Francis Mlimbika and Ishmael Thindwa will miss yet another vital match in Malawi’s Standard Bank cup final this coming Sunday despite recovering from their long-term injuries.
Nomads team manager Steve Madeira confirmed that the duo has recovered but they are not ready for selection this week in the Standard Bank Cup final.
“Thindwa and Mlimbika have now started training with the entire Nomads team but they will miss this year’s Standard Bank final as they are not yet ready for selection,” said Madeira.
Midfielder Raffiq Mussa will also miss the game against Civo as he is still nursing a knee injury.
Meanwhile, Wanderers coach Elia Kananji has today named a 20 man squad that will represent the Blantyre based giants in the final.
The Nomads full squad travelling to Lilongwe: Goalkeepers Richard Chipuwa Peter Munthali Defenders Bongani Kaipa Tedson Boston Kabango Kondwani Lufeyo Enock Likoswe Peter Nselema Stanley Sanudi Midfielders Isaack Kaliati Mike Kaziputa Jacob Ngwira Kondwani Kumwenda Alfred manyozo Jnr Ibrahim Sadik Sparrow msowoya Strikers Jabulani Linje Victor Nyirenda Muhamad Silumba Luka Bruno Milanzi
This year’s Standard Bank Cup winner will walk away with cash amounting to K10 million.
*Additional reporting by Chikondi Magalasi.
Zabwino zonse Noma….kuti kweeeeeee
Palibenso zoti nthawi izakwana apa,,,,, Osanamizira nthawi ,, iyaah ,,,
A judge aja angoti chija chija muona sunday noma ndi deal ukuziwa kale
NEBA ADAMENYEDWA KU CIVO PANO AKUTI AGANYULA YOMWEYO CIVO PALIZELU PAMENEPO NEBA UZIFUSE
Neba akuphwanya mutu kkkkkk
Zithe ka
kkkkk iwe matebule usandipatse phwete neba zake zada akubweza kaye ngongole
pa 1 ife tiwonkhetsa zikho neba awonkhetsa mapoints zako izo
the cup specialist frm rale luban road mafana osamba weekend tionkhesa zikho pomwe wina uli pazilu kudalila kukatuluka mma group stage ku caf kakakakakaka koma manoma amatha
BB ndi more
Chifukwa Chake Ndife Nyere No Plural Zimatheka Thindwa Ana Mlimbika Get Wel Soon,ana Achepa Neba Ganyu Amapha Take Care
All the best my lovly team Noma!!
noma ndi dhilu!!
woxachuluka zone amat sindidaziwone adachezela kuziwona wina akaziwona kumeneko
Ine ndi apa banja langa tikufunirani zabwino zonse.
noma ili ngt mlimi wazelu olima kawili pa sexon timinda tochepa km ku user sasakawa kukolola zochuluka mlimi opusa (naba) kulima chiminda chachikulu kuzala chimanga 3 3 zokolola zochepa zinganizileko neba
ndiye sumadziwatu,U love de team ndimene imasewerera not kuwina zikho!
Nelson Kangunje wakukonzelani mphatso pitani pa Civo akakupatseni,Koma musiye kulankhula kwambiri coz mpira ndipaground 90min+ kkkkkkkkk
No panic, nyerere ndi deal. Nomads for the cup!
Shaaah!! mwati awasazamenyanawo
Ngati STD bank sitinatengepo ndiye kut nthawi yathu siinakwane coz mpira ndiye timasewera mumadziwanso koma kut panthawi ino ma cup sanapatsidwe kwaife mmalo mwake tili ndi mwayi wotenga ma league xo osamatha mau
Mumenyedwa kaa anoma inu
Its Not A Blow, Asanamizire Apa Kkk
Kkkkkkkkkkkkkkkkk ,,,,,,,, Kodi Matebule, ukunena Bibi Bullets Unbeaten Futball Club ?
sulumba sulumba sulumba ndanutchula kangati ndiye zigoli kwa zero
sulumba sulumba sulumba
Eeeeeeeeh alipo! Koma timawakonda! Ndipo inu simumagona tulo chifukwa cha iwo! Kaya simukuvomereza zilibe ntchito komano ndi Team # 1 ku Malawi kuno! Inu otenga zikho inu takumverani chisoni! Mukhala pa #9!
