Anthu a mipingo ndi ena onse amene akudana ndi lamulo loti amayi aziloledwa kuchotsa pakati asayese Mafumu ali mbali yawo.
Malingana ndi Mfumu Yaikulu Lukwa ya a Chewa, Mafumu akugwilizana ndi lamulo loti amayi aziloledwa kuchotsa pakati.
A Lukwa amene ndi mlembi wamkulu wa bungwe la Mafumu ati iwo monga Mafumu ali okonzeka kuchita zionetselo ngati aphungu akane kukambilana za lamulo limeneli.
“Takonzeka kuvala mikanjo yathu ya ulemelero ndi kupita ku nyumba ya malamulo komweko kukawauza a phungu kuti nkhani imeneyi tikufuna ikambidwe,” anatelo a Lukwa.
Iwo anaonjezelapo kunena kuti Anthu amene akudana ndi lamulo lochotsa pakati sanakhale ndi nthawi yowelenga zimene lamulo limeneli likukamba.
“Nkhaniyi ena angoyankhula mwaphuma, sanawelenge za lamulo limeneli ndi komwe. Anthu otelewa asatisokoneze,” anaonjezelapo.
Lamulo lovomela amayi kuchotsa pakati linakolela moto pakatipa a mipingo atachita chionetselo chokana kuti pakhazikitsidwe lamuloli.
Mfumu yopusa ingathe kutero koma yozindikira singalole zopusazo ndipomwe tidziwe mafumu opusa ndi ochenjera
Ayambe achotsa yakeyo kenako azimayiwo
Mafumu otumidwa Ndi satana kuti athandize nawo pa nkhani yosocheretsa anthu.
Mbuzi za anthu zimenezi, chifukwa chani koma
Musatiwawitse mutu ndi nkhani za nkutu ngati imeneyi mamfumu sakudziwa kuti kodi kuseli kwa mchitidwe umenewu kuli chani akapatsidwa timalawasi basi asintha zolankhula.stupid
Uli ndele chomeni.vitosi vako.
Useless sentiments from ‘uncultured traditonal leaders’
Zopusa mafumu auchiziru
Phwaaaa!!! Landira chiMbama Lukwa,chitsilu chako
mafumu kapena fumu lukwa???? uzitolere
Ndi mphatso yaulere chotaira ndichani,mfumuyo sete zake
Zaugaru Akufuna Kuti Azimayi Athu Azifa Pamodzi Ndi Zimu Wamwanayo Kd Yiyeyo Fumuyo Akanaramurira Athu Ake Akanachotsa Mimba Amake Kupusa Aziuza Ana Azichemwari Ake
Iyeyo akutchedwa mfumuyo achotse kaye mabulazi akewo kenaka anenebwino zochotsa mimbazo
Akupangazo ndizachamba, Mulungu anati, tibelekane tichulukane ndipo tiligonjetse dziko lapasi, ndie zimenezozo kumbali yanga sindikugwilizana nazo
Mafumu ake ati?lukwa ndi azinzake ndi adyera agalu amenewa
kuchosa mimba ndikupha akanati mai awo atayepathupipawo bwezi akupeza mpata woyankhula zopusazi
Wasowa zonena wampatsa ndalama Ndani kupusa basi.
Pepani amfumu ngati uli ufiti, kapena u hawe pachitumbuka, kapena usawi pa Chiyawo, mwaonjeza, muli ndi udindo ngati mfumu kulimbikitsa amayi apakati kuti azidya mokwanira kuti mwana alimmimbayo akhale wa mphamvu, koma inu mkuwalimbikisa kuti azipha, zedi amfumu? Mwina mukufuna timichombo??
lukwa wazolowela gule wamkulu wakulamba bas
Kuchotsa mimba ndi kupha.
Mimba ndi chipatso cha kukondana komwe kumachitika m’banja.
Chiwerewere chimankhala tchimo (chigololo) chikamachitika pakati pa anthu awiri omwe saali pabanja.
Kuchotsa mimba ndi kuchimwa kawiri kwa anthu amene achita (chigololo)
Kuloredza kuchotsa mimba ndi kukanika kuletsa anthu kumvera Mulungu lamulo lake losachita chiwerewere musali pabanja kuli kusefukira kwa utchisi.
NOW READ THE WORD STRAIGHT FROM GOD HIMSELF NOT THROUGH HIS MESSENGERS!!! Bible Verse:…. Deuteronomy Chapter 28 Verses 1 to Chapter 31.
“If my people, who are called by my name, humble themselves, ………to do my commandments (which include Not to do Adultery) …….
Mafumu mumudziwe Mulungu wamakamu kuopsya kwake. Sikuti nonsenu ndi agule wamkulu kuti simumudziwa JEHOVAH WAMAKAMU mphamvu zake.
Pajatu mntundu waanthu ukachimwira JEHOVAH, mngakhale nthaka, agalu, nkhuku, mitengo, currency, morality, mvula imene zimalawa nawo mnkwiyo wake.
TAKE CARE MAFUMU musadatokosole mnkwiyo wa OLENGA DZUWA.
