Angry residents beat three Police officers

134

Three police officers have sustained serious injuries after being beaten by angry people from Dedza district following the arrest of a suspected thief.

According to reports, the police arrested Samalani Chikwita, 44, whom they suspected of using a boy to steal from shops in the district.

Following the arrest, bicycle hire operators commonly known as ‘Zobanduka’ mobilised to free the suspect.

The residents invaded the police station and started to beat officers on duty to force them to release their friend.

Confirming on the local press, Dedza Police spokesperson Edward Kabango said the three police officers have sustained serious injuries.

The police have since arrested two men suspected to have taken a leading role in the attack.

The two, Nyumani Katunda, 28, and Christopher Filimoni, 26, come from Katande village, Traditional Authority (TA) Kamenyagwaza and they are to appear in court soon.

Share.

134 Comments

 1. Think what could have provoked the situation? mukadatifunsa ife eni ake omwe timaona zomwe zimachitika, Just because wa police akakhalapantchito samalakwitsa but things went wrong somewhere, it is very unusual for oldinary people to beat the so called law inforcers! am not behind this habit koma nawo apolice adzigwira ntchito monga mmene adaphunzilira ntchito yawo munthu amene akuti anawamenyayu analiyemwenso wathandiza kugwira mbava ku Bembeke kuno mwachitsanzo the very same guy helped the same officers to recover astolen motorbike just to mention afew lero munthu yemweyu waipa chifukwa chani fufuzani before God the officers know why they were beaten and adzakhalabe akumenyedwa ngati siasintha kagwilidwe kawo kantchito

 2. Guyz why, why, why, I believe the police wil do something to those foolish why beating pple who help us lets work up guyz.

 3. Angry thugs in Dedza beatup Police officers or could be that the arrests were aimed at bringing a few extra Malawi Kwachas to the officers’ pockets on Police payable “BAIL BONDS”.

 4. iiiiii angoni kuba kwambili,kutsitsa,kutoma,ukapsyala ngochuluka and this dedza area mlanda area in ntchewu,mwamasasa mmenemu anyamata salibwino!aboma muthandizeko pilizi!

 5. Ndiye Kutiona tapolice tache,m’kumati awa ndikugwila munthu awa?!! vuto la ntchito zogula ndikulembana chibale.mukamapanga zopusa n’kumati ndiwe gaurd wa police muzikwapulidwa!

 6. Shit !! Umbuli basi !! Wy beating police officers ? If they beat u people said our police doesn’t know their job but if u beat them u boast and say apolice ndi opepera nosense . That’s wy ma soildiers ( mdf) akumalawi amangokhalira kutibula anthu ndawona anthu ndi zitsilu

 7. Guys police matsiku ano ayayamba kunyanya akumangomenyedwa zina zilizose eti!Mmm kukhalangati sanapiteko Ku training. Nanga kwa mbamva angalimbe ? Eeeeeeeh kaya aziona…

 8. Ndikuona ngati uthengawu suunalembedwe bwino!! Apolice pa ntchito yawo ayenera kugwira ntchito moyenera ndi mulandu m’mene ulili!! Sono mukutiuza kuti amenyedwa chifukwa amanga mbava?

 9. Kkkkk Guys Zinali Zoseketsa Komanso Zomvetsa Chisoni,komabe Awachita Bwino Coz Anaziyamba Dala Anaonjeza Kkkkk! Am Eye Witness Ndithu!

 10. Kkkkkkk enanu tengelanipo phunzilo; mumaonjeza azilonda inu;tisagulitse mankhwala kunsika mukutilanda;ndiye mukatelo mudzikalemelela uko; naneso ndakonzeka;ndipedzeni ndikuonetsani agalu inu; mulindi unyolo omangila amphawi okha osati chaponda; ndidzimene amakuudzani ambuye anu pitter; kkkkk akupwetekedzani mudziona agalu inu;

 11. They are the ones that send the suspect thas why we beat them all leter Meyerhalika told us to do so , mavi ghinu mose.

 12. so you mean you people are in support of that suspect? come on! when a police officer beat a civilian you say police officers are cruel and when you beat them you say they are powerless, mind you pollice is there to protect and enforce the law they are not there to fight with the public.

  • sometimes chikakhala kuti chinthu sichinakuchitikire you can never see the importance of police officers, until utakumana nazo, mukanakhala kuti okuba amakamupulumutsayo anakuberani nyumba mwanu, and katundu wanu wambiri wasowa mukanayankhula chonchi? sometimes sibwino kumangoyankhula for the sake of kuyankhula

  • kkkkkkkkk a pricilla yakukwanani eti? kaya ndiwe wa police kapena ayi, koma chilungamo ndi chakuti ngati kuli apolice osadziwa ntchito ndiye apolice a ku Malawi aise!! phuma too much” ndiye akamathizimulidwa ifeyo timasangalala hevy kkkkkk

 13. Plz tamawaphunzitsani self defence ngati momwe amachitira nthawi ya KAMUZU BANDA.Wapolice wosadziwa ndewu shame! Ayambenso kupita MDZIKO la CHINA Kukaphunzira KARATE!

 14. Ndikakumbuka pa 22 December 2015 ai ndithu agalu amenewa bola mukanango wapha kut anzawo osusuka ndi ndalama atengelepo phunziro

 15. Muvutika nokha anthu ku Dedza ngati apolice amapemphapempha ndalama alibwinobwino ndiye lero mwawapasa zilema muziona mwakula mwatha

 16. apa ndiye axipangako mantha ķumapatsa chilango kwa ma suspect. continue. gud work kumsiya chapoňda nkumapezelela anthu oganizilidwa koma munthu aamene anakubelani ma millions mukumudziwa zopusa.

 17. Kikkkkkk! A Police amatsiku ano anatha kufowoka ndi ma Rider komanso Win. Police yakale zimenezi sidzikanatheka. Matsiku ano anthu amakhonza kupita ku police masana nkukatentha ma office eni ake akungoyang’ana. Anafowoka basi mphamvu alibe.

  • Musiyanitse police yakale ndiyalero. Yakale inali police force pomwe ya lero ndi democracy yi akuti police service ngati ku tchalitchi, so u can spot the difference. Had it been a policewo anawathyola anthuwa miyendo yo could have been the first kuwapanga criticize a policewa

 18. kukhala wa police sizinthu anthu amafuna kutchukila pa iwe kuti anamenya wa police ena amene anamangidwapo ngakhale sunawamange ndiwe mkwiyo wawo bola akakuona mu jezz ya police mkwiyo wawo umakhala pa iwe tingoti kukhala wapolice ndikuyenda ndiifa yomwe chifukwa anthu akafuna kumenya wapolice amamenya ndi mkwiyo ngat wakuba zoti olo wapolice wafa anthu savetsetsa amamenyabe mtembo bolani ngati mtembo wavalabe unifom ya police mkwiyo wonse umakhala pa unifom basi ..

%d bloggers like this: