Bingu National Stadium contractors have informed government that they have completed construction works at the magnificent stadium which is in Lilongwe.
The government of Malawi initially communicated that the deadline for construction works at the new soccer mecca is November 30th 2015 but the contractor wrote a letter to government on 28 November to inform it that they are ready to hand the stadium over to Malawi Government.
Minister of Youth and Culture Grace Obama Chiumia confirmed the development to the media and she also revealed that the stadium will be first handed over to Ministry of transport and public works before officially being handed over to the ministry of sports.
“It’s true the contractor finished all works and they only ask government to give them three days notice before the actual handover,” said Chiumia.
Bingu International Stadium will attract the soccer fraternity since it has 60,000 capacity, a far higher capacity than that of the old soccer cathedral, Kamuzu Stadium.
Amalemu amasomphenya RIP
Goodmove
Sopano tizizionela pafupi silute to mr bingu zikamachitika zabwin kumakodwako nyasaland ,zikachitika mbola kumakwiyaso koma iyo ndikuyenela kukodwa basi
ntchito za manja ake zidanchitiradi umboni rest in peace ngwazi, otsakhala izi tuwonapanozi, panja penipeni, uko!!
State of the art.
State of the art.
I salute that late Bingu reason,reason if u look at houses we were at the tall of the africa no sameone came to construct something better why not says thanks
JB palibe anachitapo,nde ikhale bingu yemweyo
Congraturation Chinise Govt, Mwatimangila Stadium Yamakono Ndie Chitukuko. Chenjezo Amalawi Sizandale Ai Stadium Ndiyaboma Mainawo Aaa Mchizindikilo Chamalo, Ndie Chiwewe Ai Tose Ndi Amalawi Palibe Tsamunda.
Congraturation Chinise Govt, Mwatimangila Stadium Yamakono Ndie Chitukuko. Chenjezo Amalawi Sizandale Ai Stadium Ndiyaboma Mainawo Aaa Mchizindikilo Chamalo, Ndie Chiwewe Ai Tose Ndi Amalawi Palibe Tsamunda.
Malawi ili bhooo .keep it up. May God bless Malawi.
do you call this world class
Thanx Abingu Poganiza Zomanga Stadiam Yamakon Chifukwa Tpitilixa Kukukmbukiran {RIP}
The last time i checked it was Chinese gvt doing the construction and not Malawi gvt, mwatani kodi
Zilide mdolo iz
nice one.
Bingu rest in peace
Joyce banda soccer city
yathuyi ndi Bingu stadium ngati mukufuna dzina lina pitani kamangeni yanu malo ndi ambiri-mbiri ……anthu osaganiza inu !!!! Demeti!……ng’ombe mumagawa zija mukazipatse mayina zonse zikakhale Joyce Banda
yathuyi ndi Bingu stadium ngati mukufuna dzina lina pitani kamangeni yanu malo ndi ambiri-mbiri ……anthu osaganiza inu !!!! Demeti!
build another for Blantyre right at Kamuzu stadium.
So what about the oldest Stadium Kamuzu? what are you going to do with it are you going to leave it old like that or you will maintan it? Do something with it pls.
poor malawian, u r failing to build ur own 1 bedroom house and rent a house wth other 5 people to save…… but u r busy insulting the great works of a wise and well visioned Bingu… Shame on you.
chili khenge
chili khenge chi international stadium chathuchi bwanj
I support u clement osat mayina aaa anthu oziundikirawa iyaah! Cinthu chapakapito azikacisamutsimula pakhomo pake uko komwe kumapeto kwa dziko
Why Bingu stadium?it should be rather Lilongwe/JB stadium!
MALAWI-CHINESE Woyeeee ngakhale ngongoleyi ndiyakanthawi ana athu azabwenzaso
jb jb wachani?? Apa…ku zambia kuli levi mwanawasa stadium..ku john kuli moses mabidha nde bingu walakwa chani
Mpira wake ndiye uli kutitu?
stadium ndi imeneyo,wina akabemo ma pipe amadzi ndi nthambo zamagetsi.
jst call it CHINA STADIUM
did is wow
it is not proper to give national structures personal names. It does not matter who signed or what because it is their duty to bring developments in a country. so giving personal names to national structures as if its their investment or business.Should we assume president aliyense wobwera adzitcha dzina lake chinthu chomwe wapanga? it doesn’t make sense!
