A 23 year-old Malawian lady has been admitted to Ntcheu district hospital after she was shot by a person suspected to be a Mozambican police officer.
According to information made available to this publication by the Malawi police, the victim has been identified as Allena Maliko who met her fate last Thursday, October 19.
Police says the lady stays together with her husband in William village, Traditional Authority Mpando in Ntcheu but her parents are from Mozambique.
It is reported that on this day, Maliko left Malawi for Mozambique at Chingumi village where she wanted to pay a visit to her grandmother and other relatives.
But upon reaching Mboni area in Mozambique which is on a distance of over 2km from Malawi border she saw people in Mozambican Police uniforms who were firing bullets from the bush. One of the men then shot her on the left arm and right leg.
She was later helped by some well-wishers who were using the same road and she was taken to Ntcheu hospital where her condition is said to be improving.
Meanwhile, government of Mozambique has not arrested anyone in relation to the matter and it is still unknown whether the shooter was really a Mozambican police officer or not.
The Malawi police have also confirmed that a Mozambican identified as Samuel Petro was also shot and he is admitted at Ntcheu hospital where his condition is said to be improving as well.
There have been clashes between Mozambican government forces and rebels led by Renamo leader Afonso Dhlakama who wants to take over power in some provinces where Dhlakama claims his party won elections.
Komaso anthu amenewa asamayiwale kuti malire ndi pa Tete ( Zambezi River) zimatiwawa ngakhale sitiyakhula, orther wise angathe kutsutsula zilonda zopola tingathe kuchita nawo
Stupid apwitikizi nonse
Kumangoziwa kuba ndalama zathu koma kutiteteza kulephera.
Guyz pena pake ngati ulibe mphamvu kuopa ndi bwino.boma lathu lilibe mphamvu chonde.keep it up Malawi Government for doing nothing.
Ndakwiya ndikukaotcha ku refugee camp ku mwanza… malawian soldiers koma kulimbana nd amakala….
BOMA LOZELEZEKA ANTHU AKUMOZAMBIK KUMALOLA KULANDILA THANDIZO LAMANKHWALA KUMALAWI ZODABWITSA ZEDI
Nomally mozambican they don’t treat malawians like their neighbours they are so cruel with us ,,,,,kodi timawalakwila chani?
Tidawaphera Samora Machel
Samara Machel sanali munthu koma chigawenga put this idiot Samora out of human being
akutionjeza kwambili nalo boma lathu limangoyan’gana zimenezo tizachenjela liti kumangovomela
Malawi Government will send Soldiers to guard fellow Malawians from cutting down Viphya plantations but Will not send Soldiers to Safeguard Malawians from Attackers……. This is Intetesting.
Yayi tereee! Tikumaphana tokhatokha mkumati ndi alendo. Chitetezo kulibe, dont 4get we’r in de handz ov stupid dogz.
I’m just wondering what these hooligans think they are,they do as they please,they find happines in torturing us yet when they need us,we are always there to help.our government on the other hand keeps turning a blind eye to all these matters.why do we still have to be their hunchbags?
kodi anthu amenewa amationa ngati ifenso aititha ndewu et, Bomanso angomva nkhaniyo aitsekera basi osaxhitapo kanthu mukudziwapo kathu we’ll enter into the bush fight for our unity
Akutionjeza
Iiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiihhh!
If it waz John chilimbwe’s,kulowelerapo basi,adafenji !!!
Whats the matter?
MALAWIANS, HANDLE THIS WITH CARE
Tilindimavuto ambili kwathu kuno,zinazi akamapanga amakhala akufuna poti tiyambanilanepo kenako nkondo ibuke
Amamva kuyabwa akapanda kuyamba ndianthu. Pano muziwe kuti akufunisa atayambana nafe koma amasowa poyambila chifukwa ife sitibweza choipa
So pliz anthu musatengele puma khazikisani mitimapasi,
Tilekhe kuma pezeka muma teritory awo chisawawa.
Kuli madela ena amafunisa atawalanda munjira yankondo koma brcouse ndife antenfere amakanika.
mmmmmm trouble yoooo Mozambique? anthu oipa HEAVY….SHAME!!.
On what astep do the Malawi Govornment take about this issue?
the government must do something indeed if not we will sort out our self about this ndithu
Zenofobia basi ndakwia nazo ulemu winau kuphesa malamulo amalawi pa ma folenas anphwekesa mopusa
If President he was born in Malawi
And he was supposed to send soldiers there
Koma poti ndichobwela kuli duu
hahahahaha u have made ma day
palibe chomwe boma lingachitepo apa..simunthu wakumudzi amene wawombedwayo. koma akadzaphako mwayimodzi nduna za boma I think pamene mudzawone ngati a nzeru. poor government kudziwa kupana a Malawi koma kuwalephera kuwatetezera.
Chalu mphakat pose osat vosankhana mtundu iyondingozi basi ife timadalira ulimi ku zambia koma ndife aku Malawi
Umphawi to
Koma kunena chilungamo anthu akumozambique amatipezerera koma kuno akungogwiritsa ntchito misewu yathu opanda vuto lilinso y? Boma lichitepo kanthu
Bwanji ifeyo mayiko anawa amatitola?tym yoti tidzibweza sopano asaa.Aliyese waku moshiko aona nw
Akumozambiki Nose Muno Malawi Paulendo Basi Mupakile Tisakuoneni Muno After 24 hrs
Both people mentioned here seems to be Mozambicans.
Blacks against Blacks
Malawians are victims anywhere in the world. We suffer a lot in foreign lands, but the funny thing is we are very warm to the foreigners ourselves.
