Masiku otsiliza mudzaona zinthu zosiyanasiya zina zoona komanso zina zomusemera Mulungu koma iye asananene kalikonse mkamwa make, malemba amatero mu buku lopatulika.
Izi zikupherezera pamene m’busa wina m’dziko la Zimbabwe akuti walumikizana ndi mulungu osati mu pemphero koma pa foni yake ya m’manja.
Mmalingana ndi ka vidiyo kamene Malawi24 yawona, kakuonetsa m’busayu yemwe dzina lake ndi Paul Sanyangore mpingo wa victory world international ministries akuti akulankhulana ndi mulungu pa foni pamaso pa khwimbi la wanthu mkachisi.
Ka vidiyoka komwe kawanda kwambiri pa masamba a mchezo pofika lolemba pa 22 March kadali katawonedwa ndi anthu okwana mazana 77 pa tsamba la mchezo lija lotchedwa You tube. Ndipo kakuonetsa m’busayu ali ndi mzimayi ovala zovala zoyera ali kutsogolo manja ake ali okweza atagwada pamaso pa m’busayu.
M’busayu akumveka ndi kuoneka akumufunsa Mulungu kuti alankhule chani kwa mzimayi yemwe wagwada pa patsogolo pake ndipo waoneka akumvetsera modekha kusonyeza kuti wina akuyankhulana naye pa foni yake ya mmanjayo.
“Halloo! Kodi ndi kumwamba kumeneko?, kodi ndiyankhulenji kwa mzimayi amene ndili naye panoyu?” (Hello, is this heven? I have a woman here, what do you have to say about her) Adafunsa m’busa pa foni pake.
Mpingo onse mosakhulupilira ukuoneka ozizwa komanso idabwa kwambiri ndi zomwe m’busayu wachita. Pamene mnyamata wina akumveka akuyankhula mozimuka kuti “oooh Mulungu alemekezeke”
Povomereza zoyankhulidwa pa foni, Paul wamveka akuvomereza kuti “ooh ok ndimufunse kuti Sibo ndi ndani?” Anayankhula m’busayu.
Atafunsa iye kuti Sibo ndi ndani? anaoneka akulankhulanso pa foni kumufunsa uyo amayankhula nayeyo kuti anene chinachani mzimayiyu, ndipo anamufunsa mzimayiyu kuti “mchifukwa chiyani
Akundionetsa mtima” ndipo ziyankha za mzimayiyu sizinamveke popeza amayankha monong’ona.
Mulungu akuti tipempherere ana ako onse awiri, akuti m’modzi ndi odwala khunyu ndipo wina ndi wa matenda obanika kupuma” (he says we should pray for your children, two of them, he is saying one is epileptic the other one is asthmatic) adauzidwa mzimayi.
Anthu ambiri a mumpingiwu awoneka akusangalala kutamanda mtumikiyu pochita zodabwitsa kulankhulana ndi mulungu pa telefoni ndipo analankhula mwa thamo kuti kumwamba kukupezeka pa foni (heaven is here) ndipo anauza mzimayiyu kuti nyengo zake zasintha.
Komabe izi zadzetsa mafunso ambiri ndipo anthu enanso a mu mpingowu sakukhulupirira kuti izi mzowona.
Wasuta KANUNDU shupiti
So this guy has followers with brains?.
If it was a clip i would believe. is that the only story you can create from that picture?
mboli yake
Osamalimbana ndi anthu a misala inu
Apolice anthu oti muziwamanga ndiye amenewa.Kuyambira lero aPolice mangani yense obweletsa chipwilikiti panthawi yopemphera.
