Chakwera asambwadza a Mutharika: Ndikusosola nthenga mu 2019

Advertisement
Lazarus Chakwera and Peter Mutharika

Msogoleri wa chipani cha Kongolesi, m’busa Lazarus Chakwera, wasambwadza Pulezideti wa dziko lino, Pulofesa Peter Mutharika, kuti asiye kuloto zoti n’kudzapambana pa chisankho chapatatu chomwe chichitike mu chaka cha 2019.

M’busa Chakwera audza a Mutharika zoti adzagululidwa mano, kuchotsedwa nthenga ndikusiyidwa ali zoli ngati nkhuku ya chitopa.

Lazarus Chakwera and Peter Mutharika
Chakwera: ukuopa chani?

A Chakwera anati ndi onyangala ndi mzuzulo omwe a Mutharika ananena oti zipani zotsutsa zikufuna kulanda boma mwaupandu kudzera mu ndondomeko yavotera ya fifite pulasi wani (50%+1). A Chakwera anati ili ndibodza la mkunkhuniza.

“A Mutharika athiridwa mphepo ma chaka mu 2019. Iwo asiye kuloto zoti pali wina akufuna kuwalanda boma mwa upandu. Bomali titengadi, koma titawathibula muzisankho zomwe zichitike mu chaka cha 2019” anayankhula mwamangolomera a busa a Chakwera.

Azipani zotsutsa ndinso othandiza dziko lino akhala akufuna kusintha njira yomwe amalawi amasankhira pulezidenti. Koma ndondomekoyi inakanidwa ndi a phungu kunyumba ya malamulu ku Lilongwe.

Advertisement

413 Comments

 1. Dzikoli lizingolamulidwa ndi zi anthu zosaziwika bwino ndithu ati aPetala,aChakwera oti mu History mulibe uuu Malawi

 2. iwe chakwela ndi chipani chako chakhaxacho pitanacho kumanda kt mwina mixukwa ikaku votele kma ife amalawi takana kaye mutu ngati Bomu loxala pansi..

 3. iwe chakwela ndi chipani chako chakhaxacho pitanacho kumanda kt mwina mixukwa ikaku votele kma ife amalawi takana kaye dadxi…..

 4. Chakwera sangawine ndikuti! ngati ukuyaka wauwisi nde mungasongezere wouma? nzeru mulibe mmutu! come 2019 mudzandivomereza ife sitivota chifukwa chotchuka mayazi 2019chakwera will fall down and down pamenepa nde adzadziwe chabwino ndi choipa ife sitifuna munthu wa Nsanje,Mtopola,Mwano, & Kuzipopa akhala pansi ameneyu azakeso ankatero koma iyeyu anali asanabadwe nthawi imeneyo kkkkkkkkkkkkkkk Malawi woyeeeeweeeeeeee!!!!!!!!!!

 5. Iyeyo akunena bwanji choncho ngati kuti amavota yekha? Nanga tonse amene timavota titati tisakavote angachite matama amenewa. Ngati ndi kusambwadzana ,akasambwadzilana kwina osati kuno, ife tidzavotera chimanga chomwecho, chifukwa ndiye moyo. Ngakhalenso tambala wakudayo kuti akhale ndi moyo amafunika atole chimanga chomwecho. Vuto lilikwathu kuno ,azitsogoleli amakanganilana pa mpando cholinga azibapo ndalama. Ngati iwo ali ndi fundo zotukula anthu ndibwino azibweletse poyela mothandizana ndi boma cholinga choti miyoyo ya anthu itukuke. Tangoganizani kadziko kathu ndikakang’ono kwambiri, koma boma likulephela kuyika magetsi m’mizinda ndi m’midzi, nanga limalandila zithandizo kuchoka maiko osiyanasiyana ndalamazo zimapita kuti.?

 6. no more mutharica kingdom.chakwera is indeed correct.apm is too old for presidency,clueless to problem resolution,will struggle for runningmate,habouring chaponda a big fish,5 to 1 loss prophesy downfall of dpp

 7. Koma let’s be serious guys ena we are just commenting we don’t know wat z happening on the ground like how our economy is driven… don’t vote for fools pliz pliz ….professor dzina lokha palibe akuchidziwa

 8. Mbuzi yamunthu ngat chaska singawne dziko,Ubwino wake amamvotera ndi atumbuka Anzakewo,Mumuudze kut iye ndianxakewo chipani chawo ndimavampaya mbuzi za anthu fk u chasika.

