Two men jailed for stealing bicycle

The Mulanje First Grade Magistrate’s court has handed prison sentences to two men who stole a bicycle.

The two Sinodeni Sompho and Samson Sayenda have been sentenced to 10 years and seven years in prison respectively.

The court heard that on October last year at Livetere village the two robbed Mazunzo Mulatho of his bicycle and ran away.

The victim recognised Sinodeni and reported the incident at Chambe Police Unit. Officers from the unit arrested the two and recovered the bicycle in the process.

Appearing in court, they both pleaded not guilty but after police paraded witnesses, His Worship Smart Maruwasa found them guilty and convicted them.

In submission, the prosecuting officer Sub Inspector Annock Fumbo asked for a stiffer penalty describing the offence as dangerous.

Fumbo also said Sinodeni showed that he is stubborn since he has previously been convicted for other dangerous offences.

His Worship Smart Maruwasa agreed with the state and sentenced Sompho to 10 years in jail and Sayenda to seven years in prison and the court hoped the sentences would deter would-be offenders.

Sompho comes from Livetere village while Sayenda comes from Shaibu village both of Traditional Authority Nkanda in Mulanje.

Advertisement

236 Comments

 1. let v judiciary go 2hell.thts y malawi will stll remain fuckn ignorant.if v bicycle is recovered y cant yu giv them afair judgmnt?we’ll 1day stand tall in burning these courts for blinfolding malawians long enough.

 2. eeesh!!!mpaka pamenepo bandulo yoseyo yazaka zaoba njinga ee!! zotheka kuti amayesela koma wayesera mwasoka,munthu omwatiyi azamwaso olozitavuta bwanji,ophyanditiyi sasowa amakhala ochenjela nkamwa olo atalakwila boma lopusakaleli sangidwa komakumuveka udolo,malamulo mwaonjeza chifukwa mwaposa amulungu,amulungu anali ten wabwera yesu wasisa akhara 3 inulelo mwapanga over 50 achokerakuti nchifukwa mukulakwisa zinthu you think mukukoza zinthu koma mukulakwisa zisiru inu akubawa sikufuna koma kusowa jobs mapepara alinawo zimatiwawa fizi mungokweza kufuna kutikololabasi mukugwesa maphuzilo akumalawi muli angafuse ndani onse ndiogona inu ana anu mukuwatumizakuma school akunja akabwe kufikila muofesi wa univesity yamalawi muli akhale khuki wake nde ndizimenezizi ndani sangabe,anthuwambafe tikuba inuso mukuba ntchimo lofanana kusiyana zilango izi zithe lamulo limenelo ndilopusa nanuopanga malamulo munangotaya time yesu anapangakale malamulo okhwima 3 omwe ziko likawasatila likhoza kukharala bata vuto ndi matayio a!!

 3. kapalasa yemweyu mpaka 10 yrs in prison km oba ma billions of Malawi kwacha 3yrs kenako kumukhululukira atagwira ukaidi chaka chimodzi mkumati iye amaonesa khalidwe labwino ku ndendeko

 4. Hahahaha mwina bola akanaba Ku Lilongwe kuno ikakhala 4 months Ku mulanje value ya Njinga ndi lorry nzofanana kanjinga nkachaninso

 5. I can see where all this poverty in our country is coming from. We have laws that can never transform our country for better. It is logically poor to imprison a person for 10 years for stealing a bicycle and imprison some one for millions or billions of kwachas. Koma adzapezeka mtsogoleri amene akhoza kudzakonza zinthu mdziko lathuli? I think we are still in the total darkness. Our education is not even giving us any bit of logic on issues around us. I hope the British shud come back and take us again. One thing they shud do to us, they shud recognize us as human beings who like them too needs recognition and respect for their humanity. Zachikudazi ndithu zalephera. Zangobweretsa umbava, tsankho komanso ulesi ndi nkhanza. Zoti azathu a kupanga ma amendments to laws that have negative impact to their security, interests and development. Pamene ife ma amendments omwe timachita ndi okhaokhawo oteteza ma interests a okhawo akuti ruling party. Total Shame. Pliz Britain don’t give us your money but let us be one of your state in your vast Kingdom.

