Msogoleri wa chipani cha Kongolesi, m’busa Lazarus Chakwera, wasambwadza Pulezideti wa dziko lino, Pulofesa Peter Mutharika, kuti asiye kuloto zoti n’kudzapambana pa chisankho chapatatu chomwe chichitike mu chaka cha 2019.
M’busa Chakwera audza a Mutharika zoti adzagululidwa mano, kuchotsedwa nthenga ndikusiyidwa ali zoli ngati nkhuku ya chitopa.
A Chakwera anati ndi onyangala ndi mzuzulo omwe a Mutharika ananena oti zipani zotsutsa zikufuna kulanda boma mwaupandu kudzera mu ndondomeko yavotera ya fifite pulasi wani (50%+1). A Chakwera anati ili ndibodza la mkunkhuniza.
“A Mutharika athiridwa mphepo ma chaka mu 2019. Iwo asiye kuloto zoti pali wina akufuna kuwalanda boma mwa upandu. Bomali titengadi, koma titawathibula muzisankho zomwe zichitike mu chaka cha 2019” anayankhula mwamangolomera a busa a Chakwera.
Azipani zotsutsa ndinso othandiza dziko lino akhala akufuna kusintha njira yomwe amalawi amasankhira pulezidenti. Koma ndondomekoyi inakanidwa ndi a phungu kunyumba ya malamulu ku Lilongwe.
Mcp yomweyo Ili boo
Dzikoli lizingolamulidwa ndi zi anthu zosaziwika bwino ndithu ati aPetala,aChakwera oti mu History mulibe uuu Malawi
Abusaso amasambwaza!koma abale zandale iziii!
iwe chakwela ndi chipani chako chakhaxacho pitanacho kumanda kt mwina mixukwa ikaku votele kma ife amalawi takana kaye mutu ngati Bomu loxala pansi..
iwe chakwela ndi chipani chako chakhaxacho pitanacho kumanda kt mwina mixukwa ikaku votele kma ife amalawi takana kaye dadxi…..
Kwacha!!!!!
Chakwera sangawine ndikuti! ngati ukuyaka wauwisi nde mungasongezere wouma? nzeru mulibe mmutu! come 2019 mudzandivomereza ife sitivota chifukwa chotchuka mayazi 2019chakwera will fall down and down pamenepa nde adzadziwe chabwino ndi choipa ife sitifuna munthu wa Nsanje,Mtopola,Mwano, & Kuzipopa akhala pansi ameneyu azakeso ankatero koma iyeyu anali asanabadwe nthawi imeneyo kkkkkkkkkkkkkkk Malawi woyeeeeweeeeeeee!!!!!!!!!!
CHAKWELA MBOMA LA MWANZA NDI NKHUNGUNI ZOOPYA ZIJA ZOKOZELA MASO ZUNUKHA BWANJI
ndili pheee patheba zivotan zopanda kumutuzo from here ndikulowa Zimbabwe
Iyeyo akunena bwanji choncho ngati kuti amavota yekha? Nanga tonse amene timavota titati tisakavote angachite matama amenewa. Ngati ndi kusambwadzana ,akasambwadzilana kwina osati kuno, ife tidzavotera chimanga chomwecho, chifukwa ndiye moyo. Ngakhalenso tambala wakudayo kuti akhale ndi moyo amafunika atole chimanga chomwecho. Vuto lilikwathu kuno ,azitsogoleli amakanganilana pa mpando cholinga azibapo ndalama. Ngati iwo ali ndi fundo zotukula anthu ndibwino azibweletse poyela mothandizana ndi boma cholinga choti miyoyo ya anthu itukuke. Tangoganizani kadziko kathu ndikakang’ono kwambiri, koma boma likulephela kuyika magetsi m’mizinda ndi m’midzi, nanga limalandila zithandizo kuchoka maiko osiyanasiyana ndalamazo zimapita kuti.?
za ziiiii
Amenewo ndi anthu ena ake akufuna kuzavotera mbavaz osaphuzira ajaa akuchigawo chakuuuuuuu
come 2019 Dr. Lazarus Chakwera owina wina
come 2019 Dr. Lazarus Chakwera woyeeeeee….
Zaziii
Tiona 2019
Asavutike Peter Degree Yake Yatikankhila Umphawi Wadzaoneni
Asavutike Peter Degree Yake Yatikankhila Umphawi Wadzaoneni
Are u sure MCP ilamule Malawi zamanyazi
OVota ndi anthu osati achakwela ndale zakale zinatha masiku ano koma fundo.
no more mutharica kingdom.chakwera is indeed correct.apm is too old for presidency,clueless to problem resolution,will struggle for runningmate,habouring chaponda a big fish,5 to 1 loss prophesy downfall of dpp
Let’s not Fight let’s just wait mwatjwana anthu opanda nzeru. . Mcp my vote
muzipanga edit zolemba zanu musanapange post!!!
mukungoti chakwera sa wina chifukwa chani? Nde kuti Dp p yabera kale mavoti thruogh national Id et?
Za kaizara perekan kwa kaizara za kwa Mulungu mpatsen Mulungt, tisamanenenso kt M busa km mtsogoleri wa chipani cha Mcp.
ACHAKWELA chaonanzako chapita mawa chlikwa iwe
Chakwera Mbuzi yamunthu .
Don’t vote for MCP
Pa chisankho amavota ndi anthu osati munthu.Komanso dziko osati dera.Tiyeni tidzingomvera akutukwanizana.
Kkkk Peter ali ndi nthenga ndye amusosola kkkk koma kumeneko
kkkkkkk kaya tiziona
Akuchepa bora abwelere supongo
Koma let’s be serious guys ena we are just commenting we don’t know wat z happening on the ground like how our economy is driven… don’t vote for fools pliz pliz ….professor dzina lokha palibe akuchidziwa
Chakwera wayiphula APM akudziwanso
Uthenga omveka bwino
Afunse atembo zakazingati auponda kusiya kutumikila mulungu , kulowa usatana ongotukwana
Akanangodkra nthaw ikwane yokha chfkw iye sakzwa zansogolo asaiwale tmavota ndianthufe,Ameneyu akuyenela kupitad kumental ndwachamba kwabas.
Afunse atembo zakazingati auponda kusiya kutumikila mulungu , kulowa usatana ongotukwana
Inetu sindili mbari ya chakwera koma na boma ili lokha lipite laminyama mmmh ndaona zosaona ine
Akulota kapena ayi,afuna tidziti kwacha kwacha lero,zachikape DPP woyee!!.
Mbuzi yamunthu ngat chaska singawne dziko,Ubwino wake amamvotera ndi atumbuka Anzakewo,Mumuudze kut iye ndianxakewo chipani chawo ndimavampaya mbuzi za anthu fk u chasika.
Tikungotaya nthawi yathu pachabe ndikutukwanizana amalawi,andalewa alingati mabar girl zikomo nonse.
