Ngakhale Atoti Manje anadandaula kuti pa galimoto zonse zili mdziko muno palibepo olo imodzi ya m’bale wawo, Mtsogoleri wa dziko lino a Peter Mutharika wati a Malawi moyo wawo ukuyenda bwino kamba koti mu dziko muno mukulowa galimoto zochuluka.
Mu uthenga wawo wa chaka cha tsopano, a Mutharika anati chuma cha dziko lino chinaphukila mu chaka cha 2017 ndipo chinkilakila kukwela.
“Kutukuka sikophweka iyayi, zimafunika kuleza mtima. Pang’ono pang’ono tifika pamene timafuna,” anatelo a Mutharika.
A Mutharika ananena kuti umboni oti zinthu zikuyenda ndi galimoto zambiri zikuyenda pamseu.
“Muli galimoto zambiri m’dziko muno, zambiri zalowanso chaka chomwe chapitachi. Ndikamayenda ndikuona galimoto zambiri zabwino. Tikutukuka,” anatelo a Mutharika.
A Mutharika anaonjezelapo kuti kubwela kwa galimoto zochuluka m’dziko muno kwabweletsa mwayi wa ntchito m’dziko muno maka kwa achinyamata.
“Chifukwa cha galimoto zambiri, kwabwela malo ambiri othila mafuta. Malo amenewa akulemba ntchito achinyamata ochuluka. Apa kuwathandiza kuti apeze ntchito,” anatelo a Mutharika.
A Mutharika anaonjezelapo kuti ngakhale ku midzi, anthu akusiya kuyenda pa njinga ya kapalasa ndipo ayamba kuyenda pa yamoto tsopano.
Iwo anaziyamikila kuti ngakhale anthu othandiza dziko lino analeka kulithandiza, koma iwo agwila dziko lino mpaka osapunthwa.
zoona anthu tilibe pabwino
zili bwino bravo APM
Ambiri amene tikuyankhafe ndamene tilibe galimoto.Koma eni magalimoto ali phe.A President akuyerekeza ndi m’mbuyomo pamene magalimoto ankabwera ochepa mdziko muno.sakuti mavto muno mulibe ayi.DPP WOYEEEEE!P!!!?!!!!@&#*;%:??.;!!##**#!!!$_$@@*^_^*:-D:-P:-X:-X:-**^_^*-_-#-_-!:-|$&#**;!!!!!!!!
chuma chikuyenda bwino kunyumba kwanuko osati kumalawi mbudzi iweti tikubwela komko tiswana chamba eti
vuto lawo loyamba ndilimenelo.Sakudziwabe kuti malawi muno munthu modzi amatha kukhala ndi galimoto 1000pamene wina akadalipidwabe ndalama yokwana 20000.ndalama yogulira galimoto aiba kuti.Mwina akatangale womwewo.
The gap between the rich and the poor is so huge
Ine anga ndi matha basi ,anthu akumudzi akukhala movutika,kusowa zakudya inu abwana ndi kumati zinthu zili bwino.zoona zimenezo anthu akumwa madzi oipa inu abwana muli pheeeeeee,lero mukuti zili bwino.owo ngati abwana ananu akugula magalimoto dziwani kuti anthu ambiri akuvutika chifukwa cha inu abwana.kuba too much boma lanuli mr pitala
Ine anga ndi matha basi ,anthu akumudzi akukhala movutika,kusowa zakudya inu abwana ndi kumati zinthu zili bwino.zoona zimenezo anthu akumwa madzi oipa inu abwana muli pheeeeeee,lero mukuti zili bwino.owo ngati abwana ananu akugula magalimoto dziwani kuti anthu ambiri akuvutika chifukwa cha inu abwana.kuba too much boma lanuli mr pitala
munthuyu simmalawi,ndichifukwa chake mavuto wa amalawi akumudzi sawadziwa
Apite kumento ameneyi zikuoneka kuti mmuto sizienda
Inenso ndi me anthu andare koma kunenena chirungamo kumalawi kuno kukusintha or miseu ikumag’ edwa yabwino yabwino kusiyana ndi mbuyomu and sizingachitike zosezi one time ai tiyeni tixithokodza ( guys) and mpano kwayamba kumangidwa ma mall ,shoprite ndizimene zili ma process and mwina ndikutheka kuti simuwerengako now’s Malawi muno
Mbuzi ya president
Galimotozo ndi zako? Who the hell are you, to talk shit in front of poor people in the country? When boosting you mustn’t forget that nothing last forever mbudzi yamunthu inu, onsewa sangakhale opusa mkukhala ochenjera inuyo nthawi ikubwera muzatilipira izo nde mudziwe,
Eee u mr president dont be wise otherwise u will realize nxt yr
Kkkkkkkkk
To him kulemela n galalimoto. TSano galimoto liziyenda mmwamba? Paja aZuma miseu yathu anayipasa gemu. Meaning they are sub standard.