Mafumu ufti 2 much mboli zanu mafumu nonse
Amawauzila kuti zimenezo? Hard to trust him mwina ma allowance achizunguza mutu chalo
After all who is Mfumu Lukwa to mislead as? Just bcoz is called Mfumu ndiye tizingonvera ndi za nonsese zomwe? Mwazolowera inu kupangira business miyoyo yathu. Kwagwere uko ndi ufumu wakowo
mpasu got arrested not that he stole money but there was corruption in the process of purchasing education material so why chaponda can’t be prosecuted for maizegate
#zausilu
Aaa amfumu akut chan kma iz zaunsiru
Mfumu yopanda mnzeru yosaopa MULUNGU, mudzi wakowo ukanakhala wopanda anthu ukanatchedwa mfumu?? Ufiti wakowo kumudzi kwanu konko!!! Wanva … Umalankhula kt akutame ndani¿? Ndi nzeru zako zopusazo. Uzimvere chisoni
Mfumu yopuuuuuuuuuuusa
Zopusa zeni zeni…wats the use of condom….
Thula pasi udindo pala zeru ulije fumu yifwiti iyo yikupereka fundo yakupusa ngani iyi
Alikwa ndi mfumuso pano
Siziona
Iwe mfumu mayako anakachosamimba yomwe imayembekezera kubadwa iwe unakabwadwa osamapusa watch out
Fumu Lukwa ndi yamisala. Money monger
Mafumu adya money kuti anene izi
Mafumu akuti?? ufiti eti!!! kusavinidwa!! umbuli!! kusasamba!! chimakhala chili chani_kweni kweni??!!
Eeee
bwa??
Amfumu ake ati?? Amfumu ake aku malawi kuno akuziwa chani even ku school sanapite. Kkkkkkkk
Lukwa has a point
Mbuli ya munthu, kuteloku amabungwe aja azera mwa iyeyu. Mwalemba m’madzi never happen ngat afuna iyeyo ana ake azitero ife ang’eke.
Aziyamba ndiwowa mafumu kutaya pakatiko. Why men are busy pushing to legalise abortions? Did they consulted women the pregnancy bearers or they just have thought it by themselves to push for it so that issues of wreckless impregnation takes its course in future? This is no bho mafumu sayenera kutero iwowa ndi ma custodian of our culture not to support destructive cultures of foreign men of underworld.
Mafumu nde xchaniso znthu zakumidzi ngat izo zosayenda KO’d ziliso ndi umfulu hahahaha
Iyeyo ndi muiungu
Akazi ache ndi ana ndi omwe awaloleze kuchotsa mimba.
Mmmmm Ndezinasot Zimenez
amfumu inu mwapenga? kapena mwatan? zikanakha choncho mukanabadwa? nanga ufumu wanuwo bwenzi mukulamula ndani? mumadya fodya? ndkanakonda mukanandiyakha apo ayi ngati ndakunyasani mungondiloza mutchuke ndi inu.
Reasons?
Chifukwa??
this is against the will of God
Foolish kings & satanic
Mimbayo akanachosa amayawo iwowo asanabadwe bwenzi akuyankhula ali kuti?chifukwa chakuti iwowo anabadwa ndiye atinyase.Azimayi kumbukirani kuchosa mimba ndikuchimwa pamaso pa Mulungu.
Osamuyiwala mfumu lukwa ndiopenga misala osamuyiwala ndi wakwathu
Kodi mafumu akungotengeka zilizonse bwanji? moti iwo saziwa kuti kuchotsa mimba, ndi chimodzimodzi kupha. Komweso kuli kuchimwa pamaso pa mulungu. Mfumu yosasamara moyo wa azimayi ngati imeyi. Mbuzi ya munthu. Umbuli omwewo kukulamuliran amfumu zoona! Ndakwiya nanu kwabasi. Muyenera mubwererenso ku school za kwacha.
Lukwa akuvomeleza zimenezo amayi ake akanachosa mimba yaiye akanakhalako zopusa zakezo akanalankhukira kt?
Before you think of the procedure,you must also consider the risks of terminating a pregnancy,
Triumph anakana zimenezo ndiye mwati ma Fumu? Aaaa sindikuona kuti ziphula kanthu
ALukwa alibe mzimu woyera
anthu.amene.anathama.ngamisala.ndikutha.misalayo.ndiku.marowa.ufumu.ndiye nga.amene.zachamba.bas.osata.mimba.yakazako.bwanji.sisisiiii.
Kodi a Lukwa amai anu akadachotsa mimba inu mukakhala amfumu kodi ndinu mfumu yowopa Mulungu.
Ngati zili choncho, mafumu onse apange lawo dziko. Tione kuti adzitsogolera ndani?Manyazi alibe mafumuwo. They are fools
Mfumu imeneyo ndifit basi amagona munyanga tamuuzani ayambe walowanso m,mimba mwamace akamumwele mukhosweo amuchose.
Mfumu yopepera…ayidwetsa yellow bun(s) achina Chaponda
Kodi Lukwa amafuna ange yani? Siyemweyinso uja amati tilole mathanyulayu?
Koma chambachi abale, ndi mafumu omwe?
Mundu ameneyo anapasa ndani ufumuwo machende ake nditu mayi ake akanachosa mimbayake ufumuwo akanawupesa nyini yamayike nditu
Ndichifukwa anthu akuti ziko lathu tsopano Satana akukulira kulirabe.Dzikoli ndilosauka kale ndiyenso tikuputa mkwiyo waCHAUTA pakukuyenda bwino?.Mafumu ngati mwasowa chochita museke pakamwa panupo,kodi kupanda anthu unu mukhalanso mafumu?.Mfumu amene wanena zimenezi amangidwe chifukwa ndikupha kumeneku,komanso ngati kwaiyeyo ili njira yabwino imeneyi: ayambe iye kupha ana ake onse anthu akuona kenakono anthu ayambepo kutaya Mimba.Mfumu yopusa kodi ndikusauka kapena ufiti?.
