Flames coach Ernest Mtawali has named Simplex Nthala in goals for Malawi national football team with Miracle Gabeya starting at the back Cecafa senior challenge cup encounter with Sudan this afternoon in Bahir Dar, Ethiopia.
The Malawi mentor has also include Civo united defender John Lanjesi into his starting first eleven and will be partnered by Stanley Sanudi, Yamikani Fodya and Miracle Gabeya in defense.
Gerald Phiri junior, Chimango Kaira, Dalitso Sailesi and John CJ Banda will be operating the engine room with Chiukepo Msowoya and Schumacher Kuwali pulling the strings upfront.
Flames starting 11 against Sudan
GOALKEEPER Simplex Nthala
DEFENDERS Yamikan Fodya Stainley Sanudi Miracle Gabeya John Lanjesi
MIDFIELDERS Gerlad Phiri Jnr John Banda Dalitso Sailesi Chimango Kaira
STRIKERS Chiukepo Msowoya Shumaker Kuwali
koma maule i well done gabeya msowoya and dalitso
Bola guys
WELL PLAYED GUYS PROUD OF U
Hopeless Team..
its a goal ………..ooooooooo shumaka kuwali kuwali
koma pagolopo inu..
Nde mmalawiyotu. Ntchito yake ndi yotsutsa basi. Atengera nzeru za leader of opposition.
Maulee!
Malawi kunyoza ndie ndikwao taonani tawina game inja #musiyekunyoza kaoneka #malawi sakutukuka kusangwilizana
Tiyamike bas onse alibwino
Keep it up zigoli zonse kuchokela ku bb nanga mukut bwanji
Amwene tawina basi dont talk to much
Mmmmmm ndakaika mpaka Gabeya nkuyamba?…………. Tiziowa.o de best.
Flames woyyyeeeeee 2-1
flames leading 2-1
All the best
Are you watching guyz
Flames fire kt bUuuuuuuuu!!!!!!!!!!!!!
ilibho
abale mpirau uli pa radio chani,plz tell me
tikuguna ma update apa aaaa
Koma pa golopa eeeeeeh. Ine nkhawa biiii
yoluza imenei gabeya wachani
kodi uyamba nthawi yanji guys
inu a Malawi24 mitu yanu nonse. bwanji mumakonda kupereka nkhani zopanda nthawi? mukut ife tizichita kulota nthawiyo? zandinyasa!
Koma Malawi pamenepa tilimba
panopa game ikutha bwanji,,?
1 zero flames kusalila
mmmmmh man, ndu 2-1 malawi leading first half
Which chanel the game to be watched
O the best mafana
Kodi Flames inakalipobe?????
Supersport ikawonese mbwelelazi hahaha zazii
Kodi akuwonesa pati?
Pa goal lathu pali yede apa.
game tiphula basi ili bwino goooooooo
sudan 2
flames 0
kod mpila tikupitilizabe kkk ths z another part komwe tikutaya ndalama ndizopanda ntchito,,,nde muone 3-0 malawi ku luza tizangoti “komatu imamenya bwino
at the back gabeya and lanjesi poor coordination it will not work.
Zili bwino
kip de 5re burning ma flames whozaaa
Flames imaonetsa kut ilibe mtsogolo,
Free to air wake uti titaone mpirayu, kapena Zuku tv? I see ali yense angoti super sport lol
Gabeya ahhhh mbola
umafna ndn iwe pita kalowe ngat kut umaswerapo mpira
akufuna mwanayu apeze experience ali ndi tsogolo lowala
inu bola Lucky Malata n Zoya nanga amangodya thabwa ku bb
Chipuwa anayambana naye chiani coach?
ngati ndi wabhoo nde bolaso simplex emweyo.
Palibe kuwina lero.ife tinazolowera kuluza basi.bola kungothetsa national team yi basi
Flames oyeeeee!
Zofunika kumaonera utadya kale izi,otherwise utha kugona ndi njala
Sindingataye nthawi yanga kufunira zabwino abwampiniwa angandikhumudwise. Palibe chomwe tingachiteko kumeneko. Ngakhale Jibout wakonzeka kuti abweze chipongwe takhala tikumuchita chija.
Hhaaha flames siimatha mpira siingawine ndipo siizawina….zatengeni coach wa ku england muzimulipra 15 million azizacoacha
Zabwino zonse Malawi ya moto
Go flames go
Bola ayambe kulimbikira tisanachinyitse
Bola Ili Pa Go Man
Bola Osakatichitisa Manyaxi Ndie Pot Mudaxolowela Kuluxa
Bola Osakatichitisa Manyaxi Ndie Pot Mudaxolowela Kuluxa
Sindingasekelele Zimenezo Paflames Inachoka Pano Ndi Bullets Imeneyo
Goalkeeper sanaganize bwino
ZABWINO ZONSE MA FLAMES TIWINA
Mpira omangosewerera dzina muzienda ma bomamu muli anyamata odziwa mpira koma mumangofuna uyo watchuka
Ndi national team iyi si select, nde mukati mmaboma muli osewera mukutanthauzanji? Asiye amma club aketenge ammaboma? Kkkkk eish
Aziwayesa ku maderakunso kuli ma clubtu and ma player ambiri amakhala ma noma ndi bb nde iwe ukunena ma club ake ati
Kaya kumalawi mpira suzasitha anthu ake ngati iweyo
Zabwino zonse flames.
flames yoluza iyi
We go we go,,,flames winning !!!
Kaluzeni
Malawi Amoto
Ilengeza radio yanj? Tiuzen plz
I DONT LIKE THIS FLAMES STAFF kumangoluza
Jah bless
supersport chani plz? ???
ss9
Thanks bro
Oky
Wat tym??
When is the kick of?
goal keeeper yo aaaaaaaaaa
thax kuti flames tiluza
oh! very bad
Ana okanika
makion 7
a malawi mwagula kale ma panado??
Kunena mopanda mantha ndakwera Sudan
supersport 9 on Dstv & Gotv
all de best ngakhalebe imangotikhumudwitsa.
O D BST FLAMES!
Ok
Ili bho team
Shapaaaaa Nyasaland
My malawi my flames go and blek th recod
All the best
Ma xoba amenewo ife takwera inayo
CHI TEAM CHODWALITSA ICHI
Guys kodi aionetsa pa channel yanji mmalawi muno?
pa nyasa tv
Kkkkk ok
y gabeya nt sankhani?
all the best
All the best flames
Mafana a juju tsopano! Hope they win. Painkiller wanga ndagula kale, ana opweteketsa mutu awa
kkkkkkk mpaka kuguliratu painkiller
National team yathu siyachibwana pa nkhani zokhumudwitsa. But we wish them well owez
nthawi yanji
9C GAME…..
all the best FLAMES
Tipephe wamwambamwamba ayikepo zanja lake, all de best
Flames woyeeee
Flamez xitimu!!
Atibulidwa amenewo
Best wotan kwa akaligondowo? angoononga ndalama .zaziii
All the best the flames