Akukana a Malawi kudyela suwiti mpepala: ochepa okha akutchena

Advertisement
condoms

Sikuti ndi yodula kwambiri jumboyo, imathekanso kupezeka yaulere koma a Malawi ochulukilapo ndithu akumayizemba.

Malinga ndi kafukufuku, zadziwika kuti a Malawi sakugwilitsa ntchito kwambiri chitetezo pokasamba. Angolowa ndi mutu basi. Itchoke itchoke.

condoms
A Malawi sakutchena

Pa mwambo omwe unachitikila ku Bingu International Conference Centre ofuna kupeza njira zatsopano zoyenela kigwilitsidwa ntchito kuti a Malawi ochuluka azigwilitsa ntchito kondomu, zinaululika kuti pa chaka munthu mmodzi ku Malawi kuno amagwilitsa makondomu anayi basi.

Malinga ndi kafukufukuyo, mu chaka cha 2016, anthu 260,000 anatenga matenda opatsilana pogonana zomwe zikusonyeza kuti anthu ochuluka samatchena ayi.

Poyankhula pa mwambowu, a Atupele Muluzi amene ndi nduna ya zaumoyo anati Malawi akufunika dongosolo la kagwilitsidwe ntchito ka kondomu kuti nkhondo yolimbana ndi HIV ndi Edzi komanso mimba zosakonzekeleka ikhale ya phindu.

Advertisement

172 Comments

 1. And am agree ndi nzanga wina wanena kuti azungu ndi dzitsilu amapanga matenda thenvakupanga ma arv then condom zomwe zikuonesa kuti ndi mphanvu zakumidima chifukwa edzi inacita kupangidwa

 2. Satana ndi amene wakula padziko mulungu azitikhululukila ndi kuti aztipasa kulimba mtima tikakumana ndiyeso limeneli chifukwa kuyesedwa si tchimo koma kugwa mmayesero ndiye tchimo . And the thing iz this world is going to the end, and the satan grows its power wht needed its to confence our sins and god he will 4give us our sins there iz no sach way as to run to god coz nzeru ya paziko ili chabe

 3. mmmmm!!!!!!!!!! life is what u make just have one and be faithful God forbid………..

 4. Iwe kukupasa sweet kuti udyele mpepala ungayimve kukoma .nanga tichulukana bwanji ngati sitikudyana lata lata .bible lidati tichuluke ngati mchenga

 5. kkkk man aids inatha kuli matenda ambiri BP etc mankhwala 3times aday while arv’s 1tablet aday which is which zisalani muzazindkila pasogolo ife ttakwapula kale tabwinot.

 6. Kukhutisidwa pa chigololo ndi puleni mboniyanga ndi Robert Mugabe analesa anthu ake kugwilisa ntchito kondom chifukwa imayambisanso matenda

 7. Best way ndi kuziletsa chigololo sichabwino. Tiyeni tikhale okhulupilika ku azikazi komaso azimuna athu. Ine olo zitavuta maka condom sindizavala ndipo imandibhowa koospa. Amzungu asatipepelese ife.

 8. A Malawi anzanga tiyeni tigwiritse ntchito ma paketiwa. Zikumveka kuti amalobodola nkhongono koma ndibwino kusewezetsa kusiyana ndi kutenga HIV or STI.

 9. Give us figures as in percentage, coz kafukufuku pamayenera kupangidwa analysis. So don’t just say a Malawi ambiri, & of course tell us mode of information gathering used and who participated in the process, and major stakeholders if any, kuti titsimikizedi kuti panali kafukufuku

  1. achite kutani mlembiyu?.if u have a bachor’s in joulnalism at chanco,u’re very suitable,go get employed ku mw 24.otherwise,go search further 4 urself,wabwino atan onga fungwe

 10. Akati a Malawi ndi a Malawi basi kaya muli mommuno kaya ena muli kunja M’malawi ndi M’malawi basi. You can take a banana from Malawi to England but it will still be a . Anyway, anena kuti chiwelengelo cha a Malawi ambiri sanati onse ayi. Kumamvetsa chichewachitu.

 11. kaya ugwiritsa ntchito kaya sugwiritsa koma ngati ukugwiritsa ntchito kunja kwa ukwati ndi tchimo basi dzina lache chigololo, tiyeni aMalawi tilape tisiye njira za nseri Yesu akubwera posachedwa AMENIIIIIIIII

 12. Condom si dhilu mmm olo pang’ono kufakufa bas tinabadwa kunasala ndi kufa nkhan ndikukhala ndi one partner komanso kukayezetsa kut mudziwe chomwe muli!

