Chichokereni mu nthaka ya dziko la Malawi mtsogoleri wa dziko lino Peter Mutharika pamodzi ndi omutsatira pa 16 September chaka chino kupita ku United states of America, Maso a amalawi ali tcheru kufuna kumuonanso atamusowa.
A Mutharika akuyenera kufika kuno kumudzi dziko limene amalitumikira lero lamulungu pa 16 Okotobala malinga ndi chikalata chochokera ku nyumba ya boma.
Kukhalitsa kwa mtsogoleli wa dzikoyu kudadzetsa mpungwepungwe pamene anthu ochuluka amafuna kudziwa za komwe iye ali ndi zomwe akuchita koma amalawi samakhutitsidwa ndi zomwe nduna yofalitsa nkhani a Malison Ndau amanena kuti a Mutharika akugwira ntchito zothandizira kutukula dziko la Malawi pomwe samatsindika za komwe iwo ali.
Anthu miyandamianda akhala ali tcheru maso awo pa khomo la ndege 1 koloko masana kuti awone mtsogoleri wawo yemwe anamusowa kwa nthawi yayitali atapita ku dziko la chilendo.
Kufika kwa a Mutharika, kukhala kokwanira kufufuta kotheratu mphekesera zonse zomwe anthu anali akukamba kuti sakupeza bwino m’thupi ndipo ali ku chipatala, enanso amati a Mutharika ali mwa kayakaya uko kumene anali.
Mtsogoleriyu adachoka kuno ku Malawi mwezi watha kupita ku msonkhano wa atsogoleri a mmaiko osiyanasiyana (United Nations General Assembly) ku America, koma adaonjezera masiku ake okhalira ku dziko la chilendo ngakhale masiku a msonkhano adali atatha kale.
Nawo atolankhani ali tcheru kudikira kuti awone ngati akanizidwe kudzakumana ndi a Mutharika kapena ayi pamene pamamveka kuti kufika kwa a Mutharika kudzakhala kouma ku nkhani ya uthenga pomwe “pakumveka kuti atolankhani sadzaloledwa kufusa mafunso mtsogoleri wa dzikoyu”
Koma a ku nyumba ya boma atsutsa manong’onong’owa, ponena kuti pulezidenti Mutharika ali okonzeka kulankhula ndi atolankhani.
Taona anthu osowedwa ife, ndiwo anthu amene utsogoleri wao udachokeradi kwa mulungu. Osati izi ayi, sichimomodzi opanda president yapa.
Bora kudikira ambuye yesu ndiamene ali nd phindu osat munthu ngat ine ndemwe ot sitingapeze nae profit
Akumapita kukapempha chinthandizo ndiye kumati boma langa muli .njala ndiye ndimafuna ndalama kwapasamo akukamangisa nyumba zawo achokedi loko atamwalira vuto palibe mungadandaule ndi inu osadulidwanu atumbuka opanda nzeru pussy funk your president
Kwa nonse a mane mumati akugwilitaa ntchito left arm yonkha po baibitsa mbuzi
Jodi gayez tiuzeni zoo a mesa akuti mkono olonjerasiukugwira ntchito ndizoonadi koma
Koma asamazimitse phone koyenda mumuuze plz
Kodi Ali moyo?
Anabwela sanabwele
Pa chichewa pali mawu omati “mawu msamatha” tsanu onthu wena ongutha mawu koma dala sibwino ntha zina kuti ozanu okutameni. Galimoto imaphweka okamayendetsa wina onthuni.
Iwe Munthuyu Anayimika Mkono Umodzi Ndiye Ukutipatsira Ataimika Mikono Iwiri Bwanji? Nawe Wayamba Ziphuphu
Mesa wafika
God is great
Comment reserves
Mtsogoleri wadziko lino amwarilad inu simukuwona kuti akugwilitsa ntchito dzanja la madzele kkkk.
Kkkkk akapalamula mwayankhulatu si fisi wa satanism uja amamutchukitsa a koma akunama tilinayenaye pa 2019 pa ma vote ake tamusungila azapitilizatso kuwadyetsa atumbuka onse zitete kkkk pantumbo pa tumbuka.
mmmmmm kom sindikukhululira kut ndiyewmeyu ayi tiunseni bwino
ameneyu kuno sikawo ofunika apatsidwe 30 days muziko lathu lino,dziko la masiye lino atsogoleli amangopanga zomwe iwo akufuna, cz amalawi timapheledwa ufulu olankhula ,President akakhale dziko la eni mwenzi okwana ndithu ,osaopaso anthu amene anamuuika pa ,pampando
A Malawi opusa adyera komanso ankhanza.Mumafuna atafa kuti mubenso Ndalama zina. Mwalephera.HE is there til 2024 .
Mukakhuta madeya anuwo musamaelekezele nzanu kut wamwalira mutayambe ndinu iye aliphee mulungu ndyemwe azamutenge osat inu ayi
welcome back ambuye! we all love u!
Kwa amene mukunyoza ndinuzitsilu komaso wopandazelu ndiye mwapambana chani kubwelako?
May God bless our President,Long lives, Genuine Democrancy.
long live Muntharika
Satana nthawi zonse ndiwolephera, welcome Mr president, ife tili nanu, zikumuwawa akachite report ku police yomwe ali nawo pafupi,DPP chipani chawanthu.
Osat nama akuyimika mkono umodzi not mikono yonse
MUNTHU WOSAPEMPHERA YEKHA NDIYE CHITSIRU AMANENA ZA BODZA ZA A PETER OSATI ATUMBUKA ONSE
Koma ndiye mwatinyoza atumbukafe,eeeeee. Komabe ineyo ndimawakonda a peter wa. Wina aliyense ali ndi kusankha kwake. akamwalila ndidandaula.
Mphindu lake lilipo coz iye ndi tsogoleli wanthu wadziko ndiye ali ndi phindu osawona phindu lake ali ndi vuto coz petter sitindingamufanizire ndi yesu coz yesu ndi mwini moyo munthalika ndi tsogoleli chabe
Akudzatani??,Palibe wamusowa m’dala wadaziyu
Wat iz wrong with his right hand?
Osati kumusowa koma afotokoze kwa mtundu wa malawi momveka bwino kuti nchifukwa chani watha nthawi yaitali chotele? Kenako adauza ife ngati amene tidamusankha?ngati ayi nchifukwa chani adapanga mwayenkha?kumbukilani kuti tsogoleri ndi otumikila anthu osati opanga zinthu mwayenkha
nonse onyoza mulungu azikhululuka ana anjoka inu
Respect One Another.
Ndilibe nazo attend
Zabwino lobert kayesa moni kwamavuto mkwakwa
Julia banda mulibwanji
Mulibwanji Ku nkhotakota kwanyalubwe.kwaluwanda .chipando yonse afanaam.chipando luwanda village
Ndizoona, palibe phindu lirilonse tiyeni tiyike yesu patsogolo osati nyasizi ai!!!
Ngakhale ife tonse tilikuziko layeni tikudikira yesu chopindulitsachamuyaya
Madolo masokwa yesu kwaife osauka tonse
Chofunikadi ndikuyembekezera yesu ndamenealindiphindu osatipitayo Samuel mziko kayeni mzinda wa johasberg
Waiting for the updades when he comes
tiyeñi tizikadikila komweko tikawalandile wolemekezeka
Muonesese kuti ndi iyeyotu osati chikhale chofanana naye
Tiuzeni Zoona Inu Atola Nkhani.
Nde ife monga nzika tinve ziti? Zoti apitaso ku india kapena akubwelela kuno kwawo? Tiuzen zoona
kodi combo 5-6-7 a airtel achotsa?
Abwera sabwera mutiwuzi
Koma abweradi?
