
Kwavuta ku Mwanza: anthu akugonana kwambiri, sakudziteteza
Pamene boma komaso mabungwe osiyanasiyana akulimbikitsa kuti anthu azigwiritsa ntchito njira zozitetezera pogonana, zadziwika kuti m’boma la Mwanza sizili choncho, chiwerengero cha odwala matenda opatsirana poganana chakwera kwambiri. Izi ndimalingana ndi a Samuel Simbi amene… ...