 million at Kalinyeke Primary school. The suspect has been identified as Henry Msampha of Chifisi village in the area… ...