Malawi Government finalizes world class stadium construction in Lilongwe


Bingu National stadium

Bingu National Stadium contractors have informed government that they have completed construction works at the magnificent stadium which is in Lilongwe.

The government of Malawi initially communicated that the deadline for construction works at the new soccer mecca is November 30th 2015 but the contractor wrote a letter to government on 28 November to inform it that they are ready to hand the stadium over to Malawi Government.

Bingu National stadium
Bingu National stadium: Completed.

Minister of Youth and Culture Grace Obama Chiumia confirmed the development to the media and she also revealed that the stadium will be first handed over to Ministry of transport and public works before officially being handed over to the ministry of sports.

“It’s true the contractor finished all works and they only ask government to give them three days notice before the actual handover,” said Chiumia.

Bingu International Stadium will attract the soccer fraternity since it has 60,000 capacity, a far higher capacity than that of the old soccer cathedral, Kamuzu Stadium.

331 thoughts on “Malawi Government finalizes world class stadium construction in Lilongwe

 1. Sopano tizizionela pafupi silute to mr bingu zikamachitika zabwin kumakodwako nyasaland ,zikachitika mbola kumakwiyaso koma iyo ndikuyenela kukodwa basi

 2. I salute that late Bingu reason,reason if u look at houses we were at the tall of the africa no sameone came to construct something better why not says thanks

 3. Congraturation Chinise Govt, Mwatimangila Stadium Yamakono Ndie Chitukuko. Chenjezo Amalawi Sizandale Ai Stadium Ndiyaboma Mainawo Aaa Mchizindikilo Chamalo, Ndie Chiwewe Ai Tose Ndi Amalawi Palibe Tsamunda.

 4. Congraturation Chinise Govt, Mwatimangila Stadium Yamakono Ndie Chitukuko. Chenjezo Amalawi Sizandale Ai Stadium Ndiyaboma Mainawo Aaa Mchizindikilo Chamalo, Ndie Chiwewe Ai Tose Ndi Amalawi Palibe Tsamunda.

 5. yathuyi ndi Bingu stadium ngati mukufuna dzina lina pitani kamangeni yanu malo ndi ambiri-mbiri ……anthu osaganiza inu !!!! Demeti!……ng’ombe mumagawa zija mukazipatse mayina zonse zikakhale Joyce Banda

 6. So what about the oldest Stadium Kamuzu? what are you going to do with it are you going to leave it old like that or you will maintan it? Do something with it pls.

 7. poor malawian, u r failing to build ur own 1 bedroom house and rent a house wth other 5 people to save…… but u r busy insulting the great works of a wise and well visioned Bingu… Shame on you.

 8. I support u clement osat mayina aaa anthu oziundikirawa iyaah! Cinthu chapakapito azikacisamutsimula pakhomo pake uko komwe kumapeto kwa dziko

 9. it is not proper to give national structures personal names. It does not matter who signed or what because it is their duty to bring developments in a country. so giving personal names to national structures as if its their investment or business.Should we assume president aliyense wobwera adzitcha dzina lake chinthu chomwe wapanga? it doesn’t make sense!

 10. Ulemu wanu mai JB pobweretsa stadium kuno ku Lilongwe, mudaonetsa kuzindikira kwanu,paja adafuna ipite ku Ndata.Dzina achotse aike lina,bolaso akadati J B Stadium chifukwa adagwira ntchito yabwino.

  1. keep on dreaming u ‘ll tell us whn u’re done papa..hihihihihihihihihihi í ½í¸²í ½í¸²í ½í¸²í ½í¸²í ½í¸²í ½í¸²í ½í¸²í ½í¸²

 11. A Malawi ! Bvuto ndi chani ndi dzina ili ? mangani yanu nanu mutchule maina anu apo ayi kakolopeni nyanja kapena mukayanike ufa pa chingwe. nsanje , dakha ,kaduka nd nkhwizi ndae zake za munthu okhala ku Malawi ,,, dzina limasewera mpira

 12. THATS UR FIRST PROBLEM!! WAT’S THE MATTER WTH THE NAME??? LET IT B BINGU YEMWEYO. APO BII TEL UR GRAND PARENTS KUT AMANGE CAO TICITCHULE DZINA LAO. MUSOVA!!