Naa mayi olingalira bwino sangachosese mimba chifukwa akuziwa kuti kuchosa mimba ndi tchimo chifukwa wina aliyense akamapanga zimene amaziwa zosatira zake ndiye ngati usakufuna kutenga mimba kulibwino kumangopewa chigololocho chifukwa ndiye tchimo limeneliso lafika poyipa dziko lathu lino
Basi tingoti mulungu amukhululukile Santana akumuzunguza ameneyo
I Wonder How Relevant These Cartoons We Call Chiefs Are To The Development Of Human Values In Malawi? They Are A Total Waste Of Space- I Wish The Country Aborted Them Instead Of Aborting Innocent Babies!!!
Alukwa nawonso ndochitsiru ati? Pamsanapawo!!
Opani mulungu osaopa munthu
Ankanfunse Dan-Lu kuti mimbatimachotsa?Fumu yopanda nzelu imeneyi siyomwenso ilikumbuyo kwambava yotentha ma file a maize Gate xuiiiiiiii!!!
Mafumu chawakulira ndi mantha akakana ufumuwo ukutha ndiye kumangovomela chilichonse
they r muder!!!!
A lukwa mutu sugwila avetsetseni
Lukwa politician kkkkkk chamahala palije
Oyambe ndi mwana wawo bwanji. Ufumu wakewo ngotani mukuti olukwawo.
Osamaone ngati Ochewa timakogdwa omachita iwowazi. Omewa omapembedza Mulungu uti kodi?
Olukwa msatengeke ni onthu o ndale, tsatani chikhalibwe chanu tele!!!!!!
Chalandila ndalama I hi mbuzi
Malawi wanga ukupita Kuti?
Ya amake Lukwayo
Kodi lukwa ndindani?who is lukwa?very stupid &fuck you nonses,mafumu ake ati anenanawo zimenezo? Shit lukwa you decieve yourself &fuck you!
Mafumu akumalawi ali ndimayina,ndeye inu tatchulani dzina la mfumu yavomereza izi
God says do not kill,how deay u want to go against him.
Aaaa Koma Galu Ameneu
kaletu inu mafumu munali dambo mozimilamo moto lelo mwasanduka zinyalala zokolezela moti
Agalatiya oyamba ndizabwino kutsirizira ndizoipa….anakulodza ndani?
Amako adakachosa mimba bwezi uli mfumu?Galu iwe eti
Malowa sataniki mukufuna mudzitenga magazi panya pako
Zopusa zaimenezo akanakhala agogo ako anachosa pakati abambo ako akanabadwa?.Ngati uli ufiti munene .ayambe ndi akadzi ako iwe lukwa
Akanayambira pa iye mai ake bola,…… Mfumu zozolowera ufiti ndichoncho koma ndi galu bwanji
Papa Lukwa lamulo limeneri akanavomera a Lukwa oyambirilawo inu nkukhala mgulu lochosedwa mukanauziwa kodi Ufumu wa dziko la pansi mukutumbwa nao lerowu … ???//??? Shame on u … !!!!
Iyo ndiye galu yamafumu onse
Jesus may you slap this man?.
He is idiot
Ndipo poti wanena kuti ndimfumu ya achewa koma akangokhala ndimisala ndikubwela kuno kumwela azaonachimene chidameta nganga mpala lizamuthela ziko komkuno ndipo uziti mafumu anyau osati mafumu akuno kumangochi fack you mind like animals
Lukwa ndchtsru chenchen amay ake anakachotsa mimba yake anakakhalako iyeu mesa mumat Malawi is God fearing nation ganzranpo
Chitsilu chamfumu mapazi ake
Satana wapolamira malawi
Ndichisilu Chiuze Mkaziwake Azitaya Mimba Or Amayi Ake Akanataya Iyo Bwezi Aliko Iyo
Iweyo akanakutaya amai ako ukanakhara mfumu?
M’yeyo achimutaya bwezi ali mfumu mdichitsilu ameneyo
Adya za nao zakumidima
Pantumbo pake
mfumu yokonda ndalama tingopempha wamwambayo kuti akukhululukireni mfumu co simudziwa chimene mukupanga?{mwakutidwa ndimphavu za satana dyerekezi}
kodi iyeyo LUKWA amanamuchotsa amayi ake? shupiti
Ku chotsa mimba ndi kupha komwe,ndie popeza iyeyi akugwirixana Nazo ayambe iyeyo kuchotsedwa,chitsilu cha munthu,ana NDA tsogolereri amawa,ngati anthu achuluka kuli bwino kuchotsa akalewo opanda nzeru komaso mbuli ngati zimenezi,akupatsaniko ndalama za maize gate zo eti, munthu ukakhuta umapita ku chimbudxi kukakhuthula ngati mwakhuta go to the toilet rather than coming here talking za uchitsiru.
zachamba iwo mayi awo adatayapo mimba ?
Mfumu yongaza imeneyo!
Mfiti
Lukwa atchuke ndi zopusa
Yesu akabwera akuwona ngati adzakhala mpaka mpaka makape panonso mamfumu anatha angokhala mayina chabe komweko mimba imabwera yokha ? Ngati sunakozekele anakugwiririla ? Mwakhuta basi tichotse mimba tiyamba tachotsa inuyo inabwera. Asanakozekere amayi anu kuti berekela anthu opanda nzeru ngati inu ndinu ndani kuchintha zimmene mulungu anakoza ngati uli ndi ana akazi okha okha basi tsakulani. Ma Bar kkkkkkkkkkkk
Mafumu adyera ngati awa sakufunika mdziko muno.