 9. Linda madzi apite ndiye udziti wadale, Sibwino kumatukwana ng’ona iwe uli mnyanja ili ndi dziko mukadzitukumula Mulunga adzakusisani baibulo limatero

 10. Forget Dpp no intelligent person can vote for Dpp family party zipani zopasana pa chibale ngati ufumu unless malawi want to become a kingdom kkkkkkkk rotten party

 11. May I know your school of thought you praising chakwera,on what ground are you judging chakwera as a better performer since he has not been a state President,mind you theory is not practical, chakwera is talking much on theory. I find it meaningless to compare a party President and a state president because the too play different roles

 12. Kodi ndi liti limene MCP idanenapo kuti idzaluza masankho? Kuyambira 1994 kufikira lero MCP imati tidzawina bwerani masankho kuyambira 1994 kumangoluza,ndiye pano muti chiyani,m’ busa wa fake iwe

 13. BOla kupatsa achakwela mavot kusiyana ndi mzika yaku USA,Ndicifukwa akutizuza siwakuno mulungu akuwona zosezi awonatu!!

 14. Dziko lathu silikuyenda bwino ndipo silidzayendaso bwino olo pang’ono. Chikondi ndi chomwe chikusoweka pakati pathu. Kodi ngati wina ulamuliro wake sukuyenda bwino bwanji inu otsutsa osabwerapo ndi mfundo zabwino zothandiza kutukula dziko lathuli? Taonani mmalo mwake mukungobwera ndi kulalata, kutukwana, kunyoza etc. Ndi zoona ndithu kuti mdziko muno tili ndi mavuto ambiri omwe chipani chimodzi sichingathe kuthetsa mavutowa pokhapokha zipani zonse zitakhala pansi ndikumanga mfundo imodzi kusiyana ndi kumangonyozana basi. Dziko ngati silikuyenda bwino, ndi udindo wanu ndithu inu otsutsa kukambirana mwachikondi ndi omwe akulamula momwe mungathetsere mavutowa osati zomangolalatazi ayi. Dziwani ichi kuti dzikoli anthufe tikusowekera chikondi chifukwa nawoso olamula akumva kuwawa ngati inu otsutsa mukungotukwana ndi kulalata and zotsatila zake inu mukadzatenga boma zidzaonekaso ngati ndinu olephera chifukwa simudzapezamo ndalama m’boma zoyendetsera dzikoli chifukwa olamulawa adzaziba ndi cholinga choti iwo asadzanyozeke. Aliyense amene akufuna mpando umenewu ayembekezere kukumana ndi zokhoma chifukwa olamula pochoka adzatenga ndalama zonse. Chikondi ku mipando chasoweka ndiye panoso zatsikira ku ife anthu. Akuluakulu akungotukwaniza mmalo momanga mfundo imodzi, ifenso anthu wamba tabalalika kusowa kolowera mapeto ake za ndale zomwezi tayambaso kumatukwanizana kudzera mma comment athu. CHIKONDI CHATHU CHAPITA KUTI AMALAWI!

 15. Maloto achumba ndiye DPP. Kumalota ngati apereka mimba. DPP is now almost water under the bridge. Ndani gonthi amene adzavotere chipani chambabva, cbakupa,chotukwana. We”re counting down towards 2019.,muone momwe dziko litenthere. Anthu akuvutika ndi DPP and bwampini wao. DPP ithangati makhatani. No matter how lalatafulu u may be, u’re just fishing in the dry river.> MCP 2019 bomaaaaaaaaa!

  1. ukuvutika ndiwe….dont think an2 akumwera and kumpoto tingavotere chakwera…..stop dreaming…. olo Peter atakhala kuti wafika pa worse….. we love our president…. chakwera is a goat….ofunika kungomangilira pa mtengo

 16. Ma Kadeti pano afatsa kulongolora kunyoza a Chakwera! Atawatibula pa by elections anangoti ziiiii gada kukamwa yasa! Uja wakudedza councillor atawina pa DPP, only after 3 days he went to MCP! Taonani, Chakwera 6 Gogo Mtchona chopanda many 0 ! Kkkkkk NDE lero mukunyoza Chakwera okutibulani uja! Amvekele Chakwera sangakhale President was Malawi, sure? DPP followers are funny idiots!! Kupanda nzeru zoonera! Afro Barometer yinati chani! Lero mwaziona? Keep on supporting Thieves and Failures! Kupanda umunthu!!!!

