Kwabuka kusamvana ku NONM pa zionetsero
Kwabuka kusamvana pakati pa anamwino ndi azamba pomwe mamembala a bungwe la National Organization of Nurses and Midwives of Malawi (NONM) akonza zokatseka ofesi ya bungweli Lachisanu ku Lilongwe ndipo akuloza chala atsogoleri a bungweli… ...