The National Registration Bureau (NRB) has announced that it will be undertaking mass registration of Malawian citizens for issuance of National identity (ID) cards starting June this year.
In a press statement, NRB which is under the ministry of home affairs and internal security says the registration exercise will begin in the Central Region.
“The mass registration will be carried out through phases 1 and 2 which will cover districts in the Central Region and phases 3 and 4 will cover districts in the Southern Region while phase 5 will cover all districts in the Northern Region of Malawi.
“In each phase, up to 2000 registration teams will be deployed to register Malawi citizens in registration centres for National IDs and it will be done at the same location which was used by the Malawi Electoral Commission (MEC) for the registration of voters,” it said.
The National ID cards will be issued to all Malawian citizens aged 16 and above while children under the age of 16 will be registered by their parents or guardians.
NRB says in the statement that there will be continuous civic education campaign to guide Malawians through the process of registration.
However, during the process Malawian citizens will be required to provide proof of their citizenship and they can do that by providing valid identification documents such as drivers licence, Voter ID, birth certificate or other acceptable documents.
Citizens with no valid ID documents can use the village register together with the testimony of the village head or local leaders or get testimony of two community witnesses.
The identity cards will allow Malawians access bank loans, free primary education as well as social services such as healthcare.
The mass registration project is led by Malawi Government’s NRB with technical support from the United Nations Development Programme (UNDP). The Government of Malawi is contributing 40% of the project cost and the remaining 60% is funded by the Department for International Development (DFID), European Union (EU), Irish Aid, the Government of Norway, the United States Agency for International Development (USAID) and UNDP.
Nanga amene nthawi imeneyo kulibe Ali kunja kwa dziko lino makoza ndondomeko yanji ndipo apanga bwanji?
Government should be very sensitive on this
Kodi lD imakhala ndi exper date?
Kukanika kwazinthu kaya kumeneku. Cholinga azikatibela tikamakapa renew.
Ku mwera Konko,ine ivo yai!
Zintchito za bwampini.#expiredate
chonde ndikufuna number ya malawi 24 tolakhan moz by me mdf chiyabwe.pls pls send to me ngat ilipo
Chonde Chonde Amene Ali Ndi Number Ya Atolakhan A Malawi 24 andipase pls pls
kufuna kubela anthu expiry date hahahah sorry for u
Dziko lokhala langa mungandizunguze nd izi?
koma mumuyambe kaye Peturoyo chifukwa akangoluza 2019 azathawa ndi black card yake ija
Koma Luka..kkkkk
inever seen ID with expiry date that is not ID u just robbing us now eishhh voice mail box
A MALAWI!! ID NDICHINTHU CHABWINO! NANGA KUMACHITA KUITANILA ANZANU KUTI AKUTHANDIZENI POPITA KU BANK POTI MULIBE CHIPHASO!! SIKUTI NDI ONSE A MALAWI AMANKA KUNJA KWA DZIKO KUTI AKHALE NDI PASSPORT,M’MALO MWAKE NDI BWINO NZIKA IKHALE NDI ID: A MALAWI SIBWINO KUNGOTSUTSA ZILIZONSE!! LIMENELINSO NDI BVUTO LA PAKATI PATHU: NDIWAPEMPHE A BOMA KUTI ZINAZI MUDZINENA MO TSINDIKA {CHILUNGAMO} CHIFUKWA NKHANI YAZIPHASOYI TSONO YATENGA DZAKA ZAMBIRI: IDAYAMBA MU ULAMULIRO WA PRESIDENT BAKILI MULUZI, MPAKA LERO, NYIMBO NDI YAZIPHATSO!! TSONO ENAFE TIKUENDELA CHIKHULUPILIRO CHA THOMAS-DIDIMO,”MPAKA NITAONA NI MASO NDIPO MANJA ANGA ATALANDILA,”!!! TISAMALILENI IFENSO NDI AMALAWI–ZIKOMO!!!!
I prophecize ID Gate. Bwino ma bwana tisawotche zala ndikusiya anafe pa dzuwa. Mwanva?
Akufuna apereke ma id’wo kwa anthu amene asali a Malawi cholinga azabele bwino chisankho it’s very clear akufuna aputsitse nda? id yeni yeni siimapanga expaya, ⚠ tsegukani kumaso a Malawi anzanga ndi mbava zimenezo zisakuphimbeni mmaso⚠⚠
Tibwera tizawapangira a fake ma foreigners
666 is around the corner. Watch-Out
idzayambira ku Refugee camp ku Dzaleka ma foreigners kenako amalawi ochepa.
koma guys anthu mukunyoza kukhala ndi ID zoona paliwepo or chitupa ulibe choyendera dziko lakunja tapita maiko anzuthu or tchula dziko liti munthu angoyenda ngati mkhumba ukafa azichita kunena wamtali oderako wezi wasitsi lofiila nanga zimenezo ndizinthu galamukani guys ntchito zaboma ndiye zimenezo guys osamangoti akanagula chimanga ever year. inu misewu mene adayambila kumanga muja simukuona kuti pankhani yama ID ndife osalilako padziko pano just think Mozambigue Zambia Zimbabwe south Africa Botswana up to Swaziland or lasutho alindizawo koma ife timachita kunyozedwa kambaa ka kanthu kochepa basi mmmmm malawi ine ndiye sadzatheka ndithu nanga boma lipange chani kuti inu nonse mukondwer
ndikuona ngati nanu simukuwatsata maganizo anzanu pankhaniyi. anthu akudana ndi ID yokhala ndi malire/expiring date. osati ngati mukuganiziramo.