 13. This is going to be a traffic and parking nightmare because no one thought to develop any of the infrastructure AROUND the colossal new 60,000 seat stadium!

 14. Thats wonderful,Malawi ryt now has avery beutiful stadium,,,So much thanks go to Dr Joyce Banda 4bringing bac to Lilongwe the capital city not how Bingu was thinking to shift to BT,,,&mor’over pple from chitipa&nsanje shuld meet “pakati”,osat munthu kuchoka ku Mzuzu ulendo wa ku BT ayi sizoona…..Dzinalo asinthe osat Bingu…yaku BT ndiye azatche Bingu.

 15. Why? politics ndi fotobolo yomwe naima ndi ambiri if you don’t have one please ask people to give you one, Osati zofuna ufumu wanu upitilire ….!!!…. Bingu samadziwa ndi sanamenyeko mpira wamapazi zinazi kumafuna anzanu bkoz mudzasochera zano ndiika dzina la munthu okufa and expect our national team to do better hehehehehehede mwapenga eti name ndikupeleka ine pano Lilongwe national team……!! …. Period

 16. By the way…we owe the Chinese for this. It’s not free….our childrens taxes will pay for it over the coming years

 17. Bwanji sadatchule ndata ija dzina lake or university ija kuti Bingu wat wat? Mesa zonse zinali plan yake? And yet farm yo ndi ya personal, stadium siyapersonal anakapeleka dzina lina iiii kaya amalawi poti timangomvera zilizonse

 18. No gvt structure’s to be named after an individual…that’s my take…its the MW citizens who will be paying for that stadium. Straight from their pockets…..HKB named most of the projects in his era in his favour…just to be changed by big headed Muluzi…So if the nx leader will not agree to whatever it will be called now..she / he is going to change it too….stop confusing people…Let parliament decide…how many things does DPP want to be named after Bingu…hey..?

 19. bingu initiative..even if chakwera will be a presdent and ask donors to build a museum and name it chakwera museum tilibe pulobulemu,,,,this was one of bingus master class developments!!whether Chinese or who so ever !!! don’t hate the player!hate the game! Amayi had all the resources, support and everything…but she failed to build even a hospital in her village,she was busy with cows!

 20. Mpia ku Malawi kulibe so wats the use of the stadium!!!?????

 21. China 4n 1year Garantee….! China Torch 2month Garantee…..! Pariament…Yayambapo Ming’alu Kkk Stadium Mot Mudzikhala Anthu …????? Ma China Nkumamanga Chinthu Cholimba Awa? Komanso Team Yake Iti Yongokong’onthedwayi Apa Ndie Taluzatu Simplex Ndiuyo Waswela Nchitokos Bao!Kkkk Kumalaw Mpira Udatha Akadamanga Bar Kut Maplayer Azipikisana Kumwa Ndi Kubanda! Komanso Aliense Olowa Mmboma Akapanga Chinthu Aziika Dzina Lake? Kupenta Komweku Ku Area 30 Akut “peter Waz Here B4 U” Munthu Wophunzila Ameneo “Zamanyazi” Kwakula Nkuzikonda

 22. Mmmmmmmm Mmmmmmm too much boring comments rolling out.
  World class? Mmmmmmm
  Bingu stadium? mmmmmmm
  Thumbs up to Chinese government .laponda la mphawi.

 23. Kodi zomapereka maina awanthu pazinthu zotukula dziko zilipobe,suja munasintha kamuzu central hosp kukhala lilongwe central.tsono chadza ndiyaninso chotinso bingu stadium?lf its a world class structure y not give it a simple,specific,reasonable sportive name than malabishiwo.koma kunyasalande sikudzathekaso,kwenikweni vuto ndichani amalawife.nanu alilongwe city council kuvomera?

 24. Boma liitane Brazil ndi Argentina azasewere tsiku lotsegulira. Saizi yathu ife mpa Civo, Namkhaka ndi Kamuzu stadium. Malo ovemchera alipo, nanga ngalande zilipo zoti tizikafikira ku ma stand zilipo?

