“Chakwera amange chipatala china nkuchitchula dzinalo” – atelo a Malawi ena
Anthu ena mdziko muno awonetsa kusagwirizana ndi zomwe mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera achita posintha dzina la chipatala cha Phalombe kukhala John Chilembwe ndipo ambiri alangiza mtsogoleriyu kuti mwana omupeza sumamusintha dzina, umangolimbikira,… ...