Can the authorities take measures to ensure that Malawians only are issued with the IDs! We do not want the illegal foreigners to have access to them! They ate already occupying a lot of our land! Please be strict on this issue please!!
Kwa amene tili kwa aluya ife titani??
Keep it up with IDs process, m’malawi aziziwika
What about Malawians who are outside da country & why having expiry date?pliz lets not tolerate this nonsense,it’s gud to have an I’D but not with expiry date.
Y expirely date that in professional
Nice but it must be to every Malawian
Ndi chifukwa chiyani ID imeneyi ili ndi nthawi yake yolelezera kugwira ntchito? Mwachidziwikire ndi chakuti zikukhudza ma vote a 2019, chifukwa kudakakhala KT sakukhudzana ndi China chili chonse,sadakakhala ndi malire ogwilitsidwira ntchito. ID ya dziko,sikhala ndi malire oyigwilitsira ntchito
National ID imakhala ndi exp date kod? Thandizen akuluakulu mwina mbuli ndine!
Siyimakhala ndi expire date,angofuna kuti tizapangenso ma renew kutibela ndalama basi
Imakhala nayo
Alexander Ayeyeye
Cashgate iyo
Zachamba izi
Aah zopanda ntchito yanga ndi passport basi zimenezo ndi zanu. Find ways of helpng youths ntchito zikusowa mdziko,tithawila kuti pakuti ntchito pano yalowa tribalism.
Wareng Wenna Yassin Nna ake dule ko Malawi Ok wenna Bua nna ke dula kae ko Malawi
ID
Peoples from Malawi Be careful about Ur ID Government there are too clever Don’t go to take ID now 2017 VOTE 2019 please Malawi people u must first think Ur Government Needs ur All them ur ID to mix with Vote………
why the ID will have an expiry date?
My name Is John winesi i am from South Africa Good work for ID but am not thankful too much coz u make Expired Why Please talk to me Government
Akekho u john winesi wa la emzansi umqambelani amanga wena?? Ndinu akumpanje madala musapusitse wanthu ???????
hahahaha! why can’t say you’re staying in SA? uuh u John! uyapapha.
Kwanu nkwanu madala since when a south african citizen become concern with malawian IDs? mmmm msamakane kwanu coz of the poorness of your country mpakana kusilila dziko la eniake hahahaha am proud to be a Malawian citizen
Even dressing ikusonyeza kt ndi achimwene awa, kungopita mukapeze yanu ID osanena ngati muli ndi yadziko lina chosecho umalawi ukudikilani kkkkkkk so funny mwandiwazatu abro kwambili ?????
ine ndipita ku ayaoku
Dzuro ndi mawerenga Bible chapter cha #SAMUEL oyamba. koma ndinazizwa ndita peza nkhani yonga yomweyi!,DAVID anatuma kazembe wake ndi akuluakulu ena kuti akapange kalembera ndi cholinga chofuna kudziwa chiwerengero chonse cha ana A israel. koma zosatila zake #Mulungu anakwiya nalo ganizo la David ndipo anamuwusila mulili Anthu ochuluka anafa. so ife tilindimatha kodi izi sizizatigwera ife!? chonde akumipando musatibwereseleso milili ina mziko lanthu lino talangika kale ife! mavuto tilinawo ambiri.
Nice idea
Why mukuika expiry date??
Zifukwa nzambiri.Anthu ena akakula amasintha maonekedwe komanso technology imasintha kumbali ya chitetezo.
Owky ndakumva mkulu
Good development, we r waiting
Why expiring date in 3yrs gv it 10yrs
I can’t wait
Kusonyeza kut card idzakhala yokhayi osati dzimacard dzambirimbiri dziko lake limodzi lomweli
NONSENSE
useless kd titakhala opanda ID chingachitike mchan?
Ndi mlandu utha kukagwila ukaidi.666 ija munkangomva yayamba kubisalira mmalamulo adziko.
Fuck the president
Kulingana ndidziko lathu lakatangare mosakaika tizamva kuti the exercise siidafikile aMalawi onse kamba kakuchepa kwa ndalama. Pempho langa, please ngati akuona kuti ndalama ndizochepa asayambe the exercise mpaka atisimikizile kuti ndalama zapezeka kuti ntchitoyo ikayambika aMalawi onse apeze ID kwakufuna kwao and all Malawians are in need of ID don’t deprive them of their right because of your greedy of money.
Ife tili kumaiko aini tizapange bwanji kut nafe tizapeze
Muzabwera sizothamangila a bigie.
We are coming home for registration
Big ! Musawotche transport ndi zinthu zopusa ngati izi. ID mulinayo kale passport.
Kkkkkkkk best advice
Aaaaaa kod ndi ID yanji ya expired kkkkkkk km ya ya ya ya..nde mwati tisabwele
Akufuna awononge ndalama za boma pano mumalo momanga museu wa a M1 mmmmm kaya ziko ili
Zilibwino
Why does it hv expiring date….?
Kodi utha Ku user kutenga ndalama Ku bank or kutsegula acc??
kkkkk koma ma comment enaa…..nanga NRB ndi Escom?Elijah B Erick Aaahh zachamba eit mmalo mokhala busy ndizakuthima thima kwama ges
kkkkk koma ma comment enaa…..nanga NRB ndi Escom?Elijah B Erick Aaahh zachamba eit mmalo mokhala busy ndizakuthima thima kwama ges
tatopa nazo zamkutu
Aaahh zachamba eit mmalo mokhala busy ndizakuthima thima kwama ges
Good move
Good move
What about those in diaspora?
they must come back home 4 Reg
What’s the use of embassies then
can’t their passports work?
shaaaa zitiphonya izi
monse muja! khalanazoni