Kupenga basi mafumu a chimalawi.Kod ngat inu akanakhara ndi maganizo ocotsa mimbayo bwezi mulipo?Mulungu akulandan ufumu
zizindikiro za masiku osiriza
Lukwa Lukwa iwe, koma uli ndi ubongo? Mafumu ake ati? Lamulo lake liti? Umadya matewera a ana? a Lukwa a Lukwa… allow only women within your chieftainship tione ngati uzakhale ndi bumba in few years to come, kupusa! Chitsiru chimati mumtima kulibe Mulungu, oti kulibe Mulungu amati azimayi azichotsa pathupi, ….. Mukufuna kutinyazitsa a chewa bambo, ngati mwalandira chithumba from those pushing for the law, ingodyani bambo, mukutiboola m’makutu ife
Chindere chamunthu ichi
Shupit Chief, Why Talking Shit Like That? Dont U Know That It Is Killing? Child Of The Devil
Mamfumu ena zitssiru akuoneka ngat azeru kufuna kukhala mbali yaboma kut alandre zambiri mfumu yopanda nzeru chitsiru mfumu imeneyi
Mafumu ake aboma lakwanu fokolo ndipo kuno ku Nkhotakota tiwathyola miyendo akayerekeza kubwera nditifundo tawo tamakoponi fiti ua chabechabe imeneyi
Mfumu yopusa yosayeneraxo kusogolera anthu mbuz yen yen ,ngat wapasidwa ndalama zochuluka ukhaula,azichosa akaz ako
Iyeyo akadachotsa amai ake bwenzi pano ali mfumu, mbuzi yamunthu, kwanu komweko ndi mbumba yanu
Mafumu opanda nzeru achotsedwe paudindo
Lukwa akanayamba amiako first kukutaya iwe bwezi zikuveka wava undiyakhulisa pambali pakati ndikupakuona wava
Zonsezi Mukumva Ndikuona Izi Ndizizindikilo Zoti Mfumu Yama Mfumu Ili Kudza Patsala Pang’ono Kuzaweluza Tingokhala Okonzeka
Mfumu Lukwa ndiamene avomeleza osati mafumu iyayi; chifukwa amfumu athu kuno amakana nkhani imeneyo.
Machende ake lukwayo
Kumbukirani tsiku lomwe muzakhala muli kunfunsidwa ndi angelo odziwa ntchito yawo kuti, kodi munkachotseranji mzimu wamunthu? Ndipo kaya muzakhala ndimayankho koma dziwani kuti mayankho anuwo sazaphula kanthu.
Kodi nawo mafumu ake atiwo omwe akulamula zombwambwanazo mfumu ndindaniso mesa ngati akufuna mesa aziwawuza azikazi awowo kuti azichotsa mimbayo ndiposo iwowo akulamula ngati zikanakhala zimenezo ndeno iwowo akanabadwa mafumu mwandikwiyitsa kwambili ndipo achitsilu apresident kumangolamulila zilizose usilu okhaokha basi koma choti mudziwe chawuta akuyang’ana zonsezo ndipo chauta akulangani muwona ndipo azakulangana
Osati mafumu…..mziti lukwayo
Afuna dzimatumba azika sungamo ndalama ndi ndondocha zaziiii zamkutu
muzingotamba osatipusitsa ife, mukufuna muzikadya eti
mwati asing’anga akuti chani. ??
Ufiti palimbe ku chosa mimba. Panja mafumu Ufiti. Ineyo mfumu [email protected]. Sindingamvomereze kuchosa mimba
Kodi inu mazifum akadankhala azimanu adakuvulani ndi kukutayani mchi mbudzi bwezi mulipó munganize bwino osati mopusa ndinu opusa
OSATI MAFUMU OSE MFUMU LUKWA YO NDIYOMWE IKUFUNA. KULIMBANA NDI MULUNGU AKAKULANGANI. MA DEMONDS.
malawi for sale! the offer goes to devil first
Kamfumu kopanda dzeru n pot peter mthalika anangokula mutu dzeru alibe dat y ali phwi mu ofece kukhalira kudya zigege pamoz nd lukwa wakeyo mafumu otero ndkanakhala ine kut ndkulamula dzikoli ndkangotuma ma bombocrat akangomotchera munyumba n kupasa ufum nd munthu oti dzeru alibe n iwe lukwa ngat ukuona kut ufumu ukfuna ukhalepo wekha chosesa mimba imene mkaz wako ali nayo!!!!!!! Ndwexo kape n ndangokuklangiza usabwere kuno usiku ndzakhala ndtagona ndaona ngat magaz a anthu akukuyenda kumaso coz unazolowera kumpha !!!!!ufit bas
Ngati kuli munthu wopenga, gulukunyinda, mende, kwidemtete, ndi lukwa. Muli yamunthu. A P M naenso kupepera ndikumamva zokamba zambuzi izi, lundu, lukwa. Iti nditiwanthu tokonda katangale maningi
Lukwa padzakuti pako wanva?umve komwe uliko mapazi aambuyako
Lukwa uchose nyini ya mkazako kut. Asazabelekeso mbole yanuyo man
Stupidity
Mafumu ake ati?, poti nanenso ndimfumu ndipo sindikufuna
Kodi Lukwayo wadyesedwa chani, kungo dzambatu basi from Noway?
