Mlimbika, Thindwa to miss second Nomads final


nomads

Francis Mlimbika and Ishmael Thindwa will miss yet another vital match in Malawi’s Standard Bank cup final this coming Sunday despite recovering from their long-term injuries.

Nomads team manager Steve Madeira confirmed that the duo has recovered but they are not ready for selection this week in the Standard Bank Cup final.

“Thindwa and Mlimbika have now started training with the entire Nomads team but they will miss this year’s Standard Bank final as they are not yet ready for selection,” said Madeira.

Midfielder Raffiq Mussa will also miss the game against Civo as he is still nursing a knee injury.

nomads
Nomads hit with injury concerns.

Meanwhile, Wanderers coach Elia Kananji has today named a 20 man squad that will represent the Blantyre based giants in the final.

The Nomads full squad travelling to Lilongwe: Goalkeepers Richard Chipuwa Peter Munthali Defenders Bongani Kaipa Tedson Boston Kabango Kondwani Lufeyo Enock Likoswe Peter Nselema Stanley Sanudi Midfielders Isaack Kaliati Mike Kaziputa Jacob Ngwira Kondwani Kumwenda Alfred manyozo Jnr Ibrahim Sadik Sparrow msowoya Strikers Jabulani Linje Victor Nyirenda Muhamad Silumba Luka Bruno Milanzi

This year’s Standard Bank Cup winner will walk away with cash amounting to K10 million.

*Additional reporting by Chikondi Magalasi.

92 thoughts on “Mlimbika, Thindwa to miss second Nomads final

 1. the cup specialist frm rale luban road mafana osamba weekend tionkhesa zikho pomwe wina uli pazilu kudalila kukatuluka mma group stage ku caf kakakakakaka koma manoma amatha

 2. Chifukwa Chake Ndife Nyere No Plural Zimatheka Thindwa Ana Mlimbika Get Wel Soon,ana Achepa Neba Ganyu Amapha Take Care

 3. noma ili ngt mlimi wazelu olima kawili pa sexon timinda tochepa km ku user sasakawa kukolola zochuluka mlimi opusa (naba) kulima chiminda chachikulu kuzala chimanga 3 3 zokolola zochepa zinganizileko neba

 4. Nelson Kangunje wakukonzelani mphatso pitani pa Civo akakupatseni,Koma musiye kulankhula kwambiri coz mpira ndipaground 90min+ kkkkkkkkk

 5. Ngati STD bank sitinatengepo ndiye kut nthawi yathu siinakwane coz mpira ndiye timasewera mumadziwanso koma kut panthawi ino ma cup sanapatsidwe kwaife mmalo mwake tili ndi mwayi wotenga ma league xo osamatha mau

 6. Eeeeeeeeh alipo! Koma timawakonda! Ndipo inu simumagona tulo chifukwa cha iwo! Kaya simukuvomereza zilibe ntchito komano ndi Team # 1 ku Malawi kuno! Inu otenga zikho inu takumverani chisoni! Mukhala pa #9!

 7. Manoma palibeso opikisana nawo, standard bank cup yapitaso ku lali lubani, tsikuli manoma akangopangila umboni kuti iwo ndi madolo pachikopa osati enawa akukuwakuwa zaziiiiii! Ziwiri simasewera ambuye ndiwankulu ma no ma wo ye e e e e!

 8. Manoma palibeso opikisana nawo, standard bank cup yapitaso ku lali lubani, tsikuli manoma akangopangila umboni kuti uwo ndi madolo pachikopa osati enawa akukuwakuwa. Ziwiri simasewera ambuye ndiwankulu ma no ma wo ye e e e e!

 9. ati ndi ma champions, ati aluza kamodzi, ati last year amenya CAF, ati amatha mpira, hehehehedeee musandisekese usatengako cup imodzi yokha bwanji ngatimuli madolo, sindikunenatu bulletsless the peopleless teamless apa.