 17. Chakwera Akuchita Matama A Ng’ombe Onyera Choyima! Kapena Ngati Chule Odumpha Popanda Zenje, Kodi Mwati Adalidi M’busa Ameneyu?

 18. Ino sinthawi yoti mudzitukwanizana koma kuona kuti Malawi wanthu timukoza bwanji kuti akhale wakaka ndi uchi owina sakudziwa apa nonse ngolephera patsani ena akoze Malawi kkkkkkk

 19. Ino sinthawi yoti mudzitukwanizana koma kuona kuti Malawi wanthu timukoza bwanji kuti akhale wakaka ndi uchi owina sakudziwa apa nonse ngolephera patsani ena akoze Malawi kkkkkkk

 20. Basi tikhalira zongosambwazanizi??? Remember, mmene mukusambwazanamo ukuvutike ndi udzu not you coz kumbali mukumakumana nkumagulirananso ma fanta

 21. Unprofessional journalism,this news headline can bring anger,confusion,fear,enemity among the general public.The reporter shows the side of the story at which she/he belongs.

 22. Achakwelawo ndiye ndani? ngati zikumuvuta peter palibe mene angadzatenge malawi ndikuyenda bwino guyz kuti tilimbane ndiboma tizingotaya nthawiyathu pachabe lucias anayimba kale kut takumana okhaokha akuba inuso mukufuna muzizatibela misonkho yanthu amene kunalembedwa kuti azasankhidwa kuti abeleanthu pamalawi ndiamenewa jb bwanji sanabe?siuyuaangodyelele

 23. Achakwelawo ndiye ndani? ngati zikumuvuta peter palibe mene angadzatenge malawi ndikuyenda bwino guyz kuti tilimbane ndiboma tizingotaya nthawiyathu pachabe lucias anayimba kale kut takumana okhaokha akuba inuso mukufuna muzizatibela misonkho yanthu amene kunalembedwa kuti azasankhidwa kuti abeleanthu pamalawi ndiamenewa jb bwanji sanabe?siuyuaangodyelele

 24. Chakwera bwezid atazawina koma mmmm wayamba kundikaikixa too much kuwawatawawata,zikuchita kuonekeratu kut first term yake siizakhala yopanga chitukuko ai koma kulimbana ndi kumanga onse omwe akuxogolera DPP panopawa

 25. ooooooooooohh zosakhara bwino pomwe panalakwa ndi poti mtsikanayo analetsa ekha ndiye zinafunikakumuguliraaaa galimotoyo mpamene afisi aja amagwira mbuzi basi ndangozindikira ndimalota

 26. Impossible dream, Chakwela alibe mfundo chimene amadziwa Iwo ndikunyoza mtsogoleri wadziko koma sadziwa kuchitapo kanthu koti nkuthandiza dziko lathuli.
  So it’s his freedom of expression but he must forget that he will rule this country

 27. Ma Group Ndionse Koma Kolite Ya Group loooo #MALAWI_WATHU Ili Ndi Group Lokhalo Lomwe Kukumakhara Nkhani Zasopano Zomwe Zachitika Kumalawi Ili Ndi Group Lomwe Kulibe Zonyozerama Mitundu Olo Zipembezo Ku Group li Tikumachezako Bwino Bwino Kuphatikizanso Apo Tikumapasirana Nkhani Zosiyana Siyana Zomwe Zachitila Kumalawi Funso Mkumatu “Kodi Munajoina Kalee???” So Ngati Simunajoine Mukudikirira Chani??? Tangopangani Search MALAWI WATHU Mukatelo Mupange Join Kuti Nanunso Muzilinjoya Group li #Malawi_Wanga #Malawi_Wako

 28. Ngatidi antadzavote yekha mmalo mwatosefe. Wayamba ndale za Muluzi eti zoti mufune musafune iiiiii leroso? Amavotatu ndi anthu a Chakwerawo asiye matama its too early to predict for that.

