Boma ndi Lomweli – Usi
Atakhala kwa kanthawi osatulutsa mawu oyikira kumbuyo utsogoleri omwe ulipowu mwachindunji komanso tsogolo la chomwe akufuna, wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino a Michael Usi lero abwera poyera kuwatsimikizira anthu za ubwino waboma ndi utsogoleri… ...