 13. if u talk of pokasamba wat does it mean …….. jst heat the nail than kt mugwilitsi ntchito m zembaitso mukuganiza kt adziwabwanji kt akulakwitsa

 14. mvutondilakuti makondomu ena amatulutsa tizilonda mphechepechi chitsazo chishango kapena kuti mdidi nde ambili amati bola osauza

 15. Kafukufuku Amenei Yekha Anawakanika Amakhalako Ku Groundko Pot Gameyi Nthaw Zambiri Imaseweredwa Usiku Ndichfukwa Angot Ambiri

 16. Edzi inkaopsya kale pano Kuli matenda ena ngati a shuga akupha fast. Tonse tidzafabe thru Aids or somehow. Munthu ukhoza kudzisunga bwinobwino kupewa kudya akazi owoneka bwino plain koma ndithu galimoto mkuchita ngozi. Mwapindulanji chomcho posaphwanya zokomazi? Yinu mukhoza kupewa bwinobwino pamene wachikondi wanu okhulupilikayo mkuchita mistake kamodzi kokha basi zinthu mkuonongeka which means mwaluza phwando nthawi yose mwadyera nsima mplastic. Cowards die many times b4 their death. Phwanyani zonenepa bwino za health. Koma zina zimachita uonekeratu timafupa ndizo zofunika Ku zipewa. Munthu ngati akuoneka healthy akudya ma ARV ake bwinobwino m’phwanyeni chifukwa akuti simungatenge matendawa since her or his healthy is strong. Fear will make u lose nice food. Madzi mndimbo kudya kopanda mtafuno. Tonse tidzafa ndipo Edzi is just ina mwanjira zambiri. Simudzakhala dziko lapasi moyo wanu ose yinu.

 17. Condom doesnt mean anything to HIV prevention. Even ku nkhondo wanthu amasya futi nkuyamba ya manja. Munthu ukafika malo a chigololo nzeru za umunthu zimachoka and it’s very difficult to resist wina akauza kuti usavale condom. The best way ndi kupeweratu osati zonamizana za ma ma condom’

 18. Honestly mulili ulipo mfunso loyamba maiko amene akutchena mwakathithi muliliwo ndi ochepa kapena ochuluka ? aliyese akafuna kudziletsa asamaganizile za mkazi / mwamuna wake kuti mwina akuyenda udyo ukaika maganizo amenewo palibe kudziletsa aliyese achite mbali yake ,zinthuzi zinalakwika poyambapo kuvomela mwachinyengo kuti jumbo ndi yotetezera matenda pano ndi izi anthu mpaka pano ena sanatcheneko

 19. Zimenezo ndizachabe anthuwo pomazikana zimenezo anaziona kuipa kwake. Ukagwilitsa ntchito Condom ukamalizaumaluseche umatentha moto komanso panchombo pamapweteka kusonyeza kuti ndizachabe. Komanso zimafuta zija zimaonongam’mimba mwa mkazi ndichifukwatu Cancer yamchibelekero ikuchuluka kwambiri. Azungu akutipusitsa ifeyo tisamalenazo zimenezi imeneyi ndimzeru ya Satana komanso azunguwa athakuikamo Poison kuti azitipha mwachinsisi. Ofunayo adzivala zimenezo koma adziwekuti akudzipha yekha. Macondom ndioipakwambiri nangapoti mkazi amasangalara akathilidwa mphamvu zathuzo. Kkkk koma ziliko.

 20. The problem starts in houses. Most women doesnt care about their husband only concentrate with office work.When they come they say tgey are tired. So what do you expect from men???

 21. Koma anthu tiziopa Mulungu wakumwamba ndithu chifukwa tsiku lakubwera lokaweluzidwa.ku Genesis akuti mwana wa Yuda amati akamagona ndi mkazi wake amataira pansi mbewu zake ndipo Mulungu adamupha Chifukwa chomatayira pansi umuna wake ,ndie lero kwabwera macondom , mchimodzimodzi mukagona ndi mkazi mumataya mbewu zanu ,ndipo Mulungu akulemba izi mabukhu mwanu , chofunika ndi kuzilesa basi . Lero Satan akubwera ndi zintchito zambiri.