Civo bullets fc kozeka pakut ana ofewa aja afikaso
Manoma palibeso opikisana nawo, standard bank cup yapitaso ku lali lubani, tsikuli manoma akangopangila umboni kuti iwo ndi madolo pachikopa osati enawa akukuwakuwa zaziiiiii! Ziwiri simasewera ambuye ndiwankulu ma no ma wo ye e e e e!
Manoma palibeso opikisana nawo, standard bank cup yapitaso ku lali lubani, tsikuli manoma akangopangila umboni kuti uwo ndi madolo pachikopa osati enawa akukuwakuwa. Ziwiri simasewera ambuye ndiwankulu ma no ma wo ye e e e e!
WINA AFUNE OR ASAFUNE B4WARD NOMA NYERERE IKUTENGASO CUP
ati ndi ma champions, ati aluza kamodzi, ati last year amenya CAF, ati amatha mpira, hehehehedeee musandisekese usatengako cup imodzi yokha bwanji ngatimuli madolo, sindikunenatu bulletsless the peopleless teamless apa.
Choka usalimbani nd maule iwe nd soka limenelo,mauleeeee! woyeeee ife ndwamkaka always
11 month contruct = k15 million ndi wina akuti 2 month contruct = k10 million ungasakhe iti? Kkkkk neba kugona pa town uzichenjela kape kikikiki noma ndiyajugatuuu usamale
ati ndi team yaikulu koma formula yotengera standard bank sakuiziwa kkkkkkkkkkkkkkkk
Zaziii
wayamba liti kusapota iwe nyani
ine Mahule sry ndimafuna ndinene kuti maule, bwanji sima’mafuna kuvomereza kuti ndiinu olephera,
Kkkkkkkkkkkkkk ,,,,, Kodi guys eti ndi zoona zoti ena ake sanayambe atengapo Standard Bank Mmalawi muno ??? Sindiwatchula akudzidziwa okha ,,,, Kkkkkkkkkkkkkkk
zoona zake m’bale
komatu a civo musatichitise manyaxi tili pambuyo panu
Ena kusewela kaya osasewela koma Noma yakozeka ndipo any mistake civo ilira chokweza ,All the best Nomards
Osewera A BB Apempha Kut gemu Yawo Imenyedwe Loweluka Mmalo Mwa Lamulungu Kut Adzawonere Nawo Mafinals Amatimu Akuluakulu. Nyerere Woyee
nyelele yomweyoooooo kkkkkkk
Sitikugwedezeka
neba unathambikakale noma woyee
Civo ntima mmalo ife tili pambuyo panu
Timufunila zabwino fra komanso thindwa kuphatikiza B4 manoma pa chiweru tikutenga cup
We have been doing well in STD bank cup games in the absence of them why not making it to champiohship? The dual will join the squad in the other coming games
Noma kamakawa.
KODI MPIRAWU UKHALA LIVE PA MBCTV? NOMA WOYEEE
nyerere woyee!! i lke that team
Worry not Nomads Ayaya will assist u guys
noma 4lyf
INE SIWANOMA AYI KOMA CHILUNGAMO NDICHAKUTI NOMA ILIBWINO MOTI KUSAPEZEKA ANYAMATAWA SIZODETSA NKHAWA KOMA AKADAKHALA VENDAYU MUKADAVA ALI GAME IIME KAYE ANYAMATA AMBIRI SALIBWINO.KKKK
Ttengaxo cikho cina apa Manoma Woyeeeeeeeeeeeee.
Noma woyeeeeeeeee! Ena alemphera kusewere sunday kamba ka vinyanga vawo vakana kkkkkkkk
kakakakakaka tel dem
Manoma woyeeeeeh, aganyu alira, game timphura basi
Zanu zimenezo.
mlimbika, thindwa . nditichani timeneti ?aaaaaaa ma player opimangati amenewa. musova sunday lino. ifewamkaka ndiye tayamba kumwela2. palibe zayaya ulendo uno. kkkkkkkk
man inu si anoma mwamva ndiwe waganyu zikuonekela sandelo ndi ganyu yakoyo
wamwai ndi wamwai ngakhale ata tyoka mwendo timwambe mkk nyerele mtima mmalo zolembalemba .nyerele oyeeeeeeee.