Ulemu wanu mai JB pobweretsa stadium kuno ku Lilongwe, mudaonetsa kuzindikira kwanu,paja adafuna ipite ku Ndata.Dzina achotse aike lina,bolaso akadati J B Stadium chifukwa adagwira ntchito yabwino.
keep on dreaming u ‘ll tell us whn u’re done papa..hihihihihihihihihihi í ½í¸²í ½í¸²í ½í¸²í ½í¸²í ½í¸²í ½í¸²í ½í¸²í ½í¸²
A Malawi ! Bvuto ndi chani ndi dzina ili ? mangani yanu nanu mutchule maina anu apo ayi kakolopeni nyanja kapena mukayanike ufa pa chingwe. nsanje , dakha ,kaduka nd nkhwizi ndae zake za munthu okhala ku Malawi ,,, dzina limasewera mpira
THATS UR FIRST PROBLEM!! WAT’S THE MATTER WTH THE NAME??? LET IT B BINGU YEMWEYO. APO BII TEL UR GRAND PARENTS KUT AMANGE CAO TICITCHULE DZINA LAO. MUSOVA!!
Muzane anyau nosesipovinila pamenepo
kkkkkk improvement
ntchito za manja anga zindichitire umboni
Amalawi umbuli basi
faz enanu ndinu opanda zelu! mumafuna itchedwe kut chan? fuk u!
faz enanu ndinu opanda zelu! mumafuna itchedwe kut chan? fuk u!
hahahaha mkuti World Class….. kikikiki uluuuuu iyo ndi community ground ya ku America.
BINGU MUFUNE MUSAFUNE
#BNS BASI
This is going to be a traffic and parking nightmare because no one thought to develop any of the infrastructure AROUND the colossal new 60,000 seat stadium!
Thats wonderful,Malawi ryt now has avery beutiful stadium,,,So much thanks go to Dr Joyce Banda 4bringing bac to Lilongwe the capital city not how Bingu was thinking to shift to BT,,,&mor’over pple from chitipa&nsanje shuld meet “pakati”,osat munthu kuchoka ku Mzuzu ulendo wa ku BT ayi sizoona…..Dzinalo asinthe osat Bingu…yaku BT ndiye azatche Bingu.
Why? politics ndi fotobolo yomwe naima ndi ambiri if you don’t have one please ask people to give you one, Osati zofuna ufumu wanu upitilire ….!!!…. Bingu samadziwa ndi sanamenyeko mpira wamapazi zinazi kumafuna anzanu bkoz mudzasochera zano ndiika dzina la munthu okufa and expect our national team to do better hehehehehehede mwapenga eti name ndikupeleka ine pano Lilongwe national team……!! …. Period
naima? ukutanthauzanji
Zopeleka maina aanthu pa chitukuko cha dziko zinavaya kalekale man ndiye bwenzi kuli Queen stadium ku mangalande
zachi china izi zosalimba china ndi china zosalimba
Zili bwino.
flames iyambe kugazidwapo tsopano, shaaaa
malawi 24 ngat mwalembako nkhani yamzeru nde ndiyi
By the way…we owe the Chinese for this. It’s not free….our childrens taxes will pay for it over the coming years
Zinchito za Joyce Banda izi
Bwanji sadatchule ndata ija dzina lake or university ija kuti Bingu wat wat? Mesa zonse zinali plan yake? And yet farm yo ndi ya personal, stadium siyapersonal anakapeleka dzina lina iiii kaya amalawi poti timangomvera zilizonse
Kusaganiza kumeneko kamuzu ndiapesono chisiru
Kkkkk, nanga KCN, KIA nza personal?? Kukonda ndale ngat m’madya bwanj?
vuto la a malawi ndilimeneli kusayamika munthu akapanga chinthu chabwino that’s why timangokhomelerana …..mumafuna atchule dzina lanu mwene?
waat kkak is going on in ur mind. Bingu staaand out fo his term…. atleast I cnt point wat he achieve not achemwali….
Kongoti Boma Likapanga Chinthu Chokhudza Mpira Mmalo Moti Tiyamike Timalowetsa Ndale Koma Choncho Si Bo
tamusiyeni uyu inuuuu asatidwalise mutu….mwina amutuma uyu kkkkkkk
Hehehe hahaha kkk koma kumeneko !!
iyi ndiye minyama mukuyiputayi, stadium ikakhale bingu zoona?
it need some strategies to care the stadium
I am happy because atlist now MALAWI has astadium, but my worry don’t sale it. This will be difficult to take it to CHINA.ichi ndicho timati CHITUKUKO.
Mawulle titsegule zimenez basiiiii
Mawulle titsegule zimenez basiiiii
Hand over poti nzika za china azigwira ndminyanga ya njovu ati muyiwale,azingokuberan ameneyo ndye mchina.