Tikudikira timuone ali moyo kkkkkk
Ineyo ndili ku BT airport ndikudikila a bwana. Kaziwanga ndamutumiza ku LL airport Kut naye akagadile kumeneko.panopo sitidikila ma repoter ayi.tizionele tokha.
ine lero ndizingowerenga macomment basi,,,dpp ya shoota
Akuti atitengelako masola ayi vuto lamagetsi latha sopano ……anyamata mutani makasu m’manja tikayike nyasi zakhalitsa zikununkha kkk
Palibeso zobwela apo asowera limozi ndi president waku Cameron nayeso 19 days sakuwoneka , yakwiya mzimu
Amen Patrick Katsabola
kwanu nkwanu mtengo mudalaka njoka
angofera nkoko sitimadya za kunyumba kwawo atiziwe ndi chauta
angofera nkoko sitimadya za kunyumba kwawo atiziwe ndi chauta
Kkkkkk…zaziiii!!!
skazi ake okha ndiwomwe ayisowa osati ife tizisekerera zopusa kuti chani
skazi ake okha ndiwomwe ayisowa osati ife tizisekerera zopusa kuti chani
Thats only the news I gonna like, not about humanity but Holy spirit, remember faith comes from hearing the word of christ(Romans 10:17)
nkhumene.amadyelandalama.simakuziwa.mukulimbanazithu.zazzz.kodi.munafusaakubanjakuti.wawoanatisiya.mukuchulukitsa.kutokota.kapena.amapkupatsani.simandiye.pangani.zithuzoti.mupange.ndalama.osati.kutaya.time.ndizinthuzotisim
Tsiku lobwera yesu amalawi onse adzakhala okwiya.
Just wait for a moment bcos mlandu opanda mboni umavuta.
Everyone who says peter is dead is a stupid proffessor interneter,
Ameneyo Ndilibe Naye Tchito Tidazelera Kusakha Khalamba
Mulungu ananena musulat yasini kuti amaika paudindo unthu amene wamufuna panthawi yake ndpomso amatha kuchosa munthawi yomwe wafuna ndiye chomwe tingaziwe inu ndi ine tilibe mbavu zochotsa peter paudindo tiyeni tiyang’ane maso kwamulungu ndipo mavuto a2 azachepa peter ndchabemso pamaso pake,
kodi ndi bwino kumafunila anzanu zoipa?Afe ameneyo,mau amenewa akuchokera mkamwa mwa a Malawi ozitcha opemphela ,oopa mulungu.Nzomvetsa chisoni kumamva ndemamga ngati zimezi kuchokela kwa anthu oopa mulungu koma mphamvu yake adaikana. Ena mwa inu ndi mamembala a machalichi otchuka amene akumanamiza anthu kuti mulemela kapena kuti mavuto anu atha.
Zodabwitsa kwambiri…
mzanga anthu ambiri asochera sakuziwa kuti akupita kuti
Mabvumbulutso akutha kwa dziko ngambiri lol
Bodza
Za kaisala mmpase kaisalayo.
its 13:06pm now where is the Guy??
1:04 pm
Gayz malo modikira ufumu wa amene adatirenga nde tizidikira kapeyi gayz musakomedwe ndimaudindo aziko lampasi ngachabe
Amalawi sitisunga nthawi ndiye atiwonjezela nthawi imene afikile munthu wamkulu apo biii amene atope samuwona big man akutsika chimbalame pa KIA lero
Zoonadi palibechopindulakudikilamunthu yemwesangatipindulilekanthu koposakudikila kubwelakwamulungu.
Ndi Fumu ya Dziko Yesu Chrisitu bansi, Tonse Ndife Maliro, Kaya Wina Amayenda Ndi Bodigad Mumbuyo Amenewo Phindu Palibe, Ine Kuchoka 2008 Ndinapatsidwa Mtendele Wa Mtima, Koma Ndinaudzidwa Kt Ndisaiwale Malango Khumi Aja, Ife Si tinga Njenjeme Ndi Munthu Obadwa Ndi Munthu Mzake Ai, Kukanaveka Mbili Yoti Kwalira Lupenga Ine Ndikana Njenjemela, Koma Zandalezo Inafe Tinaluza Makolo Anthu Nkhanizake Zomwenzi, Pitani Mukamulandile Mukalowe Naye Kumwamba, Ife Sititama Mukono Wanyama Ai, BRIV TO SPRT, HE HAS MADE YOU
Mbuzi Yamano Kunsi Manyaka Onsewa Mdziko Muno Sukuwawona?
Odala ndiamene akuyembekeza kubwela kwa ambuye.
kulibe zofika mkuluyu mngotayanthawi yanu pachabe akuti mdikire ndege yachiwiri yikubwerayo
Eni Ake Tinamuvoterafe Tili Phee Ndipo Tizamuvoteranso,inu Mungobwebwetuka, Simunati Mukhaura Anthu Odalira Kupempha Inu Mutambulenge,
Welcome back mr president
Wina afune asafune Peter ndi M tsogoleri wadziko lino kumakhala ndi ulemu a Malawi
12:30 mwayamba kukankha nthawi mukuti afika 3pm bwanji kodi APM
Bola abwele okufa tilandile zipepeso mwina tingakokele ndiziko lathu losaukali
Azibwela Kt Amalawi Tikhale Nd Cikhulupililo Kt Ali Moyo Kapena Nd Malemu
Tiwalandile a pulezidenti athu ndichimwemwe, stl waiting
Asowa nkanakakhala nawo kolandira mlidzi wathu…
yasala 45 minutes kuti bwana president ti aone
nthawi zonse apresident amapita kunja kumisonkhano and sipankhala zoyankhula zambiri and ngati akubwera dziko lonse limatekeseka ndi kubwera kwa tsongoleriyu,,,,and akafika amayenera kulandira ulemu wapadera asanayankhule kenaka anena zomwe watibweretsera kodi lero chikuvuta ndi chiyani,,,,nanga ngati ali moyo sanamvepo kuti anthu akuwaganizira kuti amwalira bwanji osaonetsa ku mtunda wa amalawi mwachangu kuti ali ndi moyo,,,nanga ambali ya boma bwanji mwagoti ziii
zundimvetsa chisoni coz Malawi yenseyu palibe amene akuziwa za apulezident athu. bolaso mpiratu mmatha kulosera kuti atawine ngakuti. kwangosala 45m yokha kuti tiziwe zoona zake…..
Kusowa zozisowazo? ife tikusowa magetsi ndi madzi kungotchula zochepa osati,……? aaaa mutilakwitsa kunena apa!
Chitsiru chosalabadila anthu onwe anachiyika pa mpando…..Bambo akachoka m’nyumba ndikukakhalitsa komwe anapitako amayetsetsa kudziwitsa banja lake chomwe iye wachedwela……mbuzi ya munthu
Well, anthu didn’t put him on the post – he put himself on it!
how
By using teachers and airtel ……. remember that?
kkkk okay
HenhryHe
Nthawi Yakwana Yoti Atolankhani Mulembe Zoona Bodza Ayi
Welcome home mr president we luv u, ena kumasangalala kut wamwalira en nw hearing dat he is coming here in sound health so frustrating, long live mr president
Kkkkk a Malawi khalan tcheru
Zadziko lapasi zakutha izi zenizeni zili kwa mulungu ndiye zosatha ambale tiyeni tidikire ku bwela kwa mbuye
nanga akalephera lero? mwachidule Ndiye kuti ma rumours amene akumvekawa tizangoti ndi oooooooòna !!!!
Abwere asabwere Palibe chomwe chingasinthe magets sasiya kuzima mavutowa satha bola kungotsamira kwa yehova bwezi lopanda bodza losakhumudwitsa
Abwele Mwina Magetsi Angasiye Kuyakayaka.
