…chipani cha DPP chikhumudwa nawo
Wachiwili kwa Mtsogoleri wa dziko lino a Saulos Chilima anauza a Malawi kuti apite ku zionetselo pa 13 December chaka chino.
A Chilima ananena izi mu mpingo wa katolika ku Lilongwe. A mpingo wa katolika anayika pa zolengeza zawo nkhani yopempha ma membala a mpingo wawo kupita ku mseu kukaonetsa mkwiyo wawo ati poti a boma akuchedwa kukamba nkhani ya malamulo a kavotedwe.
Pa mpingo wa St Patricks umene a Chilima ndi membala, iwo ndiwo anapatsidwa zolengeza kuti anene.
Atafika pamene mpingowo umadziwitsa ma membala awo zopita kumseu, iwo analengeza.
“Pa 13 December, tiyeni mukamatche. Muzavale yunifolomu ya Tchalitchi,” iwo anatelo.
Anthu ena otsatila chipani cholamula cha DPP ati akhumudwa ndi khalidwe la a Chilima amene amamema anthu kugalukila boma lawo lomwe.
“Izi si zoona anachita a Chilima, mesa iwo ndi gawo limodzi la boma? Tsopano iwo sakanatha kupempha kuti asanene zolengeza? Apa sanaganize bwino,” anatelo wina otsatila DPP.
As long as the voice comes from his mouth ndiyeyu wanena kuti anthu avee
Funso langa nali kodi week iliyonse amawerenga kalata ndi Chilimayo kapena anangowerenga week yokhayo basi?????
Amalawi tinazolowera kufalisa nkhani zabodza ,this is umbuli koma kumati anthu ophunzila bwino, ooooooooh! kuzindikira si kuphunzira pepa m’bale samala ndi mlomo wako.
That’s True ngat chilima samamema anthu kut apite kuziwotselo why being on that position of announcing? Kunalibeko ena akanalengeza? Chilima is people you may know in Dpp
Amalawi kusinjilila macholowe anakudandaulani asanamwalile
This page z fokofo
journalist anapagila kut akanganya amenewa
ka tsamba aka ndi ka anthu amisala, iwe walembawe uzivere mtolo muziyamba mwafufuza nkhani musadatumize ngati ndi ndale zakukanikani
chilima sanalakwitse,nanga ukanakhala uthenga woipitsa chipani cha MCP mukanati alakwitsaso kupanga zolengeza??? mmmmmmmmmmmmm asiyeni achilima
Present your story in the right order please. He was just presenting the letter by the PAC which he was asked to read in church.
Chilima was at church as a catholic member and not a government delegate, He had two things to choose, God or DPP. If you were in that situation what could you have done? Leaving God to serve a political party?
Malipota apa Malawi,why do want to comfuse the nation chilima anawerenga kalata ya ma bishop. Or iweso ukanatha ukanatha kuwerenga ukanapatsidwa mwayiwo….kupusa
A’chimwene Limeneri Ni Boma Tadzanu Tayamba Karee Kuponya Mavoti
A’chimwene Limeneri Ni Boma Tadzanu Tayamba Karee Kuponya Mavoti
M24 stick !!!
Chilima zochitika zake zisilibwino
ZABODZA ZIMENEZO
Hahahahaha ndaluta nane
That’s good governance
Chipani chitha kukhumudwa nanu bwana VP koma Mulungu sanakhumudwe nanu,just look upon God, the creater of heaven and earth
I hate Malawi24 atolankhani ake ndi mbuli, odanisa, osokoneza, okolezela ziwawa. Kuli manthu wa chiwanda chopasula.