Koma chonde anzathu achikhilisitu tazilemekedzani mulungu don’t take God like ur friend
Kkkk tel him to share with me God contact number
Ndiye mulungu ameneyo akugwilitsa ntchito ton mtundu wanji kkkkkkkkkk
this total nonsense…God have mese
Hello pastor! If your stomach is full with all rabish u ate yesterday, go!! to the Toilet right now! .
matsiku ake ndiwochepa akanalapa
The worst still to come. But they shall be expose. Kuyamwa mabele,cucumber, drink petrol,doom, lot of stupid funny things. And the worst part ladies are taken so fast because they are desperate for marriage and money. If they join they say they are born again and ali ndimakani koopsa. Mudzalangidwa
That’s fashion preachers how I wish I could go back in old time religion Lord helpe us rapture is near
Don’t play with God, pezani China chocchita
Chamba eti chikumakupwetekani osamango kalima bwanji ngati ndalama zakuzutani
Kkkkk padziko lapasi,, zochitika mbwee,, ngat zilichomcho nde bwez tikuyakhulana ndachina malemu Bingu muthalika,, kamuzu banda,, vic Marley,, matafale
Indeed these are last dayz .how can he speak with God thru phone
I think he is getting mad
Koma munthu ukadya ndikukhuta Osama mphatikiza Mulungu ukamafuna kulankhula Chifukwa tembelelo lake limakhala loopsya kwambili tamvana!!!!
Mwina Nambalayo anaipeza m’baibulo momwemu. Nafeso tifufuze boo titha kuipeza
Tamuuzani andigawile Nambala ya Mulunguyo
Don’t play with God he going to punish u
fodya wamkulu
The Bible says,don’t mention the name of God invain,so b careful.
Ameneo nde masiku omaliza
Mpititseni Ku Mental asylum.
Angondigairako number ya jah jah yo nziyankhula naye ndekha
Mmmh guys take it easy, i hope you don’t know who this guy is, he is a comedian not a prophet kk search his name or bio on google. its drama kk
ikakuonalitsilo,tiye nazoneba,umayenda mbali
Ayiiiiii kulibe izooo
Mwafikapotu ana anjokainu
These days u black people u had know money. ur are going to dstry the Earth. White ppl thera quite. It’s really real that black one thy are not created in the emage of God. If you are emage of God why you are playing with him
U black people? ????? R u white? ?? Inu ndi nzungu?? Chizungu chakeso chimenechi emege nde chan
kkkkk anzangaaaa osangolemba chichewa bwanji hahaha iiiii zoopsya
Ine ndili chikomokere mmasomphenya ndaona kuti babawa ndi a a ku bangladesh
Can you put your. …..
..pastors in black plastic bags
Yelemiya 5:30 to 31
Welengani nokha ine kumeneko.
KKKKKK
Mwina upangiri uwu mudachitapo anzanganu Chim Exodus Dante Kaunda Yung Jay Päùl Schwéigèr Nèwå Victor Nthutha Phiri Gule Enangu Rombeziz
haha ine ndimangodziwa kut #Paul analowa kusiling,i mkumauza m,dala wake kut amugawile gawo lake lachuma,..m,dala posaziwa kut nd paul ali musiling,i ati amkaona ngt nd Mulungu akumulankhula
Hahaha atigaile number yo nafe tiyimbeko
Hahaha# yung j wakuonjeza paul, kkkkk ma phone ake mose wa leroyi akutheka zimenezowo???
haha ndamuonjeza???zinachitika izi
Kenako timva Ambuye alipa WhatsApp and pa Imo eish last days
Koma ngati mpingo wakewo muli anthu ndiye ndi amisala okha okha ndithu.
Kikiki
Kkkkkl
Ananena Kale Yesu Alah Salamu MTendele Ndimadali Amulungu Ankhale Pa Iye, Kt Matsiku Omaliza Kuzabwera Aneneli Onyenga Namanenela Mudzina Langa Namat Alikuno Yes Musamukeko, Km Lero Ndizomvesa Chison Kwabas Tingoti Tikamva Kt Kwabwera Proft Anthu Komko Koma Tisamale Ndi Aneneri Onyengawa Alemelera Painu
Serious?