Alwayz DPP moto kuti buuu
That’s what we wanted
Kma abale kkkkkkkkkkkk! Akt PP yanyamuka kikikikikiki! Ndye lerodi kulibe inayenda kkkkkkkk!
Stadiums won’t benefit us let’s develop our beautiful beaches.China go for hotels along the lake please
woow thats great luking very beautiful
No gvt structure’s to be named after an individual…that’s my take…its the MW citizens who will be paying for that stadium. Straight from their pockets…..HKB named most of the projects in his era in his favour…just to be changed by big headed Muluzi…So if the nx leader will not agree to whatever it will be called now..she / he is going to change it too….stop confusing people…Let parliament decide…how many things does DPP want to be named after Bingu…hey..?
Nice stadium. Koma tisiye kuluza sopano
Fisid wizzardz stadium iyi..
bingu initiative..even if chakwera will be a presdent and ask donors to build a museum and name it chakwera museum tilibe pulobulemu,,,,this was one of bingus master class developments!!whether Chinese or who so ever !!! don’t hate the player!hate the game! Amayi had all the resources, support and everything…but she failed to build even a hospital in her village,she was busy with cows!
I willl be the gate collector and no salary
Bingu national stadium??? What a name
Mpia ku Malawi kulibe so wats the use of the stadium!!!?????
This Ground Is Suitable For Supper League Games Not Becoz National Team Eee Ndimbola Man.
gud development,ma heterz munya!!!
ok
Amfiti nonse kayambeponi kuthamanga lero
its agoog
The one & only which has been never ever been kkkkkkkkkkkkkk L city ndi more
Osat BT
China 4n 1year Garantee….! China Torch 2month Garantee…..! Pariament…Yayambapo Ming’alu Kkk Stadium Mot Mudzikhala Anthu …????? Ma China Nkumamanga Chinthu Cholimba Awa? Komanso Team Yake Iti Yongokong’onthedwayi Apa Ndie Taluzatu Simplex Ndiuyo Waswela Nchitokos Bao!Kkkk Kumalaw Mpira Udatha Akadamanga Bar Kut Maplayer Azipikisana Kumwa Ndi Kubanda! Komanso Aliense Olowa Mmboma Akapanga Chinthu Aziika Dzina Lake? Kupenta Komweku Ku Area 30 Akut “peter Waz Here B4 U” Munthu Wophunzila Ameneo “Zamanyazi” Kwakula Nkuzikonda
Mmmmmmmm Mmmmmmm too much boring comments rolling out.
World class? Mmmmmmm
Bingu stadium? mmmmmmm
Thumbs up to Chinese government .laponda la mphawi.
Kodi zomapereka maina awanthu pazinthu zotukula dziko zilipobe,suja munasintha kamuzu central hosp kukhala lilongwe central.tsono chadza ndiyaninso chotinso bingu stadium?lf its a world class structure y not give it a simple,specific,reasonable sportive name than malabishiwo.koma kunyasalande sikudzathekaso,kwenikweni vuto ndichani amalawife.nanu alilongwe city council kuvomera?
chabwino tamva koma dzina musinthee
Stadium imenei amangila amapemphero nd oimba kkkk ku mw kulibe mpila gyz asavutike
Boma liitane Brazil ndi Argentina azasewere tsiku lotsegulira. Saizi yathu ife mpa Civo, Namkhaka ndi Kamuzu stadium. Malo ovemchera alipo, nanga ngalande zilipo zoti tizikafikira ku ma stand zilipo?
mwaine ndikuyenela kuyamikila pa prjc iyi kuti inatha bwino stdum ilibwino kwambili zinalo sivuto.
A Malawi kukonda kudzithiramo World Class mwati?
guyz amene akuti that stadium imayenera kukhala ndi dzina lina than bingu kwa ine if i may ask who sighned the deal of constructing the stadium? let me also assure you one thing joyce was just following the foot steps of bingu because bingu had already signed in agreement with china just like zomwe peter amazupopa peter zoti wabwereka ndalama from if you dont those things were agreed when joyce banda was in office of president penapake osamangolalata ndipo dzina loti bingu sounds much better
Man bingu anali kape coz amafuna chithu chikakhale Ku nthyoro komwe kuli kwawo pamene amayi aja ndi amene anapanga zithu zotsatila ma paper so
Kape nd iweyo mwana wa hule!joyc banda wa chan?machende akonso kwa masiku atatu
Joyce Banda did nothing for her two years udindo unali ongogwilizira for that moment, no project that joyce sign on behalf of Malawians lets just admitt now
Chifukwa chake zina ndi kanswala machende ake
#Kanswala mwana wa hule iwe amayi ako hule,bambo ako chidakwa,iwe mbuli machende ako wamva
Name it Xi Jinping
As we ar celebrating the completion of this magnificent bingu stadium, lets not 4get 2observe a minute of silence for those who lost their lives while on duty constructing this stadium i understand 3people died when they fall from the top R I P
Thanks to China,shame to homo donors
Great achievement.