Linda madzi apite ndiye udziti wadale, Sibwino kumatukwana ng’ona iwe uli mnyanja ili ndi dziko mukadzitukumula Mulunga adzakusisani baibulo limatero
akazangotenga boma kkkkkkkkkkk tzpanga nafe ziko lathu “chilombo chingalamulire?,gule kwawo”
Big up my president, you r the best candidate for 2019 polls, let this one hand man,who doesn’t even knw how to speak,wofoilayu knw he z on leave kkkkMCP Bomaaaaaaaaa
achakwera akhale chete amavoti ndife koma akachulutsa zoyakhura zitivuta nditu don’t 4 get AMAYI amati chani
Angotitayitsapo nthawi,mfundo zanu ikuzifuna osati mukupangazo
Mcp Iwalani Zokhala Presdent 10yrs sizinathe Dpp Woyee Mpaka 2019
Forget Dpp no intelligent person can vote for Dpp family party zipani zopasana pa chibale ngati ufumu unless malawi want to become a kingdom kkkkkkkk rotten party
May I know your school of thought you praising chakwera,on what ground are you judging chakwera as a better performer since he has not been a state President,mind you theory is not practical, chakwera is talking much on theory. I find it meaningless to compare a party President and a state president because the too play different roles
GOD KNOWS
Kodi ndi liti limene MCP idanenapo kuti idzaluza masankho? Kuyambira 1994 kufikira lero MCP imati tidzawina bwerani masankho kuyambira 1994 kumangoluza,ndiye pano muti chiyani,m’ busa wa fake iwe
Mfundo less, tidzidzati kwacha kwacha kwacha kuMalawi kuno maloto kukoma ochakwera
Chakwera ndi mfana heavy pitala ndi lidala
CHAQERA SANGATLAMULILE IFE NDPO ASIYE KULOTA MALOTO AMENEWO ZAUSILUUU!
Whether we like it or not Chakwera will be our state president come 2019. Inu tikuwona panozi ndi zero
Takuvan Bwana Zabwino Zose
Chakwera not lying
Pajatu a Mutharika ndi a Chakwera onse adapikisana ndi Amayi JB
Mamuna anawoneka…Tonde adatenga boma
2019….zilikooooo
Zopanda umboni …….ine sindingavotere lazaro
Pitala ndi Lazalo siyani kukangana tidzavota ndi ife ma blackout atikwana
Zikavota anzanu azizagula magalimoto mutawavotera
i hate not my president Peter Munthalika,but i will vote for something new ey! i will try chakwera
i hate not my president proffesor au
Mmmh
Aya galu amenyi watkwana ineso voti yang singpite kwa iye!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!
No more DPP we are tired, Si zaufumu izi.
Kkkkkk
Limbanani kma ovota ndiife
Voti ndi mumtimaaaaa!
kulota saletsanaaa
Chakwela my foot!!!!!
Kod munthu akakhala mtsogoleri Wabwino wa mpingo. Ndiye kut. Athanso kukhala mtsogoleri wabwino Ku dziko la Malawi????
BOla kupatsa achakwela mavot kusiyana ndi mzika yaku USA,Ndicifukwa akutizuza siwakuno mulungu akuwona zosezi awonatu!!
Eeee abusa amenewo? Shame to himwoooooo
Ine sindingabetse voti yanga kuvotera m’busa wabodza kumangolalata monse anayambila president wake adzakhala otani ameneyu
When Chakwera speaks, all Cadets and toothless mtchona get shaken and bark like mad dogs!!!
All the politicians are crooks and none of them is good
I cannot vote for an old toothless imbecile! Better Wandale !
Dziko lathu silikuyenda bwino ndipo silidzayendaso bwino olo pang’ono. Chikondi ndi chomwe chikusoweka pakati pathu. Kodi ngati wina ulamuliro wake sukuyenda bwino bwanji inu otsutsa osabwerapo ndi mfundo zabwino zothandiza kutukula dziko lathuli? Taonani mmalo mwake mukungobwera ndi kulalata, kutukwana, kunyoza etc. Ndi zoona ndithu kuti mdziko muno tili ndi mavuto ambiri omwe chipani chimodzi sichingathe kuthetsa mavutowa pokhapokha zipani zonse zitakhala pansi ndikumanga mfundo imodzi kusiyana ndi kumangonyozana basi. Dziko ngati silikuyenda bwino, ndi udindo wanu ndithu inu otsutsa kukambirana mwachikondi ndi omwe akulamula momwe mungathetsere mavutowa osati zomangolalatazi ayi. Dziwani ichi kuti dzikoli anthufe tikusowekera chikondi chifukwa nawoso olamula akumva kuwawa ngati inu otsutsa mukungotukwana ndi kulalata and zotsatila zake inu mukadzatenga boma zidzaonekaso ngati ndinu olephera chifukwa simudzapezamo ndalama m’boma zoyendetsera dzikoli chifukwa olamulawa adzaziba ndi cholinga choti iwo asadzanyozeke. Aliyense amene akufuna mpando umenewu ayembekezere kukumana ndi zokhoma chifukwa olamula pochoka adzatenga ndalama zonse. Chikondi ku mipando chasoweka ndiye panoso zatsikira ku ife anthu. Akuluakulu akungotukwaniza mmalo momanga mfundo imodzi, ifenso anthu wamba tabalalika kusowa kolowera mapeto ake za ndale zomwezi tayambaso kumatukwanizana kudzera mma comment athu. CHIKONDI CHATHU CHAPITA KUTI AMALAWI!
Peter n Lazarus stop making noise pliz becoz u are not voting but the judgement belong to the voter not u shut up pliz!!
Maloto achumba ndiye DPP. Kumalota ngati apereka mimba. DPP is now almost water under the bridge. Ndani gonthi amene adzavotere chipani chambabva, cbakupa,chotukwana. We”re counting down towards 2019.,muone momwe dziko litenthere. Anthu akuvutika ndi DPP and bwampini wao. DPP ithangati makhatani. No matter how lalatafulu u may be, u’re just fishing in the dry river.> MCP 2019 bomaaaaaaaaa!
Simukunama Ndikunena Pano Anthu Akugona Kuchigayo Kufuna Kuti Agayitse Kuphatikiza Apo Zinthu Zafika Posauzana
MCP ndi boma kale ndili pa mbuyopo
ukuvutika ndiwe….dont think an2 akumwera and kumpoto tingavotere chakwera…..stop dreaming…. olo Peter atakhala kuti wafika pa worse….. we love our president…. chakwera is a goat….ofunika kungomangilira pa mtengo
Ma Kadeti pano afatsa kulongolora kunyoza a Chakwera! Atawatibula pa by elections anangoti ziiiii gada kukamwa yasa! Uja wakudedza councillor atawina pa DPP, only after 3 days he went to MCP! Taonani, Chakwera 6 Gogo Mtchona chopanda many 0 ! Kkkkkk NDE lero mukunyoza Chakwera okutibulani uja! Amvekele Chakwera sangakhale President was Malawi, sure? DPP followers are funny idiots!! Kupanda nzeru zoonera! Afro Barometer yinati chani! Lero mwaziona? Keep on supporting Thieves and Failures! Kupanda umunthu!!!!
Eeee!!Koma Ziliko Ku Malawi.Tieni Ubwino Wake Zikumenyana NJobvu Zokhazokha.
Chakwera Akuchita Matama A Ng’ombe Onyera Choyima! Kapena Ngati Chule Odumpha Popanda Zenje, Kodi Mwati Adalidi M’busa Ameneyu?
who can forget MCP for it’s cluelty that it murder innocent pple,so vote MCP it is like forgeting past.