 29. I dream last nit ndikupita kopeza ndalama kuworkshop siiyo ndaitanidwa, dream come true if God say yes palibe munthu olengedwa ndiye angati no ,,,merry xmas abale nonse apa FB

 30. Ife Ovota Tikuvomelezaso Kuti Aiwale Za 2019 Tazunzika Mokwana Tizaone Zina Siufumu Kuti Mtundu Umozi Ndiumene Uzilamlira Simlakho Ilindiziko

 31. Siyani kudzinyenga ndi chala nokha malume…….. Boma la zunza azigogo athu limeneroro…….. Bola ndidzizunzika ndili mfulu not ndizisangalala opanda freedom

 32. Mgwilizano akupanga a DPP kumanyengelela tizipani Tina ameneo ndi mantha kuiopa MCP aludziwa MCP ndi chipani chaphamvu komanso chachikulu olo naye muntharika akudziwa zimenezo

 33. Ngati Chakwera/chatsikayo Akadzivotere Yekha Adzawina!Koma Ngati Ovota Ndi Anthu Akumidzi Asiye Kulota Zimenezo Akanakhala Oganiza Chatsika Sibwezi Akuima Pachulu.

 34. Mcp must forget the dream of wining 2019 election other wise they will sing the same story called: (atibela ) zileso kungoti zizavumbaso) swing person dosnt talk but this rubbish pastor is busy sweling the president oooo!! Akhalila yomweyo

 35. Inanu mungotokota zambili vote yanu kapasene omwe mufunayo DPP ulibe vuto koma pitala ndiye chakwela ngati ine aona athandiza asiyeni koma chakwela azawina ndimene waonela

 36. Voters are just quiet. what Hon. Chakwera who left the Temple but failed the 2014 elec has said is clear,and with their naked eyes pple’ve cn the curent mw state president P.A.P Mutharika’s works of his hands. COME 2O19 plz one to shade tears!!

 37. kunena zoona captain oyendesa sitimayi salibwo posatengera chipani chomwe tikusapota ! ndichani chodziwaka bwino chomwe angaloze wapanga pazaka zomwe wakhala pamupando? tisalole kukwera sitima imene oyendesa wake ndi wa blind oti zoti magetsi akuta iye sakuwo,zoti muli katangale sakuwo ena mpaka kumaotcha ma office oti anzawo anamanga bwinobwino,zoti amalawi tikukhala mwamantha sakuwona eg issa njaunju ,chasowa,bunda student , ma strike muma departiment abomawa ngamwezi uliwonse ,macampani ambiri asamuka muziko muno economy silibwino koma zonsezi capitani sakuziwona.nde tizipitirizabe kuombera mumanja munthu akulunjika nafe kuphompho ,kumyala ?AMALAWI NOOOOOOOOOO!!

 38. Kod iwe ukuti m’busa mtumiki wamlungu iwe ngat ukusiya kulabadira zamwini moyo uzalabadira zaife?mot utenge Bible uziyenda mmisasa mkuwauza anthu za ukulu wamulungu koma kunyoza anzako ndi 1 m’busa wanji ameneyu, shame on u.Mlungu azakukantha.

 39. A chakhwera mukanakhala kuti ndale mumatha, ino sikanakhala nthawi yosambwaza president ayi koma inali nthawi yoti muzikamba zomwe mungapange mutakhala president kut mavuto ali Dziko muno muzathana nawo bwanji ndiye anthu tikhutire ndi fundo zanuzo koma kumangoti ee 2019 suzawina mmmm mamuna zako pachulu amwene ndipo campaign director wanu sakukuthandizani bola mukanatenga inenso kkk

 40. Keep dreaming, after all. Dreams comes. When u go to bed with full stomache, kukhuta ma allowance amisonkho yathu,
  Iwe chakwerA olo zitavuta bwanji suzawina 2019, uzingokonzeka kukatenga injunction

 41. Mmmmmmm koma zikanakhala bwanji, ngati mmbusa munthu wa mulungu ozozedwa mukanazisiya zandalezi mkubwelela mmanja mwa mulungu bwanji, sakanawelengela zoti mwasusa zitukuko zingati mwalephelesa ma bill angati mwatukwana angati sakanawelengela zisiyeni mkasa anati ungoona kutha mau okwilila mnzake saziwika.

  1. Popeza Chilembwe, Kaleso Ndomondo, Dumbo Lemani anali akumwera nzowayeneleza Ku lowa ndale koma popeza Chakwara ngwa chigawo cha pakati nzosayenera? Mitu yanu yozungulirayo ikagwere uko! Upgrade ur oblangata to 6g pliz

 42. I think there is something in chakwera why akayakhula zithu boma limat ndwopenga ? hahahah wake up malaw it’s tym to change

 43. mukamati kusambwadza mukutanthauzanji a news 24? choncho ife tikayankha muziti adpp akunyoza eti? mukamuuze chakwerayo kuti iyeyo asamalote zotenga boma. musaiwale kuti : chakwera savomeleza kuti adaluza, APM atawina 2014 chakwera ankati wabeledwa. tsono adziwiretu kuti dpp sikubwera mocheza,

 44. Regardless any political affiliation. Am below 40yrs. At my youthful age ndikavotere Agogo a zaka 81 kukhala mtsogoleri wa dziko for my next 5yrs. What will I benefit on his leadership? Am I mad?