 25. guyz amene akuti that stadium imayenera kukhala ndi dzina lina than bingu kwa ine if i may ask who sighned the deal of constructing the stadium? let me also assure you one thing joyce was just following the foot steps of bingu because bingu had already signed in agreement with china just like zomwe peter amazupopa peter zoti wabwereka ndalama from if you dont those things were agreed when joyce banda was in office of president penapake osamangolalata ndipo dzina loti bingu sounds much better

  1. Man bingu anali kape coz amafuna chithu chikakhale Ku nthyoro komwe kuli kwawo pamene amayi aja ndi amene anapanga zithu zotsatila ma paper so

  2. Joyce Banda did nothing for her two years udindo unali ongogwilizira for that moment, no project that joyce sign on behalf of Malawians lets just admitt now

 26. As we ar celebrating the completion of this magnificent bingu stadium, lets not 4get 2observe a minute of silence for those who lost their lives while on duty constructing this stadium i understand 3people died when they fall from the top R I P

 27. That’s cool but do we have the capacity to maintain it? CapeTown is crying because the stadium is useless after World Cup

 28. in my own school of thought I think it would have been better to give the stadium a proper name than a name of a person despite who made the plans of it to be built n who acted on the plan n turn it in reality. tikavula magalas andale kod sitingayitchule stadiumyi kut national stadium or even Lilongwe stadium amene than dzina lamunthu? I think zimenez zingapangitse kut malo adziko lanthu lino I.e lilongwe atchuke world wide than kutchukitsa dzina lamunthu and at the end zidzalowa mitundu from ndale kut stadiumyi ndiya alomwe ndepopewa zonse izi tipange ka referendum kut tipeze dzina labwino la stadium yi. nanga bas chili chose kumalawi kuno chidzikhala mudzina lamunthu? kamuzu stadium,bingu stadium,ethel mutharika maternity wing etc zinthu zadziko zizikhala ndimayina adziko osat mayina a anthu tisiyanitsa bwanj chinthu cha private ndi cha public? maganizo anga amenewo

  1. Maganizo abwino koma abodza… Wake up man, everywhere you go, you will see names of people who made history on magestic structures….they do it in respect

  2. #Moyo maganizo oputsa ndipo xool yako sunapindule nayo ubwelelenso mkalasi uzikatenganso history pa ma subject ako wamva

  3. #Moyo maganizo oputsa ndipo xool yako sunapindule nayo ubwelelenso mkalasi uzikatenganso history pa ma subject ako wamva

  4. I said it at the very beggining kut in my own thoughts,get me right wasn’t representing your thouhgts nop so mind your language ok

  5. Don’t mind these people Douglas, they’re educated blind, history is about things that have gone. we’re in modern society where modern knowledge is applied. malawi is one of folish nations that name almost every public infrastructure in somebody’s name. This is Malawi not the leader. Wake up guys And be Creative don’t driven by history.

  6. chifundo these people think like their shoe sizes not age. how will we differenciate between a private property n national thing? guys wise up now….Malawi kugona

  7. ajobe you talking of roads n they r of no use since u can’t get fame through road. if its so can u jst downlist any.foreign country roads u know. and concerning those given names kamuzu n the likes I already talked of it in my 1st status kut its useless. what’s thah benefit of naming something of national concern a name of a person? at the end president ali yese adzifuna atchule chili chonse dzina lake nde dzimayina dzidzangot mbweee

  8. the stadium deserves the name Bingu. sizachilendo zimenezi anthu wochita zinthu zikuluzikulu timawadziwila ntchito zawo nde polemekeza kulimbikira kwawo njira yake ndi imeneyi …..mudzasiyanitsa bwanji John Tembo ndi Bingu ? this is the best way .