That’s cool but do we have the capacity to maintain it? CapeTown is crying because the stadium is useless after World Cup
Umange yako kumene ukufuna, komanso uyipase zina limene ukufuna!
#Atleast!
koma ili kutali nd anthu iyi, anthu amakhala ku BT
Vitu ukunama thank God if ur in Lcity cause anzako ali ku BT n MZ Lcity ndi deal
hahaha man to be honest BT nd dhilu, am in lcity to xplore
No more words just use dat stadium its for ours…..
in my own school of thought I think it would have been better to give the stadium a proper name than a name of a person despite who made the plans of it to be built n who acted on the plan n turn it in reality. tikavula magalas andale kod sitingayitchule stadiumyi kut national stadium or even Lilongwe stadium amene than dzina lamunthu? I think zimenez zingapangitse kut malo adziko lanthu lino I.e lilongwe atchuke world wide than kutchukitsa dzina lamunthu and at the end zidzalowa mitundu from ndale kut stadiumyi ndiya alomwe ndepopewa zonse izi tipange ka referendum kut tipeze dzina labwino la stadium yi. nanga bas chili chose kumalawi kuno chidzikhala mudzina lamunthu? kamuzu stadium,bingu stadium,ethel mutharika maternity wing etc zinthu zadziko zizikhala ndimayina adziko osat mayina a anthu tisiyanitsa bwanj chinthu cha private ndi cha public? maganizo anga amenewo
Maganizo abwino koma abodza… Wake up man, everywhere you go, you will see names of people who made history on magestic structures….they do it in respect
#Moyo maganizo oputsa ndipo xool yako sunapindule nayo ubwelelenso mkalasi uzikatenganso history pa ma subject ako wamva
#Moyo maganizo oputsa ndipo xool yako sunapindule nayo ubwelelenso mkalasi uzikatenganso history pa ma subject ako wamva
I said it at the very beggining kut in my own thoughts,get me right wasn’t representing your thouhgts nop so mind your language ok
Don’t mind these people Douglas, they’re educated blind, history is about things that have gone. we’re in modern society where modern knowledge is applied. malawi is one of folish nations that name almost every public infrastructure in somebody’s name. This is Malawi not the leader. Wake up guys And be Creative don’t driven by history.
chifundo these people think like their shoe sizes not age. how will we differenciate between a private property n national thing? guys wise up now….Malawi kugona
#Moyo this z a nud idia look kenyatta road…du u know kenyatta? paul kagame road mugabe road kamuzu central hospital just to mntion a few
ajobe you talking of roads n they r of no use since u can’t get fame through road. if its so can u jst downlist any.foreign country roads u know. and concerning those given names kamuzu n the likes I already talked of it in my 1st status kut its useless. what’s thah benefit of naming something of national concern a name of a person? at the end president ali yese adzifuna atchule chili chonse dzina lake nde dzimayina dzidzangot mbweee
the stadium deserves the name Bingu. sizachilendo zimenezi anthu wochita zinthu zikuluzikulu timawadziwila ntchito zawo nde polemekeza kulimbikira kwawo njira yake ndi imeneyi …..mudzasiyanitsa bwanji John Tembo ndi Bingu ? this is the best way .
iwe kondwan zachikale zimenezo kod mesa president akakhala pampando ntchito yake ndiyotukula dziko? vuto amalawi timayamikila chinthu chot chimayenela chichitike,mesa munamusankha kut azatukule dziko nanga ndalama amatukulilazo ndiza mnthumba mwake kapena zanu amalawi? good example undipatse k1000 @ the end ndikupatse packet la sugar mkoyenela kut undiyamakile mesa ndi ndalama zako zomwe had it been mnagula ndi ndalama zanga it would v been a different issue altogother. nanga president aliyense akhale pampando akachita chinthu I.e chitukuko ndekut azichitchula dzina lake? nde kudzapezeka kut chili chonse mmalawi muno ndidzina la munthu,sinthan kaganizidwe amalawi anzanga ndi nchito yake president kutukula dziko lino nanga kapena timamusankhilanj? or else dzina likhale laku china sinanga ndamene apanga chinthucho ndi chichili chonse chawo? ganizan mofatsa makosana
Flames izifera pabwino timu yopasa manyazi
tizizaluzapo bwino
magetsi sanaike ndi ma tv
Joyce Banda stadium za Bingu zo ife sitikuzidziwa.
