Zambia yatenga mbali ina ya Malawi
A Malawi ena omwe amakhala mmalire mwadziko lino ndi Zambia apezeka ali m’dziko la Zambia kutsatira kudulaso malire pakati pa maiko awiriwa. Izi zikutsatira kulengeza komwe boma la Malawi lapanga kunena kuti mbali ina yomwe… ...