Koma bakha ameneyutu akafika afusidwe mafuso ndi atolankhani osati angopitilila kunyumba kwake chifukwa watiwonongela ndalama zambili z.
Mukulankhura ngati amzeru mpaka bakha bwanji ndi mzeru zanuzo mukamufuse mafusowo ndinu
Timuona lero mtsogoleri wathu aMalawi!!!
kubwela or kusabwela chimodzi modzi
yhooo yasala 1hr sitigonasitigona,,,
Tikudikila zoona basi
inuso a 24 ndizisilu.ndiomwe mumayakhura zambiri zoti wafa.munakhala bwanji?zolemba zimakusowani eti?koma afe achakazanu or amu tiwone ngati mungasangalale.ifeyo peter timamunyadira and ndiyemwe amatisogolela or sitili kumalawindikanakonda peter asayakhure ndi mtola nkhani aliyese coz ndinu zisilu zanthu.mukasowa cholemba muzingopita ku toilet
All foolz thy walk together coz ur presedent doesnt hv a hope in our country so if someone aays he iz dead he mst die y nt
Tikudikila maloza kkkkkkkkkkk
Tamupanga surgery kuopa chilima kutitengera ku tambala wakuda
ine sinamusowe
Tinthire diso basi
This president if at all z alive,is self centered osamva and extravagant, Last year msonkhano ngati womwewu ananyamula anthu ambiri plus mafumu. He was blamed for that but this time akupanganso zamkutu over spending while we r in problems here.
Malawians want hin dead but God wants him to live so that he can save poor people. .. stupid Tumbuka hyenas want him dead. .. kubadwa mtumbuka ndi tchimo… umakhala onyansa zonse…. atumbuka ndi zinyama zoopsa…. munthu kuwachitila zabwino sayamika… anangokula mitu kma ndi nkhumba zopanda ntchito…. ali busy kunena kti Peter wamwalira …. the only president with vision. .. mukamati athetse njala mutanthauzanji? sakukuzani za ulimi othilira? mukufuna azizakulimilani? ? kodi iye amagwtsa mvula? mukukhala ngti ku USA ananyamula makasu anu…. kapena anatenga chanu chokodzela chanu kti uhule simupanga….. a Tumbuka mbuzi mbuzi… tiyamba kukuphani….. inu a chewa nde kaya sindinena zambri
Atleast u cud ve save ur data than writing this u brat
We’re all malwawians don’t discriminate bcz if u carry on saying that you will make things worse. You telling me that all who were talking about Peter are tumbukas? You bursted
ofcorse ,do think all tumbuka are stupid to u, then if u r better to them wt hv u done ,about ur father mnthalika for going to USA ,just worsing money for nothing ,go to hell with ur fakiiii father
masende ghako mnyamata atumbuka akulakwila chani mbuzi iwe mtumbuka sungamuthe tu mwana wachepa
you Raymond Chimbala, last time u commented the same bullshit and today you do the same..but to day i will choose to ignore your primitive tribal “bigotry” comments but u have to note this: we are watching your stinking comments very carefully and wait and see your harvest very soon. mind you, ” still waters run deep” today i’ll not comment much like i did last time. you cruppy and wretched son of evil one!!! next time we will be fed up… .
Basi mulungu akukhululukile uli ndi mwai poti lero ndi sunday uzalembeso izi mawa wava
i wonder if ur not mchewa bwezi ukulakhura chi Portuguese cause we use to describe Malawian as mchewa
Primitive garbage and gallon head worst to this generAtion if u hate tumbuka fo personal reason go live under the rock stone age man
Mufa oasuka choncho akulu inu
Patumbo pako mwana wa hule iwe..kodi umaona ngati atumbuka si anthu….
you chewas fulish ,and you guyz yo busturd chifukwa chake umbuli kuuchewako ukupitililabe coz ndinu anthu osazindikila palibe zomanyozanaapa olo ku sankhana mtundu,oky wary not akanat wafa ndikanadya phwando coz mwapitala mulibe chonde zausogoleli tsakuziziwa.alindi dwela kwa eni.
Ndipo uziwalemekeza aTumbuka coz mawa akakuthamangisani pamene mkufunsira ntchito kwao,yolima fodya.Ife ndife mabwana anu mwaiwala!.
Go back to school Reymond your English gives us the whole picture of how you look like. Zabwino mumazifuna koma munazithawa.
serious guys aliposo amamusowa ameneyu
Koma Yeah,lero ndi tsiku lija.
Tidziwepo chowona apa.
Munkati Sunday kuona ngati linali kutali.
Tikudziwa chowona koma tikudikira tione nzeru ZANU.
Zooonadi
Hello friends, my name is Susan Mwanza this a testimony of how i got cure fully from HIV/AIDS, i was diagnose with HIV/AIDS FIVE year ago, i contacted a doctor who later gave me some treatment, but it was like the treatment he gave to me were not enough i was desperately in need of something that will get rid of the deadly virus from my body, my life was miserable i lost my job and few of my friends, not quit long a faithful friend of mine came to me one afternoon telling about what he saw on net a testimony of how DR Abumen cured people from various kind of virus including Herpes, i was like this is a scam, but he old me he believe in what he had read on line’ he told me he will contact DR Abumen on my behalf and he did so, after some days he receive a parcel containing DR Abumen herbal medication, he present it before me to use it, that when am cured i should pay back the money it cost her while negotiating for the medicine, after taking the medicine for some days according to DR Abumen instruction, then i decided to go for check up and i was happy to see that no sign of the virus was found in my body, i am very thankful to my friend, if you are having a similar problem or you need his help you can reach him on ([email protected]) or you can call or chat with him on whattsapp through +2347085071418, please share to save life.
Anakangokhala konko nkulu ameneyi.
11:49 countin down
Kubwela kusabwela ndichmozmoz bas okadikilao alibe zochta apidula chan pussy ameneyo abwele komwe anali olo titakhala opanda pussy yo zkusiyana bwaj amaleka kufela koko bwaj
BUKHU LOPATLKA LIMT PMBAL POYAMKA MULUNGU WANU MOONA LEMEKEZAN AKULU NDI MTSOGOLERI OSAMFUNIR ZOIPA
Bola asatiuze kt ndege yamuthawa kapena yagwa..lol…1hr 10min 2 go
Apopo nde eeeee kaya komano asabwere ataseka maso we want him to pay back pliz ngat atabwera ataseka maso ndie ndi waku Ndatha farm
Kungoti 01:00 yayandikira
za peter mungosiya kunena chifukwa anthu ndiwokwiya ndi njala
Beware of Face Masking! !!
I also think the same way akuti wont talk to pipo they might change voice and face too serious
Ndkuuzani..these guys are too clever for cheating
Ukanama sikuchedwa kucha ndlera tzwe zoonazake.
Ukanama sikuchedwa kucha, ine ndiye ndafika kale ku KIA kuti ndione ndekha akuyendera parade. Welcome home.
olo zoti kuli tsogoleli tikuva inu malo mopita kumunda tizikadikilila muthu wandalam oti kumunda sakuziwa
Afika ali moyo mubvomelezaso mulungu simunthu
Pepani bambowa anatisiya ku New York mu hotel
Tinamusowadi! mmati? agulukunyinda inu andiphule ndipume pangani zanu
Pepani akuti lelo sabwela chifukwa ndege imene amafuna kuti akwele yamuthawa . Abwela next week.
Pistol on the flash!
Abweresa #Frozy waku Amerika?….koz ngat sabweresa ther z no point yopita ku airport
16 october i think kuzikhara holiday tizikumbukira tsiku lobwera mdala ameneyu. lol.
