Football Association of Malawi (FAM) has fined Be Forward Wanderers for misconduct and has also banned Nomads captain Alfred Manyozo.
The Nomads have been fined K500,000 for incidents that occurred during their Carlsberg Cup encounter with Blue Eagles on 12 August, 2017 at Civo Stadium.
According to a statement signed by FAM General Secretary Alfred Gunda, the club was found guilty of failing to take precautionary measures to control their supporters from throwing objects into the pitch and towards the Second Assistant Referee.
“This disturbed the normal flow of the match as the match was stopped for five minutes thereby bringing the game of football into disrepute,” says the statement.
The club has been told to pay the K500,000 fine before their next official fixture.
The statement also says Nomads captain Manyozo has been banned for four matches after he was found guilty of inciting crowd trouble during the same game as his actions of protesting a referee’s decision led to the throwing of objects into the pitch.
Wanderers are free to appeal the ruling, according to FAM, but they have to pay K500,000 appeal fee.
500 poti ndi manoma koma akanakhala enafe mpaka Million.
FAM yanyanya.hiyaaaa
you guyz u need to put de reasons why it is fined
you guyz u need to put de reasons why it is fined
What about the ref who started it?
komano zomwe akumapanga ma Referee penapake ndizopweteka aliyese kuti awine game amayivera kuwawa sikuti poti B4ward ndiyomwe ikuyang’anira mwambo wogawa mtibu wa zigoli nde muziona ngati sitimazivera kuwawa ayi, Penalty yowoneka ngati imene ija kutibera nafesotu mtima umawawa mwava? kukhala pa top sikophweka or kampopiyu akudziwa.
ndi mmene amapezera chuma chao
Mwachita bwino a FAM .Noma team yopanda khalidwe inazolowera milandu
mapazi awo a fam.
Inu a FAM pezani njira zina zopezela ndalama osati kumangolipilitsa ma team nkhani zopanda pake….mmene kumakhalira ku stadium how do you expect a team to control hundreds of supporters?
Mumagend cz a ref med a mistek and leta blame FAM fo a punch??
Nyamilandu must step down
Ndiye mwati mpaka HALF MILION Koma neba ukwanisa????????????.??????
zodabwisa manyozo watani mpakaba 4 games
No one is above ze Law, akuyenelakulandila chilango basi…..Maule mukuonabwa??.
Hahahaha koma zampira zake zoseketsatu hetiii mwati manyozo anatani?
Ngati pali chaka matimu akumenyedwa ndi ma fine ovuta kwambiri,ndi 2017-2018 season,chizindikiro chosonyeza kuti mpira sukuyenda bwino
FAM is in economic crisis. …..akungofuna kupeza njira zopezerapo ndalama apa to support their budget…………
choziwa Walter nchimeneco. ban.fine.koma zampila nde ai
Exective yonse ya FAM itule pansi udindo yalephera ntchito
Ma Noma tanyanya tikumango gawa ma 5 -1 next wk a AFM sazaika magolo ngat game ya neba dzulo kkkk
Zikuyenera kutero bas, chomwe amaponyera mabotolo mu ground ndichan? Ine ndiwanoma koma izi zomafuna kut team izngowina ikaluza kumagenda zimandinyasa, kuwina, kuluza kapena draw, vomerezan.
iwe ndye sapota wozindikila, ine wa bullets koma ndakunyadila kwambiri
Koma akalemba mulungu walemba league tiwinabe nyamilandu akuwona
kkkkkkkkkkkkk,anakozela pagolo LA moyale kuti awine 5 kwazii
man kumazisata kae b4 commenting
Fufuzani bwino musanayambe kulongolora bwana
Manyozoyo watani nanga???
Ntchito yayikulu ya FAM ndi kulipilitsa ma team otsati kuyendetsa mpira. Team zoona ikwanitse kupanga control masapota onse nanga ntchito ya security ndichani? A FAM amatuma masapota kuti azita ziwawa ndi cholinga choti azipezapo ndalama Ku ma team. Kodi oyendetsa ma team simungakale pansi kuti muwachotse akuluakuluwa kuzera Ku Court.
I dont think FAM ingatume anthu akayambitse chisokonezo bro! Unless you prove it, Bwanji tinene kuti ndi udindo wa munthu aliyense okonda masewero a mpira wamiyendo kuletsa mnchitidwe waziwawawu, Becoz mukati chitetezo chimayamba ndi mwini Not azachitetezo.
ndimkona francis shaba…akumashatapula
basi zomwe amadziwa ndizimenezo, ufumu wa fam tauyeza ndipo ndiolephera
?
why manyozo has been banned…..?
#NyamilanduMustFall
ati chaninso??!!!
Timaziwa a FAM aka akawona kuti nbb ayilipisa amayesesa kupeza tizifukwa ku Noma kuti nayoso ayilipilise.
Paja FAM & SULOM most of them are bullets fun.
Man kungot pot maganizo saletsana!fundo yanu skplka chlimbkitso
Am Noma fan, but am 100 percent with the decision by FAM, remember we lost lives of our friends due to this stupid act of supporters. Lets be civilised supporters guys!!!!;
Welings u must know dat no one is above ze Law.Just accept ze panishment couz is Legal
So why they have punish only noma
,@wellings just follow futbo activities properly b4 u judge,masapotaz anoma anagenda kmanso kuyambisa chisokonezo thats the genesis of the punishment
Thus y i hate this FAM President, everytime when kampopi ayipeza ndi milandu he also tried very hard kut noma nayoso ipezeke ndi mlandu, why banning manyozo for 4 games? This guy sickens me
Manyozo wataninso abale anga a FAM? Mwakhala mukungana ndi Shawa lero mukufuna mubwere ku Lali-Luban?
Nkhan yake iti!!!!