Tichita bwino mpira umenewu ngakhale maprayers ena anavulala .B B Ikanakhala kt imadziwa mpira bwenzi zikho zonse itatenga koma yalephera ngakhele lowelukali silver izapheratu B B.
Palibe chotilepheretsa kuiphula manoma ……aganyu mulila kuti mtooooooo
nyerereeeeeereeeeee at it again.
kwaife amanoma sinkhani yabwino
They r vital but we cant force matters Jah RASTAFARI Will guide us bravo NOMA!!
Civo will carry aday
Mwayi Wa Civo Umenewo Kkkkkk
Nyerere nyerere basi cup waku Lali lubani
All the best neba kumene mukupitako.
That’s good mwano muleke
kkkk aganyu akupanga like koma ife sitikudanda coz noma yafika kumafinals yopanda anyamata amenewa mwinanso ndibwino coz akanadzasokonedza gear yemwe anyamatawa akhoma nomatu sili ngati bullets yomangomenyetsa maplayer amodzimodzi ayi, inalemba maplayers okwana 28
Kodi Bullets simagona nayo tulo eti?
tikalephele kugona tulo ndi timu ya bullets ngati imatha mpira ife sitimagona tulo ndimatimu odziwa mpira basi ngati anzthu a Civo .tikati mmalawi muno muli matimu odziwa mpira Ndi WANDERERS ndi CIVO ena onse ndi manyaka
Nanga kuitchula bullets yakuputa chani??? Koma abale, mmalo mongopanga comment mukulimbana ndi bullets?? Or itaseweletsa ma player omweomweo vuto ndi chani??? Pangani comment zanu basi.. Leave bullets alone
Nanga kuitchula bullets yakuputa chani??? Koma abale, mmalo mongopanga comment mukulimbana ndi bullets?? Or itaseweletsa ma player omweomweo vuto ndi chani??? Pangani comment zanu basi.. Leave bullets alone
ife tikulimbana ndi civo not bullets ,tikalimbane ndi bullets ngati imatha ife maplan athu ali pa civo basi tizikalimbana ndi timu yomwe imadana ndi chikho cha standard bank e
hahaha inu otha mpira bwanji muli pa position 9 mu TNM??ikakusiyeni Silver yoti inali pansi kwambiri eeeeeeeeeee vomerezani kuti simuzitsata
ife sitimalimbana ndi chokho chomenyedwa zaka ziwiri ndalama zakenso zonyenyeka chikho choondetsa ngati chimenechi,kumaiwerenga 3games 10 mita pathumba moyo mkumayenda bho sizaka ziwiri 9mita hahaha aluya munapanga bwanji kumaiwerenga kupandatu mzeru simulemera pamalawi pano kkk expenditure kuposa ndalama za league.
Neba tikunthamangisa ku Bt kuno coz sitifuna matimu ogona ngati bullets contruct ya 11 month kupeza k15 mil wina akuti 2 month k10 mil iwe mutu zeee!? Kkkkkk neba kumachenjera pa town kikiki
masiku ano mpira ndi mkalasi mboba kumawerenga kaye olo noma itatsilidzira pa no.13 tidzavotera mkutenganso cup inu osavoteredwa inu kumangothothoka kuma round 32 ife focus yathu ndima kapu osati chikho chimodzi mpaka zaka ndalama zake kudzalandira kumapeto a season ngati mlimi wafodya kkk tnm ikusaukitsa ikusiyani mulibe kanthu muzangonyamula chikho chokhacho ndalama zitathera kungongole
Neba neba changamuka pano ndipa town ziyiwelega kaye usauka ukalimbikila TNM mulibemo ndalama ufela kutchuka kkkkkkkk
u wl regreat to say these words, Maule for ever
ndipanga regreat bwanji tikukamenya finals? Inu mungobwera muzaonere mpiqa wa mphongo mmene timamenyera mu standard bank
Ndakuonadi simulimbana ndi #chokho
muyisova
Ndiye is it a blow?? We have never used them in the padt games as well and came out victorious
Any sensible coach would not feature them in the first eleven. Its a cup final and that will be a gamble.
Any sensible coach would not feature them in the first eleven. Its a cup final and that will be a gamble.
no football in Malawi