Kkkkkkkkkiest koma yaaaaa
Iiiiiii,koma,kwatsara maola ochepa kuti abwana afike muno malawi, lets weit four the truth..,.
kkkkkkkkkkkk ndiye mukamuona mutani ?
ineyo ndilikale konkuno ndatengelathu mutolankhani yimoz ndikufuna ndiziwe zomwe amakapanga uyu mumati pitala kaya wakuba uyu
akuti “mutolankhani yimoz” kupusa kwake kumeneko akaleke kukubelan
hehehehehehehehehe koma #Lane usandiseketse kkkkkk
nanunso pantundapo anabere inu???mumafuna kuti akhale president wabwino azikukugulirani ndiwo zakunyumba kwanu??hehehehehe nsiyeni nzanu ngati akuba akumaba chifukwa chamaphunziro ake,,,anachita kulimba kuti akhale president
mmmm komaaaaa maphuzilo asakhla kubela,,za miracle kupanda achair analindani onse ndi mkuluwake amalemu 2,asova ndi maphuzilo awowo,,,lero yasla 40 minuyes
#Blessings tiuzenitu mesa ati wafika nde he’s dead?????akakhala malirowo onse omwe akumufunira kuti amwalire akadya malirowo komanso nawonso ziwachitikire kunyumba kwawo muone maliro momwe amaopsela
Ndivutikilenji ndi nkhani zaziiiiiiii!!! President kwathu sanabweleko kuzandipasako kanthu, NDE ndimulilire chifukwa chani?? Iyaaaaa
Kkkkkkkkkk
ovutikafe sitinamusowe ndi chani chimene angatipindulire kwa anthu osauka ngati ife zoyenera anthu a ndalamamanu zimenezo
Inu nonse achingolopiyo ,asaona aku Yerico perekani ulemu kwa nsogoleri wina aliyense wa dziko lino kaya mlomwe. Batumbuka , machawa,mitonga masena .msogolwri wa dziko sachepa chifukwa amakhala ndi mphavu zonse ziti atha kukusaukisisa or kukupasa mavuto mpaka ukakhala kuti ndiwe zofuna kudziwa akulankhula. Koma achingolopiyo yonse sitingakhale ma president ayi chauta amasankha pa nthawi yache.Ngakhale mutanyoza bwanji inu ndi ine kwathu nkulira basi
2 points
kumusowa mwat kkkkk
Ndilibe Naye Ntchito Akagwere Uko Palibe Chosintha Kubwera Kapena Kukhala Konko Mumuuzeso Kut Asabwere Kuno Malo Kulibe Tidagulitsa Akhale Konko Shut Up Sitikumusowa Ayi Tizikhala Mwachonchimu Opanda Iyeyu
Ndinu zitsilu inu a malawi 24 mumalemba nkhani za bodza mkusokoneza anthu mitu lembani nkhani yomwe mulinayo ndi umboni kale ninkaesa mumalemba zowona ndinu zitsilu kwabasi
Sitinamusowe (except ma cadets mwina ndiwo amusowa). All we r looking after is to hear komwe anali, zomwe amapanga & y he went AWOL. Alongosole momveka bwino. Kungoononga ndalama za boma basi mmalo mogulira mankhwala mzipatala.
Ndiwe ndaninso kafucheche ngati iwe
Johanz Phunyanya shes a tax payer.. Paja u r unemployed so u cnt understand… Ukhalira kudya zicheche zomwezo
Tiwonge Nkhwazi my dear dont mind him. He’s just a blind follower.
Kkkkkkk guyz mukuchezana udyo lol
Macdonald Phiri, I visited bwana Johanz Phunyanya. He looks twice my age but his brain’s full of mucus
kungoti anthu ena amafuna kusokoneza maganozo awanthu ena we must know dt everyone has its opinion never mind odrs opinions mind urs
Osman Makanga u’ve spoken boss
mukudziwa kale abwana apa aliyese akupeleka maganixo ake nde wina amafuna adzikuonetsa iweyo ngati fosha ngati iwe uli ndi comments yako osangolemba bwanji naweso
Zodabwitsa Boss.
Kkkkkkk koma abale inu
aft atafa osadanda thupi likubwela
Welcome back Dad,we missed u a lot!wishing you traveling mercies!Long Live APM
I think something is wrong why you post old photos
Hello friends, am Anthony Maqebelo by name, i was one of those millions of people living with HIV, i received my breakthrough with the help of Dr Olumo whom i met through the testimony of someone he has helped, after some series of conversation with the person sharing the testimony i decided to contact Dr Olumo which i did, after some negotiation he sent me the medicine with an instruction on how to use it, i notice some change in my body when using the medicine, after completing the dose as instruct i went for test only to be confirm negative by the doctor after the result came out, words on the internet can not express it all, if you are in the same condition and you are looking for a way out of it you can contact Dr Olumo on his email address, [email protected], or you can call or whatsapp via +2348138956767.
Hahaha abwera wamoyo kapena…..????….Nanga akatinamiza titani?….nthawi yatha kale apa…amauser money yathu nde tikuenera kudziwa chililichonse chokhudza iye…abwere ayankhe mafunsowa…kwa ine nde bola angokhala konko coz palibe chomwe wapanga pa dzaka zapitaz…#
Ndalama ZANU zake ziti man
Haha kutopa uku man!
Aaaaa tiyeni tiwasiire komko Ife ndi umphawi wathuyu tizingoyang’ana
Pena nkumazisiya izi koma zimaonjeza…atsogoleri athuwa achuluka dyera man…
Kodi ndani azakomere onse man thawi ya kamuzu alipo amanjoya ena Ai komaso ya Bakili even Bingu pano asiireni enawa
Lol…tadzisiya man….ndi nthawi yawo…zoona sizingakomeredi aliyense…tizingoyang ‘ana.
Basitu kumangolimbikira patokha Kaya ntchito ndi ma business
Basi nanga nkutani…pena osamakuladi nd moyo odalira…komanxo osalora kuti tiponderezedwe
Kkkkkk nkhani yake ndi imeneyo boss
kkkkkk eyetu boss…nde enafe sitimachedwa kulankhula penapake pakalakwika…kkkkk koma za ndalezi ndikumanzere boss.
Aaaaa Kkkkk munakali achichepere muzafa muli ana asiyeni anthuwo
Kkkkk koma nde mwaticheza…koma zoona zake boss….kkkkkk
Kkkkkkk eyetu Ine basi.ndadya nsima ya therere ka radio kanga kammanja kumvera basi
kkkkkkkk nafenso man…maso konko…
Kkkkkk sure
Kikikikikikikikikikiki
anatani kufela komko?komaso bolani abwere ali mtembo kupanda apo nditidzachita kupha ndi mwala
Kod Ndiye Chikukhuzen Ndichan Or Atabwela Atafa Ndi Mmbale Wanu..Kapen Budjet Yamakomo Mwanumo Amapanga Ndi Iyeyo Nde Sanasiye Ndalama Y Amalawi?
guys ndine mbuli mu nkhaniyi koma nanga chilima alikuti???
It makes no difference kwaine,alipo,kulibe,ndumadya nsima ndiwo masamba,basi,life goes on
Kkkkkk
I Miss My Prezdent! Welcm Back Mr Prezdent……. Koma Mbuyo Mwanu Muja Anthu Anka Mudali Mukudwala! Koma Tikudziwa Kut Ankangopeka….. We Love You Mr Prezdent, Muaaaaa!
mmmmmmnmmmm
Zazi
he he 1hr 43 minutes remaing to see the president
Koma dziko…, kumatenga anthu a bwino kusiya chitserekwete ngat chimenechi?
