Chipatala cha mpingo wakatolika cha Pirimiti achitseka
Chipatala cha mpingo wakatolika cha Pirimiti mu Boma la Zomba achitseka potsatira kusamvetsetsana komwe kulipo pakati pa ogwira ntchito ndi akuluakulu atatu woona ntchito zapachipatalachi. Malinga ndichikalata chomwe Malawi24 yawona ndipo chasayinidwa ndi wapampando wa… ...