Some people are just fools in the making….y being so superstitious a name is just a name…zaminyama zanuzo thats in your head…..n we dont give names to a thing because one built it ….its out of honour that we name a thing after a person….respect thats all. For example South africa built stadiums for world cup and named them after some dudes…madolo amene aja sanamange those stadiums……daah think before talking…..Masauko Chipembere for example….Bingu was a genius….a hero….he left a legacy …whether one agrees o not…..Thats wat we call a self actualised person….it takes guts to get to that state…..not many of us will get there….speaking my mind…no offence if you are offended go and lick your elbow…kkkkk out. Thats y they named it after him…am not a politician but i totally support that name.. BINGU…KAMUZU….CHIPEMBERE…totally venacular language…mother tongue…Chichewa cheni cheni
World class as per Malawi standards sure. This has not being constructed by Malawi government but by China, both money and labour. It is an insult to call a stadium Bingu, for what. Malawians tulo kwambiri. Lets give structures appropriate names not names of thieves, murderers, killers, dictators, swindlers. Even China called their magnificent stadium in Beijing, “Birds Nest Stadium, why don’t we call ours, Lilongwe Arena or National Arena or simply Lilongwe stadium and by so doing selling our capital city whenever an event or match takes place there Lilongwe is mentioned, not Bingu what’s that???
Mwati Bingu anakulakwirani chani?
So is it worldclass, yes or no? No to me
Not world class, seen and been to some fantastic stadiums, these is complete average. Has it got a swimming pool underground?
Sintha iweyo dzinalo sukuoneka ngat ul nd nzeru kwmbr.Kapena ungomanga yako kwanuko nde dzina lirilonse lomwe ukufuna
To say the truth this stadium is not going to help why didn’t you use that money to build a five star hotel along the lake? We have most beaches worth development. Nzeru zayekha. …….. Next time please request the Chinese to help us develop our tourism industry not stadiums
You have a point Harold
I hope your not a citizen of Malawi, go to hell Bingu will always be remembered for his great achievement, udzasauka ndi ntima oipa
i think ndiwe mbuli pakhaniyi mesa tibwaza ndalamazo ndingngoletu
Mbuli ndi iweyo, didn’t you hear that China has written off some debts, anyway since you know more, how much ngongole is for this stadium??
harold mesa mukukaniza malo kumangochi ndiye amanga mwanba?
zikomo china
ndiyo yake
Why should we thank the chinese government?
welcome development what about these poor roads around this #Stadium?????
welcome development what about poor these roads around this this magnifiencent #stracture?
I,ts a dream vision of the late presedent Bingu by changing state relationship fr Taiwan to China.
Bingu’s leadership was one with a vision. We always support u baba. Rip
My eyes iz going to see some changes
Thank you so much for the good job you are developing our country ” AFECC /GOLDENPEACOK GROUP OF COMPANIES””?✌
World class ma my foot
welcome to Lilongwe the Capital City
Its better to named it “captal stdiam” not bing as wel.
Kamuzu stadium pano nd miseum very old and ugly
jb stadium
waku LL tsopano.
malawi sinafike pokhala ndi stadium, tiyeni tiigulise
Kkkkkkkk tizipangapo rent eti kkkkk dollar yakeyo tigule chimanga lol
Kkkk koma ma zoba enawa hahahaha Kodi umachokera chigawo chit cha Malawi iwe?
cha China sichilimba, chikayetsetsa ndi 4 years. vuto lakenso muzikalowetsapo a kasinja, pa in dependence day ndinso kuvinirapo senderani ndi mapazi azikang’a. chitimu chake chofoiranso chosewera ngati ZiDakwa Socials. Mxieuuuuuuuiui.
Love it.
World class?
Tiyeni tiyamikire ichi sichopangira kampeni ichi ndicha amalawi tonse
Zilibwino
Good work.but do we have the money to maintain the stadium?
Mufune musafune nd Bingu national studium coz t woz hz plann kt amange ku elaz ena angomalizitsa
Malawian readers u r a full of sheet
R,I,P BINGU WA MUTHALIKA
koma mukuyiwala kuti amafuna kuyipititsa ku BT,koma jb anapangitsa yimangwidwe pa LL zina kumayamika
wow, atleast we have something to boost about although its from china. Many thanks to China.
wow…das gud development…thumb up chinese goverment..w r appriciated…
Peter Stadium
Ngati atsiliza ya ku lilongwe,nde kuti abwerer adzayambe yaku blantyre.