Admin Ukunama Bwanj Ine Ndili Ku Nkhatabay Maso Anga Akhala Bwanj Ku Airpot
he hw koma lero
even phuma amakapangaso greeen card ya newone mxanu kkkkkkkkj
my mother malawi bodza lizatha liti kaya
Kuchalilatu ngati game ya bullets ndi wanderers kkkkk counting down continues,,,
game imeneyi imvutatu yopanda refu kkkk
Ivuta koopsaa
Kikkkkkkkk
mwayamba kusintha zichewa mesa padzulo paja mumatiwuza kuti wamwalira lero mukuti amalawi tikudikira kubwera kwake. ndiye tiwuzeni zoona kuti tikudikila munthalika kapena mtembo?
Azagwile ntchito cozi ntchito analembedwa kuno not amelika
KODI MWAMVA ZAKUGWA KWA NDENGE??
Satana achita manyazi lero dpp boma Muthalika boma
Pankholo pako ndi DPP yakoyo
kkkkkkkkkkkk collabo oooo
Odala amene akuyembekezera kubwera kwa Yesu Christ osati munthu wawamba ngati pitalayu, mwanva a Malawi24.com
Mmaso mwachambwiyanu ndinu.. mesa mmati wamwalira… simunati mumva mbebe..ife tiri ku Airport konko kuti timulandire…. afisi inu mwagwa nayo amene atafe ndi ambwiyanu.. our president is alive and will rule this nation until 2024 … DPP WOYEEEEEEEE APM WOYEEE
Ine sindikumvetsa za kubwera kwa bwanawa , news ina mukulemba za ku Lilongwe komanso ku Chileka airport ndiye tilowele kuti?
Sikoyenela Kukamba Zambili Tiyen Tidikile Zokamba Zidziwika Madzulo Ano
odala ndi anthu amene akuembekekezela kubwela kwa Yesu mkhilisitu munchoonadi,pakuti kubwela kwake nkopindulisa.ndi phindu lanji lomwe Peter wa Mutharika afike nalo lelo kubwalo la ndenge?kodi anthu amene akugona ndi njala ayamba kudya chifukwa choti iyeyu wafika muziko muno?kubwela kwakwe kwa Peter kulibe phindu kuntundu wa Malawi.moo wanga ukuyembekezela kubwela kwa Yesu chifukwa nkopindulisa.
Auzeni chilungamo bwana
nanga kuli ndi phindu lanji kubwela kwakwa?poti anthu omwe adawasiya osauka ndiosaukabe,ndipo omwe adali olumala ndiolumalabe,koma kubwela kwa Yesu mkhilisitu kudzachosa zowawa zonse.#Mniembilee Ausward WaChelse
mau anuwa bulaza ndi onzuna kwambiri kupambana uchi ndiyo pindulitsa munthu aliyense mu ziko lapansi
Kumaona Malo Olalikila And Kumaganiza Ngat Muthu Wakulu Shupt
Amen. Iwill take u with me to Chez-Mtemba tonight
true…a big amen to that…..Kubwera kwa Peter Kulibe phindu, instead kubweresa mavuto ankhaninkhan
U talk de talk bra !! @ Patrick Katsabola
Amen
Amen
Amen mwanena mau ondigwila mtima kwabasi
Mr Andrew Nuxwe Chirwa ngati ndikunama nenani pomwe ndanamapo,komati mukudziwa kuti sndikunama y mukunyoza?idont hv ur tym mr God bless u.
akulu kubwera kwa bwanawa kuli ndi phindu.phindu loyamba ndi kuchepetsa ndalama za boma zomwe zikupitilila kugwilitsidwa ntchito kunjako…phindu lina ndilokuti abwanawa azapitiliza ku gwira ntchito zao zaboma…ngakhale m bible atsogoleli adziko analimo…achina sauli ndi anzao…do you think zikanachitika chonchi nthawi ija ya china sauli anthu sakanadabwa…muli ndi uthenga wabwino bro koma mwaubwelesa molakwika.. God bless u
my sis harriet yesu sanali ku sankha malo yolakira ndipo mu pemphero ananena kuti ufumu wanu ubwera nichifukwa ciani ananena mau?, maufumu ena analiko panthawi iyo.
Harriet Jere,mau aMulungu akuenela kulalikidwa palipose pakuti ndicho chinthu chofunika kwambili.Yesu ankalalikila ngakhale mahule ndiokhomesa msonkho nde pali kusiyana kwanji?kodi inu mutafa lelo mutha kuiuza infa kuti yabwela nthawi yolakwika?nanga bwanji mukuti ndabwelesa nthawi yolakwikwa mau AMulungu?
Awa nde mau amene andigwira mtima.Amalawi kupusa mmene dzuwa likuotcheramu wina kaliki liki akuti akukalandira mtsogoleri amene anapita kunja kukalandira mankhwala chonsecho wasiya mzipatalamu muli mavuto osayamba.
amen Mugabe Masah Phiri
amen my bro
Amen aliodala omwe ayembekezera kubwera kwa mwana wa Mulungu. Zadziko lapansi nzachabe.
amen Saka wa Saka
get me right sir I said presentation yanu sili bho….munakatha kulalikila pompa koma nt moweluza awo Ali worried
Mr. Patrick Katsabola. Zikuonetsa kuti inuyo zadziko sizikukhudzani, koma nchifukwa chani mukutsata nkhani zandale? Tsamba mwapanga comment li likukamba zandaletu limeneli. Sikuti amene ali interested ndikubwela kwa a president ndiye kuti chauzimu alibe.
Harriet Jere,ine sindidaweluze munthu koma ndikulankhula chilungamo.chilungamo changa ndi ichi.monga mau akunena pa Luka 6 vs 21 mpaka 23 akuti ndiodala anthu omwe ali osauka chifukwa ufumu wa Mulungu ndiwao,komaso akuti ndiodala omwe akunva njala chifukwa adzakhuta.nde kubwela kwakwe kwa Peter kulibe phindu coz anthu omwe adawasiya akutika awapeza akuvutikabe anjala ndi anjalebe,olumala ndi okumalabe.amasiye ndiamasiyebe.koma Yesu akadzabwela zosezi zidzatha ngati mudamudikilila munchoonadi.
True that Ken…kodi yesu ankawalesa anthu kukhuzika ndi nkhani za boma…mukuweluzatu atsogoleli mukuiwala kuti ambuye yesu amakonda aliyense…atsogoleli tikuwadikilawo yesu amawakondanso nde kukhuzika ndi mmene zilili panopa mmalawi muno si tchimo..instead tionese chikondi kwa onse then it will be easy for a us kulalikila mmalo ngati awa
Mr Ken M’ baya ll u plz tell me y Yesu khilisitu ankalalikila ngakhakhale mahule ndikudya ndiokhomesa msonkho then ill answer ur question
mmangodana ndi Peter yo…that’s why kubwera kwake phindu lake simuliona…comparison ya kubwera kwa Peter ndi Yesu aint right…Pete ndimunthu yesu ndi mwana wamulungu wamoyo it’s obvious kuti yesu kubwera akhungu aona and palibe wanena kuti Peter akabwela olumala ayenda mavuto sikulumala kokha
kuti muone malo omwe mukuchitika za dziko lapasi ambili amakhala nazo attend nde pamemenepo nde pofunikila mau aMungu kuti afikepo.palibe muthu amene amafuna dokotala chosecho sakudwala,odwala ndiomwe amafuna dokotala.komaso y asadayambe misonkhano ya chipani amati tiyambe tapemphela?nanga nchifukwa cha Yesu adasanduza madzi kukhala vinyo chosecho kudali kuukwati osati kutchalitchi?nanga nchifukwa chani Yesu adanena kupita kalalikileni mmiseu mmisika komaso mmabwalo ngakhale mmizinda?
y amati amamulumbilisa presdent atawina?