  9. iwe kondwan zachikale zimenezo kod mesa president akakhala pampando ntchito yake ndiyotukula dziko? vuto amalawi timayamikila chinthu chot chimayenela chichitike,mesa munamusankha kut azatukule dziko nanga ndalama amatukulilazo ndiza mnthumba mwake kapena zanu amalawi? good example undipatse k1000 @ the end ndikupatse packet la sugar mkoyenela kut undiyamakile mesa ndi ndalama zako zomwe had it been mnagula ndi ndalama zanga it would v been a different issue altogother. nanga president aliyense akhale pampando akachita chinthu I.e chitukuko ndekut azichitchula dzina lake? nde kudzapezeka kut chili chonse mmalawi muno ndidzina la munthu,sinthan kaganizidwe amalawi anzanga ndi nchito yake president kutukula dziko lino nanga kapena timamusankhilanj? or else dzina likhale laku china sinanga ndamene apanga chinthucho ndi chichili chonse chawo? ganizan mofatsa makosana

 29. Some people are just fools in the making….y being so superstitious a name is just a name…zaminyama zanuzo thats in your head…..n we dont give names to a thing because one built it ….its out of honour that we name a thing after a person….respect thats all. For example South africa built stadiums for world cup and named them after some dudes…madolo amene aja sanamange those stadiums……daah think before talking…..Masauko Chipembere for example….Bingu was a genius….a hero….he left a legacy …whether one agrees o not…..Thats wat we call a self actualised person….it takes guts to get to that state…..not many of us will get there….speaking my mind…no offence if you are offended go and lick your elbow…kkkkk out. Thats y they named it after him…am not a politician but i totally support that name.. BINGU…KAMUZU….CHIPEMBERE…totally venacular language…mother tongue…Chichewa cheni cheni

 30. World class as per Malawi standards sure. This has not being constructed by Malawi government but by China, both money and labour. It is an insult to call a stadium Bingu, for what. Malawians tulo kwambiri. Lets give structures appropriate names not names of thieves, murderers, killers, dictators, swindlers. Even China called their magnificent stadium in Beijing, “Birds Nest Stadium, why don’t we call ours, Lilongwe Arena or National Arena or simply Lilongwe stadium and by so doing selling our capital city whenever an event or match takes place there Lilongwe is mentioned, not Bingu what’s that???

  1. Not world class, seen and been to some fantastic stadiums, these is complete average. Has it got a swimming pool underground?

  2. To say the truth this stadium is not going to help why didn’t you use that money to build a five star hotel along the lake? We have most beaches worth development. Nzeru zayekha. …….. Next time please request the Chinese to help us develop our tourism industry not stadiums

  3. I hope your not a citizen of Malawi, go to hell Bingu will always be remembered for his great achievement, udzasauka ndi ntima oipa

  4. Mbuli ndi iweyo, didn’t you hear that China has written off some debts, anyway since you know more, how much ngongole is for this stadium??

  1. Kkkkkkkk tizipangapo rent eti kkkkk dollar yakeyo tigule chimanga lol

 31. cha China sichilimba, chikayetsetsa ndi 4 years. vuto lakenso muzikalowetsapo a kasinja, pa in dependence day ndinso kuvinirapo senderani ndi mapazi azikang’a. chitimu chake chofoiranso chosewera ngati ZiDakwa Socials. Mxieuuuuuuuiui.

 32. Thanx should go to Dr Joyce Banda poganizira kuti Stadium ikamangidwe ku Capital City ya dziko lino to the Chinese government may the good Lord Bless ur nation and the Leaders

 33. Iwe #Dambe kod munthu amene amapeleka ndalama yokagula sugar nd munthu wot wangopita kukagula sugayo kod mwini wache ndndan? we luk @ the source/founder nt the consumer

 34. JOYCE BANDA IS THE ONLY MALAWIAN PRESIDENT WHO DIDN’T ESTABLISH OR COME UP WITH PROJECTS THAT BENEFITED THE NATION…ALL SHE DID WAZ BUILD A COUPLE OF HOUSES AND DISTRIBUTE A FEW COWS!

 35. Maganizo ochuluka amene Ali pamwambapa ndiopanda nzeru why can you be buisy comparing our beautiful stadium with stadiums of the developed world yet your country is on number one on the list of undeveloped countries tangoyamikani apa,the following deserves my appreciations,Bigu for brilliant idea of bringing international standard stadium to Malawi,Joyce Banda for taking back our stadium to LL ,China for constructing the magnificent stadium saving us from kamuzus death trap

  1. Are we going to maintain it? We are failing to maintain Kamuzu Stadium in Blantyre you we have balls to do it. May be China will be doing it for us

  2. Tell us where Bingu got the Money to build this stadium as per your confused claim? If he did then he was foolish instead of building a hospital or bus station bola