Timabongoto mukunyadilato kkkkk
akatengera masewera 5 -1 ija idzamugwera ndiiye yemwe 2019
Bwana Ndinu Ochimwisa
Bwana Ndinu Ochimwisa
Chisilu cha munthu chimenecho
Ukugawa? ?????????
Za ziiiiii basi.galimoto ndi zawo
Wachamba uyu
Kodi apresident mutu mu amakumetani kodi amameta choncho ngati mkaziyo ndani munakadziwa kapena kuona zimanyasa bwanji ameneyo ndiamene amachosa nzeru zanu za u professor wanu bambo
Anthu akugula magalimotowo ngati umaunza ndi iweyo ndinzeru nzao zimenezo alippo muthu unamuunza kuti apange chitukuko ndindani umuchulue dzina kuti dziko lidziwe ,koma chaponda munawaunza kabedwe kandalama kuti asangalala ndi Ana ake onsati Ife iwe ndiye nyani Monkeys
Mkulu yu kachasu akupweteka heavy
Chuma cha president choka ndi chimene chikuyenda.azaona chaka cha mawa ayenera kuzampasa mazilo okha.muwera 0 makati 0 ndiponso kumpoto 0.achoke chotawa mmmmm
wandale uja anangomulakwila kumutumiza ku zomba akanapitako amenei.
Masende ake muthalikayo afuse kuno RSA galimoto ndi njinga zakapalasa ku malawi koo
I will never trust politicians chifukwa amalankhula mosalingalira zawo zikamayenda amaona ngati wina aliyense zake zikuyenda koma akanadziwa mmene amalawi tikuvutikiramo akanachepetsa kulankhula motumbwako
zatikwana tioneko dzina
Zoopsa2!!!
kupusa
I remember bro wake anatiso,,ngati kulibedi fuel mdziko muno pitani pamsewu tikaone ngati sakugundani kkkkkkk mutharika family
Olo tikugona mu mdima
Fodya wamkulu weni-weni akuluwa ali ndi mbwelara chonchi? Kkkkkkkkkk!
Sakunama bwanawa
Tiyeni Ku mudzi tikaone if people have the basic needs then we can say all is well. Mu town mwachuluka cash gate it won’t be the right litmus paper for good economy
Zoti 2019 ikubwela ndipo tidzavota sakudziwa,ndipo amalawi tigwilane manja ameneyu ndie wotionjeza, mbavazokha ndizomwe zikunjoya mu bomalake losekelela umbava ndi umbanali.
ife tizamuvotera emweyu
tiyenazoni
Za chinazo
Stupid Malawians they speak
Ine magalimoto onsewo palibepo ya m’bale wanga……..
Galimoto? Magalimoto akeso makatoni aku Japaniwa? Koma akuluwa akudziwa mmene anthu akuzunzikira mmidzimu plus mma town ang’onoang’onomu? What about street kids ali mbwee mtowniwa? Ichi ndi chitsirudi eti?
Iiiii Kaya
Zawo kaya zimenezi nanga paliso chifukwa chonyadila pamenepo?