Mawu amulungu alibe nthawi kapena malo, ndcho chifukwa bible limati mwana wa mulungu adzabwera ngat mbava palibe yemwe azadziwe . Odala iye akhala nd njala muuzimu nd chikhumbo cha mawu ake
.ndatsitsimuka koooowopsa blaza keep it up
Mulungu akudalitsen
Za Bingu aaaaa ndngomva kwa Anthu ,
Za wanga wapamtima Yesu ndilingalira usana nd usiku
amen Brenda Queen
what I know is pali mmalemba oyela pamene analembapo kuti kudikilila ntsogoleli wadziko yemwe anthu sakudziwa kuti Ali bwanji ndi tchimo ine Monga mmalawi ndimakonda Yehova yemwe amandiphunzitsa za chikondi ndipo chikondi chimenechi ndimakonda dziko langa that’s why I won’t stop being worried kuti big man abwera what time and Ali bwanji?…that won’t stop me from waiting upon the second coming of our Lord Jesus Christ…
Patrick Katsabola what an encouraging message from buh ….The world needs people like you
ine sindikuweluza or kukuumiliza or kudana nazo kuti mudikile Peter iwon’t do that,koma iweo usandilese kulalikila mau a Mulungu pakuti ndiofunikila kuposa moo wanga.ukandilesa kulalikila am teling in the name of Jesus christ the only son of God miyala ndiyomwe adzalalikile pakuti chosatheka ndi munthu kwa Mulungu ndichotheka.iwon’t stop to talk more about the second comming of christ its now o never.Ndi Mulungu yekha adzathese mavuto osati mtsogoleli wadziko.Harriet Jere
sikukulesa kulalikila and I like kuti wabwelesa this pa page ngati iyi koma wabwelesa mauwa ngati ukuweluza anthu amene akudikila kufika mziko lino kwa apresident ukuziwa nkutheka out of anthu ameneo alipo anthu opemphela zedi oti their relationship with God ili very fine…komanso mawu amawaziwa
Today iz Sunday, Amen and Amen!
a Katsabola, mu comment yanu muli sarcasm tone yakuti onse amene akukadikirira APM ndiopanda nzeru koma achikhala m’manyumba mwawo kumamudikirira Yesu. Yesu timamudikirira daily koma that does not stop us from engaging ourselves with day to day activities. Inutu mu comment mwanu simunalalikire koma mwaweluza ndikunyoza anthu amene apita kukachingamira mtsogoleri wadziko lino. Inuyo a Patrick Katsabola palibe chilichonse chimene mumapanga koma kudikirira Yesu basi??
zako izo ken, ine zomwe wakamba brazaman patrick zandigwira mtima kwabasi.
Patrick Katsabola, you are very wise person and your post has been of inspiration to me, keep it up telling people about the kingdom of God which is aready at hand…..
hahaha even Jesus Christ new what to say at the right place and right time thats why nkhosa zache sizinali scattered..
hahaha even Jesus Christ new what to say at the right place and right time thats why nkhosa zache sizinali scattered..
How funny hypocrites are!!
@ Harriet, ingopitani mukadikirer mtembowoo basi
Zoti ndi mtembo mukuziwa ndinu what I know is he is God’s creation whose state is currently unknown …kuteleku thats why tikudikila tinve
Nanenso mauwa andiphunzitsa zedi,ndibwino kudikira Yesu chifukwa nthawi yatha!
Akadakufunsani inu funso lija lakuti “kodi nkoloredwa kukhoma msonkho kwa Kaisala kapena nkosaloredwa”…. Inu ndinzeru zake zimenezi mukadayankha kuti “ayi sikoloredwa”, mukadadzetsa chisokonezo ndi mpungwepungwe mdziko. Koma Yesu anali wanzeru kwambiri. Ngati mukutumikira Yesu mudzipemphera akuninkheni nzeru
Komenti yabwino kwambiri Patrick ndakunyadira amene wazitengera pena ndizake, mzukwa ubwera lero hahahahahaaaaa
hahaha that’s why sali mulungu ndipo sazakhala mulungu iwowa Ken
Inuo mr Ken M’baya ndiomwe mukuweluza pakuti mukunena anzanu kuti ndi achipha maso nanga inuo muli mbali iti?ndakufusani mafuso ambili koma simudayankhe coz u know very well kut am talking the truth n even God knows this.pakuti tonse tinachimwa tilephela kufika kuulemelelo wake.Mulungu akuydziwa ekha amene ali akedi nde musandilese kulalilikila pomwe Mulungu wandiuza kuti lalikila pakuti simukulimbana ndiine koma Mulungu pakuti ine sindiuchita manyazi kukamba zamau ake palipose.komaso ine sindikudzitenga kukhala munthu wangwilo ayi koma kochepa komwe Mulungu wandiuza kuti ndigawane nanu ndikuyenela kukaika poyela.in fact inuo mwandiweluza kuti ndikosaenela kulalikila pa page ino y?kodi nchifukwa chani kunyumba ya malamulo kuja amayamba ndipemphelo?again y ngati presdent wawina amamulumbilisa atanyamula baibulo nkukweza manja ake kumwamba?y amipingo amasonkhana nkumapemphelela kuti dziko lathu lizienda bwino? mundiyankhe
Harriet Jere u wrong n God must 4gv u coz ur mic use the words of God.there is only one God n pa anthu osewa palibe amene wanena kuti iye ndi Mulungu or ine sindidati ndine Mulungu.so what’s the shame like that iweo nkumati sitingakhale Mulungu,iweo umafuna utakhala Mulungu kapena?let God b God.
hahaha zakuwawani atsogo? mawu mukuyesa mmaziwa nokha? kapena mukuyesa olungama ndi nokha…among anthu odikila a presint palinso opemphela and mwati polumbilisa amakweza manja kumwamba presenting them kwa Yehova that’s why this is also the right time to call upon Jehovah alowelelepo pa what’s happening paMalawi pano nt kuweluza anthu odikilila a president tili ndi ntchito atsogo…to interceed for our nation Malawi
hahaha zakuwawani atsogo? mawu mukuyesa mmaziwa nokha? kapena mukuyesa olungama ndi nokha…among anthu odikila a presint palinso opemphela and mwati polumbilisa amakweza manja kumwamba presenting them kwa Yehova that’s why this is also the right time to call upon Jehovah alowelelepo pa what’s happening paMalawi pano nt kuweluza anthu odikilila a president tili ndi ntchito atsogo…to interceed for our nation Malawi
hahaha zakuwawani atsogo? mawu mukuyesa mmaziwa nokha? kapena mukuyesa olungama ndi nokha…among anthu odikila a presint palinso opemphela and mwati polumbilisa amakweza manja kumwamba presenting them kwa Yehova that’s why this is also the right time to call upon Jehovah alowelelepo pa what’s happening paMalawi pano nt kuweluza anthu odikilila a president tili ndi ntchito atsogo…to interceed for our nation Malawi
Iwe ndi M’banga weni-weni, ulemu wa Mfumu
hahaha a Tiya ku Chez kuja mmati muwatengela atsogowa????lol
Harriet Jere nde chalakwikwa ndichani ine kulemba kuti chofunikila kwambili ndikuyembekezela Yesu mkhilisitu?tandiuze iweo kodi utadwala umapemphela kwa peter kuti akuchilise or kwa Mulungu.tandiuze chofunika ndichiti kwa iwe pakati pakuembekezela peter ndikuembekezela Yesu?tsono ngati munymba yamalamulo amayamaba ndipemphelo komaso akawina amamulumbilisa nde ine ndalakwa chani kunena mau aMulungu pa page ino?Mulungu ndiye akudziwa amene alidi ake so don’t tell me kuti alipodi anthu ena omwe ali opemphela munchoona iweo ndi Mulungu kuti uwadziwe opemphela munchoona ndiochimwa?we know nothing about it but what inkow is that palibeso chinthu china chopindulisa pamoo wamunthu wina aliyese pano padziko choposa Kuyembekezela muchoonadi zakubwela kwa Yesu mkhilisitu amene ali mwana wa Mulungu.
