The Public Affairs Committee (PAC) has announced venues where the protests will start from in cities of Blantyre, Zomba, Lilongwe and Mzuzu.
The protests are against the failure by government to table the electoral bills.
Hot in the bill is the 50+1 bill which will see a winning president will have to amass at least 50+1 percent of the national vote.
There has been a massive support for the demos nationwide.
In Blantyre the demos will start from Clock tower to Civic offices where a petition. In Zomba, they will start from Zomba Community Ground to Mponda Freedom Park.
In Lilongwe the vigils will start from Community Centre Ground to the City Assembly offices and in Mzuzu from Katoto Secondary school ground.
Among other issues, PAC wants Malawi to pass and implement Electoral and Local Government reforms, and the freeing of the Malawi Broadcasting Corporation (MBC), conclusion of corrupt cases in court as well as implementation of functional activities to end the ongoing power outages in Malawi.
Apa tili nyengo yovuta ofunika zinazi kumupepha mulungu ndi tima odzichepetsa tili nthawi yotsiliza mwana wamulungu aimba lipenga zonse zikuonekazi ndi nthawi yake osalodzana dzala .
Malawi will never be rich by doing demos,Change your mind sets first.For Malawi to be rich Malawians must be rich first.Look @ Nigeria its citizen have opened businesses every where you go.AMalawi nikulila Gvt chabe,Stop being cry babes.Even if you chose people from the moon as long as you are cry babes Malawi will never change.A country can not rely on donor money.For how long will e country move with a begging bowl!!!!!!
You call it red Wednesday, all you need is to shed blood don’t you remember what happened last time with 19 innocent people who lost their lives, so how many lives do you need this time around, by the way what are you protesting.
Ukuyambisawe Upite Ndi Ana Amako Ine Sukandiwona.
Musavomereze amalawi
Ine ndiye ndalowa momo
ukakhala ulibe mano usaswe mphale asiile anzako azikazingira. nthawi zambili tikakha kt ndfe olemphera tisamapange zinthu zofuna kukhaulisa ena asiyen ife ngt a malawi mavutowa tidayambira kuwaona kalekale & zinthu sizikusitha ndye iwe nzanga ndine dyera kuthiko ukungoona kuzivutisa anzakowo apeza mphindu zikantha zimenezi asiyen apange.
mukazaona izi muzangoziwilatu kuti zikolatha ili kwasala ndichigamulo
Am Nt A Politician! Pitaniko Nokha
R.A.C USA Sponsorship Scheme. Robert Allen Company USA is currently offering free sponsorship program to study and work in any of these following countries.
USA
Canada
UK
Australia
Italy.
For more details contact us on +2349036422260
red wedsday for blood wedsday as july 20.
Time has come people must walkk to cry our country Malawi
Accountability
Can’t wait
kulimbana ndi ndale ndi za zii! kukamba zofooka za boma ndi za zii!! kulimbikitsa mademo ndi za zii! sindingapange nawo zanuzo inu a pac chfkwa ndi za zii!
Agalatiya inu chikhristu chongovala nkuchivula mwataya chipangano, musamatinamidze m’machurchmu.
Only idiots will match to participate, but to pple wth normal mindset will never, why? Ihave never seen any changes since Malawians started demos.
More fire!!!!!!!!
Pa 13December kuzakhala chimvula heavy tikuonela ndi Mu Roma wakoyo
Shame my Malawi of today. No time for hard working. Wherever you go on Medias, radios,news papers, in video rooms, on bawo games politics is there. Anthu agundika kuchimwa kusowa anthu amulungu kuti awalalikire koma bzy ndi ndale
Sure!mmalo mopempherera dziko lathu,tikufuna kugwiritsa ntchito mphamvu zathu.Ngati opemphera tizikayenda osapemphera azatani?GOD should help us.
ur mind is so ill……change ur mindset
Pitan kafeni..Anthu akadyeko nyemba kwan
Tizngomacha_mpakana_siku_lomwe_azanene_ABOUT_TURN
Tizngomacha_mpakana_siku_lomwe_azanene_ABOUT_TURN
Mesa ati avomereza kuti the bill will be tabled…?