Ziwawa kuyambika pang’ono pang’no ngati aboma akupanga zimenezi ndiye mphanvu akuyitenga kwa gwebuza chisilu chaku Mozambique
Why????
Timve zothaitha kumeneko. Diso kwa diso basi. Mpaka ndichoke Nkhotakota anthu muliko kumeneko???
Why can’t we start war
Chodabwitsa ndi choti boma likupana amalawi pa chiri chonse koma kulephera kuwateteza kapenanso kulephera kupanga control apwitikizi pomwe akukhalira kutizunza…. Why?
If the government do nothing to the matter,we will move a revange to mozambican people they do rely everything in malawi.we see them,other mozambicans have houses in dedza especially airfield,maBush and mandala.ndiye atisamale aku mozambique
Wapolisiyu anangosowa nkhalidwe la umunthu, komaso sizikukhuzana ndi nkhani zolandira mankhwala muzipatala ai. Zolandila mankhwala zinayamba kalekale masiku aKamuzu, komaso anthu okhala m’malire ndipovuta kuti azipita zipatala zakutali pamene alinacho pafupi chipatala. Inu amenenso, mutha kuyamba kunena monyoza eeh talionani boma lakhanza ili.
Inu mukungonena izi .
Galimoto yochokera Ku Malawi inagwa mu mozaq mmalawi modzi kuvulala enao apwitikizi .koma itabwrra galimoto ya Mozambique inatenga wokhawokha apwitikz kumsiya mmalawi pompo koma chonsecho amapitanso Ku chipatla cha Mwanza.mmalawi uja anakafika kumwanza mochedwa ma doctor kufunsa kuti iwe unalikuti azako angozi afika kalekale .mnyamata ananena kuti anandisiya ati ndine mmalawi .Doctor kumva nchoxho anatamangisa onse amene anali mma bed rest.Apwitikiz ndizilombo aise
Apwitikizu ndi anthu oipa aise ungonena
I saw dem in sukasanje boarder,they are so selfish
its time for revenge , nkhondo iyambike basi akuona ngati tikuwaopa etiii
mphwanga ine ndiwakumozambigue ku des tricto ya demotiz so lero ndingoza kukuchapa iwe ndewu umayidziwa dikilani amalawi tikuduladulani mapisi kadziko ngati m’manjamu ndiye munyele mwano amuwombela bwanji mtsikanayo ndipo amakataniko kumalo ankhondo ngati amwenewo zopusa mahule simudziwa kuti amagwiritsidwa ntchito ahojas tamja tuku xatspa pontho.
wautsilu iwe kuthawa nkhondo kwanuko kumapita kwathu ukufunako chani??
anthu nonse aku moshiko kazipitani kwanu mukutithera chakudya kuno ngati simukufuna tikutibulana muona mwayamba kunya mwano inu anthu othawa nkhondo
Agalu amenewa akumapanga chiponge amalawi chosecho anthu ambiri amene ali mphepete mwa moxambic akadwala amakalandira nthandizo lamankhwala pachipatala cha Dedza boma.osadzawathandizaso anthu oipa mtima adazolowela khondo kwao
ooooh what e tragedy .
Chachitikani ndi chani?
Amatiderereaaaaa
kubwezera sikukoza zinthu kom mkofunika kuti aboma akambirane azathu kumozambiquiwo kuti nkhani imeyo itheretu ndimayiko oyandikana awa
Kod asirikali athuwa ndie kut sayiziwa chito bwanji tibweze bas iyambike nkhondo basi
Chiyambi cha nkhondo2
Boma lathuli,penapake sindikudziwa kuti limaganiza motani. Iikumalola bwanji kumasunga zi wanthu zothawa nkhondo kwawo ku Mozambique,pomwe athu anthu akumachitidwa nkhaza ku Mozambique? Si kuti ndi woyamba muzimayiyu kuwomberedwa. Tikakumbukanso bwinobwino, driver wa truck waku Malawi,anawomberedwa pa zifukwa zosadziwika bwino, munthu ali chikhalire mu galimoto. Anthuwa aku Mozambique akumatizdolowera kwa basi. Nkofunika kumawabwezera zipongwe zawozo. Tikakhala chete osachitapo kanthu, azitiwona ngati kuti timawawopa.
tipusa mpaka liti?nyanja mavuto malo atilanda pano ayamba kutipha
Wht actually happened?
Sorrl
why??
Wages yauhule ina ndi imeneyo
Boma ili ndi lopusa kwambiri, mchifukwa chani anthu akumozambique akuloledwa kulandila chithandizo mzipatala za mdziko lino maka maka ku dedza chonsecho akutipangila nkhaza zosiyana siyana ife anthu aku malawi
Ok bola
Munthu waombeledwa panopa ali mu uluru waukulu kwambiri, iwe ukuti [ok bola] bola kuombeledwako??
Eya
Umati bwanji?
Kanundu CHAMBA please kumaona nthawi yosutila kkkk
Hahaha ine akaz amsndinyasa nde kuphedwa ndilibe nazo ntchito
Labu’mxiiiiii
Swazz
Bola kukhala swaz kusiya ndkukonda akaz
Kkkk koma iwe udandisekese apa @ulemu likongolelenji dxina kkkk
Dont judge the book according to its cover coz u never know wat was written inside….kkkkk my is just fine
I understand why akazi amakunyasa,u was born frm a man.
u was born??? Check your grammer
Ulemu, check your spelling. It’s grammar, not grammer.
Ifeso tibweze mamozambiki ali kunowa
Y?
Is pay back time.
dont start a war that you cant finish
Tsek
Hw y?