Harriet Jere,tandiyankha fuso langa lakuti kodi ukadwala umaitanila padzina lapita or la Yesu mwana Wa Mulungu?nanga kudikila peter ndikudikila kubwela kwa Yesu chofunika ndichiti kwa iwe?utandiyankha plz
eyetu nafenso tikuyembekezela kuza kwachetu atsogo…koma that does not mean kupita ku KIA ndiuchimo nafenso tikuziwa ndi Ana amulungu okhulupilila mwa ambuye wathu Yesu Khristu nde stop acting ngati ndinu olungama pondiweluza… mwanena mwambiri kuti u mis using mawu amulungu I didnt answer that coz I know am nt am just trying kukuunikilani kuti tsiku lina mukamazalalikila pa group ina musazaweluze zaikeni uthenga omangilila osati kuphwasula polalikila mwa chikondi mosasankha mbali coz yesu anawakonda ochimwa amawafikila mosawaweluza ndipo amatembenuka mtima nkulandila chipulumutso…muli ndi uthenga wamphavu bro koma presentation yanu muchosemu ka element ka kuweluza……have a blessed day
sudayankhe fuso langa in fact ine sindidaweluze koma iweo ndiamene wandiweluza.u too hv a blessed day.
stop asking a question with an obvious answer palibe amapemphela kwa Peter nde uzifunsa ukuganiza Peter ndi munthu olengedwa ndimulungu…ndipo reference ya ili poor pokhapo popanga compare Peter ndimulungupo…olo mwana wa 5 years akhoza kuyankha kuti timapemphera kwa mulungu nde musayankhe mwaphuma ganizani bwino bwino komanso afunseni a mzimu oyera akupaseni yankho loyenela musangoyankha kuti muyankhepo basi
nchifukwa chake anthu opemphera we missing the target….spread the gospel and bring people into the kingdom of God…how can that be possible? love from the book of Corinthians .unconditional love tiafikile yes koma nt moaweluza coz tikatelo athawa sabweranso kuzanva uthenga wachipulumutso uja…..
Kodi ndani pa ma komenti osewa wanena mzake kuti ndiochimwa or kuweluza mzake?iweo wandinena ine kuti ndine ochimwa ndipo wandiweluza.iweso ukufunika mzimu oyela kuti akuunikle ndikukuziwisa choona chomwe komenti yanga ikutanthauza.komaso iwant u to know this from now on ukafuna kulemba dzina lakuti Mulungu uziyamba ndi chilembo chachikulu osati chaching’ono.
Palibe kuweruza koma akuphuzitsa ndipo vumbulutso la mlalikiyu nd lakut tisamataye nthawi nd mzadziko pakut ndizothera pansi pano
Same same bible anthu timalimasurira mosiyana mmalinga nd maganizo nd conditioning yomwe alili sadziwa choona chili mmawuwo
Bra #Patrick katsabola zikomo pondiunikira choona cha moyo ukudzawu
Za pta aaaaa sizikundikhudza wandisangalasa ndiwe wandipasa chakudya cha uzimu
I think you are pastor
this is it ma ccta Brenda queen,titayilenji nthawi ndizosala zadziko lapasi.amen in Jesus name ma ccta
Afika a president aja tadziwa ali moyo kwa tonse amene timadikilila nkhani ndiimeneyo…tisaleme kupemphelela Dziko lathu la Malawi…zikomo
we r waiting the most important thing in our lyf which is Jesus christ the son of our most high God.
Hahaha Mr. Katsabola seems to have the biggest problem, he looks at everything in this life negatively as if there’s nothing good. Ur not yet in heaven Pastor Katsabola, ur still here on earth and by the way ur not the only 1 who believes and awaiting God’s kingdom. Stop ur funny hypocrisy and blasphemy here. Inuyo mukamafika pakhomo kuchokera kotumikira, ana anu sakuthamangirani / kukuchingamirani musanalowe mnyumba “eyaa adad eyaa adad!” akatero ndiye kuti ngochimwa sakudikira Yesu?? Hahaha some people are obsessed with negativity and they are blind to positive life. Case of hypocrisy of highest order!!!
Ken M’baya sumukudziwa tanthauzo lakomenti yanga ndipo simungavesese or pang’ono,koma ndikuyamika Mulungu kuti pakomenti yanga sindidazitche olungama koma ndati ndiodala omwe akuyembekezela Yesu munchoonadi.kodi chinakunyasani ndichani pakomenti yanga?inuo musathe mau or kudzivuta ndikunyoza ine sindidakunyozeni koma inuo mwandinyoza kuti ndine wachipha maso komaso ndili ndi ziwanda, in fact mwati ndine wakhukhu.here is the words if want or not in my lyf chinthu chomwe chili chofunika kuposa moo wanga ndicho kuopa Mulungu,or mutandinyoza momwe mumadziwila koma ine ndili nga pa Yesu no kusuntha.ndipo sindidati ndine olungama ayi koma inuo zaonekelatu kuti mwangodana nane chabe.ineo sindingaleke kupanga post komenti yokhudza mau aMulungu pomwe ndikuona kuti ndingathe.meaning ya koment yanga ndiyakuti anthu asamataye nthawi ndzaziko lapasi koma azikumbukila kuti pali wina amene ali ofunika kuposa amene akubwela ponpano.osati zomwe inuo mukulankhulazo.
am just reading the comments basiiiii
Inu aKatsabola simudzamupeza munthu amene satenga gawo pamoyo wadziko lapansi. Munthu ndithupi ndimzimu. By the way ndaona mwamudzudzula Harriet Jere zakalembedwe ka dzina la Mulungu. That was also not necessary coz Mulungu sadzaweluza munthu kuti umalemba motani dzina lake. The most important are those ten commandments. Tidzakapulumuka mwachisomo osati chifukwa cha ungwiro Mr. Katsabola
muli ndi milandu inu inu mr Ken M’baya but its ok choice is yours n me ihv my choice also,so plz musandilese kukamba za kubwela kwake kwa Yesu coz ine sindidakuleseni kukalandila peter.ndipo musandiweluze chifukwa ine sindidaweluze.musandinyoze poti ine sindidanyoze.litchulidwa ndi tiana takuyamba kulankhula nanga ine nchitilenji mantha kutchula zadzina lake.
Mr. Patrick Katsabola mukadakhala ndi mphamvu yoletsa anthu kupita ku KIA lero mukadawaletsa koma poti mphamvuyo mulibe nchifukwa chake mwangowanyoza kuti alibe nzeru popita kukadikirira APM m’malo momadikirira Yesu. Inu mukuganiza kuti onse anapita kumeneko alibe chauzimu? Ena anapita kumeneko kukagwira ntchito monga atolankhani, asilikali, ena anapeza mwai okagulitsa malonda, ena anapitila transportation business, ena anapitila kungosangalatsidwa. Onsewo inuyo a Patrick Katsabola mwawapanga disqualify pa moyo wauzimu?