 45. Guyz don’t think like MCP it will be win no u must take example is it 10 or 20 tambala there are two elephant it impossible small elephant to big nothing so don’t waste u time to think like chakwela or MCP it gonna win

  1. Mwina mukadalemba chilomwe kapena chiyao anthu akadamva chomwe mukufuna kunena bwana. Nanga kungoti pa facebook pamakhala chizungu ndiye nkulemba kalongonda wanuyu? Timvapo chiyani zoswekasweka mwalembazi?? Kuzolowera kudzola penti basi..

  2. Hahahahahahaha! I’m enjoyin ths guy’z comment. I jst cnt stop laughin @ hiz deformed english… Man’wa di anali pa Chanco

  3. Hahahahahahaha! I’m enjoyin ths guy’z comment. I jst cnt stop laughin @ hiz deformed english… Man’wa di anali pa Chanco

 46. Peter akuyenera kuba ndalama zambiri kuti onse a Chakwera amve kuwawa ngati tinamvera ife nthawi ya Joice ndi Bakili osakwiya ndi misonkho yatonse iyi kkkkkk

 47. Kunena zoona malawi ndidziko lomvetsa chisoni..anthu aba kupangitsa malawi kukhala dziko losauka kwambili padziko lapansi ndiye wina amvekele ndidzavotalebe mbavazi kuti zidzapitirize kuononga zoona? Ndipo anthu timakhala kunja kuno timakumana nazo,akati umachoka dziko lanji ? Ndiye umvekele malawi , palibe amene.amakupatsa ulemu..anthu amveke Malawi dziko losauka kwambili zimandimvetsa chisoni osanama kubadwila ku Malawi..kunena zoona sikadakhala yosauka tikadakhalandi anthu amaso mphenya.

  1. KAYE MMENE INACHITA POTIBELA MCP, KUTIPHASO KUPHA KOPANDA CHISONI. NDALAMA AMANGOBA OPANDA OWATSUTSA MUFUNA MUNAMIZE NDANI ZOPUSAZO. TINACHOTSA MCP NGATI TIKUCHOTSA CHIPANI CHAZUNGU.

 48. Iwe chakwera usiye kulota ndi iweo wava zot uzawina..m’busa wa chinyengo ngat iwe ukuganiza ngat tingazakuvotele ifeo,,ufuna usokoneze Malawi y??A bambo opanda Nzeru inu ndithu,Ana anu mumauza za nzeru kma?.fake pastor ngat ukuganiz zot uwina uyiwale

  1. AKUlu thnk wise b4 u talk hw many ppo dey r crying due 2ptrs rigim? if ur enaf 4wat pter is doing god be with u thanks.

  2. Bingu ndinu nomwe mukat sali bwino,bakili mukat sali bwino,Joyce banda mukati sali bwino even kamuzu mukatelo nde mukufuna chan ndi kusayamika kwanuko…mukufuna Chan nde muzeni yesu abwele azalamulire bcz is perfect

 49. sometimes if think this person deserve to go to mentor hospital not wandale. He seem to be confused and lack focus. please court exchange him with wandale

 50. Do you Think that Reverend Chakwela can be state president His excellence Chakwela,i doubt, i doubt, i doubt, anyway he is a president at party level, Malawians? Malawians?do you think Mcp can produce results in an election to elevate Reverend L Chakwela to be state president? I’m deeply concerned about comments of staunch Mcp diehards predicting that Mcp boma to 2019, this mcp of Reverend L Chakwela is a last kick of dying horse mfundo mulibe kwa ntukwana basi za zii

  1. Ndipo mukunama siufumu ndizosithana izi muzapanga manyazi ndani amaziwa kuti UDF izatha amalawi enatu simakape oti akuona DPP ikuonanga kumati ndizaivotela kuganiza mopusa malawi ndi watose anthu akonnda chakwela

  2. koma anthu ena mumandidabwitsa Mabvuto Ali mbweee wina nkumatchula Kuti Peter azawina?Magesi pano azima kale anthu simene akubvutikiramu ndima business nde wina aziti Dpp Za ziii

  3. #Pilirani monga anaphwisira pa by election asiyeni adzamva nkhwangwa iri mmutu ati kugula Uladi Musa ngati samudziwa eeh! satana mutuojadaa!