 36. gud development kuchoka kwa a presdent a maso mphenya prof Bingu wamutalika rest in peace wawa zanu mnapanga kale

 37. Koma guys china chirichose ndale, dzina la stadium lalakwa chiyani, ATI bola adakapeleka kut likhale JB pot adamanga ndiyeyo, zabodzatu man zandale zanu zonamazo muzikanamiza ena, ife stadium tasangalala nayo posatengela kut yabwela mulamuliro wandani chifukwa stadium iri ku malawi

 38. Tigulitse stadium yi kwa zungu ndicholinga choti tipeze folex mwina kwacha mkupezako mphavu +fodya ndiekuti mavuto achepa yes Malawi!!!

 39. Padzadza osazisata zampira makape am out check borrin ground,st james park,whitehartlane etc they all r used in premier league some look like civo stadium

 40. kaya chipani cha dpp chinatani kaya chinatan koma chilungamo chake ndichakuti stadium iyi ndi project ya bingu and dzinalo anapeleka yekha mwini wake si wina ayi…….. nsanje ai apa chilingamo ndunenachi…..komaso mpila wa anyamata nde odziwika kuno nde chi dzina cha nzimayi chizitani pa football stadium…..analephela kumanga ndka netball stadiumm bwa?????

 41. But of all namez Bingu??? Hahahahahaha! Pliz kuipatsa minyama2 stadium kumeneko. Nd more over chinthu ichi anayamba kuchimanga anali Joyce Banda, y nt name it Joyce Banda Stadium??? U guyz munangogweramo kti ths project yatha mu nthawi yanu

  1. Ndipo sizandaletu izi. Bingu kaya Joice no problem. Ndemukat kuipatsa munyama y? Kodi Joice wachita zabwino zokhazokha paulamuliro wake? Cashgate mkoyamba ine kuinva ndi amaiwa. Bingu basiii!

  2. Akanaitha CASHGATE STADIUM,cause wopanga plan anaba 91 billion kwacha pomweso omanga anabaso zake zosachepela 3billion kwacha.kwaine kuitcha BINGU kaya JOICE mainawa amangondikumbutsa umbava wandalama za boma.

  3. Asafuna aziphe yekha kuli iyeko ndipo ukalephera ukakolope nyanja ife amalawi tikuti ndi Bingu nation stadium …iwe wa pp uvadi kuwawa

  4. Kunoso ku Ndola stadium yathu ndi same ndi that 1, named after the late Levie Mwanawasa, I see nothing wrong with that name Bingu, all the best Malawi!

  5. #Dambe mimba yamateweyo komanso panyopako ndi #JB wakoyo wamva! Ngati uli dolo upite ukafutepo dzina la Bingu ukaikepo lambuyako nyani iwe mxiii

  6. Koditu amwene eshiiii mukanakhala ena mkanangokhala olo kumangowelengapo ma comment omwe ena akulemba kusiyana ndi ubanditi mwaonetsa apawu

 42. My fellow malawians lets take care of it lets avoid vandalism coz this stadium is ours lets be civilised posamalira chinthu chimenechi.thanx should go to late bingu wa muthalika for his vision to bring this kind of stadium here in malawi.may his soul Rest in Iternal Peace

  1. Its “world class” indeed, akati world class tanthauzo lake mukuidziwa koma? why anthu timangonyoza always even pa zinthu zabwino kapena ur addicted to kunyoza? #SHUPITI

  2. Some stadium used in England cannot be compared to our BINGU NATIONAL STADIUM u dont watch premier league ur simply a stupit idiot magot i hate DPP but dont cheat ppo

  3. Iwe Ku Halale Kwanuko Ilipo Community Ngati Yathu Ukutinyozerayi? LEARN TO BE PATRIOTIC TO YOUR COUNTRY OR “BWELELANI KU HALALE”

 43. waste of resource which team to play there maybe Chipolopolo of Zambia mudzipangitsa rent

  1. simukudziwa chomwe mukukamba akulu…jst bcoz u bought a K500 chinese shoe and it didnt last long, doesn’t giv da authority to judge the durability of chinese funded buildings…kaguleni shoes ya 60 grand made in china…muzadziwa dat chinese products got quality

Comments are closed.