Ronald shumba tsopano! kkkk akunena zoona bwanayu
Ndianthu Angati akumudzi omwe agula magalimotowokodi pulezidenti sanganene kuti zinthu zikuyenda bwino kamba kowona anthu atown andalama kale ena mza cashgate mkumati chuma chikunda bwino aaa!kuu apite ku midziku ndipo adzapepesa mawu amenewa kumudzi uku kuli mavuto oopsa osati chibwa akunenacho atown ambiri zimawayendela ndikale mchifukwa chake odathawa ku mudzi kuja kapena akulamulira anthu atown okha pamene anthu mbeu abeledwa ndi K30-50 fodya amwayi$2 ndiye munthu wakumudzi angagule galimoto pamenepa tiyeninazoni 2019 mposachedwapa mwatilanga osatimasewera zikomo.
Ichi nde nchopepera kuposa mkulu wake uja. Udzalira 2019
Fodyaeti!!!!
second cars ngakhale titan mkuipeza bora ogeya nyama alibe problem
Muthalika everytime umafuna uzindiyakhulisa pa mbali
Muthalika everytime umafuna uzindiyakhulisa pa mbali
Kkkkkkk
Zomvetsa Chisoni Presdent Kumayankhulachoncho
Zomvetsa Chisoni Presdent Kumayankhulachoncho
Ganja petr sakuphafa bho
kupenga eti akuba inu. mwause a Custom/MRA achepese umbanda akuba too much
Don’t wast your tym kulemba comment yaitali imatopesa kuwelenga try 2 be brief
iwe wachamba pasana pano,,,m’mene ukukwapulira/kuba custom mo,tazipanga ngt Ku Mozambik ndku Zimbabwe kumatchipa macustom,,kmaso usuye zomatilanda magalimoto paboda KT Malawi itukuke
Atoti manjewo ndi amene tikufuna atalamulira dzikoli kamba ka masomphenya awo pa anthu osauka osati olemela amagalimoto anuwo
Kkkkkkkk Mr .President stop weed
Magalimoto bwenzi akudutsa apa, koma boma likutibela ku nkhani ya Custom, its toooooooo much
Ine koma ndinayamba kumumvesesano munthuyu…pena amakhara zoti akuyankhura zanzeru koma vuto ndi malongosoledwe ake…1 day I quoted “dziko la Malawi ndi la fodya kwambiri, nde za fodya zomwe mukupangazo musasiye chifukwa zimabweretsa chitukuko mdziko muno” just imagine
kkkkk
Akuti Musasiyetu Zellie Tasanga Chirwa
Koma #Papias hahahahaha #Zellie ukumtchurayo ndi wa fodya nayenso ndekuti et lol..
kkkkkkkkkkk
Kkkk Ayi # Ronald Kungoti Amathanso Kuzukuta . Angathe Kutipatsa Matanthauzo Ambiri Amawuwa
Hahahahahahaha komatu inu mukufuna mundimenyesepo apa kkkk akakwiya a Zellie wotu mpaka AU ichite convene basi
our president is Massa pussi
uchitslu,wa mun2 wophunzr,, if he prezdise the malawians sakanalankhula zopusazo ,kumamidzi alind magalimoto ndyangt?& thoz hu owns magalimoto anagula ndyeo ?b4 expressn ua speech u shud draft it,,, prezdent wa ntown …
Nanga miseu ndi kukwela kwa zinthu akuti mbwa?
