Onse okonda nyerere ndi akufuna kwabwino, sonkhani limodzi limodzi kuti ulendo wa akatswiri a ligi opita ku CAF asauyende wapansi. Wa ana a Israeli mu chipululu.
Ngakhale anakwela pachulu, kuziguguda pa chifuwa kuti iwo zivute zitani chuma ali nacho chochuluka chokawafikitsa ku mpikisano wa CAF, manoma tsopano abwela poyela ndikupempha oikonda timuyi achite limodzi limodzi kuti ulendo wawo wa ku CAF ukhale wa thyathyathya.
Nyerere zatulutsa uthenga opempha ndalama za ulendo wawo wa CAF. Iwo mwa njira ina akumema a Malawi akufuna kwabwino kuti atumize kangachepe kudzela ku Airtel Money ndi ku Mpamba.
Manoma ayamba kale kupempha ngakhale kuti sanasewele ndi komwe masewelo awo oyamba amene akuyenela kuti asewele ndi AS Vita ya ku DR Congo.
Koma mlembi wamkulu wa nyerere a Mike Butao ati kupempha kwawo si ndiye kuti ali mmaluzi ayi.
“Tili ndi ndalama zokwanila ndithu koma sikuti kangachepe sikangatithandize penapake. Tifunika kusewela masewelo opimana mphamvu ndi matimu ena akunja. Zifuna ndalama zimenezo,” anatelo a Butao.
I don’t think i belong to this page. Am out
Why R they donating money in schools while they know that they have got a long journey fack off
Eeeeeee ayenda Wa pasitu amenewo
JAMES CHUMA and his fellow bigots can sponsor Nyerere. We thought ma vendor ogulitsa magalimoto will “be forward” kuthandizapo apa!
Ife ndalama tilibe. Ngati mukufuna ingopangitsani promotion.
Nthawi yoti “Anyakhavi” ndi “Akharupa” omwe akhala akudya ma gate collections abweze ndi ino.
Osamayamba kufuna kupita ku chimbudzi musanadye. Mwathamangira kukumba chimbudzi pano mukutivutitsa kuti tikudyetseni chifukwa mmimba mwanu mulibe tudzi toti mukanyere! Lol!
Koma page ya Malawi 24, imalolelanji mabulutu kumalemba nkhani mopusa chomwechi,,,?
Anthu azikutenga serious ndiuchitsiru wake umenewu
Amalawi kuzolowera kupemphetsa!,kodi simesa muli ndi sponsor!,simunamuwuze!,anzanu aBullets nthawi yija ankapephetsa chifukwa analibe sponsor!,nanga inu!,osamatelo munaziyamba nokha!,osadalira kupemphetsa!
kkkkkkkk koma admn,,,, enanu olo mutukwane chosangalasa nchot “you still like the page”, usasiya bwanji? hahahaaaaaaa!!!
Machende ako admin we can all see ur bullets fan go to hell
This Zambian is not knowledgeable with what has happened to Zambian kwacha. The Zim kwacha has undergone a process called redenomination, where some zeros are removed from the currency or a decimal point moved some places to the left. This is done because monitory headaches and high inflation. Remember in Zambia, there were K20,000 and K50,000 notes. So to reduce the dead weight of carrying money to markets and shops, redenomination has been considered. However, the value and buying power remains the same because this is not revaluation. I think I have schooled this stupid Zambian who thinks the redenominated Zambian kwacha is any better than our Malawian kwacha
Kkkkkkk ngati angakawine
Uisovenge umayesa ndulere
inu mwasiya ngongole zingati agaru inu zomwe simunabwenze
Kkkkkkk tipanga mmmm time ya mabwana
Poor nyerere
Auzeni anthu aziwe imeneyo ndiyo ntchito ya mtolankhani
Mumkati muziyenda pa ndegetu matama basi mpxiiiii
Ayenda pasi bwanji ngati sanawine bus akwele yomweyo kah kkkkkkkkkk
koma malawi 24 munapeza style yabho yopangira introduce nkhani …..maka ija mumkat akana kumwadxi abibi a minister
Even ruling parties, government and private organisations they do fundraising so what more a football club? Mumudziwe yesu
MMMMMM Musadzivute Guyz ndipo ndikupempheni kuti mudziwe kutseka pakamwa panupo, zomwe mukunenazo ndithu ndimaganizo anu amenewo ndipo nyerere sixikusowekelanso kuti inuyo mupeleke Kali konse khalani ndichingambwe fc yanuyo koma nyererez zamyamuka waku Caf basi inu khalani nsanje yanuyo
Nkhani ndiyaboh boh we need more fundng…..kma Wa page iyi I thk ndiwamaule nkhani kuitembenuza lyk da team has nothing for da CAF
Kuyankhula kwa munthu opusa ndiye kumeneko ngati mwasowa zolemba osangokhala bwanji
Kkkkkkkkk
Nanga osapita ndiweyo bwanji useless mmalo momalemba zinthu zothandiza Malawi ulibuzy kulimbana ndi team ya noma imakumvetsa kuwawa eti kakolope India ocean
Kkkkkkk aziwona amenewo.
