Tabitha Chawinga yemwe ndi katswiri posewera mpira wa miyendo wati iye adzayamba kuganiza zokwatiwa akadzafika zaka makumi atatu (30). Chawinga yemweso ndi mtsogoleri wa osewera mpira wa miyendo ya atsikana ya dziko lino ya Scorchers,… ...