Ino sinthawi yoti mudzitukwanizana koma kuona kuti Malawi wanthu timukoza bwanji kuti akhale wakaka ndi uchi owina sakudziwa apa nonse ngolephera patsani ena akoze Malawi kkkkkkk
Ino sinthawi yoti mudzitukwanizana koma kuona kuti Malawi wanthu timukoza bwanji kuti akhale wakaka ndi uchi owina sakudziwa apa nonse ngolephera patsani ena akoze Malawi kkkkkkk
iwe samagona bwnj? boza ife ai
iwe samagona bwnj? boza ife ai
I hate dpp and its leader just as much as i hate satan.
I hate dpp and its leader just as much as i hate satan.
INCLUDING ME I HATE CHAKWELA LIKE SATAN
Utandala . Its good we don’t like the same people
Boma ilooooooo 2019
Kumeneko mumati kusambwaza haaa? nkumene ndizowona peter olo kuba chauta sazalola ntaaaaa,
Basi tikhalira zongosambwazanizi??? Remember, mmene mukusambwazanamo ukuvutike ndi udzu not you coz kumbali mukumakumana nkumagulirananso ma fanta
Unprofessional journalism,this news headline can bring anger,confusion,fear,enemity among the general public.The reporter shows the side of the story at which she/he belongs.
Achakwelawo ndiye ndani? ngati zikumuvuta peter palibe mene angadzatenge malawi ndikuyenda bwino guyz kuti tilimbane ndiboma tizingotaya nthawiyathu pachabe lucias anayimba kale kut takumana okhaokha akuba inuso mukufuna muzizatibela misonkho yanthu amene kunalembedwa kuti azasankhidwa kuti abeleanthu pamalawi ndiamenewa jb bwanji sanabe?siuyuaangodyelele
Achakwelawo ndiye ndani? ngati zikumuvuta peter palibe mene angadzatenge malawi ndikuyenda bwino guyz kuti tilimbane ndiboma tizingotaya nthawiyathu pachabe lucias anayimba kale kut takumana okhaokha akuba inuso mukufuna muzizatibela misonkho yanthu amene kunalembedwa kuti azasankhidwa kuti abeleanthu pamalawi ndiamenewa jb bwanji sanabe?siuyuaangodyelele
CHAKWERA NDALAMA ALIBE
Chakwera emweo.
Chakwera bwezid atazawina koma mmmm wayamba kundikaikixa too much kuwawatawawata,zikuchita kuonekeratu kut first term yake siizakhala yopanga chitukuko ai koma kulimbana ndi kumanga onse omwe akuxogolera DPP panopawa
ooooooooooohh zosakhara bwino pomwe panalakwa ndi poti mtsikanayo analetsa ekha ndiye zinafunikakumuguliraaaa galimotoyo mpamene afisi aja amagwira mbuzi basi ndangozindikira ndimalota
Impossible dream, Chakwela alibe mfundo chimene amadziwa Iwo ndikunyoza mtsogoleri wadziko koma sadziwa kuchitapo kanthu koti nkuthandiza dziko lathuli.
So it’s his freedom of expression but he must forget that he will rule this country
Iweyo chitapo kanthu, ulibe chani??
Iweyo chitapo kanthu, ulibe chani??
What are u after all? NDE Murchona wako wopanda manuyo ali ndi mfundo zanji? Zozimitsa magetsi ndi Kuba?
Maloto achumba amenewo iyenso Chatsika aiwale zoti adzalamulira Nyasaland 2019 Prof APM BOMA!!!!!!
chakwera gets my vote come 2019
DPP WOYEEEEE 2O19 BOMA PALIBESO WINA SITIFUNA ZIPAN ZOKUPHA
AKULOTA ABUSA
Chakwera ukunama ndiwe mfumu ya anamalila ukalephela umati akubela timakudziwa
Its time for change yes but not with so called CHAKWELA
But with you?…yambitsani chipani chanu tikuvoteleni
Osayambisa iweyo bwanjiiiii
Osayambisa iweyo bwanjiiiii
Ma Group Ndionse Koma Kolite Ya Group loooo #MALAWI_WATHU Ili Ndi Group Lokhalo Lomwe Kukumakhara Nkhani Zasopano Zomwe Zachitika Kumalawi Ili Ndi Group Lomwe Kulibe Zonyozerama Mitundu Olo Zipembezo Ku Group li Tikumachezako Bwino Bwino Kuphatikizanso Apo Tikumapasirana Nkhani Zosiyana Siyana Zomwe Zachitila Kumalawi Funso Mkumatu “Kodi Munajoina Kalee???” So Ngati Simunajoine Mukudikirira Chani??? Tangopangani Search MALAWI WATHU Mukatelo Mupange Join Kuti Nanunso Muzilinjoya Group li #Malawi_Wanga #Malawi_Wako
Osewa sawina dilu bushiri hihihi
2019 DPP AGAIN WINAWE UKUNAMA IWE
Musavutike guyz,MCP singawine ameneo ndimaloto chabe chifukwa akukhuta nsima.DPP mufune musafune izawina
Am selling power bank amene angawafune malinga ndi mavuto amangetsiwa
Awo ndimaloto anachibwe awo
Ngatidi antadzavote yekha mmalo mwatosefe. Wayamba ndale za Muluzi eti zoti mufune musafune iiiiii leroso? Amavotatu ndi anthu a Chakwerawo asiye matama its too early to predict for that.
Chakwela pomwe anali presdent wa mpingo wathu (AG) palibe chitukuko chooneka chomwe anachita koma kutibela ndalama zathu
Koma pali winawake yemwe akukhulupilira kuti chakwela nkuzalamulira dziko la Malawi??? Ngati nchoncho,ndale sumazidziwa.
Analephela kusogolera kagulu kochepa ka anthu nde akatsogolele dziko,otembeleledwa chakwera
Is apm managing ?
Is apm managing ?
Hmm waboza iwe! Chakwera was the best President of Assemblies of God! Were u there? Stupid with your old mouth- drought mtchona!
Guys tamangolimbikilani ntchito chakwera sangadzasinthe dis country komanso sangadzawine
Koma ndiye kusosoledwaaaaa ngati nkhuku ya kamete
make hay when the sun shines
I dream last nit ndikupita kopeza ndalama kuworkshop siiyo ndaitanidwa, dream come true if God say yes palibe munthu olengedwa ndiye angati no ,,,merry xmas abale nonse apa FB
Ndadzara ntedza wambiri ndidya makata Chaka chino
Abusa…kkkkkkk… kicks of a dying horse
Dpp must.go it has totally failed
Ovota tilichete
Ife Ovota Tikuvomelezaso Kuti Aiwale Za 2019 Tazunzika Mokwana Tizaone Zina Siufumu Kuti Mtundu Umozi Ndiumene Uzilamlira Simlakho Ilindiziko
nkhaniyi ndi yoona nayenso ‘Donald Trump’ watsikimiza kuti mutharika agonja kwa Dr L Chakwera mu 2019
Chakwera is dreaming to be come president of this nation.
