Police in Nkhotakota are keeping in custody two women for being found with chamba.
The two, Lucy Phiri aged 48 and Rose Mithi, 20, were arrested at Kaombe Police checking point in Nkhotakota.
Nkhotakota police deputy spokesperson Paul Malimwe told Malawi24 that the women were travelling in a bus from Dwangwa heading to Salima direction.
At the roadblock, police conducted a search and came across one sack bag and two other wrapped packages containing Indian hemp.
Efforts to trace the owner of the dangerous drug led to the arrest of the two suspects.
They face charges of being found in possession of Cannabis Sativa without license as laid out in section 4 (a) of Dangerous Drug Regulation and 19 (1) of the Dangerous Drugs Act.
Phiri and Mithi hails from Mbuna village in the area of Traditional Authority Kanyenda in Nkhotakota.
chamba ndi mankhwala othamangitsira afiti. Ndiye aliyense odana ndi chamba ndiye kuti ndi mfiti
Na kunkhotakota pa ganja mmmmm palibeso
Edmund Zhong, check this greedy and non starter issue!!!!!! “Chamba” is cannabis.
Women?
Zogalu asiyeni inuso ndiye akuba zeedi shuppit zanu
Osamumanga Ogwetsa Mvula Kuti Ganja Imere?Malawi Sidzamva,asiyeni Amayiwo.
I hate this government of malawi its so proud to see its people suffering for poverty how dare ur aresting people over business they are doing, so far so good mumangeso ma hule onse mmalawi muno kamba kakuti akufalitsaso matenda a edziiii!
Nde mukufuna anthu azitani kukaba ku bank, asiyeni anthu azigulitsa chamba mmene akufunila, bvuto ndi chiyani? Chabwino inuyo chambacho mukalanda mmapita nacho kuti? Kusaukitsana ukooo, kuno kokha ku malawi mmalanda anthu chamba!!! ! Fulsek malawi government!
ndalamayo inalinso yangongole kumabungwe, chonde athandizeni sikweni
I thought these was approved by Parliament to be cultivated in Malawi so why arresting her
mungowalanda chambacho osawa zunza ai motelo mulungu apatsa olimbika tu
kazembe wakwiya azimayio amasamala ana amasiye omwe boma singa kwanise or
free up de woman…please
M’malo momanga ma cash gaters up deh mkulimbana nd azmai achamba , kumat ndnu a police ,free out dem fast akayamwise ana.
Amene wawamanga ndiye wa chambanso
zaziiii!!!!!!
Tulutseni musawamnge
Ngati achita kuba anjateni, if not free them.Women of Peace
Ngati achita kuba anjateni, if not free them.Women of Peace
anthu amangopanga bussiness osati kusuta…. Asiyeni….
Zayambali apolice kugwila olima ndi kugulisa chamba mesa kunkhotakota ndiye ulimi wawo koma boma la malawi sono ndichan chomwe angalime mkumapezela ndalama popeza fodya wa bale mukuti simukumufuna kulima nandolo simutigula mteza ndiye nyanyi tilime nyemba mukut misika munaseka,thoche ndiye mumangolanda osat kugula kubomako inu mumati awunduna owona zaulimi (agriculture) awuzeni amalawi ulimi weniweni wovomelezeka woti tikalima muzitigula chifukwa ife tinakutulukani poti chamba tikalima sitila mitengo wakuboma timangogulana tokhatokha pamitengo yokambilana ndipo inu apolice ndikuziwiseni ku chamba ndi ulimi umozi omwe tikupanga nawo ndalama kuposa ulimiwina uliwonse tisiyeni ife takusiyilani ziko lanulo nafe mutiyilenthakayathu
Good news that is coming from Lesotho they have legalized Chamba.That’s the first African country to do so hope that Malawi will follow suit soon.
Let dem free muganja muli mular ana xul fees pat u stupid police mumafuna ma dealer mukhale nokha ganja fih lyf don’t hate de plant. JAH created it
Apolosi opusa kusowa zochita eti?
that chamba powamanga munafusa kuti akatani nacho??? mwina amakapangila hair food kkk anthu oyipa
In Africa we don’t need CCTV cameras, the neighbours are enough .if you think i’m lying bring your girlfriend at home when your wife is not around and see verities of modern technology.
kkkk real ma men
Kkkklk yur right men
Robart mugabi….m
Atani
Amangeni akuzelezesa anthu ntaunimu
Buzy kumanga nzimai wodzithandiza yekha while chapinda is free ou there!!!free her!!!
oh! I wonder when the plant considered as illegal kma Malawi sazazindikirabe eti!!
Nkhaza kwa amayi, what are the CSOs saying about this?
real criminals are in streets…free the women
Musasiye comco amenewo mpaka akaonekele kubwalo la milandu
kkkkkkkkk. mwati akazi eti? ok tiwona kuti muwatani.
Kungowazunza azimai za ziii, alembeni ntchitotu. nanga akakudweleni kuchipatala??
Medical marijuana for pain relief
Free the ladies they were tryna make a living how was u gonna feel if u were them?
Mukulimbana ndi chamba kusiya opopa magazi akutizunza kunowa koma mmutu mwanu mukuyenda bwino
Ndi ma business andalama amenewo changu bail pamenepo
Free these women they be feeding their families nkhan yake chamba chomwecho
CHAMBACHO AKUFUNA AZIPEZEKA NACHO OKHA A BOMAWO???…MESA NAWOSO MA BUSINESS AWO NDI OMWEWA
bullshit let them free they are trying to make life easier they are not sķelm or thugs live them in peace
Eshiiiii koditu timadyera momo mu chamba Kuno Ku nkhotakota mbewu imeneyi imakoma ngati mpiru wotendala
Are you going to rescue them Mr Elias?kkk
police brutality
Free de women..they r trying to make money. ..go & arrest real thugs out there plis
Truly they must leave them free
Sho bru. ..