Mafumu osaganiza ndamene akumakamba khani ngati zimenezi .akumaiwala kumene anachoka .akula afuna anonge malawi watsapoyi
Ndiye chambacho chimenecho,? Iweyo mayako anakakuchosa bwezi ulipo ,ukulephera tchito yako mfumu iwe
mafumo omwe akuvomera nkhalidwe opusawo ndi opanda nzeru
Ha ha ha Fumu yozungulira thako ngati Lukwa simnaione mmalo mokamatch pankhani ya Chaponda akukamatch nkhani yopha ana heee abale zilikunooo-o-o!!
devilish useless, mafumu ndi anthu okonda mankhwala ndiye sizachilendo
Fuck them
Lukwayo ndi mfumu lero chifukwa choti mai ake sanachotse mimba yomwe munthu wake ndi iyeyo. Bakili (Atcheya)paja adati:munthu amatha kukhala wankulu koma alibe nzeru.
Mbuzi ya mfumu azichota akazako ndi ana aki ndi xi dzukulu zako anakakhala kuti amayi ako anachosa mimba yako bwezi uli mfumu iweyo
Lukwa , ukanakhalako iwe , monse muja ankavutika ndi usiwa amako bwanjj sanakutaye ? Tombolombo iwe eti .
ufumu Wabwino Ndiochokela Kwa Mulungu Apa Zaonetsakut Lukwa Ndiwamasiye Maiwake Sanaone That’s Y
Mfumu iyi imakamba zofoila nthawi zonse. Palibe chanzeru chomwe inakambapo ever since. Useless chief
It must be fake news paja ndezawanda kulikonse…… but if it true this so bad and very shameful thing.
Mfumu Yopusa
Ali ndi mantha ndi ana obadwawo kuti angadzamulande ufumu kapolo ameneyu
Asiye umfumu akalamba ameneyo basi
Kodi a Lukwa mikanjo ya ulemelero mukunenayo ndiye yoti? Makape inu mukanabadwa amanu akanachotsa mimba?
pantumbo pawo
Iweyo mfumuwe akadakhala kt amako adataya mimba yako lweo bwenzi pano uli mfumu?aaaaa,alukwa mwaganiza mopusatu bwino munyonzetsa nazomafumu amnzanu
Azifumu ambiri samadziwa mau amulungu koma nyanga basi, Auze kuti amulandire Yesu maganizo ngati awa sadzakhalapo mpang’ono pomwe.
Walandila banzi ameneyi amuuze mwana wake zimenezo mfumu yanji yophunzitsa anthu ake zopusa Ndikukuuza iwe Mfumu Lukwa udzafa ifa yowawa ukangolengeza kwa anthu ako zochotsa mimba udzafa ifa yowawa
Inkosi #Lukwa, where will you get mbumba if women are allowed to do it any how?? “i can only support maganizowa ngati pokhapo ngati mimbayo mkazi watengera pa ntchire ndipo ikusowa bambo polingalira chisamaliro cha mwana odzabadwayo”. kapenanso ngati mayi wamimbayo ali pa chiopsezo cha moyo wake apo mpo ee!!! not any how as this will increase chiwerewere malpractises.
Sinanga iye sanabadwe njila yogonana Amake ndi Abambo ake Machende ake Mfumu imeneyo
Thus why we say and believe chiefs practice witchcraft. Abortion is killing , PERIOD. !
may the God Almighty my king punish abanduntry
Kutamba
Mulungu akuthirani nkhondo tiyeni pangani muone
Ngati kuli Chitsilu China chamfumu nde ndi lukwa ndipo ngati samatamba ameneyu mmmm Matewela amadya ndithu, iweyo amai ako akadachotsa mimba yako ukanakhala ndi Moyo iwe ? chitsilu cha munthu iwe ndipo ngati ukufuna kuti azimayi azichotsa mimba iweyo uzilamulila chani kapena sumadziwa kuti dziko ndi anthu? Kopeka NDA Satanic anzakowo chitsulu iwe
Kuzolowela ufiti samapephela amenewo musachotsele kapena kuphatikiza zolembebwa mu baibulo if mumapephela simudakalakhula zozelezeka ngati izi Malawi ndidziko loopa Mulungu osati munthu noted
Zautsiru basi satanic eti
Akufunika Deriverous Amfumu Ameneyo Yapabela Bela.
Akufunabe Nyambo Azikagwirila Shaki,ndiye Alukwa nawo gaza yawo yafoila kotheratu,
Sgt. Lukwa, kodi chamba chija sunasiyebe?
Kod mfumu imeneyo bwanj ngat wasowa zochta azingozikanda?zachamba et?
Mfumu Lukwa yotengeka ndizilizose dyera basi
Komazinazi mukamapanga muzidziwa kuti mulungu akuwona ndipo adzaweluza machimoose
Tivote basi, kumvera mfumu kapena azibusa! Ine ndayambapo, mafumu olo kuwafunsa malamulo khumi a mulungu sakuyankhani, that’s y amati umfiti kulibe whay! Ali momo , ndavota pamenepo. Kikikiki
paja timafumu tambiri ntima hule tinazolowera kunyenga tiana cholinga mukatipasa mimba tianato muzikachosesa muzikati ndi ufulu zopusa basi mesa kukhala mfumu ndi chambumba kodi ndiye azichemwali anu akachosa zimimbazo lnu mungakhale ndimbumba uhule basi
#GOD_IS_WATCHING
Afumu akut ameneo
Amfumu akuchita sapoti zimenezi boma liwachose pamaudindo lero Ndinu opanda nzeru .