Moti anthu akumavomereza kuti ukuyankhuladi ndi mulungu? Ukufunika ukayezedwe ubongo iwe
waitenga kut # ya 4n yakumwambayo
Inai ndie misalano
kkkkk kodi pano mulunguyo mukumamutenga changa juice wamalambe? motomoto kwanonse omutengera mulungu kokamuyensa
Osamangoti ku zimbabwe apa muzinena ndi maina omwe azibusawo ndi madela ake. Kumangoti akuti akuti kumeneko m’busa wina. Akuti yo ndi ndani?
Koma Ku Zimbabwe Ku nchiyani wina posachedwa pompa waima poyera ndimati iye ndi Mulungu wina nkumati ayende pamadzi wadyedwa uyu ndiye aziti wayankhula ndi Mulungu nchiyani koma Ku zim
He is mad
Kumuphwekesa mulungu kumuika mutechnology while others are busy kumuika muchinyamata@wa swag kkkkk abusa awa atiimba heavy iiiiiii
Koma tikakhala tisamamutenge MULUNGU kukhala chopepuka ngat momwe tingachezele ndi abale kapen azizathu bcz mulungu ali ekha.Ndpo tizizivela chisoni chifukwa cha zonse zomwe amatipangila zaulere Tizasowa chowilingula
Fake prophet
Kkkkkkkkk bodza ili ndi waonjedza bola anzake ametenga sing’anga kumapanga za masenga kunamizila Mulungu .zikuwayendala mpaka kugula ndege koma uyu aliyense akungoziwilatu kuti ndiwabidza ndi ma South Africa omwe anthu ongikhulupilila zilizonse koma zimenezo sangakhulupilile hahaha .
Anayakhula naye kut Chan
Ndiye pofunika tafunse kuti atigayileko # number ya mulungu yo nafenso tayimbire asamangoyimba okha ayi. Nafenso tidandauleko za mavuto ali padziko panowa. Mwina angatikhululukire
Hallo,Hallo God…. Can you hear me?
I’m a pastor,from Zimbabwe am calling on behalf of the church…. Hallo…. Halloooooo eish…
Net work yavuta.
exodus 20:7.do not use my name for evil purposes….. (Forgive him lord for he don’t know what he is doing)
Koma yaaah mmmhu
Thus Why muno mu zambia anawakaniza ku bweramo aneneli onyengawa pamodzi ndi bushiri koma anaopyeza kuti iye bushiri azapha yemwe anamkaniza kulowa mu dzikoli la zambia.
you sound dumb. where did you get such information
Eeeeh,I don’t understand this
Kanundu
Azathu achikhilisitu ndiye mwaonjeza kwambiri kaya kukhata mondokwa kaya ndi chamba ndiye muziona mpaka kuyakhula ndi Mulungu pa cellphone koma yaaa ziliko
Atigaile nambayo pliz umphawi watikwana kkkkkk
Poti anthu timapembedza milungu yosiyanasiyana, wakeyo athadi kukhala ndi selefon, Ambuye Yesu Khristu okha sangakhale nayo.
No wonder imeneyo ndiye mipingo yongopeka yotchedwa chikhistu
misalatu imeneyi
Hallo Mukundimva, Ambuye Mukundimva, Nyimbo Ndaimba……… Sakunama M’busayo! I Have A Witness
Kkkkkkkk izi nde zipwisi zenizen anamupasa # ndi mulungu omweyo koma abale masiku osikiza akuti kuzakhala aneneli onyenga nde ndamenewatu
Azibusa okuba atopa ndi umphawi!
these pasters of nowadays mxiieewwww
Bible limati chani about lastdays Mark 13 verse 3-14 kaya zanu bachedwani
Koma ano masiku otsiriza.maso muli nao koma simuona, makutu muli nao koma simuva.wandituma ine yesu kuti ndiuuze mpingo wake udziwerenga mau amulungu usasochere njira yake:patie Namadingo
Tingoti phee tiwone
nzosatheka
Ooo I don’t hv more words to say but what kind of this madness ?is he thinks that all we don,t know the Bible ?wrong business sorry
Call the ambulance the pastor is sick in the head
Koma ya akhristu mwatopadi I’m proud to be Muslim
Akakhuta kulibwino kugona kusiyana nd mbwex izi
Akakhuta kulibwino kugona kusiyana nd mbwex izi
Zochitika mu Africa!
chamba ndi chifukmachake enafe tinaleka madnes is the result.