Tili komweko moto kuti buuuuu
Ndiye zachulukatu nanga Election bill zikugwiriza ndi zina zalembedwazi? ndiye mukufuna munthu sopano pitaniko nokha
Zithandiza chani zimenezo, anthu wambafe sitikuziwa ubwino omwe uli mu bill imeneyo ndiye mungomema anthu kuchita demo za dzii !!!!!
Ma mabokosi tayamba kale kusonkha komaso tamwakale madzi ambiri kuti tidzalire nthawi yaitali
cadet apse ntima ife tili konko
Mmmm simunati mupsadi mtima.kayenden koma mudzatiwuz zotsatir.boma ilo !!
kod a pac,mwaphesa anthu angati?nanga mufuna muphese anthu angati ulendo uno?nanga akafako anthu wamba mumachitapo chan?kapena mumathandizapo chan pamalilopo?Alembi ndi Afalisi inu,mumapanga zinthu modzionesela cholinga mupeze phindu!tsoka kwa iye okaluza moyo wake pa zinthu zopusa….chondigwela chindigwele koma mzaima njii pachilungamo…
Usatiwopseze iwe Cadet. Ife tili konko. Imfa inabwerera anthu amoyo ngati ife.
Negative mindset…..
Who is going there to kill????
Or maybe DPP will send cadets with panga knives????
guyz u will be fooled…..
Chilungamo chake chiti ?
afalisi awa
Zaziiiiiiiiiiii zomwe ukuyankhula mmutu mwako
pitani ine phee paden kudikira za program ya maliro a omwe atazafepo
2 Mbiri 7:14- Ndipo anthu anga ochedwa dzina langa akadzicepetsa, nakapemphera, nakafuna nkhope yanga, nakatembenuka kuleka njira zao zoipa; pamenepo ndidzamvera m’Mwamba, ndi kukhululukira coipa cao, ndi kuciritsa dziko lao.
Nawo Masalimo akuti Ine ndikuti mtendere koma pakulankhula ine iwo ati nkhondo JOSEPH KHARIKA ndakunyadila hevy
Mateo5:20
Pakuti ndinena ndi inu, ngati cilungamo canu sicicuruka coposa ca alembi ndi Afarisi, simudzalowa konse mu Ufumu wa Kumwamba.
tipita
Ndalama awonongazo bola akanathandizira anthu akumwalira m’zipatala koma buzy basi 50+1 nde kanyama kanji pa nyasalande pavuta
Is chakwerah doing the demos as well ? if no then that watery mouth idiot has to behave n change way he speaks
Ndnu Afit A D P P
Ma cadet.
Well said
bwanji inu APAC simufa ku chiwonesero koma osatira bwanji m usinthe mudzapita ku nsewu ko nokha anthu Ali chete muzizatiudza zokutha itha chifukwa simumakhala pansi kuti funsa mum aka mbilana nokha ife timadziwa zokutha itha Mukufuna mutigwuritse nchito ifeyo inu mutakhala kunyumba mumati puts is a kwambili zoti miyoyo yosalakwa imataika simudxiwa mwa phe tsa anthu ochuluka a ngati koma inu mulipobe ayi mumaika ifeyo pasogolo inu n kukhala mbuyo I pweteka dwa n kukhala ife inu siku losatilalo mumakhala ma office anu opanda kuvulala kapena kufa muwunikire bwino pamenepa mudzipita nokha ma stuff APAC we learning through the mistake ime mumapanga pamene anthu si muwaudza kudzi tete dza ayi inu mumakhala kunyumba ena ma office anu apa po kha APAC Mumati puts is a
KOMA abale?? Last days indeed!! Mmmmm
ndibeze legeni (catapult)! ma shop onse mawa kwavuta tilemera!
kkkkkk asaaaaa
Come 2019 tikudzavotera dpp kuti mudzapitilidzebe kupysa mtima zenizeni
PAC si anthu opephela bt asatana wazelu usapite malo ngat amenewa
AM Just waiting for 2019 to vote for DPP
Kuno ku mzuzu zanyasi ayi,mupange zopusazo komweko
Bola asawanyambitise mabazi lelo kuti mawa tisanzave kuti mademo alephereka azachitika mu january .
Zachamba!
I hope that no soul will be lost. Let them be peaceful indeed!