Mmmmm China men! where is the parking lot? Simunamalize no car park
Nde Dpp imeneyo, pano we have started Peter Mutharika stadium in Rumphi
Mudzikavinirapo gule wanji?
Thanx should go to Dr Joyce Banda poganizira kuti Stadium ikamangidwe ku Capital City ya dziko lino to the Chinese government may the good Lord Bless ur nation and the Leaders
tapeza kojambulirako xthuz zoti tizpanga upload pa fb….paja ndfetu
kkkkkkkkk sukunama man, ma-profile pic azizakhala ojambulitsa komweko basi kkkkk
(y) (y) (y) bingu? Kkkkkkkkk (y) (y) (y) (x)
Iwe #Dambe kod munthu amene amapeleka ndalama yokagula sugar nd munthu wot wangopita kukagula sugayo kod mwini wache ndndan? we luk @ the source/founder nt the consumer
hands up to Chinise government we salute u for changing malawi to another level GOD Bless u
Ndimayesa Bingu stadium ili ku Blantyre?
Big up kwa yemwe anabwerets dis project
welcome to LL CITY
BUILD NETBALL AND NAME IT JOYCE NOT THIS MAGNIFICENT”BINGU NATIONAL STADIUM”………the name #BINGU is unique
Wow wat beautiful stadium 15 kms frm my place allways there.
DPP moto kuti buuuuuuu 2019
JOYCE BANDA IS THE ONLY MALAWIAN PRESIDENT WHO DIDN’T ESTABLISH OR COME UP WITH PROJECTS THAT BENEFITED THE NATION…ALL SHE DID WAZ BUILD A COUPLE OF HOUSES AND DISTRIBUTE A FEW COWS!
ndendende ngati levy mwanawasa stadium kuno kwathu ku ndola zambiya!
Project ya bingu iyi osaiwala ana signer ndi bingu koma funso tukwanisa kusamala n look at our pathetic national team kaya
Apa nde ndi diiiiiii lu
Maganizo ochuluka amene Ali pamwambapa ndiopanda nzeru why can you be buisy comparing our beautiful stadium with stadiums of the developed world yet your country is on number one on the list of undeveloped countries tangoyamikani apa,the following deserves my appreciations,Bigu for brilliant idea of bringing international standard stadium to Malawi,Joyce Banda for taking back our stadium to LL ,China for constructing the magnificent stadium saving us from kamuzus death trap
iwe nde wayankhula bwno, osat enawa kumangokangana m’malo monena zanzelu, thats gud men.
Are we going to maintain it? We are failing to maintain Kamuzu Stadium in Blantyre you we have balls to do it. May be China will be doing it for us
Tell us where Bingu got the Money to build this stadium as per your confused claim? If he did then he was foolish instead of building a hospital or bus station bola
World Of Today
Nkhani yabwino
Ndkutha kuona stand ya mighty be 4ward.
gud development kuchoka kwa a presdent a maso mphenya prof Bingu wamutalika rest in peace wawa zanu mnapanga kale
Nde wina akavinilemo nyau tsopano
kkkkkiii umakwana iweyo!!!
Koma guys china chirichose ndale, dzina la stadium lalakwa chiyani, ATI bola adakapeleka kut likhale JB pot adamanga ndiyeyo, zabodzatu man zandale zanu zonamazo muzikanamiza ena, ife stadium tasangalala nayo posatengela kut yabwela mulamuliro wandani chifukwa stadium iri ku malawi
We need Rugby and Cricket national teams now to compete with world giant in sports
9c news lets take care of it
they can use night games as well?
a ken phiri ndinu mbuli yotheratu! Dat’s develpment
Tigulitse stadium yi kwa zungu ndicholinga choti tipeze folex mwina kwacha mkupezako mphavu +fodya ndiekuti mavuto achepa yes Malawi!!!
Inunso ngopepera kuteloko mwaganiza?kkk
Trouble mangwazu ndiwe wabodza ma suppoter a bullets amakonda kumwa wannkaka….za ma billboards ndi a noma….
Padzadza osazisata zampira makape am out check borrin ground,st james park,whitehartlane etc they all r used in premier league some look like civo stadium
Too bad our national team is pathetic
ntchito za abingu!!
kaya chipani cha dpp chinatani kaya chinatan koma chilungamo chake ndichakuti stadium iyi ndi project ya bingu and dzinalo anapeleka yekha mwini wake si wina ayi…….. nsanje ai apa chilingamo ndunenachi…..komaso mpila wa anyamata nde odziwika kuno nde chi dzina cha nzimayi chizitani pa football stadium…..analephela kumanga ndka netball stadiumm bwa?????
bola isamphe anthu
Thus a great development though people will never appreciate. We always judge out of hatred.