Holly Ghost Fire Malawi24
Chilima ndimunthu odzichepesa amangwila ntchito yampingo osati zandale amene uja ndi wa DPP ZANU izo mukhaula
Amatiyimilira mkuluyu
CHilima
Malawi 24 is purely Dpp and its reporting is full of nepotism. Shame
Aliyese ngakhale mwana wa dzaka 5 akuziwa kuti DPP sichipani choti munthu kumasatira,, Kkkkkkkkkkkkkk kaya kumeneko
Chilima akuziwa kuti Ku dpp kulibe Chaka chifukwa cha Bushiri atenga zithu zake ndiye alindimaganinzo opita chipani chosusa mcp ,Moto wambiri chilima
Thus Democracy.
Kkkkkkkk amalawi pitani mukabe mafuta ophikila ndi ku bwerako
Wolephele
Mmmmhh! Ntchito Zolembana Pachibale Ndichomcho Olo Ulibe Zozienereza, Chilima Anangopasidwa Zot Alengeze Ndipo Amaenera Kutero Bac Nde Inu Nkhaniyi Simukuidziwa Mukuthamanga Kuzaisia Apa Mmmm! Simukutha Ntchito
Galu kukuwa mbuyake kkkkk
big up chilima
ACHILIMA ANAITHA ….SIKULAKWA KUWAUZA ZA MADEMO IWOSO NDIZIKA ALINDIUDINDO MBALI YAO POFUNA KUTETEZA UFULU WAMALAWI NT ZOFUNA ZAmuNTHU MODZI OR 100 kusiyana ndi 17mn plus …….
a DPP ali busy kuyankhula chingelezi, akuti “This is unprofessional!” eeeh this is Bullshit”! eeh mwakuti mwakuti….. kkkkkk Muona kuti mupanga bwanji, mbwenu musovenge
What do you thinking
Typing,…………………………………………
zikanakhala za black out ndikanapita nawo
This is poor & unproffessional reporting at its highest level.Again,this is uncalled for media reporting! Mind u,was Chilima authored the epistle?He jst pronounced what the letter contained.What if it was another person without a name like Chilima perhaps who read out the letter,wud t hav gone up to this far?I beg to differ plz.Do the investigative journalism.Otherwise,Malawi won’t progress wth this nosensical reporting!!
Malawi 24. Iiiiiii bodza angowelenga.
Nkhaniyi ndiyona koma ilibe umboni kkkk
Poor reporting!!!!!
Koma Vuto Ndi Chani Apa, Chilima Amapemphera Akudzi Chomwe Akuchita, Ena Amapembedza Ndale Chifukwa Azikhumudwa Nazo, Koma A Dpp Akuopa Chani Kt Bill Ya Zisankho Akambilane, Ngakubadi Anthu Eti,
Amadziwa zolengeza munthu umawerenga kaye sikuti iyeyo Uliya muhiti ongonyamula kalata osawerenga podziwa kuti izi mwina ndambali yanga siziyenda adakakana,koma iye anapitiliza kulengezabe,ndimwana oukira mbuyache full stop
Paja ananena kale kuti osamangoimbira m’manja ndi zopusa zomwe hahahaha bravo chilima
Agong’oli inu ATOLANKHANI simudziwa kulemba nkhani MOMANGA koma moyambitsa ZIPOLOWE
M24 mulije mahara chilima mulekani waka.
Anthu timathamangila kuyankhula molakwika mofulumila mwina, posowa kupanga chiganizo poti kuganiza kusiyana, nkhaniyi achilima sanamemeze amalawi kuti azapange zioneselo pa 13 ai, Iwo amawelenga zomwe zinalembedwa ndi adindo ena komanso msikulo olengeza za mumpingo anali Iwo, osati zimachoka mmutu mwao ai Iwo anali ngati mdindo oziwisa anthu za nkhani tisamasemphanise zinthu kuti tiziika ena mmau osiyanasiyana mwina izi zinachitika mwadala kuti chikalatacho chinalipo koma China go sung idea mcholinga choti tsiku la achilima lolengeza azalengeze Iwo mcholinga chofuna kuona kuti kodi angalengeze? koma simaganizo ao ai tiyeni zonse tiisiile mulungu tisaweluze potinso tonse tikudikila kuweluzidwa.