 6. Chomwe mungaziwa Boma silingamange munthu oba ma million ochuluka coz amaziwa kut Boma lisauka coz ndalamazo sizigwila ntchto iliyonse mpaka munthuyo adzatuluke. Ngt simukusimikiza pezani mwayi oba ma million ochuluka simungamagwidwe a long period. Km nkhuku, ng’ombe njinga nd izi 79yrz in prison.

 7. Nanga awa akuba ndalama za cashgate mywatani panya panu mwamva, okuba za cashgate mukuwapasa 3 month’s in prison but others 10 years of what? That’s bulshit pamtumbo panu aboma nonse and pankholo panu zandibowa hvy

 8. Ndiye nyalasand imeneyo wina kuba njinga zaka 10 okuba ma billion kukhala week imodzi akuti awonetsa khalidwe labwino ku prison atuluke zoonadi ndende ndimalo awanthu osawuka ndakudandaula #Malawi

 9. malawi ukomela anthu achuma munthu kuba njinga 10 yrs koma ena akuba ndilama zambili osawa panga kathu osauka tikanasaukabe mulungu sangadalise ndipo malawi sazatukukaso achuluka adyela not oti atukule dziko

 10. Court found him guilty let the law do its work. Those who are hiding today the law is looking for them soon or later will catch them.

 11. 7-10years in prison for stealing bicycle? Ndiye kukhalire atibera 10billionwa eeeeeeh! moyo wawo wonsetu. Dzikoli limakomela opata basi. Mumva nati zilibe umboni.

 12. Ndie zopusa zimenezo zoona akagwire ndende kwa zaka 10 coz cha njinga yakapalasa…… Mpamene ena anaba zindalama za nkhaninkhani munangowasiya

 13. njinga ten yrs,cashgate nkhani ili ku bwalo lamlandu,,maizegate pali commission yomwe ikuunika,,kodi cholinga chanu mkufuna kutithandiza kapena osauka ife tingofa? mulungu akuona nanunso muzawelezidwa ndi judge odziwa kuweluza amene ndi namalenga

 14. Bicycle price 100,000 kwacha ok. Then 7 years. Therefore the one who has stolen k10,000,000 from government Will serve…. 10000000 divide by 100000 times 7. WA cashgate apa akuyenela kugwira ukayidi more than 700 years in prison.

 15. When u judge u must think bcz those on cast gt thy have given 3yrs bt njinga mukumpatsa zaka zochuluka why making faver 4 those who have got money let God judge u bcz of fage judgement

 16. Yes!thats good,mukafuna kuba ibani zambiri ma million osati ma hundred,mukaba zambiri akupasani zaka zochepa kuti ndalamazo zigwire ntchito mudziko otherwise boma will run short,nde kumaba moganiza

 17. you better also be sentenced for posting nonsense,tamulembani anayambitsa kuti a Malawi aziwonetsa R3000 pa Beitbridge akamapita ku joloza,ndiye za mzeru zimenezo ,osati busy mu office kumalemba za ma spoko ayi!

 18. kma analoza Malawiyo ndi mfitidi weniweni those stealing billions of tax payers money get 3.5 years in jail kungokhalakonso chaka mukuwakhululukira but munthu oba njinga which is less than 50000 MWK up to 10 years Malawi kma ndi chani

 19. Stealing billions of kwachas being set free while a petty thing worth k30,000 being charged dozens of years. Ife amphawi tizingovutikabe chifukwa palibe otilakhulira ziphinjo zathu

 20. APOLICE NAWO AMAKONDA NDALAMA AKANAKHALA WABA NJINGAYO NDIWANDALAMA SIZIKANAULULUKA POTI NDIPHAWI MPAKE AMUUZA TEN YEARS KOMA SIBWINO AMALAWI TOKHATOKHA KUSAKHANA

 21. KOMADI YEEE, UJA WABA CHIMANGA CHAWANTHU OSAUKA UJA WANGOYENDA MMA BENZ WABOMA. KOMA WAKUBA DOWE KUMUMANGA DZAKA 10 DZIKODI LIMADANA NDI ANTHU OSAUKA NDITHU.