A good reason to stay in lilongwe
Flames izikhomedwera pamenepo ndi ma team akunja
Nde maganizo a bngu awaaa ..joyce banda wabwera litt???
Kodi paja ikukatsegulirapo ndi BB pa launch ya sponsorship yawo?,,nyasa BB woyeee!!!
lilongwe national stadium
Yes…. Bingu, not bad at all.
ma supporter a Bullets plz mumakonda ku phwanya ma billboards musazati phwanyire mipando
Jb stadium osati bingu nalema navokamba kambamwe
NO WAIT FOR NETBALL GROUND WE WLL NAME IT JOYCE. ….BINGU IS UNIQUE NAME
Nic 1
bola isakhale malo opangila misonkhano ya dpp.
Rabish.
But of all namez Bingu??? Hahahahahaha! Pliz kuipatsa minyama2 stadium kumeneko. Nd more over chinthu ichi anayamba kuchimanga anali Joyce Banda, y nt name it Joyce Banda Stadium??? U guyz munangogweramo kti ths project yatha mu nthawi yanu
Amwene Sanali Maplan A Joyce Banda Zokhuzana Ndi Studiam Bingu Ndi Amene Anali Mwini Wake Enawo Anangomanga Zoti Zili Paper Kale.
Ndipo sizandaletu izi. Bingu kaya Joice no problem. Ndemukat kuipatsa munyama y? Kodi Joice wachita zabwino zokhazokha paulamuliro wake? Cashgate mkoyamba ine kuinva ndi amaiwa. Bingu basiii!
Kod ndiwe mlendo kumalawi kuno??? Usalankhulenso…coz palibe chomwe ukudziwa!!! Zamkutu
Akanaitha CASHGATE STADIUM,cause wopanga plan anaba 91 billion kwacha pomweso omanga anabaso zake zosachepela 3billion kwacha.kwaine kuitcha BINGU kaya JOICE mainawa amangondikumbutsa umbava wandalama za boma.
palibe zakacash gate apa maina osewa mpaka bingu aaaa
Asafuna aziphe yekha kuli iyeko ndipo ukalephera ukakolope nyanja ife amalawi tikuti ndi Bingu nation stadium …iwe wa pp uvadi kuwawa
Kunoso ku Ndola stadium yathu ndi same ndi that 1, named after the late Levie Mwanawasa, I see nothing wrong with that name Bingu, all the best Malawi!
#Dambe mimba yamateweyo komanso panyopako ndi #JB wakoyo wamva! Ngati uli dolo upite ukafutepo dzina la Bingu ukaikepo lambuyako nyani iwe mxiii
Iwe ndi mlendo mdziko muno wamva palibe ukuziwapo umange yako ukayipatse JB Cashgate wamva
kkkk awa samazisata zinthuzi eti?
Koditu amwene eshiiii mukanakhala ena mkanangokhala olo kumangowelengapo ma comment omwe ena akulemba kusiyana ndi ubanditi mwaonetsa apawu
stadium iyi ndi ya a malawi!kaya wa dpp or pp nonse malo anu alipo kaya muzikatenga azimayi anu aja yonse bhoo musalimbane apa
chilichonse kulowetsapo ndale kkkk umbuli eti
When u gt noting 2 say jst dnt talk, ua 200 words gt no sense
Hehee!! Some people hey! Zomwezi mpaka kumatukwanizana? Osamangowerenga ma comment ngati ine bwanji?
This project inali ya Bingu,adapeza fundin yekha nd dpp gvt,,jb adagositha malo kut chimagidwe L city,,ndye jb chikukhuza nd chan?
Iwedi ndi Dambe eti?
#Dambe kwao ndikumphete ku malire a mwanza ndi neno kutchire kwachabechabe nde ungokhala chete
Malo abwino ovinila nyau
We dont care about its name but salute to the Chinese Government!!!
Salute those Chinese. .? I’ll do that if it’s for free..but if my children and my grand children will spend their hard earned money paying for it…I’m sorry I prefer to defer…
We oways play 2 God thru jesus i thnk u wil get me clear on dat
Nonsese…
When is it goin to be officially opened??????
Thats great. Ndifikako ndikaiwone
pano flame idziwina ku bt mkwaminyama pomwepo bb imenyerepo flames so aaa minyama yokhayokha
Bingu National Stadium is a really bad name!