Kupepera basi mafumu a chimalawi,we are losing hope in you,kungobvomeleza zili zonse.
Alukwa Bvuto lanu ndichani,,,,,,, inutu ngati mwadya zambili za dpp zikupangitsani kuti umfumu ukukanikeni kuyendetsa za ndale zikuphweteseni
Zachaba
Iyeyo fumuyo mumufunse kuti iweyo amayi ako akanati ataye iyeyi alim’mimba bwezi ali mfumu chitsilu chamuthu chimenecho
Iwe akanakutaya bwenzi ulipo. Zopusa basi.
eshiiii mafumuwo mafumuwoo! kufuna kutchuka eti? muzafa muli mphawi choncho.
Mfumu imeneyi ndimwana wa lusifala chitsilu chamunthu kod amai ake anapanga abortion bwenzi Ali ndani
Fumu yanji imeneyi, osateteza kti isatengedwe koma ikachosedwe kupusa eeeti
Lukwa a babylonian king God nuh punish yah
Kupus ngati msima mfumu yombwambwana koposa. Ufulu wanji otukwanatnkunyoza Mulungu uwu? Uwauze ana ako kapena zidzukulu zako zidzitero ndipo tizaotcha moto mukasewera. Ungalamulire dzikowe? Matambala mwadyawo akuphetsani nthawi isanakwane
2000
Kkk
U chiefs, wat if ur mam had aborted u, wud u exists/?? Mafumu nonse mukuvomereza izi go to hell before we force you ourselves!;!!!!!!!!!!!
Mafumu opanda nzeru ndiamenewo, amayi awo akanakhala ndichisankho chakuchosa mimba bwenzi iwo aliko?
Ma Ngos kaya mafumu noxe in support of this satanic point mimba zanu…funso langa ndi lakuti kodi anthu azipitabe ma church kumakapemphera kwa ma prophet kukafuna mphatso yamchibelekero atachotsa mimba 15 pa zaka 20??
#Lukwa amayi ako bwanji analekuchosa yayiwe opusa akudyesa ndalama eti
Ife Zochotsa Mimba Ayi Mafumu Opanda Nzeru Mesa Amaimilira Anthu Ndiye Maganizowo Akuwatenga Kut Ife Kupha Ayi!
Ichi ndichifuniro chakumidima izi zikavomerezeka ndekuti maiko azungu akondwera koopsa,,,,mkazi akamachotsa mimba magaziwo azitengedwa mmphamvu zamasenga nkumakathira nsembe kumalo osutsana ndimlengi ndati zikangotheka posachedwapa mumva ma redio akusokosa ma donors apereka ma million mwakuti kudziko la Malawi,,,,,chithandizo chakenso chothera kumipando!!
Ambuye atithangatire
Iwe Sukunama, Olo Kansa Yamuchibelekeloyi Ngati Yiliyachilengedwe Ndakayika,akachosamo Zibelelozo ena alinazo buznec,ndiye Alukwa Andinyasapo Apa.
Ali ndi milandu patsogolopa
Kupewa kuposa kuchira!
U r a very stupid chief….and i beg ur villagers 2 kill u in anyway .
koma mfumu iyiso inu yaganiza bwanji iyo
Mafumu nde chaniso zianthu zosazindikila kumangodalira zisamba basi mbuli zenizeni mmufunse mfumu Lukwa kuti zikanakhala bwanji iyeyo mayi wakeyo akanachosa mimba ya iye? Akanaupeza ufumuwo? Zausilu basi?
Hahahahahaha kkkkkkkkk
Kkkkkkkkkkk
Mumat malawi nd dziko lowopa Mulungu , nanga fundo imeneyi sikupha?
Mafumu a dyera
amfumuwo mukawafunse kuti mayi awo adakachotsa mimba yao iwo alipo?ngati yankho lili ayi,mafumu amene mwanena izi pokhalilapanu mafumu!
uchitsilu wa mfumu mwina naweso wadya chibaz panya pakopo galu iwe mwina ukuyankhulila kumbuyo ukamuuze mukaz wako wava chitsiluwe galu yo weta iyi isaa
Stupid Chief with no brain
Mafumu onse adziko la pansi pano alephera,Tiyeni tidikilire ufumu uwu ukupezeka pa Daniel 4:34 . Pakuti mafumu apansi pano akuchita zomwe Zinanenedwa ndi Mlaliki 8:9
chako ndi chako basi
Evil thinking!
Had It Been That Ur Mother Aborted U, Would U Be Achief Today? Think Before U Say Abortion Is Killing, God Will Punish U If U Dont Care.
Fumu yopusa imeneyo
ximezo nde za chambaxo anakayamba mayi awo kuchosa mimba yawo bwez nafe tkvomelexa
Mafumu Adyera Ndichoncho Afuna Azikadya Kumaliro Ko.Osangowaphunzitsa Njira Zolelera Bwanji.Mxieeeeee,mbuzi Zamafumu.
Ngayi kuli mfumu imodzi yopusa ndiye lukwayo ndipo amene anabvomeleza like a ameneyu kuti akhale mfumu ndi afiti anzako caus mayi wako amachotsa mimba yaiweyo maganizo opanda mzeruwa bwenzi ukulankhulira kuti kuzolowera nyawu kapena ndipo anthu akwalukwa m ulibe mfumu koma chigawenga Chopha anthu musamale
Mafumu ena anangolowera poti za Ku mtundu, koma mnzeru alibe.