 22. In Malawi prisons is for poor pipo not the rich ones It is not fair coz rich pipo steal alot of bilions but right now they walk free

 23. If it could have been 1,000,000,000….we could have here the following….6 month in prison with hard labour….or…sakupeza bwino…nde tawakhululukira poti ndikoyamba…..or umbini waniweni sitikuuwona….nde tidakafufuza mpaka ntsogolomuno…..or seeing him heavily guarded with dozen of officers….bail….then kulanda passpirt….then a freeman again…eating the billion like termites….then five years later…umboni palibe…..aaah..aaah…mesa ndalama ndizija amadya Ali pa bail zija…kkkkk….Ndalama zaBoma zinaleka KUWENGA UKAZIDYA Tiyeni nazoni…. shame on me…kkkkkk

 24. Malawian justice system is just fucked up i mean u want to tell me a person can get 10 years jail term for stealing a bicycle? I just wonder how many years will the big time thieves like Chaponda get for Maizegate Scam.

 25. Nanga awa akuba ndalama zabomawa bwanji akungoyenda freely mtauni? Munthu kuba ndalama za chimanga koma mkumamuyikila kumbuyo wakuba njinga ndiye ten years jail sentence, im sure God is watching you.

 26. Guys njinga ndikhale lomww mulandu wake ndiwokwera kwambili coz poyamba ankayendera ma DC achizungu

  Nde wokuba choyendera cha DC wachita mwano waukulu, ndipo mpaka pano lamulo limenelo silinachosedwe.

  Koma mube galimoto akupasani 4years kkkkkkkkkkkk

 27. Mean While A Cashgate Nkumapasa 3 years, mmmhu judgement day is coming tidzamva ndithu how can u punish some1 fos stealing a bicycle yet somebody stole billion killing people, ndithu mudzayankha

 28. Mean While A Cashgate Nkumapasa 3 years, mmmhu judgement day is coming tidzamva ndithu how can u punish some1 fos stealing a bicycle yet somebody stole billion killing people, ndithu mudzayankha

 29. Ena anaba ndalama zankhaninkhani ku CAPTAL HILL mpaka lero kuli ziii ndiye wina njinga ya k30 mpaka 10years amalawi kodi mumaganiza bwanji?

 30. 10 years chifukwa choba njinga??? Nanga uyu amene aba ma Billion achimangayu mwamucharger zaka zingati?

  MALAWI my country now prison is for poor people…

 31. Koma ndiye a cashgate kumatsiya walk free, I am not agree with that that unfair just because their cannot afford lawyers. Stop abuse the law and favor. give them less sentences

 32. Malawi yafunda basi chilango cha njinga ngati aba galimoto. Koma ama cashgate aja akungonenepa ,malawi yolimbana ndi ovutika basi, kuyiyamwa yowonda yonenepa akuyiwona Agalu a anthu.

 33. amalawi tkuenela kudzukadi rather than kumangoonerera zaunsiluzi wina kuba dollah zathu 1yr wa njinga 10 wat a stupid nation and its leaders

 34. MATHEMATICSif one bicycle worth K50,000 is equal to 10 yrs 7 months,(1) calculate how many bicycles are in K10 billion (50 MARKS)(2) how many years are found in that amount (50 MARKS)

  1. You said you like it because he steal to the poor, what about who steal for the poor and too much than a biycle. Maize for the poor malawian did he arrested for how long? And somebody come on the front saying memememeee what? Stupid mind with the stupid leadership and stupi judgement you all go to hero.

  1. So are these top officials not stealing from poor people??? We are struggling daily to get paid and bring butter on the table yet someone is just syphoning us without any regulations. Mxweee

 35. eeeeeee.Ku Malawi ndi kumpanje zowonadi.wokuba ma billion oti anakapindulira anthu osauka kumangoyang’anidwa osanjatidwa koma wina waba njinga imene atavutike ndi munthu Mmodzi kapena pamozi ndi banja lake basis ndiye mpaka 10 years?eeeeeeee.traditional justice maybe.

 36. Munthu kuba nkinga 10 years in prison yakalavula gaga
  Munthu kuba ndalama ma Million I mean ma Billion
  Kupezeka.kuti not guilty

  Malawi laws are just like International Criminal court (ICC)
  The court only target Africans leaders.in Malawi jail is for poor people

  So sad

Comments are closed.