Yes that’s y we need fresh blood
Iyeyo sanawameme anthu kukupanga ziwonetsero ayi koma amawerenga zolengeza koma ngati mumadana nawo kambani nkhani ina,kumbukirani komwe mwachoka,musamale pofuna kutumiza mauthenga anu,a malawi tikuona
Achilima ndimuthu odziwa ndale apa aziwa kale kuti iye Ku DPP kulibe chake mdipo mtsogoleri wathu ndibola panyani mbuzi yachabechabe
He was excising his rights
Lero ndakwerako njinga yamoto. Thank lord. Koyamba aka
Atola nkhani enanu mupitenso ku school
Modern Times…… Waiting to rise the Flag of…………..????
Cadet uyu sakuvetsa muuzeni
Sanauze a malawi onse takonzani chichewa admn
Chilima sanameme anthu inu pilizi. Chilima awelenga kalata yolembedwa ndi ma Bishop…awelenga OSATI amema. This is vague, silly and stupid reporting. Kufuna kuti anthu adane basi. Wakhuta mbewa
Chilima is a courageous man.The best VP Malawi has ever had
Vuto ndi ife amalawi,y not to unlike these idiots page y? Even agube there is no use jst wasting time for nothing
Stop lying 24
Liar mmmmmmmh zabhoza osatisokonezela chipani chathu cha DPP plz plz plz
Uku NDE timati kupanda mzeru.Kodi journalism yanu munapanga kuti?Wamema anthu ndi chilima kapena mpingo?Kuwerenga zithu zolemba ena ndiye kuti wamema ndi iyeyo?
Bwanji chilimayo powelenga sanadumphepo pomema antupo?
Please anyone making comment should make it short, so we professional comment readers (PCR) will be able to Read all comments. Thanks for making our work easier!!
Kkkkkkk
unprofessional reporting inu ndi anthu amene mukuononga mbiri yabwino ya tolankhani mzikomuno
It wasn’t wrong hence he was told to give the church announcement as a church member also one of the Gods servant. Let’s put aside political affiliations. In church we don’t do politics but to do what is the best fr the pple. If anyone feel digress on his speech m its we running away fr the track . Theirs a place where we can do politics, even in parliament, pple can fight but when they are out, they meet at a common goes , leave him alone .
Actually he was just reading a statement that was addressed to general public,he said not in his own words but according to the letter he was reading.are you dumb???
Malawi 24 kudanitsa ..be mature when reporting
Chilima sadalakwitse coz adawelenga zomwe zidalembedwa m’chikalatacho
Chilima apangidwa Mugabe posachedwapa ntayeni
Chilima more fire
Sanameme koma amawerenga zolengeza zamchurch sanapite pa radio kukamema anthu
Atolankhani a chimalawi amalemba zamutu mwawo ,pompa mudalemba zoti MCP imaba madzi zochitsiru basi tamalembani zomwe zachitika bwanji musaiwale kuti ena amakhala kumudzi amafuna azidziwa nkhani zomwe zikuchitika osati zamabodzazi
Kodi a 24 simachite manyazidi muja mnkati MCP illegal water scandal? Illegal connection amayika poyera yera anthu akuona ndi maso? MCP imakutsegulani mmimba? Simunati kkkkkkk maboza basi! Manyazi bwa?????
Sijawhai ona inchi yawapumbavu kama hii
If people were not consulted on this bill which people? If Chiefs has come out with this issue it means people were consulted. The best way just call for a referendum so that everyone has a chance of expressing their opinions.
Kumva ndi kumvesesa ndiziwiri zosiyana,wapanda za mademo ndi Chilima?,iye anapezeka kuchurch ngati opemphera pachurch po,osati ndiyemwe akuza anthu zademo.Muzapusa nazo zinthu zokumva mmalo momvesesa.