Iwe Panyopako Chakwela Usazanenenso Zimenezo Wamva Usowat
Abusa dreaming in bad colours kkkk what happened 2014???
U had no that machine to smash Mutharika esh shall see
Mamuna mzako mpachulu lol.
Siyani kudzinyenga ndi chala nokha malume…….. Boma la zunza azigogo athu limeneroro…….. Bola ndidzizunzika ndili mfulu not ndizisangalala opanda freedom
Mgwilizano akupanga a DPP kumanyengelela tizipani Tina ameneo ndi mantha kuiopa MCP aludziwa MCP ndi chipani chaphamvu komanso chachikulu olo naye muntharika akudziwa zimenezo
Kodi kudalibeko mmene tikachotsa MCP Malawi sangaifunenso olo pang’ono
Ngati Chakwera/chatsikayo Akadzivotere Yekha Adzawina!Koma Ngati Ovota Ndi Anthu Akumidzi Asiye Kulota Zimenezo Akanakhala Oganiza Chatsika Sibwezi Akuima Pachulu.
Chi style changa chili ndi Lazarous ndikunena pano Chakwera, uchiona icho chi hater kuthamangira njinga Chakwera.
Kkkkkk koma ziliko mpaka kusosolana nthenga?but I will go for chakwera am tired with blackout’s and nepotism.
Mcp must forget the dream of wining 2019 election other wise they will sing the same story called: (atibela ) zileso kungoti zizavumbaso) swing person dosnt talk but this rubbish pastor is busy sweling the president oooo!! Akhalila yomweyo
Anakutibula 6 kwa 0 kkkkkkkkk Shupiti!
Chakwela kayammati Chasika aaaa kaya zosekesa amalawi sachedwa kuiwala mzafa ndinjara
Inanu mungotokota zambili vote yanu kapasene omwe mufunayo DPP ulibe vuto koma pitala ndiye chakwela ngati ine aona athandiza asiyeni koma chakwela azawina ndimene waonela
Shame MCP, inatuluka m’boma 1994,sidzabweleramonso.
Voters are just quiet. what Hon. Chakwera who left the Temple but failed the 2014 elec has said is clear,and with their naked eyes pple’ve cn the curent mw state president P.A.P Mutharika’s works of his hands. COME 2O19 plz one to shade tears!!
MDIZOONAD CHAKWERA NDI deal
kunena zoona captain oyendesa sitimayi salibwo posatengera chipani chomwe tikusapota ! ndichani chodziwaka bwino chomwe angaloze wapanga pazaka zomwe wakhala pamupando? tisalole kukwera sitima imene oyendesa wake ndi wa blind oti zoti magetsi akuta iye sakuwo,zoti muli katangale sakuwo ena mpaka kumaotcha ma office oti anzawo anamanga bwinobwino,zoti amalawi tikukhala mwamantha sakuwona eg issa njaunju ,chasowa,bunda student , ma strike muma departiment abomawa ngamwezi uliwonse ,macampani ambiri asamuka muziko muno economy silibwino koma zonsezi capitani sakuziwona.nde tizipitirizabe kuombera mumanja munthu akulunjika nafe kuphompho ,kumyala ?AMALAWI NOOOOOOOOOO!!
Kod iwe ukuti m’busa mtumiki wamlungu iwe ngat ukusiya kulabadira zamwini moyo uzalabadira zaife?mot utenge Bible uziyenda mmisasa mkuwauza anthu za ukulu wamulungu koma kunyoza anzako ndi 1 m’busa wanji ameneyu, shame on u.Mlungu azakukantha.
Chakwera uzalakalaka kuzikhweza ndi chingwe mu 2019
Bravoh our President Chakwera, u are our hope, God is with us. Cardiac is waiting to deal with this Crocodile DPP.
Kkkk
Cardiac ikuchedwadi! Let it come very fast in April may 2018
Mcp idapita ndi madala a jzu tembo
mbuzi yambusa iyi yothawa kularikira wasatanasm uyu
A chakhwera mukanakhala kuti ndale mumatha, ino sikanakhala nthawi yosambwaza president ayi koma inali nthawi yoti muzikamba zomwe mungapange mutakhala president kut mavuto ali Dziko muno muzathana nawo bwanji ndiye anthu tikhutire ndi fundo zanuzo koma kumangoti ee 2019 suzawina mmmm mamuna zako pachulu amwene ndipo campaign director wanu sakukuthandizani bola mukanatenga inenso kkk
Keep dreaming, after all. Dreams comes. When u go to bed with full stomache, kukhuta ma allowance amisonkho yathu,
Iwe chakwerA olo zitavuta bwanji suzawina 2019, uzingokonzeka kukatenga injunction
Masiku otsiliza zilimbanani..
Mmmmmmm koma zikanakhala bwanji, ngati mmbusa munthu wa mulungu ozozedwa mukanazisiya zandalezi mkubwelela mmanja mwa mulungu bwanji, sakanawelengela zoti mwasusa zitukuko zingati mwalephelesa ma bill angati mwatukwana angati sakanawelengela zisiyeni mkasa anati ungoona kutha mau okwilila mnzake saziwika.
Popeza Chilembwe, Kaleso Ndomondo, Dumbo Lemani anali akumwera nzowayeneleza Ku lowa ndale koma popeza Chakwara ngwa chigawo cha pakati nzosayenera? Mitu yanu yozungulirayo ikagwere uko! Upgrade ur oblangata to 6g pliz
Lkklkkkkkkk awuuze awuze ngozi awuze amvetsetse lero
wina walemba comment yake ati malawi ndi dziko lomvetsa chisoni. funso: kodi nanga ukukhaliramo chian momvesa chisonimo?
I think there is something in chakwera why akayakhula zithu boma limat ndwopenga ? hahahah wake up malaw it’s tym to change
mukamati kusambwadza mukutanthauzanji a news 24? choncho ife tikayankha muziti adpp akunyoza eti? mukamuuze chakwerayo kuti iyeyo asamalote zotenga boma. musaiwale kuti : chakwera savomeleza kuti adaluza, APM atawina 2014 chakwera ankati wabeledwa. tsono adziwiretu kuti dpp sikubwera mocheza,
MCP inamwalila kale kale pamozi ndi kamuzu
Nice pic
Regardless any political affiliation. Am below 40yrs. At my youthful age ndikavotere Agogo a zaka 81 kukhala mtsogoleri wa dziko for my next 5yrs. What will I benefit on his leadership? Am I mad?
Guyz don’t think like MCP it will be win no u must take example is it 10 or 20 tambala there are two elephant it impossible small elephant to big nothing so don’t waste u time to think like chakwela or MCP it gonna win
Mwina mukadalemba chilomwe kapena chiyao anthu akadamva chomwe mukufuna kunena bwana. Nanga kungoti pa facebook pamakhala chizungu ndiye nkulemba kalongonda wanuyu? Timvapo chiyani zoswekasweka mwalembazi?? Kuzolowera kudzola penti basi..
kkkkkk kma zoonad aaa,,,english yosasathika yokhayokha…
kodi ndichiyankhulo chanji chimenechi
sukulu munathawilanji a mapuya kkkkkkkkk
hahahaha koma2 izizi izi 2018 zisalowe
Komatu ati anali ku Chanco….smh
Mr. Owen pls next time write chilomwe otherwise hmmmmm
Kkkkkkkk sukulu izo , zapa malawi
Are you sure you were at chanco bro?