This is indeed world class but my worry is we don’t have even continental class players
Hahaha.. True d@
Good development from Chinese government
But without a National team
malo osewerera mpira ndiamenewa……osanda manda a chichiri aja
malo osewerera mpira ndiamenewa……osanda manda a chichiri aja
Dream comes to perfection
Thanks to JB for bringing it back to Lilongwe, kuponda kunakanika! Hahahahaha
tiipange privatise.lets sale the shares
no more national team games in blantyre oooooh my God
My fellow malawians lets take care of it lets avoid vandalism coz this stadium is ours lets be civilised posamalira chinthu chimenechi.thanx should go to late bingu wa muthalika for his vision to bring this kind of stadium here in malawi.may his soul Rest in Iternal Peace
Nice, Govt must find a company that would be looking this stadium otherwise iwonongepa pompano.
zoona, ndi kampanda ka wire kaja mmm
BINGU?
Yaah, nobady else.
Just to remind you this is not World Class, its just Malawi class.
It is world class. The word has has mean you know
Malawi class
Thanxs Chinese government.
World class,hede!!kkkkk community centre yaku England
iweso nde mbalame bwanj, olo agogo ako anapitako ku england’ko, shame
iwe ndichitsilu eit?
Its “world class” indeed, akati world class tanthauzo lake mukuidziwa koma? why anthu timangonyoza always even pa zinthu zabwino kapena ur addicted to kunyoza? #SHUPITI
ndaniyo? #pax?
then the white hart lane is not in England
kuno ndiku malawi galu iwe, england unaptako iwe,
Some stadium used in England cannot be compared to our BINGU NATIONAL STADIUM u dont watch premier league ur simply a stupit idiot magot i hate DPP but dont cheat ppo
am very sorry for u,iwe nde kayatuuuu!! just pack ur baggages ukankhale ku englandko,bola akakukandile
OUR Dream stadium
kape iwe.
Iwe Ku Halale Kwanuko Ilipo Community Ngati Yathu Ukutinyozerayi? LEARN TO BE PATRIOTIC TO YOUR COUNTRY OR “BWELELANI KU HALALE”
Umbuli sitipanga pagulu community cetre sikhala ndi stadium malume
Its world class coz ikuposa maground ambili kumangalande monga ya chelsae,fulham,ambiri
Shame on u man.. ..learn to appreciate some other things u don’t even know a plane ticket price to England
iwe wabodza…carrow load,goodson park…white hard lane angafanane nd iyi?
mwana hule
Kumeneko Amati Kupusa Shit Of You
Mbuzi ya munthu
Ameneyu tisamusiye MCHENDE AKE NDITHU GALU
Bulutu halale,ukufuna ndkutukwane?
Unapusa iwe manyaka amunthu!
iiiiiiih capacity from 40000 to 60000??? koma atolankani. nthawi zonse mmakambaza 40000 koma lero mukuti60000?????
Time to buy a ball n play there
Gud!
waste of resource which team to play there maybe Chipolopolo of Zambia mudzipangitsa rent
Ching Jung Hondai Chong Jing Ching Ching
Zakhala Bwino Tapeza poluzira Pabwino,Pokongola.
Very good observation, brother
world class kepana malawi class?
china bora
Ok bola government ithe kusamalira bwino
Joyce banda soccer arena
exactly man I fil u!
oh yes true
PP Goverment
Analifunadi
zopusa!!.
Mwanyanazobe inu a PP mudangogwirizira
Tchulan a #pp chitukuko chomwe dziko la #China lakuchitilan
Kod mesa pp inanyamuka.mwanyera nonse munal pa mbuyo pa mabere!
Chimodz-modz nd etihad stadium…job well done..
malawi mwina nkuyamba kuwina
Bola isazagwere anthu I dnt trust these Chinese
simukudziwa chomwe mukukamba akulu…jst bcoz u bought a K500 chinese shoe and it didnt last long, doesn’t giv da authority to judge the durability of chinese funded buildings…kaguleni shoes ya 60 grand made in china…muzadziwa dat chinese products got quality
Ok boss lets wait and see
At the moment China cn reach ev 1 u cn find both fake n original interms hw cash u hv
#Felix mphamvu yaziwanda ikukulamulira ndakuwona
eti? ndiye kuti ndiwenso chiwandatu kkkkkk wadziwa bwanji hahahaha
World Class??? My foot
Bravo
World class,really???
its world class. its in the same category as stanford bridge, white hart lane n the etihad.