Makhansala ku Zomba akufuna kuchotsa khansala nzawo pa udindo
Makhansala ena amu Mzinda wa Zomba komanso Phungu wamu mzindawu Bester Awali adakonza upo wofuna kuchotsa Khansala Rams Kajosolo pa udindo wa wapampando wa Komiti ya ntchito zachitukuko. Kudzela muchikalata chawo chomwe adalemba ndipo chidasayinidiwa… ...