Hahahahahahaha! I’m enjoyin ths guy’z comment. I jst cnt stop laughin @ hiz deformed english… Man’wa di anali pa Chanco
Hahahahahahaha! I’m enjoyin ths guy’z comment. I jst cnt stop laughin @ hiz deformed english… Man’wa di anali pa Chanco
Paja mbendera uja amkalengeza za chisankho kwinaku akulira inu adpp alikuti?……..
Akuti #Daus Ndimwana, Hahahaha! Bombastic Words My Foot.
osagwa phwayi madala…..mtima ofuna kulemba chizungu mulinawo…limbikilani baxi ?????????
Hahahaha chizungu chakupetani a Ngalande??????????????
Nane dabwi chizungu my foot osangolemba chichewa bwa kllkkkkk dnt make mi laugh when am not in tha mood hhhhh chanco okhe
Nde DPP imeneyo kkkkkkkkkkk
Chichewa is the best
Mmmmmh english iyi ine my foot
Robert Mugabe left the group
Guys chakwera xangalimbe pa dpp akuchepa
Peter akuyenera kuba ndalama zambiri kuti onse a Chakwera amve kuwawa ngati tinamvera ife nthawi ya Joice ndi Bakili osakwiya ndi misonkho yatonse iyi kkkkkk
Auze anyapapiwa ati kwana umbava too much brove MCp KwAchaaaaaaaAAAaaaAA! !!
Ukuonekadi kuti anyapapi a MCP
Dpp kwawo ndikuba ,,,,tikufuna zinthu zisinthe muno chakwera yoeeeeeeeee
Azizakudulani makosi kusitha kwake mukufunako
Ntengo wautali sulila chikwangwni
Kunena zoona malawi ndidziko lomvetsa chisoni..anthu aba kupangitsa malawi kukhala dziko losauka kwambili padziko lapansi ndiye wina amvekele ndidzavotalebe mbavazi kuti zidzapitirize kuononga zoona? Ndipo anthu timakhala kunja kuno timakumana nazo,akati umachoka dziko lanji ? Ndiye umvekele malawi , palibe amene.amakupatsa ulemu..anthu amveke Malawi dziko losauka kwambili zimandimvetsa chisoni osanama kubadwila ku Malawi..kunena zoona sikadakhala yosauka tikadakhalandi anthu amaso mphenya.
Wakulu mukunena zanzeru anthu wenawa kumakula nkusaganiza,mwina kamba kosayenda
Ulibe nzeru iwe umabadwiranji kumalawi ngati Malawi inasauka inasauka ndi mbwiye wako kamuzu anathamangitsa azungu mofulumira
KAYE MMENE INACHITA POTIBELA MCP, KUTIPHASO KUPHA KOPANDA CHISONI. NDALAMA AMANGOBA OPANDA OWATSUTSA MUFUNA MUNAMIZE NDANI ZOPUSAZO. TINACHOTSA MCP NGATI TIKUCHOTSA CHIPANI CHAZUNGU.
Dpp matako agalu
Amene akupangisa ndinu amitchona
Ine paizeeee ! Marandi anga mthumba kkkkkkkkkkkkkkk
Kkkkkk koma abusa ang’ombewa ativuta eti
I surely believe Chakwela will be the president this us not prediction but fact. . My vote. . Dpp my foot
Iwe chakwera usiye kulota ndi iweo wava zot uzawina..m’busa wa chinyengo ngat iwe ukuganiza ngat tingazakuvotele ifeo,,ufuna usokoneze Malawi y??A bambo opanda Nzeru inu ndithu,Ana anu mumauza za nzeru kma?.fake pastor ngat ukuganiz zot uwina uyiwale
Tseka pakamwa iwe.
Tseka pakamwa iwe.
Iweso tseka pa kwamwa ozavota siweo wekha ay
AKUlu thnk wise b4 u talk hw many ppo dey r crying due 2ptrs rigim? if ur enaf 4wat pter is doing god be with u thanks.
Bingu ndinu nomwe mukat sali bwino,bakili mukat sali bwino,Joyce banda mukati sali bwino even kamuzu mukatelo nde mukufuna chan ndi kusayamika kwanuko…mukufuna Chan nde muzeni yesu abwele azalamulire bcz is perfect
Pastor ofoira ndale akuchepa nazo …..abwerere akawete nkhosa zamulungu
iiii!komatu zinazi abale,bola kungowelenga basi nkusiya.
Nkhosa Zake Nde Zamisalatu Zowetedwa Nd Chakwerazo Komanso Zazmuna Zokhazokha Zot Cant B Multiplied Sure.
sometimes if think this person deserve to go to mentor hospital not wandale. He seem to be confused and lack focus. please court exchange him with wandale
ok but ovutika ndife amene tili kumudzi
Do you Think that Reverend Chakwela can be state president His excellence Chakwela,i doubt, i doubt, i doubt, anyway he is a president at party level, Malawians? Malawians?do you think Mcp can produce results in an election to elevate Reverend L Chakwela to be state president? I’m deeply concerned about comments of staunch Mcp diehards predicting that Mcp boma to 2019, this mcp of Reverend L Chakwela is a last kick of dying horse mfundo mulibe kwa ntukwana basi za zii
M C P Yonse Isamalote Zakulamula Amalaw,enough Is Enough Kudakwana.
Munya manyi simunati
Chakwera mo moto
chakwera moto kuti buu,kodi peter fundo alinazo,kkkkkkkkkkkkkkk samatha ndikuyankhura ndiwe wakundatha eti
DPP singawine.
#Chakwera moto kut buuu, a DPP munya muona 2019 muchita kuphwisa kut mtiii.
mbuzi yambusa iyi yoba madzi Mcp inaiwamo chiyani mboma kkkkk ambusa asatana awa
Chakwera woyeeeee
Ndipo mukunama siufumu ndizosithana izi muzapanga manyazi ndani amaziwa kuti UDF izatha amalawi enatu simakape oti akuona DPP ikuonanga kumati ndizaivotela kuganiza mopusa malawi ndi watose anthu akonnda chakwela
Griffin Mwale ngati DPP singawine nde mmalawi muno sitizakhala ndi chipani cholamula 2019?
Ine ndi banja langa lonse tizavotela DPP
Chakwela 2019 basi…alamula ameneyo…..peter wachaninso apa watikwana
Mwati Chakwera Alibe Mfundo? Koma Ndani Alindifundo? Kkkkkk Ndiwe Cadet Ndakuona
Dpp mbava zokhazokha.zasaukitsa dziko no chance for dpp
koma anthu ena mumandidabwitsa Mabvuto Ali mbweee wina nkumatchula Kuti Peter azawina?Magesi pano azima kale anthu simene akubvutikiramu ndima business nde wina aziti Dpp Za ziii
Akatundu DPP
Chakwera yemweyooo kuti wa!wa!wa!
Kodi anthu mukuti DPP yisaukisa Malawi kkkkk MCP Nde izalemelese Malawi?if so y not for the past 30 years?