Atigaile Bas 4n Number Nafenxo, Kkkkk. Mpaka Pa WattsApp, Kkkkk…
That pastor needs delieverence be4 it goes further because his confusing the already confused “congregation”
Kkkkkk Aneneri Achulukitsa Ku Africa Kuno Kusiyana Ndi Maiko Azungu! Mpaka Kuchita Kumva Mau A Mulungu! Tilidi Mmasiku Otsiliza Eti!!
Andigaileko Number Yake, Mavuto Atopetsa, Kkkkk Zamasiku omaliza!
na wamwamba yekhayu muwopeni ngati mene timamuwopera ife
Some of these are just confusing right mindful people. Don’t make funnies with God, better shut up please.
chamba chimapengetse Akuganiza Mulungu
Atate ndikhulupilira nthawi yomwe timayembekezera ija yakwana yokha bwerani basi
Matsiku osiliza basi anaiimba iyeyo kapena anaiimba ndi mulungu
Anthu inu;mwamuyetsa Yehova ngati jemusi eti?dziwani nthawi yanu yakutherani ndipo Ambuye Mulungu akukanthani
Misala imeneyo after ganja
AKUTI MA PRPHT KOMATI INU NDI KULONSELA KWANUKU MUZAYANKHA MULANDU KWA YAWHE
Atpaseko # yake ife mavuto atitopesa
hello mukundimva…am here to read the comments…
Kkkk nde Ganja-yo.
Matsiku osiriza kudzakhala aneneri achinyengo ngati awa.
JAH alone a true Christian.
Ndiwotembeleredwa amaneyo
MULUNGU tisamuseweretse ameneyo adzalangidwa ndithu
Panopa Kupempha Kudzera Mupemphero Zatha Pano Ndi Pompo Pompo Clear Clear Pa Phone Kumvana Akane Akane ,alore Alore Alore Kkkkkk Pano Ndie Ziri Pa Easy Kuphwekeratu Ali Ndi No, Yake Andigaileko Pliz Ku Inbox Ndilankhule Naye Ameneyu
koma izi ndiye iiiiiiih anawonjeza kaya mwina iyeyo …….prophets are doing those things to attract more followers so that chopeleka chizikhala chambiri #business as usual .
inu inu uuuu….!!!! km tidikire oweruza yaaaaah
kkkkkkkk
kkkkk anthudi atopa!!mpaka kumfonera??
Kkkkkk..boza lowoneka ndimaso kopanda kuvala magalasi
Loading …. .
I even have the video with me
Can you send it to me if you don’t mind bro
Drop ur app #
send broh ±27835036112
Sorted.
Kd m busa ameneyo wakhuta chani iyeyo phone # yakumwamba waitenga kt usatanism wakewo ayaluka nawo
Mulungu Osamamutenge ngat choseweletsa chanu mukakhut ndikudzimbidwa ndi maungu
Amen sister tell them
Kkk zachamba
he is Mentally challenged
eish zaulendo uno….
Misala Ya Ikulu,nzomba Meto Sili Ku Malawi Kokha
Kkkkkkkkkk atipaseko #n yo
Misala Imeneyo .anakhuta kwambiri
zibwana zakufikapo!
Tell him to stop taking marijuana
sex prophet (aneneri onyenga ameneo
Last bad dayz
ah misala imeneo wakutha maungu