Am agreeing with Ken & Harriet lol
Mau a Mulungu powagwilitsa ntchito pakufunika mzeru zakuya zedi mwa Uzimu, chifukwa Generation ino ndiya nzeru kale zochuluka so to convince pakufunika kuyankhula modzichepetsa
zoonadi Mac and anzimu oyera ndi a dongosolo pozeka iwo pamakhala bata nde we should ask the holy spirit atiphunzitse how to present mau amene ndi vumbulutso rather than speaking it in our own way…
inu musandiweluze coz ine sindidaweluze,musadzivute muntima mwanu chifukwa ine ndalankhula chilungamo.ndipo sindikuona cholakwikwa pakomenti yanga coz sindidanyoze Mulungu koma inu mwadana nazo poti ine ndalalika.odwala ndiomwe amafuna dokotala osati anthu omwe ali bwino.kamba kamaonekedwe anga simungagwilise ntchito uthenga wanga koma mutha kugwilisa ntchito uthenga wa anthu amene ali olemekezeka ndioyenda ndi bodigadi.tisaiwale kuti Mulungu amagwilisa ntchito munthu amene wafuna komaso nthawi yomwe iye wafuna even pamalo pamene iye wafuna.Mulungu emweo amatenga zinthu zopanda pake kuti zikachititse manyazi zinthu zanzelu.musandidelele kamba kamaonekedwe simukudziwa cholinga cha Mulungu pamoo wanga.mau aMulungu akuyenela kulalikidwa ndiwina aliyese posatengela maonekedwe chuma or umphawi.ndikukuuzaniso kuti pali wina ofunikila koposa amene dzikoli likumuyembekezela amene adzathese mavuto awanthu.
in my comment ididn’t say anthu apita ku KIA ndiopanda nzelu,inuo ndiomwe mwatelo ndipakamwa panu chifukwa choti simudanvesese cholinga cha comment yanga.vuto lili ndi amalawi ndilakuti timakhululupila zokhazo zomwe athu ochita bwino angalalikile or zikhale zabwino or zoipa.koma ine sindidanyoze ndipo ndalankhula choonadi kuti sikuti poti peter wabwela mudziko muno nde kuti mavuto akutha ayi.kuti mupite kumizi even mmatauni anthu akuvutikabe sadasiye kuvutika kamba kakuti iye wafika.nde ndindani amene angakhutise anthu anjala ndikumwesa madzi anthu aludzi?ndi Yesu yekha angathe kutelo,so that is y ndikuti tisamataye nthawi ndizinthu zosala zadzikoli pakuti pali wina amene akudzifunila ulemelelo Kumwamba.Mr Ken M’baya mudapita ku xool in fact mumganiza komasoi mumaona,so ll u plz tell ngati ndikunama kuti Yesu ndiye adzathese mavuto adziko lapasi.
Am tired of reading comment plz shorten them!!!!
Lol
Mr. Katsabola. I never meant to offend u. I don’t hurt other person’s feelings deliberately. I was just trying to present my argument. Take out that inferiority feeling from within urself, I didn’t even check ur profile to see who u are. I could have still presented the same argument even if it were some other famous preacher. It was a pleasure interacting with u Mr. Katsabola
taphunzirapo zambiri pa comment yanu bro…osalema kulalikila uthenga big up…take everything discussed positively and Improve mmwina takonzanamo..ifenso tatelo atsogo have a blessed day….osalema kuyembekezela yehova…Isaiah 40 vs 31
Ususuka mpaka mwezi kkkkk
Sititopa tafika kale ku airport tiuzeni zowona andisowa abwana.WELCOME BACK HOME BOSS,Munthu monekhe makhaliwe awe!!!!
Ali tchelu koma osati loona malilo loona wa moyo osati wakufa nde mudzadzi tukwanitsa bola musakhale mwaika kwa merika konko ndiku panga prastick sajaly ndiku muveka waku banja la amuthalika ndendende osasiyana pali pose ndi piter chifukwa amerika ndiku idziwa bho bho e to z kukhani ya ma sajaly wa sianango gula manda kwa merika ma dokotala amene amapanga za masck yofanana ndi piter amaliza loweluka ndinkani mwapanga kuti afike kuno lamulungu your welcom fake piter muthalika on sunday
Chichewa and English zavuta apa, eish I don’t get you clearly
Chai amalawi kupusa inu,,,inenso I’m still nat get u,,pantundapo ka mukuti Chani? #Philip make us understand
Lelo ndi la mulungu gays osama comenta zoti ena aku oneleni ali ese imakhala yolakwa lakwa W umamu ona ngati Z timayaka komabe muku dziwa chomwe ndina tatha uza koma poti nose apa ndinu okula ntima ndinkani mwabwela ndima waizi tieni tidikile a piter muthalika a feg wo basi chifukwa boma lima bisa malilo mukumbukila ifa ya bingu wamwa lila ankakana kuti sanafe komano panalibe njila iliyose yotiphimbila nmaso chifukwa chipatala chake chinali cha sento chomwechi nde awa atipangila pran sinanga akudziwa bwino ango gula manda kwa merika khulupililani akubwelayo si piter ango panga chi prastic sajaly chofanana ndi piter amerika siyama sewela zidza ululika nthawi ina yake mudzamva ndinkani amalengeza zoti amene adzinena kuti piter wafa adzimangidwa aku dziwa ndichimene awumbacho pano n.tsogoleli wathu ndi FANO osati piter koma chidzi endela dzina lomwelo
Fokofu titsimikiza tikamuona ndi maso athu osati zammaluwszi ayi
Counting down time has began
Aaaaaaaaa bola dziko likhale opanda president …..
kungoti kulandila mtembo
osati kumusowa koma kufuna kuziwa zoona pazambiri zomwe zikumveka…chinaso ndalama zamalawi zapindula chani.ndiochepa omwe amusowa koma zoona zake zikhala zikuziwika pakubwela kwawo bwanawo.tasala ndi 1hr n some munis.
Count down? Lol
Kkkkkkk kma mdzanga wandisangalasa ukut osat kumsowa,kma ukunena zoonz kkkk
To know the true its needed very
nanga tiziwerenga bwanji….tikuchosela pamenepo.koma fundawo ndiongozipasa kapena wanu weniweni #Linda?
Wanga umenewu Nemar. Unapanga search uwapeza azichimwene anga and my sister.
koma ndendasekatu….ok ndipange kayedi search.
Asakhale atamveka ma jackets atatu kuopa kuti angaoneke woonda kwambiri after taking some vergies in USA.
Mfundao anapasa akugwira vepiyotu naweso osongoona bwanjii mpaka ugwire ndimanja basi
kkkkkk koma bro remember kukumveka kuti no media nde sitiziwa kuti zili bwanji kumeneko….komaso USA ndisuper power imapanga zinthu zosayembekezeleka.koma we still counting down sunday.1.5hr remains.
#ky ndifunda wawo ndawuona bro.basi linangokhala lachilendo kwaine.
Eya sika common tilipo ochepa. Ambiri amadabwa malo. Koma ife tinali zolowera.
Sila not sika
Akuti nl media?
nafeso pano tayamba kulizolowela moti kuzalimva kachiwili no problem……ine ndasala ndi 40mns plz kufuna kumva kuti bwana afika uko kumalawi??poti tili kudziko la eni tizimvela mumasocial net momuno.
akutelotu eti kulibe atolankhani kulowa moti akankhilako chitetezo chonkwima kuti asapezeke.
wafika
alibhobho……ndione kaye ngati malatest atuluka.
#Tambala ndemwatukwana muli ndichisangalalotu.ife timafuna kuti abwele nde azisogolela komaso kuuza mtundu wamalawi zomwe wanyamula kwatym yayitali kumene anali.
Wabwera chifukwa chofuna kwake ndiye bola akanafera konko ife tikanayimba osana
atimwe !atimwe!atimwe!
Kkkkk afe ameneyo basi
Kkkkk afe ameneyo basi
kkkkkkk kumeneko ndiye ku malawiko.
Yaaaa alongosole bwinobwino chomwe chinamuchedwetsa kuti mpaka afike lero
Kkkk watikwana ngati sanena bwino abwelera
afika nthawi zanji
Koma kumeneko
Watikwana zochita zake
Ameneyi adyeletu