Sizodabwitsa Dziko Ndichoncho Anthu Ena Amatenga Manyi Nkumati Ndiabwino Pomwe Enafe Manyi Kwawo Nku Thoyaz. WHERE DO U BELONG TO???
#Pilirani monga anaphwisira pa by election asiyeni adzamva nkhwangwa iri mmutu ati kugula Uladi Musa ngati samudziwa eeh! satana mutuojadaa!
Wekha ukuyidziwa bwino bwino kuti DPP inawina isakulamulila pano ndiye ili mboma MCP imalila kuti yabeledwa nayo PP imalilaso pano ndiye mudzalilaso
Malawi ndiyatonse moti mukamati chakwela saxawina hahaha musasapote coz ndinu mwina ndinu achilomwe ayi koma munthuyo sangawine ntaa
PETER 2019 bomanso
#Charlotte munayamba mwaganizapo kuti Malawi ankaoneka bwanji mu 1964?
Achakwera udzawina mmmmh zokaikitsa,sindikukhulupirila kaya mwina akalimbikira kusala kudya 2018 yonsei….matama too much ambusawa bolaso Tembo ndithu
panopa i hate DPP bt i cant vote for MCP……ndiganiza bohboh 2018 yi but ndili sure kuti mu2018 dpp indipanga convince ndpo mu 2019 izandpangitsa kut ndiivotele.
Mcp mbola,dpp ikungodya ndalama zamagetsi ndikumatikhazika mumdima kumangokhalira kugona kuchigayo.kaya chisakho changa ndichidziwa thawi yakampeni??
Ask Gwanda Chakwamba, ask John Tembo! Boma siliphetila! Dpp 2019 bomaaaa!
kutengela ma comments onse ali apa DPP yawina
Kuetereko mavuto mmalawi muno sazatha tizaone ngati Chakwela chanucho chikazakhala pa mpando mavuto angazathe ZACHAMBA ETI!!! ??
U tel us then.so since then nothing has changed?at oswel??anyway…peoples votes r in their hearts..MCP leader should stop ndale zapakamwa we Neva know why will win,let him not critisize the one leading nw..we Neva know who Malawians will vote for……
Koma mataya Chakwera sangafanane ndichinkhalambachi uyu Ndiye lamukanika.
Cadet cadet cadet uzafa nd mtma osamazrimbtsa mtma zabodza mcp ikuopsaaaa…
Makape opanda chochita ndi amene akulimbikila kumanena kuti dpp boma Mmene malawi akuwawila munthu kumati boma Dpp anthu akuvutila ndi kuthima kwa magetsi Mzipatala makhwala mulibe anthu opusa mwapanga bwanji Asawona akuyeliko
||Bwampini opanda mano mkamwa uja angadzawine ? wachita chani chanzeru? Kodi mumamukonda chifukwa ndiwakwanu olo atamangogona …………………………………………………mudzamuvotelabe ? nzeru alibe a Peter Thalika
Kma Ngat Kul Mbuz Ya Mbuz Zonse Ndie Ndiuyu Akut M’busa Wakugwayu Kaya Amat Chatsika,asamadznamize Zodzatenga Boma And Rule Millions Ov Malawiwans Yet Hav Got Family And Friends And Only Thousands Members.Analakwtsa Kusiya Utumik Ndkulowa Mcp,mwna Anakalowa Udf Kapena Chna Chilichose Anakakhala Nd 40%posbility Yodzawna But Mcp Yokhayo Ladies And Gentlemen Lets Get Ready Dancing To The Truck Called #atiberamavoti.Mcp Means Harsh Leadershp To Millions Malawiwans In Togetherness Regardles Ov Their Parties.
Ask ur friends chakwera chingawine? iyi ndiye mbuzi yosadziwa chomwe ikupanga! yamtopola tiyeko zibwera uziona ife sitimavota chifukwa cha kutchuka ukhala pansi 2019 uwona!
umakwana Alex….Only a mad person can vote for chakwera
Ena mpaka mukulankhula mwaukali nkhani take yomweyi ya anthu andaleyi eeeee koma amakulipolanidi atsogoleliwadi chonde tonse ndi amalawi tisaphsyelane mtima andale asamakudanitseni amakunatu anthu amenewa mkuma gawilana Magalasi a win chonsecho winawe ukudzala nkhwizi ndi nzako kaya mzanu izoo
amene safunira malawi zabwino go a heard ndi mbava zanuzo koma ambuye akukhululukira kwambiri pakuti maso anu ali akhungu
usatchule zina la a MBUYE pa chabe. chekwera ndkachaniso iwe ife sidalira politics mfana koma ameneyu ine nde sindngamvotere chakwera wakoyo
Ngati pali munthu wogona ndye yemwe akusapota A chakwera mbudzi yamunthu
I can’t vote for mbava party, like maize-gate, MSB-gate, 236 billion-gate, Escom-gate, sofa-gate, and I can’t vote for murders like Chasowa and Issa Njaunji
Hahaha!!! hahaha!!Chasowa ndi Njaunji aimanso!!!
Ifenso monga a DPP sitingavotere ng’ona party.nyakula kulanda katundu.pioneer.youthleague okupha AGadama matenje chiwanga sangala chisiza.chipembere.mphakata.kanyama .Gwede Muwalo etc ukunama tu iwe MCP nkhanza nzosayamba mphwanga sitingabwerere mbuyo
That was kamuzu and your uncle’s people like Dausi Ntaba. Ndipo zosadabeitsa kuti mbwampini akumpha athu. Koma Chakwera ndi azake alibe magazi athu.
Gama Phiri I Unayiwala anthu 21 anaphedwa ndi dpp pa 20 July Nanga mwana waku Luana waphedwa dzanali?
ngo’na mwini wake ndi Dausi ndi Ntaba pls make research bobo, iweso ukudziwa kale and pano mbava/amilandu zikulowa dpp pamene anthu abobo akulowa mcp
Phiri and Thoko muthu sadziwa chilichose imagine anthu 21 kupha pano mwapha student ku Bunda ohoooo chipani chatsoka ngati dpp sindinachione
if you hear h/her akuvomera kuti chawo ndichakuba ndipo ngakhale chili chambava koma sangabwere m’mbuyo sinanga amadya nawo
Hahahaha… Gama, MCP Inaapha Aja Anauka?
Hahahaha… Gama, MCP Inaapha Aja Anauka?
#Gama ku bunda wapha ndi peter?? what happen kut afee?? …… shupit mind like #Gama
Anali ana amenewo iwe wabadwa liti Kodi ?
@Lium ask Dausi and Ntaba these two guys they are responsible for that not our new MCP, pamene anthu 21 peter anali mu dpp, Njaunji ndiye magazi ali mmanja mwake @Chande kuti mwana amwalire anawatuma a police ndani and wavapo kuti Bwampini wanu wayakhula za Infa imeneyi?
iwe Kaliati mutu wako umayendeya madzi amanyi aku 18 eti? Dausi ndi ntaba anali mwana? if Dausi anali mwana ndiye tell me amene ali ku mcp pano analipo thawi imeneyo
MCP ili bho very clean
kkkkkk mad pple could say mcp izawina…but based on our criteria (ife an2 akumwera …sitingavote mcp olo zitavuta…we better go for chisi.. KOMA NA MCP….till death sinzaikondako
Chakwera paka kulamula kaya musapange matama ovota tilipheer
Vincent wandale 2019 bomaaaa!!
