Inatchuka nkhani yoti Wapolisi wa zachitetezo ananjatwa kamba kopita ku chimbudzi ku nyumba ya nduna zoona zophunzitsa anthu.
Malinga ndi malipoti amene amagawidwa mma Facebook ndi WhatsApp, ati Wapolisi amene amapeleka chitetezo ku nyumba ya Mayi Grace Obama Chiumia anamva m’mimba kutentha. Ati atamva m’mimba kutentha, anaganiza zokapambuka osadziwitsa abwana ake a Obama.
Ati abwanawo atabwela ndi kupeza kuti iye akutuluka ku chimbudzi chawo, basi analamula kuti wapolisiyo amangidwe.
Koma polankhulapo pa nkhaniyi, Apolisi ati ndi zabodza zoti wapolisi anamangidwa ku nyumba ya a nduna anamangidwa chifukwa chopita ku chimbudzi.
Mneneri wa Apolisi chigawo chapakati a Nolletie Chimala anauza Malawi24 kuti ndi zoona zoti wapolisi ananjatidwa kunyumba ya a Chiumia.
“Koma sichinali chifukwa choti anapita ku chimbudzi,” anatelo a Chimala.
Iwo ati wapolisiyu amene anatumidwa kuti akapeleke chitetezo kunyumba kwa a Chiumia, analedzera ali pa ntchito. Apolisi atazindikila izi anakamunjata ndi kutumiza wapolisi wina.
Amamufuna wakhalitsa osakwatidwa komaso akuluakulu a police ndinu zitsiru ndinkhani yomangira munthu imeneyo asanyere
Be professional Malawi24,,KUYAKA nde chani?
KUYAKA?
Malawi 24 siiizamva wapolice amayaka is that chichewa cholondola??
Koma a Malawi tuwente folo muzilembak zazeru nthaw zina mwava timve zit?
how can we believe its not just story-twisting, the first-hand info was the gate was unmanned coz the gateman went to answer the call of nature at the minister’s toilet, anow this time he was drunk… #God_is_watching
mwina mowawo anapatsidwa kuchokera kunyumba kwa bwanaakewo, akudziwa ndani
ali ndi umboni woti anamwa mowa ndani, mwina anali malungo
LEMBANI NKHANI ZENIZENI OSATI LERO IZI MAWA IZO. Don’t confuse us
Zachoka pokanyela paja kufika poyaka kkkkkkkkkk
Ulonda ndi sober zizimagwilizana umafuna uziionela patali nanga kunabedwa ngati? aaa ukafuse mulonda wa G4s akuuza kuti amangoyendela bola guit and nomal stuasion basi
Moti uyaka aunenako , ndiye kuti aunena zoledzela? Zinazi zimalankhulidwa koma apapa ndimaitenga nkhaniyi ngati Kuala Kwa moto
Chimbudzi chabwanawo amalowamo wokha basi? Nanga alonda alibe chawo?
Aaaaah it doesn’t make sense here,nzanu wayaka instead of kuitana a fire engine kuti adzamuzimitse mukumumanganso?
Muzilemba zomveka
kape iweti!!
So the story has changed
ena akuti adayaka,pomwe ena akuti amakanya,ena akuti amakayankha foni kuchimbudzi”tigwire ziti?
Kodi Kunyela Ndi Mulanduso? Kunya Saletsa Koma Manyeledwe.Inunso A Malawi Twete Foru Muzilemba Zinthu Zomveka Osalemba Nga Ma Sekeretare A Banki Nkhonde…Iyaaa!
Simudziwa kulembanso kodi? Reporter amene walemba izi abwelere ku school
Koma nduna imemeyo eee kukanyela phala kinjatidwa umenewo ndye utsamunda moyo wa nkhanza
Choncho Nkumayembekezera Kudzapambananso?Ndakaika Poti A Malawi Ndife Opepera
Ankhanza mayiwa munthu anamwela zake uyu anakupemphani ndalama zokamwela kapena mayi inu?
Kodi inu a Malawi 24 mukati kuyaka mukuthandaudza chiani? Mudzitiudza chichewa cholondola not kuyaka. Mukanati adamwa mowa ndipo adalezera
hahahahaha crazy country with inconsistent and stupid leaders, really mpaka arresting him? Thats a professional issue the guy was negligent he deserves some disciplinary measures…..if this is the case then peter deserves life sentence he has been sleeping on duty all along
Eish!!!! You have issue bro whts wrong with peter here wake up.
Its all about disciplinary charge not mpaka arresting him. That’s giving stupid directives
Tsono timve ziti pamenepa?
Nd dhilu kd ukamalondra ku nyumba kwa nduna uziopa kuyaka dats foolish mwanyanya apolice kulemba ana odankhwima nxeru?
ee mesa iyeo anachokapo nde amalondera nyumba anangoenera kuyaka bas