  4. Wekha ukuyidziwa bwino bwino kuti DPP inawina isakulamulila pano ndiye ili mboma MCP imalila kuti yabeledwa nayo PP imalilaso pano ndiye mudzalilaso

  5. Malawi ndiyatonse moti mukamati chakwela saxawina hahaha musasapote coz ndinu mwina ndinu achilomwe ayi koma munthuyo sangawine ntaa

  6. panopa i hate DPP bt i cant vote for MCP……ndiganiza bohboh 2018 yi but ndili sure kuti mu2018 dpp indipanga convince ndpo mu 2019 izandpangitsa kut ndiivotele.

  7. Mcp mbola,dpp ikungodya ndalama zamagetsi ndikumatikhazika mumdima kumangokhalira kugona kuchigayo.kaya chisakho changa ndichidziwa thawi yakampeni??

  8. U tel us then.so since then nothing has changed?at oswel??anyway…peoples votes r in their hearts..MCP leader should stop ndale zapakamwa we Neva know why will win,let him not critisize the one leading nw..we Neva know who Malawians will vote for……

  9. Makape opanda chochita ndi amene akulimbikila kumanena kuti dpp boma Mmene malawi akuwawila munthu kumati boma Dpp anthu akuvutila ndi kuthima kwa magetsi Mzipatala makhwala mulibe anthu opusa mwapanga bwanji Asawona akuyeliko

  10. ||Bwampini opanda mano mkamwa uja angadzawine ? wachita chani chanzeru? Kodi mumamukonda chifukwa ndiwakwanu olo atamangogona …………………………………………………mudzamuvotelabe ? nzeru alibe a Peter Thalika

  11. Kma Ngat Kul Mbuz Ya Mbuz Zonse Ndie Ndiuyu Akut M’busa Wakugwayu Kaya Amat Chatsika,asamadznamize Zodzatenga Boma And Rule Millions Ov Malawiwans Yet Hav Got Family And Friends And Only Thousands Members.Analakwtsa Kusiya Utumik Ndkulowa Mcp,mwna Anakalowa Udf Kapena Chna Chilichose Anakakhala Nd 40%posbility Yodzawna But Mcp Yokhayo Ladies And Gentlemen Lets Get Ready Dancing To The Truck Called #atiberamavoti.Mcp Means Harsh Leadershp To Millions Malawiwans In Togetherness Regardles Ov Their Parties.

  12. Ask ur friends chakwera chingawine? iyi ndiye mbuzi yosadziwa chomwe ikupanga! yamtopola tiyeko zibwera uziona ife sitimavota chifukwa cha kutchuka ukhala pansi 2019 uwona!

 51. Ena mpaka mukulankhula mwaukali nkhani take yomweyi ya anthu andaleyi eeeee koma amakulipolanidi atsogoleliwadi chonde tonse ndi amalawi tisaphsyelane mtima andale asamakudanitseni amakunatu anthu amenewa mkuma gawilana Magalasi a win chonsecho winawe ukudzala nkhwizi ndi nzako kaya mzanu izoo

 52. amene safunira malawi zabwino go a heard ndi mbava zanuzo koma ambuye akukhululukira kwambiri pakuti maso anu ali akhungu

  1. usatchule zina la a MBUYE pa chabe. chekwera ndkachaniso iwe ife sidalira politics mfana koma ameneyu ine nde sindngamvotere chakwera wakoyo

 53. I can’t vote for mbava party, like maize-gate, MSB-gate, 236 billion-gate, Escom-gate, sofa-gate, and I can’t vote for murders like Chasowa and Issa Njaunji

  1. Ifenso monga a DPP sitingavotere ng’ona party.nyakula kulanda katundu.pioneer.youthleague okupha AGadama matenje chiwanga sangala chisiza.chipembere.mphakata.kanyama .Gwede Muwalo etc ukunama tu iwe MCP nkhanza nzosayamba mphwanga sitingabwerere mbuyo

  2. That was kamuzu and your uncle’s people like Dausi Ntaba. Ndipo zosadabeitsa kuti mbwampini akumpha athu. Koma Chakwera ndi azake alibe magazi athu.

