Be Forward Wanderers FC have announced they are withdrawing from the CAF champions league.
Malawi24 understands that this is due to what is being described by Nomads officials as worrisome financial constraints.
The TNM Super League champions were slated to head to the Democratic Republic of Congo to face AS Vita.
Initial reports had suggested that the Nomads also had hiccups to register players let alone to gather funds that they would have to spend to take part in the continental showpiece.
They had set up accounts where supporters were making contributions but the funds collected are reported to be lower against the estimated expenditure.
The Nomads were along with Masters Security FC representing Malawi in continental club competitions.
In cases of this nature teams get fined but as it is CAF is yet to make a statement.
Mmadana ndi Noma chifukwa chani inu a Malawi 24? A simple investigative journalism you can’t do. You suck. Not worth to be an online publication
Mmmmmm zataniso Neba kikikiki
Apa ndiye atipangitsa manyaz….bola akanangokhala osalembetsa nawo kungotitaitsa nthawi ndikukonzekera masewera a paubale othandizira kupeza chuma ..
Eeeee sory very sad development next time
Aopakukadzola zigoli kkk
Mukusokoneza anthu tikamenya
Withdrawing fc kkkkkkk
Kkkkkkkkk zikatelo siwakuchipiku basi?
Impossible
Masapota a Noma mumazipopa eeee ife olemera iiiii inu mulibe kanthuuu or ku akaunti kwanu matama thooooooo Mulungu wafuna kuti musiye Matama kularata a Bullets osauka inu iiiiiiiiii lero ndiizi
Chibwana Noma
Hahahhhahahaha
Nooooo!!!! Beforward Wanderers,dont Start What You Can’t Finish! Mwashosha! Kudambwe…Tiye Nazoni…
Munaputa Dala Nkhondo Ya Azibambo…
What About Masters Fc?!
Hahahaaaaaaaaaaaaa…………..!!!!!!!
Basi Malawi yonse nganganga pambuyo pa Masters Security… heheheeeeeeeeeeeeeeee……….!!!!!!!
osamasaka chomwe simungachiphe//
Zinthu zina osamayetsa ngati simungazithe//
heheeeeeee koma I cant stop laughing ndiiiiiiiithu, mesa munkati club yandalama inu? mesa mumati ulendowu mudziyenda pa ndege not za Bullets zija zoti popita ku Comoros Ireland kukwera bus? hahahaaaaaaaaaaaa ulendo wa ku CAF wakanika dikilani chibhalo basi.
Ndimadabwatu ine, ka Team kopanga draw ndi Mangochi Select, chigolinso chochita kubweza pa penalty, nkumati ulendo wa ku CAF mukalimba?
Nkhani sindalama zokha zavuta ayi, komanso manthaaaaa kkkkkkkkkkkkkkk kuopa kubesa hohohooooo
ZIMACHITIKA GUYZ,,,,,NDALAMA ZILIBE MWINI…….
FAM yakana pempho la Wanderers kuti awauze a CAF zoti sakwanitsa kupitiliza ndi lingaliro lawo losewera CAF
FAM yati wanderers ione yokha zochita cz inakana kupereka 15 mita yomwe FAM imayenera kulipira zoterezi zikachitika
Tsono iwo ati izi sizikuwakhudza awauze okha a CAF
More to come
Ahaa neba ndani wakuloza kodi ndiuze ine
Ndiye muwauze abeforwad asiye kukuthandizani apa nchimodzimodzi ndi karonga utd yopanda sponsor
That’s Not Interesting.
Kkkkkkkkkk neba akukamenya caf fc,lero neba withdraw caf fc kkkkkkkk
Nomads fans eeeee mumatisokosa, tisokosenibe shame.
Matama achule odumpha palibe zenje ndiamenewo
Mutu Sukugwira Neba.
Sorry Neba this is so sad!!!!!!
Did they join without planning and consulting the sponsor? Malawi, it appears, has adequate supply of lunacy!!!
neba neba mutu sukugwira #singing
I am not suprised at all,,ma preparations a caf ungamakamenye nd mangoch medicals
mitondoli iyi
Sad news pavutatu apaa
Phuma ndi nyere sizimagwirizana. Munanyanya kuberekedwa ndi kupeza ma player mwachinyengo. Hehede wasows2 okutolani apa. Muisovenge.
KKKKKKKKK basi mwaliza Ana.
Team Yoputsa Iyi Zedi Mwatichititsa Manyazi Akanganya Inu
Bwannoni fc wandichitixa manyazi
Osamasekana inu mwanotu umenewo kkkkk
Kkkk
Team yoyalusa iyi how can you start preparing for CAF without sound financial?.Wait a minute! what are you going to to do with funds that we’ll wishers deposited in your account?.
Nanga a BULLETS mutithandiza bwanji coz we’ve started training earlier than we planned?. Neba you must be serious this withdrawing will put you in much trouble fwethu.
Point of correction, Be Backward Wanderers FC
kkkkkkkk
Munkayesa zocheza
kumangoziputa mulibe mphamvu?
Ana awa sanafike size yokamenya caf ngati akukanika kumenga ana kuno kwawo,bola kuzisiya
Total Disgrace to the nation dikilani zima fyn basi caf siphada za ana amuna izii
Maskin yamungu
Kkkkkkkkkkkkk matama neba kulowa CAF simasewera osangoti lisani pambali ndikukamenya CAF
So sad news