Pakut Zlingat Mpira,every one Say Iwl Be The Wner Yet Akudziwa Kt Sawna Akungofuna Kupeza High Molalo.Sndkudabwa Nd Aliyese Amene Akt Chakwera Adzawina Coz Iknow The Song Which U Wl Sing.Its Yomweija Ya”atibera Mavoti Awerengedweso”,if U R Wise N Clever Enough,make A plan.
Wina amva mimba ndi Chakwera
Kkkkkk a chakwera akulota maloto a shumba.
Kamuzu analamulila zaka 27 or kwawo kunalibe nseu wa tala ndiye chakwela akulimbana ndi Peter oti or zaka 5 sizinathe ndiye kupanda wiseko. Chakwala anzako akumalemela ndi ubusa iwe zinakukanika kuganiza zilowa ndale walemba mmadzi basi munthu otembeledwa iwe usamawaputsitse fans apapa palibe chomwe uzapange pa Malawi wina iweyo uzizangothyolele nthumba basi coz iweyo uli after money
kk Kamuzu brae sanali mmalawi kk fufuza bobo thats why kumene ankangopanga claaim kut ndikwao kulibe chitukuko lol
I agree with you bro kamuzu anali foreigner but still ena mpakana pano samadziwabe kkkkk
Afumbi kupusa ndiye kukukambitsani nyasi yinu ngati mwawoma kuti anthu akukulemela ndubusa yinu mwanji wosayamba wubusawo kuti nanu mulemele musiyeni chakwela man
Kkkk a Chakwera ndi mwanadi pandale, zoona iwo angasewere ndi DPP?
Mmmmmm
Mmmmmm
Chikwera chichani
Amalawi singaiwale nkhaza za mcp zachamba eti chakwera ndi opusa
ife tili nganganga pambuyo pa bushiri man of God 2019 Boooomaaa
Mbuli iweeee YOU think amalawi ngatulo ngati ana ako!!!
Mbuzi amaiti chakwera iyi?manu kunsi!!
zopusa zenzen..
Things that must be left in 2017,,,Dpp, malawi24, blackout, flames, skin jean, we don’t need this in 2018.
Mwaononga chilengedwe, komanso Ku escom kuli a MCP nkumati zithu ziyenda bwanji mukulowetsa dale pa chitukuko cha dziko lanu lomwe and omwe akuvutika si a DPP koma dziko lonse muzinganiza popanga zithu zina
MCP ndiye inasala kale mu 1994 inavundira konko pano
Kkkkkkkkkkkk thank u guys
Ai bola mulungu atipatsebe moyo tione zomwe chakwera akunenazi, ndipo tidzankhulupirira pa nthawiyo ndithuuuu
/come on chakwela mtundu was amalawi ukudalila inuyo 2019,
Do my comments show that am sending them from my new Samsung S8?
KKKK KOMA IWE ABITI! Kkkk
KKKKK Ya it show’s waitha
Kkkkkkkkk koma nawe
Hudson Chiwaya glad to hear dat
ya zvimotaridza
It’s not new anymore its several months old
ikuonesa huwei p8 kkkkkkk
Hahaha try my S8+
CHAKWELA CHAKWELA NDIYE CHIYANI, 2019 ADZAKHALA CHATSIKA SI DPP YOMWEYI NAYO INALI PA OPOSITION KU PP?? INAKUSIYA PA BENCH YA OPOSITION CHIFUKWA CHIYANI KKKKKK, MPAKA AMAI KUTHAWA PA MALAWI KUMUTHA PETER.
muuzeni asiye kuganizadi zimenez peturoyo watisaukitsa koopsa dpp ndiyazitsilu ndimmene zinthu zilimu wina mkumakamba zautsilu kukometsa dpp
Zitsiru ndi za Mcp including Chakwera chifukwa amaganiza zosatheka zokhazokha.Mcp yake iti? Yomweyi yopanda nzeruyi?.
Chitsilu Iweyo kapito pamodzi chinkhalamba chakocho chopnda mano mkamwacho.
or mumuwelu palibe kumusiya pitala wanuy
Kape iwe unaliko mmene anthu amawaponya mudziwe la ng’ona iwe?ungoti mcp woyee yachani kupepela basi
kape benard ndizakale kulibe maufulu pano sizingachitike
Azazivotera yekha kod chakwerayo?
I WILL VOTE
I’ll vote for him..
Chakwera awkward in mind
It’s you, you’re awkward
Let’s wait and see who will be awkward in 2019
Kkkkkk akuona ngati azatenga boma after kuwina 5-1 ayiwale
Yes
Cholemphetsa ndichiyani?
ngat uli Mmalawi weni weni cholephelesa ukuchiziwa if you dont know John Tembo is still ruling under Chakwera n MCP sizasntha or pang’ono Lets wait n see 2019
Tingoti pheeer! tionele
Kma chakwera ngosekesa bwanji kkkkkkkkk
Ndipo azisosole mbava zimenezi
Ur dreaming a lot, let’s wait 2019 is short n we will judge
Ndipo or tavota mawa Dpp ikuchoka
Wanena Ulere,DPP ndiye bomalo!
Kkkkk boma 5 kwa 1
achakwela asathe mau 2019 patali.a Peter athakukoza zithu kuzawinatso.zikakha la zamavuto analipo kale
Asiya kuba mkukoza zithu
Mbava singasiye kuba
Akudziwa kuti 2019 ayima komaliza mutu ukumuwawa Yona.
Aah chakwera akuyilakhulira kwa mbiri zowinira pakamwa zinatha
Koma kuwinila kuba
Inu osaba bwanji
Kkkkkkk koma guyz
Nde ngati tinabera tinsali mu boma nde 2019 muliratu kkkkkkkkkk
MCP will make Malawi a better place. Let’s be part of that change. Come 2019 let’s vote for these guys. No more BLUE #BORN_and_LIVE_UNDER_EVIL.
Maloto a chumba awa
Multiparty ndi Nkhondo anatelo mutsogoleri wa MCP Dr Hastings Kamuzu Banda ndiye musiyeni ayang’anira kaye Nkhondoyo ibwere p amene adzalowe Iye. Be Spector Ion first.
MCP? my foot
Better place it ruined the country already for 30yrs so no to MCP bra
Anthu a Dpp muli ndi maso koma simukuwona momwe anthu alili pa mbuyo pa chakwela
Temunena kaliati ameneyu ndimodzo aba ndalama zaboma pamodzi ndi chaponda mchifukwa chake athuatamakamba za mcp amalira.
I can see Chakwela on the lead.
udzanenanso kuti ATIBERA…KKKKKK
Uchitsilu saitanilana inuyo muzavotele zimenezo man,ife ayi,kuvotela mcp nchimodzimodzi kunyela nkudya wekha manyiwo.
Since wen did MCP change Malawi?