 22. Ok serious speaking Aids is really. The problem is unfaithful to one another. You find someone who is good but his wife is getting laid right left centre. The wife is faithful but the husband is running 500km/hr

 23. Inde ingakhale yochipa,koma tukulani ubwino wosatila zaumulungu zomwe zizalengesa kuti tipewe matenda ndiuciwelewele.tizapulumuka mopanda m’philayo.

 24. koma ndiye ilakweilakwedi eeeeee!!!! sitisala ambewu tintha tonse!! Atasale wambewu ndi #Fischer #Kondowe yekha baasi!! cz iye zamasewero amenewa sizimamukhuza wache ndi m’pira baasi!! kunthamanga kwambiri mground ngati kamnyamata nanga si aamangokhala mphamvu zimasowa kopita kkkkkkkk.

  1. Nanjinanji Amaiko Enawo Ndiye Kaya Bolanso Akonkunofe,koma Amaiko Enawo Akamabwera Amakhala Atatenga Chintolo Chamatenda 2-3dyz Zayambika

  2. Kkkkkkkkkkkkkkkk i am not one of them but i am telling u the truth of that.Amene tikuvulala kwambiri ndi amene tilikunofe example if u having a girl freind like south african she gonna tell u where is condom but malawian eshiii akuuza kuti chimanditentha pachombopa

  3. Kungokhala Kusaganiza Kwa A2wo Tinene Kut Kuno Kulibe Ogwiritsira Tchto Chishangocho?Ndimtima Wamu2 Basi Kunonso Tilinazo Zima2sim Zo Nditina Togwirika

 25. Wakufa saopa kuola / kapena ndinene kuti ochimwa asamaope gahena, kondomu or no condom we commit the same sin. The bible says; usachite chigololo.

 26. njila ina iliyonse ya kulera pachikhristu ndi tchimo. inu mulipati? nthawi zambiri condom imagwila ntchito ku uhule.Ndiye pamenepo anthu akuchimwa times 2 Ndiye zilango zokha zokha

 27. It sounds like half madness coz if you wont to test chocolate you cant eat while is stil inside the plastic’ take it out first then eat the real chocolate.

  1. My brother the hungry ng’ona is waiting for you somewhere to feast. Be warned, because your chocolate will become sour and bitter one day. Osazang’ong’oneza bondo, just accept the consequences. Enjoy.

  1. Si nthawi zonse mungamapeze phunziro mu nkhani, nkhani zimaphunzitsa, kudziwitsa komanso kusangalatsa. Nkhani ina iliyonse imakwanilitsa chimodzi kapena ziwiri mwa zinthu zimenezi. So mu nkhaniyi ngati mulibe phunziro ndiye muli kudziwitsa

  2. Bro momwe walembera apa ndi joke chabe palibe chidziwitso or phunziro.

   Chabwino akanati
   Abale anzanga tiyeni tisamakane kugwiritsa ntchito izi. Pamenepo waphunzitsa
   Kapena kuti Abale
   Kugwiritsa ntchito izi kumathandiza izi ndi izoo,,,,,tiyeni tigwiritse ndithu
   Pamenepo wadziwitsa.

   Koma akungolowa ndimutu,
   Itchoke itchoke what z that Bro?????

 28. Zopusa,a Malawi tiyeni tiphunzire kuziletsa,osati zamakondomu zawozo.Azungu akumapanga dala zimatenda kenako kupanga zozitetezera kumatendawo,cholinga tizigula iwo azilemera.Mankhwala akulu ndikuzilesa,kukhala ndi okondedwa m’modzi.Tisaiwale matenda amenewa titha kutenga mu second koma kundwala zaka zochuluka,komanso chauta kukatilanga pazolakwa zathu.Onani tavutika kundwala nthawi yaitali kukalangidwanso.Tiyeni tizilese osati makondomuwo.

  1. Agree wth u 4 ur good and encouragment words.Tiyen tizilese tingokhala ndinkazi mwamuna mmozi,akaziwa ndiwofanana tisamasiyanise pli pli pliz.

  1. Kuyerekeza chiwerengero cha anthu amene akufa ndi nthenda ziwirizi, Aids ikupha anthu ochuluka komanso aids, timaitenga kwambiri munjira yogonana, which is something preventable unlike cancer yomwe sikupha anthu ambiri ngakhalenso nayo njovuta kuchira.

 29. Aaa zazii zisiyeni aliyense payekha nanga moyo amasamalilana ?? Mumene munayambila kuuza anthu ngati safuna asiyeni basi

Comments are closed.