  1. 11 month contruct = k15 million ndi wina akuti 2 month contruct = k10 million ungasakhe iti? Kkkkk neba kugona pa town uzichenjela kape kikikiki noma ndiyajugatuuu usamale

 10. Kkkkkkkkkkkkkk ,,,,, Kodi guys eti ndi zoona zoti ena ake sanayambe atengapo Standard Bank Mmalawi muno ??? Sindiwatchula akudzidziwa okha ,,,, Kkkkkkkkkkkkkkk

 11. Osewera A BB Apempha Kut gemu Yawo Imenyedwe Loweluka Mmalo Mwa Lamulungu Kut Adzawonere Nawo Mafinals Amatimu Akuluakulu. Nyerere Woyee

 12. We have been doing well in STD bank cup games in the absence of them why not making it to champiohship? The dual will join the squad in the other coming games

 13. INE SIWANOMA AYI KOMA CHILUNGAMO NDICHAKUTI NOMA ILIBWINO MOTI KUSAPEZEKA ANYAMATAWA SIZODETSA NKHAWA KOMA AKADAKHALA VENDAYU MUKADAVA ALI GAME IIME KAYE ANYAMATA AMBIRI SALIBWINO.KKKK

 14. mlimbika, thindwa . nditichani timeneti ?aaaaaaa ma player opimangati amenewa. musova sunday lino. ifewamkaka ndiye tayamba kumwela2. palibe zayaya ulendo uno. kkkkkkkk

 15. Tichita bwino mpira umenewu ngakhale maprayers ena anavulala .B B Ikanakhala kt imadziwa mpira bwenzi zikho zonse itatenga koma yalephera ngakhele lowelukali silver izapheratu B B.

 16. kkkk aganyu akupanga like koma ife sitikudanda coz noma yafika kumafinals yopanda anyamata amenewa mwinanso ndibwino coz akanadzasokonedza gear yemwe anyamatawa akhoma nomatu sili ngati bullets yomangomenyetsa maplayer amodzimodzi ayi, inalemba maplayers okwana 28

  1. tikalephele kugona tulo ndi timu ya bullets ngati imatha mpira ife sitimagona tulo ndimatimu odziwa mpira basi ngati anzthu a Civo .tikati mmalawi muno muli matimu odziwa mpira Ndi WANDERERS ndi CIVO ena onse ndi manyaka

  2. Nanga kuitchula bullets yakuputa chani??? Koma abale, mmalo mongopanga comment mukulimbana ndi bullets?? Or itaseweletsa ma player omweomweo vuto ndi chani??? Pangani comment zanu basi.. Leave bullets alone

  3. Nanga kuitchula bullets yakuputa chani??? Koma abale, mmalo mongopanga comment mukulimbana ndi bullets?? Or itaseweletsa ma player omweomweo vuto ndi chani??? Pangani comment zanu basi.. Leave bullets alone

  4. ife tikulimbana ndi civo not bullets ,tikalimbane ndi bullets ngati imatha ife maplan athu ali pa civo basi tizikalimbana ndi timu yomwe imadana ndi chikho cha standard bank e

  5. ife sitimalimbana ndi chokho chomenyedwa zaka ziwiri ndalama zakenso zonyenyeka chikho choondetsa ngati chimenechi,kumaiwerenga 3games 10 mita pathumba moyo mkumayenda bho sizaka ziwiri 9mita hahaha aluya munapanga bwanji kumaiwerenga kupandatu mzeru simulemera pamalawi pano kkk expenditure kuposa ndalama za league.

  6. Neba tikunthamangisa ku Bt kuno coz sitifuna matimu ogona ngati bullets contruct ya 11 month kupeza k15 mil wina akuti 2 month k10 mil iwe mutu zeee!? Kkkkkk neba kumachenjera pa town kikiki

  7. masiku ano mpira ndi mkalasi mboba kumawerenga kaye olo noma itatsilidzira pa no.13 tidzavotera mkutenganso cup inu osavoteredwa inu kumangothothoka kuma round 32 ife focus yathu ndima kapu osati chikho chimodzi mpaka zaka ndalama zake kudzalandira kumapeto a season ngati mlimi wafodya kkk tnm ikusaukitsa ikusiyani mulibe kanthu muzangonyamula chikho chokhacho ndalama zitathera kungongole

  8. ndipanga regreat bwanji tikukamenya finals? Inu mungobwera muzaonere mpiqa wa mphongo mmene timamenyera mu standard bank

Comments are closed.