Kalindo ampeza osalakwa
Omenyera ufulu Bon Kalindo, wayamba kuchotsera milandu yomwe akuzengedwa pomwe khothi ku Zomba lalamura kuti nkuluyu ndi mfulu pa mlandu oyambitsa zipolowe omwe amazengedwa m’bomalo. A Kalindo omweso amatchuka ndi dzina lawo la pazisudzo la… ...