Koma anthu ena chilungamo chimawasowa munthu amuwerengesa za mu mpingo nde mumvekere amakopa anthu ha ha ha uyu nde azamva kuwawa 2019 azanenanso kuti amubera backward never forward ever
Chilima sanameme anthu,wangowerenga uthenga, even abusa ngakhale atakhala achigololo ayenela kuwelenga ma chapter oletsa kuchita chigololo.
Iwe chilima ndi wa cathoric, ndiye ku cathoric kumakhala m’busa? Kkkkk kamba mnga mwala
Kkkkk wansembe omwewo
Thats Y I Dnt Trust U Amalawi24.munavera momwe znachitikira?
munthu asawelenge mu xhurch walakwitsa kma amalawi iiiiii
Viva VP Viva ✊✊✊✊✊ democracy amayidziwa …….
Azatitenge…..
Kalipo waona Chilima kkkkkkk
Atolankhani Osadziwa Ntchito Ngat Inu!!
Koma ali limodzi?
Ena mpaka tsinya pamphumi nkhani zomwezi.
In fact DPP leadership has said they dont see any problem in him reading out the announcements as presented.
that is for the public to hear,koma kuchipinda kwawoko amulumila mano,,,,that’s politics
Sorry, I wasnt kuchipindako. Maybe inu munalikonu know better.
Sure……..
Znatheka Bwanj Kulola Kulengeza Zinthu Ngat Izii? Eish
kd munthu umakawelenga pagulu usanapange kaye tchek uyu akunama watenga ndale zake wakalowesa mumpingo bwana pita mthamangiseni uyu ndikapilikon akanakhala kt nd wa dpp sakanawelenga uthengau monga munthu wamkulu akanadziwa kt kungowelenga kokhako ndichisokonezo mdziko chonde amalaw pewan zionetsero zolimbana nd boma kumafa anthu osalakwa pt boma siligonjela munthu apolice mufufuzen chilimayu akufuna kuyambisa chisokonez mkwizingen asaphese ana anuwake fotsek
Comment yaitali no fundo
nawens tachoka apa mbuz
More fire VP ✊
No that’s bull sheet! Zabodza izi. Musamuyike mau nkamwa Chilima kodi inu Malawi 24 munakhala bwanji? You are too much gossiping kodi mwasowa cholemba?
zioneselo zafodya jti????
chilima is not a politician,case closed!
Koma ma comment enawa ndikhaniyi parallel eeeesh kaambanga mwala ndithu kkkkkkk ukooooo
MwNgosowa zokamba
Mwaitha avp
ndye, ife titan tinav kale kt munamuwida chilima kalekale watopa ndchilungam apap
more fire Chilima and this is a move he knows what is he doing sikuti samadziwa nanga every Sunday amawerenga Ndi Chilima? if the answer is no and why only this Sunday?
Every Sunday has a different person
Gama Phiri you are right,,they are playing a mind game,,,they knew kuti muzolengeza muli nkhani yamademo,that’s why anampatsa kuti awerenge,,Chilima is a leader,and leaders ali ndi influence,hence anamuuza kuti akhristu akamva akhale ndi chikoka choti akapite kumademo wo,,,,bravo Chilima.
Additiona from that iyeyo akanakhala wina akanaka chifukwa zolengezazo sikuti zinabwera mwazizi ai
Kuzolowera kakana ntchito ya Yehova ngati chakwera eti. Henry
Pembe point of correction chakwera is man of God kungoti vuto la Malawi ndilakuti amaona ngati pastor sangakhale pastor koma mbava, a satanic, achifwamba, oledzera ndiwo adzilamulira dziko
KOMANSO ZOLENGEZA MUMAZIWONA KAYE MUSANAWERENGE BWANJI ATAWONA SENSITIVE ISSUE NGATI IMENEYI OSAKANA? AKUDZIWAPO KANTHU
Zoonadi!