Ubwino wake sakukakamidza komanso sanapemphe page ino.
koma akunama kuti mwayamba u masikiniii inu a kumanda fc inu?
amenewatu ayenera azione kaye, masapota 2much mwano, kuyankhula chipongwe as if they are on top of world. zampira koma matama okhawo…!
This is not the way a journalist writes story..u r blamed mostly in sports so ur reporter is poor n ur editor is poor in his work.. kupemphetsa aah
Mmmmmm zikufunika ulemu guyz
Mpaja Akaseka Neba Ife Nbb Lelo Bwa? Usalile Usova
Ukaziputa limba, m’mangoxiyamba mulibe kalikonse eti,? Muisova maphwanga
eeeeh kwavuta
Pepa. nebour. limba. Mtima. osafooka umkaona. ngati kumenya. Caf. ndi. pammchenga. uziona.
Uyende pansi ndiweyo wamapazi otupawo. …
Kkkkkk Where Iz B4?
Mufune musafune tikupita olo mutinyoze muli m’mazi
Hahahaaaa Neba Neba Neba!!!!! Don’t force matters.Sitimapanga ma plan kudalira ndalama zopephetsa kodi mesa muli sponsorship??.
Inu mukatitukwanitsako basi
koma y? admin every day de same story you are against nyerere zandikwana wamva
kkkkk kma adha
And someone somewhere is comparing Zambia and Malawi. when even your clubs are failing to participate in the CAF competitions due to lack of funds. For your own own information, our Zambian clubs, just a shirt sponsorship deal is worthy K1.7 million, which is billions if not trillions in Malawian Kwacha.
you mean your kwacha is better than ours? you are wrong idiot and the other thing it is your country which is better not you,am rich but a pure malawian and i know countries like morocco,egypt and algeria as being rich countries but they don’t blow any trumpet like you do stupid poor zambians.Stop using our hospitals idiots
Which hospitals do we Zambians use? You mean shrines for witch doctors from Malawi yowa country. The so called hospitals you are talking about can’t even match our clinics.
Your Kwacha is useless google the facts
Ur suffering from cholera, mbuzi
Who is this idiot?
#Barnabas Zambia r like brothers Shame at U.
I blame his father for not using condom
No one mentioned about Zambia here I think he’s lost cat
Wested sperm
Give him bail
zopepera zomwe yalemba page yi
Y admn of dis page postng issues dat z against nyelele whether ur want or nt they w play caf dis yr i hp wandimva bwino lomwe
Truth hurts! But I’m wondering why you need help hence your sponsors are there?.
Chizungu com kkkkkkkkk
Whether ur want? Kkkkkkkkk
U know in footbal z nt sponsorns who done everthng thre z also wel wishers who contributes accesories to the teams for de love of soccer
you must play two or four games ndikuyamba kupempha at least koma ndigameyomwe siyinamenyedwe Mayamba kale aaaaaaa caf gate pepa neba
Gulitsani ma jez anu app aja kt mupeze money
And tangokumvera kulimba your English is very poor you better go to your previous school to claim your school fees back adakugwira mmaso ?? Ndiye mumazimenya pa mtima kuti ndi team ya ma graduate?? Hahahaaaaa!!!!
Kkkkkkk bola kuyesela kusiya ndi kulepherelatu
Musalimbane za English apa tonse ndiochita kuphunzira bola kumamuseka Peter coz amakanika kuyakhula Chichewa
Sumanziwa kuti ndi olumala?
http://www.noma inglesh . com
Koma noma imatha mukuziwakare
ZAZI NOMA OYEE
Malawi 24,chiganizo chimayamba ndi “wa”?
Tikupaseni ndalama ngati mukachitako bwino zachamba mesa mumadalila kukoza pagolo zikozani mwina patuluka ndalama muwapephe ambuyanu
Bwannoni ndimkweza chigaleta ulendo B-)
Mwandiwonjezatu inu…
:v
Ankayesa ndi masewera?Akafuse chingambwe fc idakodza hvy ndingongole mpakana lero ngongole zikanalipobe
If you dont have money then just stay put. Dont force matters!
this useless page ,with useless adimns, be professinal boy…..
Uli ndi vuto admin, koma ukunama zithekatu!
Zawo aziwona
Anatenga chikho koma ali busy kupempha osatenga chikho kkkk
Nkhani siuyo