Sanaganze Bwino Ameneyo
mfumu lukwa inu mukanakhala mfumu popanda anthu ? ganizani bwino musalowe ndale ndinu mfumu yawanthu taganizani bwino
ayambe ndakazake kuchotsa mibayo tiwone ngati akabwere ndimoyo
Why ?mmmmh, Mafumu Ali Ndi Ziwnda Zochuluka, They Are Not GOD fearing people, but they will be rewarded in the hearafter?
Lukwa, ndiwe mbuz ndipo ndikutembelela kwa omwe anakusankha kt ukhale mfumu, kd mayi ako akanachosa mimba iwe ukanakhala mfumu? ndiwe opusa kwambili
Ngati mfumu ameneyo walandira ndalama akabweze
Komatu mafumu ena,adzafera za eni
Mafumu openga mwapanga bwanji?.
LUKWA UR RUBISH AND FULL SHIT MBUZI NDIDAKAKHALA PAFUPI NDIDAKAKU MENYA MBAMA.IDIOT MFUMU
Kkkk yaaah mafumu ozisata kkkk
Mmm! Inunso a MALAWI 24 Musanyozetse mafumu anzeru apa amenewo ndi maganizo a # Denis Lukwa ka GVH Ka pa ntcheu akufuna akazi akewo azichotsa mimba atopa ndi kubereka ana onyasa.
Ayi ndikupha kumeneku
STUPID IDIOTS! Izizi ndiza UTSILU
mfumu yoputsa imeneyo
Afumu Lukwa its better for u if get tired ndi ufumu to handover the position to your nephew’s ngat nkumkwima mu obongo zitayeni izi .
Go to hell wth ur stupid ideas
Anthu anga akuwonongeka chifukwa chosadziwa Ambuye mutichitile chifundo
AMene avomereza ndiwasatanic mafumu nonse ndinu opusa
Crazy country with crazy leaders. I think they dont know wat they are doing or wat abortion is
Amfumu amenewo kuyakhula mosaopa Mulungu, zoti nditchimo alibe manthayi..God forgive this man calld himself Chief…
Is that mfumu on the picture?
munthu opanda umunthu iwe subelekaso iwe, usatipatse tchito,fumu ya n’tundu wanji iwe,napankhani imeneyi yandinyasa kwambiriii.Munthu wa mutu kumiyendo,galu,mphaka kalikukutu,mphevu,koma iweeee!!!eee.
That mfumu must be suspended
A lukwawo amene akuwambisayo onse ndizisilu zopanda dzelu angulu kunyinda,anthu oanda chitsoni
Mafumu amene akusokoneza ulamuliro wa dzikoli nawa: Lukwa, lundu, Kaomba ndi Kyungu. They think they are the most civilised chiefs in the country kkkkkkkkk?
Shopiti zao mafumu amenewa anthu opanda umunthu awa.
Mwaiwala Ngolingoliwa
Awa simafumu koma andale,kawirikawiri akupanga zinthu zautsiru,ngati azimayi azichotsa mimba ndiye anthu achuluka bwanji pamudzi?mfumu ndi anthu,sungakhare mfumu popanda anthu,
thats demet mfumu imeneyo ikhoza kukharaso mfiti
Lukwa. Ur foolish chief. Ungakhale fumu iweyo kopanda anthu. Be serious in thinking
Mafumu opanda nzeru amenewo.Akatangale, Osaopa Mulungu, okhwima. Aweruza bwanji akusowa nzeru ya Solomon.
satan is using you do whatever you can do but finally you will get a result
Ayambe kaye iyeyo kuchosa mimba ya mkazi wake kodi akanamupha iyeyo bwenzi pano ali mfumu??
A stupid chief & he dont fear God,he need a special deriverance.if it is money take care
Amfumu onani zanja likulemba pa khoma, ufumu wanu wapelewera ndipo pokutha pa week ino simukukhalanso mfumu
I am from Canada I don’t understand your language. But APA mafumu apenga misala. Zoona mafumu akufuna ana osalakwa azipedwa. Anywhere admin I like your handwriting keep it up
Thank you Mr Canadian
A Peter Dennis Mandevu mwati zikomo OK . ndathokoza
Good comment..ngakhale I don’t understand your language. .koma mwakamba mfundo yabwino ndakumvani..kkkkkk
Kkkk. Ndimayesa fumu ndianthu, nanga mafumu akati ana ammimba aphedwe nanga ufumu wawo upita mtsogolo. Nanga Iwo mafumu akhala mafumu azinyama zakutsire. That’s why I am a virgin and I will die a virgin to set a good example to my kids
Akulu from Canada so you don’t understand chichewa? Then how possible you put your words in chichewa?
Ameneyo Ndie Canadianyo Akapsa Mtima Amanva Cicewa Mkulemba Komweko
Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkk:Dzosangalasa kwabasi big up mr canadian
Kkkkkkk am from America I don’t understand your language but fundo yanu yokha ndamva
Kkkkkk very funny Mr Canadian what?