Kkkkkkk. Ukufunika Ku St. John of God
Kkkkkkk. Ukufunika Ku St. John of God
Am here till 2019
koma chakwera eesh! wa DPP azipya mtima
DPP ili pa front seat,
Who is #Chakwera please!? some1 can help me to identify #Chakwera in politics.
ndiwe okanika umava ndimakofi siwamudziwa petulo kamba kama blackout ndizina zautsilu ndiemkumudziwa chakwela?
let him keep on daydreaming under blackouts,will know Chakwela once blackouts will be history one day
lets wait 2019 hahahah
I am sure u live somewhere in Jupiter, Pluto or Neptune.
Mwati simuwadziwa chakwera bwana tho, chakwera ndi uyu adakuphufumulani 5_1. mubonaza anachititsa amec ija
Hahahaha are sure mr man u dont know Dr chakwela?.
Hahahaha are sure mr man u dont know Dr chakwela?.
Zimbabweans yes don’t know chakwera
Zowona Chakwera sakunama nanga muthu umangokhalila kuti kamuzu sadayike magetsi amphavu koma iyeyo ndi mtsogoreri Iweyo tayika asamango blema muthu amene adalamulila zaka 24 zapita.
hahaha opposition yakumalawi ndiyouma mitu look at south African opposition achina Malema sakukamba za zisankho koma kulondoloza kuti ma program a boma akuyenda bwanji Komanso a boma akapanga ziphuphu achina Malema akuyesesa kuti ayimbidwe mlandu shame Chakwela ndiwe olephela pamodzi ndi mzako Peter kukhalila kukangana zaii.nawe Malawi 24 ukati ulembe nkhani yimakhala ya ndale ndiwe olephela kuli GCK CAMERA KU MALAWI WANTHU mwana akulemba nkhani mbali zonse wakuposani ndithu .kubadwa musanga sikuwona fisi koma kuyenda utsiku GCK CAMERA yili bho nkhani kathithi osati kukhalila Kkulemba za ndale asaa
Julius Malema wake uti man musanamize anthu apa palibe chkusiyanapo apa opposition kwao ndkususa boma bas olo litakhala kut likupanga zolondola a chna malema ukunenawo ndye mbuz za anthu zenizen
ngati umadzisata bhobho za mlandu wa Zuma Komanso Gupta family ndati anasokola zinthu kuti ziziwike?
koma sizoti wuzinama kuti achina Malema amasekelela boma wukunama
Malema kulondoloza za boma ( ANC)? mukunama man, malema ndi zuma sapanga zofanana. Andale ndimene aliri kulikonse ndi choncho basi
Ma Group Ndionse Koma Kolite Ya Group loooo #MALAWI_WATHU Ili Ndi Group Lokhalo Lomwe Kukumakhara Nkhani Zasopano Zomwe Zachitika Kumalawi Ili Ndi Group Lomwe Kulibe Zonyozerama Mitundu Olo Zipembezo Ku Group li Tikumachezako Bwino Bwino Kuphatikizanso Apo Tikumapasirana Nkhani Zosiyana Siyana Zomwe Zachitila Kumalawi Funso Mkumatu “Kodi Munajoina Kalee???” So Ngati Simunajoine Mukudikirira Chani??? Tangopangani Search MALAWI WATHU Mukatelo Mupange Join Kuti Nanunso Muzilinjoya Group li #Malawi_Wanga #Malawi_Wako
Nonse majaba anu , kusiya kusova zaumphawi wanu muli busy kukangana pa zandale ? Kkkkkkkkkkkkkkk zokhalira zanu nonse .
Kkkk shit
KAYE KUSAMBWADZA NGATI ANAYAMBA WALAMULILAPO DZIKO MBUZI YACHABE CHABE. INE SINDINAMVEKO CHILOWELENI UDINDO KUPI MTSOGOLELI WA MCP WAPELEKAKO NGAKHALE NJINGA KU POLICE KAYA KU CHIPATALA NGATI MPHATSO, KAPENA KUMANGAKO KA BRIDGE KAMATABWA NGATI CHITUKUKO. CHITUKUKO CHAKE KUMANGOMVA ZOTI WASAMBWADZA BOMA LOLAMULA ZAZIII SITIMATU IMAPHWEKA AKAMAYENDETSA WINA.
Aaaa Jafali Iwesiwedi M’malawi Waiwalakale Nthawiija Amalawi Ku Lilongwe Amamwa Madziwosakanikilana Ndichimbudzi Munthuwoyamba Kukawatulukila Adalindani Tandikumbutsa
NDIYE ANAKUUZA KUTI ANAPANGITSA NDI PETER KAPENA BOMA LA DPP. VUTO LA AMALAWI MUMATI KUNYELA MMBALI MWA NJILA MANYI MKUMALOZA MUNTHU WINA CHIFUKWA CHA UDANI OMWE MULINAWO NDI MUNTHUYO. IWE INE SINDINABADWE DZULO NAINABADWA ZAKA 4 TITANGOLANDILA UFULU ODZILAMULILA 1964. PALIBE CHACHILENDO UNGANDIUZE ZA MCP AI.
Go Deeper Wa chakwera Adzipsamtima Zenzen
MUNTHU KUKASIYA ZA MULUNGU KUKALOWA NDALE MKUMATI NDIDZAWINA MULUNGU ANAMUFULATILA LELO MUNTHU WA MULUNGU KUYAMBA KUTUKWANA PALI MZELU??
Thus the problem Malawians have.. Wins atha kupha make kutengera zawo zidani…u will hear its peter kkkkk like serious?we can solve some matters tokha…amcp akamufunse job 2014 vite is in the heart.mukazaluza muzizati maviti aberebwa yet munayiwaka kuti simukhalako ndi munthu kovotako
Chakwera is just onother result pf unprotected sex.The guy talk too much as if we don’t know MCP
more especially u
Munayi dziwira kuti MCP kumaloto
Stop responding to peoples comments bro this has absolutely nothing to do with unless ur mind is upside down then u will respond again
Ngati yabwera pagulu athu ayenera kupanga respond.
he is mad
Mcp Unaiziwila Kuti Iwe? How Old Are U? Wasowa Zolemba Eti! Ukukanaso Anthu Kuti Asamayankhe Pa Coment Yako Chifukwa? Ukuziwa Kale Kuti Walemba Mbwelera
kkkkkk…wabooleza..kkkkk..paja ndiiwe prophert ndani? kkkkkk
u mean was born on protected sex how?
Kkkkk koma abale, the result of “unprotected sex”?????
100% In agreement wth Riaz.
100% In agreement wth Riaz.
Unprotected sex yemweyo ???????
Koma kuyankhula mwauchitsiru chonchi kungoonetsa kuti inu Munabadwa mu Uhule ndi mai anu! Kunyoza kotani kumeneko? Chakwera wakulakwirani chani? Mukutiuza kuti Muthalika anabadwa as a result of POTECTED SEX? Ndinu chitsiru chamunthu. Khala ndi umunthu, ndi pagulu apa iwe nkhomako!
Musanamizane mukachita makani mudzaona za pp iri boma kumaputhidwa zida zobeta zili manja,ndipo dpp idzaona zomwezo
loading…
Wamwa vinyo wambiri ameneyo mutu sukugwila
An empty tin make lot of noise
A toothless heap makes a lot of jealousy!!
mmene wakalambira ndalaviwe sungasapote chipani cha mu democracy koma mcp yomweyo imakukhala
Watchng
Akunena zoona