  3. ngo’na mwini wake ndi Dausi ndi Ntaba pls make research bobo, iweso ukudziwa kale and pano mbava/amilandu zikulowa dpp pamene anthu abobo akulowa mcp

  4. Phiri and Thoko muthu sadziwa chilichose imagine anthu 21 kupha pano mwapha student ku Bunda ohoooo chipani chatsoka ngati dpp sindinachione

  5. if you hear h/her akuvomera kuti chawo ndichakuba ndipo ngakhale chili chambava koma sangabwere m’mbuyo sinanga amadya nawo

  6. @Lium ask Dausi and Ntaba these two guys they are responsible for that not our new MCP, pamene anthu 21 peter anali mu dpp, Njaunji ndiye magazi ali mmanja mwake @Chande kuti mwana amwalire anawatuma a police ndani and wavapo kuti Bwampini wanu wayakhula za Infa imeneyi?

  7. iwe Kaliati mutu wako umayendeya madzi amanyi aku 18 eti? Dausi ndi ntaba anali mwana? if Dausi anali mwana ndiye tell me amene ali ku mcp pano analipo thawi imeneyo

  8. kkkkkk mad pple could say mcp izawina…but based on our criteria (ife an2 akumwera …sitingavote mcp olo zitavuta…we better go for chisi.. KOMA NA MCP….till death sinzaikondako

 54. Pakut Zlingat Mpira,every one Say Iwl Be The Wner Yet Akudziwa Kt Sawna Akungofuna Kupeza High Molalo.Sndkudabwa Nd Aliyese Amene Akt Chakwera Adzawina Coz Iknow The Song Which U Wl Sing.Its Yomweija Ya”atibera Mavoti Awerengedweso”,if U R Wise N Clever Enough,make A plan.

 55. Kamuzu analamulila zaka 27 or kwawo kunalibe nseu wa tala ndiye chakwela akulimbana ndi Peter oti or zaka 5 sizinathe ndiye kupanda wiseko. Chakwala anzako akumalemela ndi ubusa iwe zinakukanika kuganiza zilowa ndale walemba mmadzi basi munthu otembeledwa iwe usamawaputsitse fans apapa palibe chomwe uzapange pa Malawi wina iweyo uzizangothyolele nthumba basi coz iweyo uli after money

  1. Afumbi kupusa ndiye kukukambitsani nyasi yinu ngati mwawoma kuti anthu akukulemela ndubusa yinu mwanji wosayamba wubusawo kuti nanu mulemele musiyeni chakwela man

  1. Mwaononga chilengedwe, komanso Ku escom kuli a MCP nkumati zithu ziyenda bwanji mukulowetsa dale pa chitukuko cha dziko lanu lomwe and omwe akuvutika si a DPP koma dziko lonse muzinganiza popanga zithu zina

 56. CHAKWELA CHAKWELA NDIYE CHIYANI, 2019 ADZAKHALA CHATSIKA SI DPP YOMWEYI NAYO INALI PA OPOSITION KU PP?? INAKUSIYA PA BENCH YA OPOSITION CHIFUKWA CHIYANI KKKKKK, MPAKA AMAI KUTHAWA PA MALAWI KUMUTHA PETER.

  1. ngat uli Mmalawi weni weni cholephelesa ukuchiziwa if you dont know John Tembo is still ruling under Chakwera n MCP sizasntha or pang’ono Lets wait n see 2019

  1. Multiparty ndi Nkhondo anatelo mutsogoleri wa MCP Dr Hastings Kamuzu Banda ndiye musiyeni ayang’anira kaye Nkhondoyo ibwere p amene adzalowe Iye. Be Spector Ion first.

  2. Temunena kaliati ameneyu ndimodzo aba ndalama zaboma pamodzi ndi chaponda mchifukwa chake athuatamakamba za mcp amalira.

 57. Zowona Chakwera sakunama nanga muthu umangokhalila kuti kamuzu sadayike magetsi amphavu koma iyeyo ndi mtsogoreri Iweyo tayika asamango blema muthu amene adalamulila zaka 24 zapita.