If mafumu enieni osati awa akonda ndalama. Chilichonse yes bwana. No ayi bwana
Kkkkkkk koma abale fodya sizinthu guys
Mtumbuka kuonetsa kuchenjera Ku Bt
Iwe Chris Blair Mahukah go to hell .mtumbuka watani. ..tisiye ife we are loving this comment ,,,, anyway am Asian American by origin
eee koma guys mumafuna mutakhala akunja, kkkk limbikilani chaka chamawa mukabadwira ku Canadako
iwe lukwa bwanji iweyo mai ako sanafune kutaya pakati pomwe amayembekezera iwe kut ubadwe , zoputsa basi
…inu inu musatitopetsenso mwamva. tandipatsani phone number ya nkulu ameneyu plz
mafumu adyera aku Malawi,wopusa ombwambwana mfumu yochititsa manyaz dziko lanulomwe kumamvera anthu obwera,amfumu inu mundisamale ndi mfundo zanu zopusa,adzipanga akazanu ndi ana anu zachambazo
OSATI MAFUMU KOMA KUSERI KWAMA MFUMU KULI ATHU ENA AMENE AKUPANGISA NDE MUWONA KWIYO WA MULUNGU NGATI MA MP MUVOMELEZE KOMA ZIWANI ICHI MULUNGU SANGAKHALE OPUSA NDIKUKUPANGANI KUTI MUZIGONANA THEN KUTENGA MIMBA NDE NGATI MULORE ZIMENEZI MUSAFA IFA YOWAWA
nonsense
Mfumu yosaopa mulungu, kulimbikitsa mchitidwe wakupha ndakwiya nanu alukwa kooopsaa ngati ndiumphawi kaya zativuta
OFUNIKA MULUNGU AWAKATHE
kenako timva kuti mukusapota gay marriages!
mfumuyo ndichitsilu kwambiri iyeyo zoona okhala mfumu mkumayakhura zopusazo chonde a Malawi posakha mafumu mmudzimo osamasakha poti ndi mkala kale ayi
eeeee mafumu ndi choncho amafuna ana wozizira kuti azikhwimirapo , kuchotsa mimba ndikupha , amfumu inu mziwe yesu ,
Galu weniweni ndithu.ufiti kuzolowera kudya makanda eti.alukwa you don’t deserve to be a chief
Amai ambiri afera kufuna kumva chokoma. Iwo sadziwa kuti chigololo chosadziteteza munthu amatenga mimba. Inuso mukuvomelezanu amanu anakakuchotsani bwezi muli pamenepo. Uchembere wabwino sikuchotsa mimba, koma kudziwa njira zabwino zopewera mimba osati kupha ai.
You can see how money can make a chief who is corrupt to make wrong decisions.
Mukamva mfumu ikutero mudziwe kuti ayifumbatitsa kenakake,mafumu athu ndi anthu opusa omwe amgwiritsidwa pazinthu zili zonse. Anthu akamagonana amadziwa kuti zotsatira zake ndi mimba,ndie muwalola bwanji kuti achotse? Mimba sibwera mwangozi kupatula ngati mkazi wachita kugwiriridwa.
Apa timati monga mwadzina lawo loti amfumu lukwa,amfula,ufumu wawo ulibe zelu,kodi kupha ukuona ngati mkwabwino,mulungu amukhululukire ndithu zamanyazi.,,,shit!!!’,,,
I think he has been corrupted with chickens for him to support that evil and demonic idea, stupid Chief!
Zitsiru za mafumu. Zikuona ngati azipasa ndalama pajatu dyera afisi amenewa.
Think twice mafumu sizoona aliese amaziwa popanga chinthu
Pofunika azipephela sakudziwa chomwe akulakhula
Chitsiru Mfumu Imewo Akudziwa Chimene Akuyankhula Koma?
ufumuwakeuti ukumuyankhulisa mwapaujenipakewo, chisiluso chimenechi eti, boma lichitepokanthu ndithu apobi ndithananaye ndekha galuyo
mapazi anu amfumu
Chisilu cha mfumu
Its evil
#_Lukwa i think you really dont know what you are tolking come on shame on you are you indeed a true king? watch your back please.
Stupid ndiye kuti chani kuputsa
Mfumuyo muyiwuze osamuke kumalawiko ikafune malo mayiko ena omwe angalole uchitsiruwo. Ndipo tiyambe ndi mfumu imeneyoyo Death penalty palibe angasekelere zopusazo
Mukauze kamfumuko kauze zizukulu zake azipanga manyi akunenawo!!!!!!
osamangoti mfumu enawa ndumadevilz
IWE FUMU PAKO AMAYI AKO AKANATAYA MIMBA YA IWE UKANAKHALAPO zopusa ayi
NOSENSE#FUMU#ORGANISATIONS#
ndipatseni nambala ya a Lukwa wo ndilankhule nawo.. iwo amayi awo anakawachotsa bwenzi akulankhura mopanda nzeru chonchi,, kodi munthu watenga yekha mimba, ayichotseranjinso? amene asafuna mimba akabaise kulera, osati kumatenga dala mimba nkumati mkachotsa , ayiiiii.
Open your eyes guys dzko likutha ili
mfumu yakumidima fire in Jesus name every demon aut mukuyenela mamasulidwe
stupid
no to abortion. zochosa mimba zanuzo a Lukwa opusa inu
Satana iwe!!!!! Ayambe amako kutaya mimba ya iwe. Ukuona ngati udagwa kumwamba eti. zoti iwe umavala ma tewela ndikumabibidwa ukuziwa? Ngati uli umphawi amalawi, Bola tingoyamba kugulitsa malitseche athu. tonse tokhale othena kuti mwina tikhale olemera komanso mimba zichepe kusiyana ndikumayikila kumbuyo mchitidwe onunkhawu. Ukutero akazako achitatu aja mimbayo achotsa liti???? Mxiiiiii!!! Ndakwiya nawe koopsa!!!