YES D PRESIDENT HAV MANAGED TO BUILDING AHOUSE IN NYAMBADWE THE ECONOMY IS IN GUD SHAPE KKKKKKKKKKKKKK
Iwe pitala iwe!!!!!! oh ndingalakwepo kod ukuwagawira naiwe ndalama zogula ma galimotowo? So umafuna kut anthu asiyule2 kugula ndikumaliza kugulitsa amene anali nawo kut udziwe kut anthu akuvutika? Palikundu shit;!!!!!;
whether u want or nt bt u as our father malawi plz sometimez if u want 2 talk 2de public like dis plz first of o u suppose 2 think abt de pipo hu were poor at o so w as malawian pipo w masn’t look how number’s of cars w hve in dis country nop. Bt w need development from u father malawi das y w choose u 2b our reader ok so mukamalakhura muziyamba nkaye mwaganizira athu omwe amakhala mkumuzi omwe mpaka mpano sanayambepo kulota maloto ozagula galimoto coz 2much cars is nt a development wht pipo excepted 4rm u 2019 is nt far mchimenecho mudziwe. Long live malawi
Amadya Chamba chowawa
Pitalala muthalikalala
IN THE PAST KALIATI SAID NGATI MAFUTA KULIBE KAGONENE PANSEU TIONE NGATI SIKUGUNDANI NOW D WHOLE PRESIDENT TALKING TO THE WORLD KKKKKKKKKK MALAWI IN TOP 3 Ov The Poorest God Hav Mercy
where did you do your reasech about malawi be on postion number 3 of the poorest in the world can you please do reasech again and see what position of malawi
PLS DO IT FOR ME KKKKKKKK NOTE MALAWI IS POOR LIKE IT OR NOT
Government cars or private cars?
Ma used cars ndi omwe akuyandira?
All These Car Plus Gertrude Road.
Uyende owone galimoto ukunena za China. Anthu akukwera galimoto osati za China komanso galimoto nzosala wauze anthu za yesu kumalawi tikuvutika kuposa maiko onse apansi chifukwa chainu azigoleri adyera amkhwizi mulandile yesu
PITALA 2019 ULENDO
Amene Akugulatu Magalimotowo Ndiwomwewo Amene Alinawo Kale Zikanakhala Bwino Atamakhala Omwe Alibe Ndiye Ndiponi
Kkkkkkk u see now, that’s the problem when u vote for a Professor
President sitinamupezebe a Malawi he’s childish like his brother.
Peter mutharika quotes
Mbuli
KUNKHALA NDI GALIMOTO SIKUTUKUKA KWA DZIKO KOMA KUKHALA NDI MA COMPANY AMBIRI NDIWO MAYAKHO ADZIKO chifukwa aliyese apeza zochita .sizamisala ukukukamba apazi
Bvuto ndilakuti Malawi ali magawo awiri tsono poti apresident amakhala ku malawi (1) mpake kumayankhura zopusa ngati zimenezi Sinanga umphawi womwe akukumana nawo anthu ochuluka omwe amakhala ku malawi (2) iwo sakuwudziwa komano chobvetsa chisoni ndi chakuti malawi wa anthu ambiriyo ndi amene akunzuzika ndi umphawi komaso ndi yemweyo amene amawavotera ndiye poti pali mawu ena akuti (m’dya nyemba amayiwala koma mtaya makoko samayiwala)mudzawadziwa amalawi nthawi ikubvera bwana wanga mungoti pheeeeeeeeeeeeeeeeee
joke of the yr 2018
Hahahaha stupidity
Do u buy for them?
kutukwana kumeneko
custom its too much komaso miseu bwana mutiganizire
Uli bho aixe!
Eti mpakana custom kuposa nyengo wagulira galimoto!
IYI NDIYO MISALA
Nkuluyu saganiza anangowona magalimoto ntown ali anthu Zikuyenda kkkkkk Prof uyu ndi wa China ndithu.
Come 2019 ife nde tizavotera atoti manjewotu
Kkkkkkkkk oho
but can a gratuate or a normal person be happY ,n sayn tht our life standards has been improved ,jst bcoz of incoming of cars to our country, do i look lik ,i own a car?, if u r grown old ,,don’t deceive us please!!!
Tafusa atoti manje iwe pitala wamva
Zachamba
Kkkkkkkkk koma uyu samatha kuyakhula Eeh! Magalimoto nde nd chuma cha dziko
Kkkk kkkk komano Ku Malawi,ma galimoto etiii….mm!
Munthalika akufunika alondole komwe kuli Vincent Wa-Politics
To him chitukuko ndi magalimoto,magalimotowo alinawo ndi anthu angati,Kapena mmene iwowo amayamba kulamulira anthu ku Malawi analibe magalimoto?
Inu KO’d malawi news 24 imapang za serious?
Banja la anthu wa onse ndi amisala
Peter ok fyn….. Kma atot…..