ESCOM yakana kuti ikulumikiza magetsi mwaulere
Pamene anthu ena chimwemwe chinadzadza tsaya kuti nyumba zawo zilumikizidwa magetsi mwaulere, kampani yogulitsa mphamvu za magetsi ya Electricity Supply Corporation of Malawi (ESCOM) yatsutsa malipoti oti yayamba kulumikiza magetsi mwaulere kwa aMalawi. Kumayambiliro kwa… ...