 58. hahaha opposition yakumalawi ndiyouma mitu look at south African opposition achina Malema sakukamba za zisankho koma kulondoloza kuti ma program a boma akuyenda bwanji Komanso a boma akapanga ziphuphu achina Malema akuyesesa kuti ayimbidwe mlandu shame Chakwela ndiwe olephela pamodzi ndi mzako Peter kukhalila kukangana zaii.nawe Malawi 24 ukati ulembe nkhani yimakhala ya ndale ndiwe olephela kuli GCK CAMERA KU MALAWI WANTHU mwana akulemba nkhani mbali zonse wakuposani ndithu .kubadwa musanga sikuwona fisi koma kuyenda utsiku GCK CAMERA yili bho nkhani kathithi osati kukhalila Kkulemba za ndale asaa

  1. Julius Malema wake uti man musanamize anthu apa palibe chkusiyanapo apa opposition kwao ndkususa boma bas olo litakhala kut likupanga zolondola a chna malema ukunenawo ndye mbuz za anthu zenizen

  2. Malema kulondoloza za boma ( ANC)? mukunama man, malema ndi zuma sapanga zofanana. Andale ndimene aliri kulikonse ndi choncho basi

  3. Ma Group Ndionse Koma Kolite Ya Group loooo #MALAWI_WATHU Ili Ndi Group Lokhalo Lomwe Kukumakhara Nkhani Zasopano Zomwe Zachitika Kumalawi Ili Ndi Group Lomwe Kulibe Zonyozerama Mitundu Olo Zipembezo Ku Group li Tikumachezako Bwino Bwino Kuphatikizanso Apo Tikumapasirana Nkhani Zosiyana Siyana Zomwe Zachitila Kumalawi Funso Mkumatu “Kodi Munajoina Kalee???” So Ngati Simunajoine Mukudikirira Chani??? Tangopangani Search MALAWI WATHU Mukatelo Mupange Join Kuti Nanunso Muzilinjoya Group li #Malawi_Wanga #Malawi_Wako

 59. KAYE KUSAMBWADZA NGATI ANAYAMBA WALAMULILAPO DZIKO MBUZI YACHABE CHABE. INE SINDINAMVEKO CHILOWELENI UDINDO KUPI MTSOGOLELI WA MCP WAPELEKAKO NGAKHALE NJINGA KU POLICE KAYA KU CHIPATALA NGATI MPHATSO, KAPENA KUMANGAKO KA BRIDGE KAMATABWA NGATI CHITUKUKO. CHITUKUKO CHAKE KUMANGOMVA ZOTI WASAMBWADZA BOMA LOLAMULA ZAZIII SITIMATU IMAPHWEKA AKAMAYENDETSA WINA.

  1. Aaaa Jafali Iwesiwedi M’malawi Waiwalakale Nthawiija Amalawi Ku Lilongwe Amamwa Madziwosakanikilana Ndichimbudzi Munthuwoyamba Kukawatulukila Adalindani Tandikumbutsa

  2. NDIYE ANAKUUZA KUTI ANAPANGITSA NDI PETER KAPENA BOMA LA DPP. VUTO LA AMALAWI MUMATI KUNYELA MMBALI MWA NJILA MANYI MKUMALOZA MUNTHU WINA CHIFUKWA CHA UDANI OMWE MULINAWO NDI MUNTHUYO. IWE INE SINDINABADWE DZULO NAINABADWA ZAKA 4 TITANGOLANDILA UFULU ODZILAMULILA 1964. PALIBE CHACHILENDO UNGANDIUZE ZA MCP AI.

  3. MUNTHU KUKASIYA ZA MULUNGU KUKALOWA NDALE MKUMATI NDIDZAWINA MULUNGU ANAMUFULATILA LELO MUNTHU WA MULUNGU KUYAMBA KUTUKWANA PALI MZELU??

  4. Thus the problem Malawians have.. Wins atha kupha make kutengera zawo zidani…u will hear its peter kkkkk like serious?we can solve some matters tokha…amcp akamufunse job 2014 vite is in the heart.mukazaluza muzizati maviti aberebwa yet munayiwaka kuti simukhalako ndi munthu kovotako

  1. Mcp Unaiziwila Kuti Iwe? How Old Are U? Wasowa Zolemba Eti! Ukukanaso Anthu Kuti Asamayankhe Pa Coment Yako Chifukwa? Ukuziwa Kale Kuti Walemba Mbwelera

  2. Koma kuyankhula mwauchitsiru chonchi kungoonetsa kuti inu Munabadwa mu Uhule ndi mai anu! Kunyoza kotani kumeneko? Chakwera wakulakwirani chani? Mukutiuza kuti Muthalika anabadwa as a result of POTECTED SEX? Ndinu chitsiru chamunthu. Khala ndi umunthu, ndi pagulu apa iwe nkhomako!

Comments are closed.