Zoona akanatha kukana
conflict of interest! Anayenera kukana
kkk komaditu zolengedza umayamba waziwerenga kaye usanakalengedze kkk
Dziko lili pamoto why pple tiyen tizikangana za nzeru cause these cant help sitingapange zoti tikayende kuonesa kukwiya magesi akuzimiramu pple tiyen tidzuke timamenyera nkhondo ena tikuvutika
Dziko lili pamoto why pple tiyen tizikangana za nzeru cause these cant help sitingapange zoti tikayende kuonesa kukwiya magesi akuzimiramu pple tiyen tidzuke timamenyera nkhondo ena tikuvutika
Uli boo chilima tulukamo mwa galu wa sky nama amashe bas tivaya
Kodi ma demo abakalipobe eesh…..zinaluza test pano
Sindikuona cholakwa chilichose powelenga ndiye kuti or kuwelenga buku loyela ndikulakwa?chalembedwa chimawelengedwa bola ngati umatha kuwelenga ukakhala wa DPP usamapephele?
Tili pambuyo panu achilima
kodi zimene mukulemba izi Malawi apita patsogolo??Chjlima amawelenga zolengeza mutchalitchi koma pazolengezapo panali zomema anthu kupita kuxiwonetselo Eeeish atolankhani athu muli kutali kwambili zamanyaz heavy
Kkkkkk ine mulibe mmenemo
Mwagwa Nayo Peter Will Not React The Way You Think
More faya Mr Vip mumatipanga represent zimasowa zoterezi tilikomko
Malawi 24 bodza chilima sanameme a Malawi kupita ku zionetsero ,komakuti anapatsidwa kalata yo khudza zionetsero kuti awerenge ndipo ananena mwini wakeyo .
zochitisa manyaz Malawi tili kutali kwambili atolankhani autsilu .why akumapotoza polemba nkhan?
ndekuti chilima qmawerenga zolengeza every sunday
amene amawerenga tsiku limenelo anali iyeyu ndiye atambwaliwa anapezerapo mwayi pofuna ku kwaniritsa zokhumba zawo ,pogwiritsa ntchito munthu amene kwa iwo amamuona ngati crowd puller komanso kufuna kubweretsa udani pakati pa sau ndi peter m’malo mobweretsa mtendere.
Chifukwa chiyani amzakewo zikuwanyansa?
Poor reporting just to bring Comfusion among pipo,its Catholic Church not Chilima,Chilima was just making Church Anouncements for that Sunday Service
Malawi 24 imudziwe yesu
What a very poor interpretation from the whole well known social media, can’t you write properly pliz!
Kwalowa ena uku
kodi inu simunamve kuti radio yakuti aitengera ku khoti chifukwa cholengeza nkhani yakuti?
Masamba ,wekhatu ukut radio osati Mpingo kapena Munthu wazorengeza mumpingo.pitan ku khoti mukasumire Catholic & mipingo inayo pomema anthu kukatenga gao pazionesero zapa 13/12/17
thats political spirit we always desire osamangoti yes bwana mzopusa zomwe ng Chilima olo atakuchosa mu corruption family yawoyo uzakhala ndi mbiri ya boh
Iiii….bro u r commenting right things on a wrong report…he just had to read the bishops letter…..not his actual words….mwina akanalankhula on his own on aradio o tv osat kuwerenga kalata mu church…. Thats ur view….
kkkkk cc* u right thought he made speech2 ine, vuto ma reporter athuwa
Kkkk…..he just read a letter not a speech these reporter have their own reasonz i guess….
exactly dey used to hv their own negative political feelngs
Mbuzi za dpp zingomusiya salalakwitse chilima. this is not the 1st kuti alengeze mu church bwanji simunamuike mu news nthawi imeneyo.
Ndi Zoona Zimenezi ? Icant Believe it, The Vip Can’t Do This.
kikiki thats sweet ummmh so sexy mmmh sweet
eeeh….. ndie zit?……kkkkk
Inexo Am Wondering Kt Kma Ndzomwezi?
Kkkkk…. eeeh zaopsa2
Kkk
if i made him i can break him,zimbabwe its not malawi
Big up chilima