President Peter Mutharika has appointed a new Malawi Electoral Commission (MEC) chairperson.
According to a statement from the Office of the President and Cabinet (OPC) this follows the nomination by the Judicial Service Commission.
Mutharika, has appointed Dr Jane Mayemu Ansah, SC as the Chairperson of the Malawi Electoral Commission.
Yesterday Mutharika also appointed four legal people as judges of high court of Malawi.
Mutharika is in USA and he will be back on Sunday 16 th October , 2016, according to government.
Ansah’s replaces Maxon Mbendera who died some months ago.
T
whether this is true or false, time will tell. lets wait til 2moro. zakuva ziphweteketsa makutu
Ok tamva tiyankha mawa Sunday
is peter alive
zasolobana mu kalasi B
MALAWI SAZATHEKA
Wanenera kuti zimenezo munthu sitikumuva olo pa BBC kuti walankhula
we will hear goverment deadly plan it will be no longer a hidden agenda.
Kodi APM ali ndi moyo-be eti?
Malawi wavuta
So you think you can undermine the constitution,,wish you quick recovery or rest in peace
Nanunso Mukutinamiza Mukungot Lero Mulemba Izi Mawa Izo Eee Wamwalira Eee Wauka Munthu Omwalira Angasankhe Mec Chairperson?Kulan A Malawi Mmaganizo Pa Ndale Mwatikwana.
i am Mr jang from zambia, iam really happy
that i and my wife are cured of HIV with the
herbal medicine of dr sule , i have
been suffering from this disease for the
past 3 years without solution until i came
across the email of this doctors who have
cure so many people with his herbal
medicine, i also chose to give him a chance
to help me and my wife, he told me what to
do and i kindly did it, and he gave us his
herbal medicine and direct me on how to
use, i also follows his direction for use and
he ask us to go for a check up after 2
months and which i did, to my greatest
surprise our result came out as negative,
we are really happy that there is someone
like this DR who is ready to help anytime
any day.to all the readers and viewers that
is doubting this testimony stop doubting it
and contact this Dr and see if he will not
actually help you. i am not a stupid man
that i will come out to the public and start
saying what someone have not done for
me. he is really a great man contact him
now.dr thruough whatsaap +23462447651
Where is our President plz?
Mmmmmm kaya
Akamabwela mawa akhala atawondatu
Zopusa izi I leave Malawi tomorrow to USA
kkkkkkkkkk
I smell arat with diz apointement.chilipochilipo
How can u apoint pple.anthu asakudziwa kumene uli mr bwampini
BBc ikuti bwanji kodi?
please allow me to be afool on this one,,,,,
Ndikhale mbuli pa khani imenei ndikalakhulapo eeeeee andimanga
Amalawi anzanga ine ndiliku sauth africa funsolangandiloti aprezident peter alikuti?
Mesa mumati wamwalira???shameless and mannerless creatures. Mxiiiiiii
kkkkkk eeee koma a malawi,,y always we live on speculations, nkhani yoti pitala wamwalira/akudwala yathano mwayambisa yot he z tryng to harm Chilima,from 1964 ndkale amalawi lets be civilised,,
kkkkkk eeee koma a malawi,,y always we live on speculations, nkhani yoti pitala wamwalira/akudwala yathano mwayambisa yot he z tryng to harm Chilima,from 1964 ndkale amalawi lets be civilised,,
Wait until tomorrow. See if he’ll even hold a Press briefing…let’s bet…kkkkk
de issue ts nt holdng press briefng,Last yrs UNGA he conducted press briefng days after his arrival,,does that mean he was sick,eee wamwalira,,ee amupanga operation,,eee afuna achose chilima,,kusowa zochta bas
Amalawi tatani zafika kumafunilana imfa,choti mziwe aliyense ali ndizitokotoko zakhe or angalakwe bwanji tiyeni tikhale ndi umoyo waum’nthu plz.
The question is why appointing pple today, when he is coming on sunday. Why not appoint these pple on money when he will be back in office. Are these appointments urgent?. Cant we stay a week without MEC chairperson.
Alikut amenewa achikulile
Hello search Kim Ancin BBC reporter then uzani anthu zoona zake
Where is our President?
Ine ndawerenga pena pake kuti APM wapezeka atafa mmawa wa friday pa 14 octber 2016 mu hotel ku New York.True or false?
I think something that I fear has happened, otherwise these appointments are some of the preparations of fooling unnoticing Malawians. but what you gonna do as you know God is watching you!
A president a Saulos Chilima udindo wanu mwauyambatu ndi moto ayi zilibwino koma dziwani zobisika pasi pathambo ziululika sunday pano
making appointment from the brother hood
A Chilima maudindowatu nde mwagundika nawo kusankha koma dziwani sunday ndi mkucha lomweli lomwe tidzaone thambo lakuda
Sankhani bwana olo muli kutali ndinu mtsogoleri wa dziko lino la malawi. kaya wina afune kaya asafune wasankha basi. NG’OOOOOOO. !!
Congrats mama
Kumangolembana olemela komanso nkhalamba zokhazokha pamtumbo panu .
To me it doesn’t matter where the president has made the appointment.In Malawi or outside the issue is he is the was who is mandeted by our constitution to do such a thing,our constitution is silent on where the president is supposed to be when making appointments.Things are not okey in this country but we should not politisize everything.For our democracy to grow we need these people to hold vacant positions.Diso lanji lomangoona zofooka zokha basi?
Why the urgency??? Someone is firefighting an imminent blaze….kkkkk
Drama ilo…
Somebody is being successful playing with the masses ,where is the law society in all this?
Several apointiment death threat no welcome president by ordinary people no media house arrival midnight what a game lets wait and see what will happening on sunday
Peter Akuwawasani Simunati.
No!!!!! Who is making all these appointments? The reports indicate he is not alive. If he is alive then why not waiting until Monday after his arrival on Sunday? Why koma kuti anthuwa azifa chonchi pachibale? tizi jb project ija ndiyowona? If it is true then mwalanga otsalafe!
kkkkkkk death is naturally bra waka
posachedwa pompa timvera programme yakusowa kwake kuno ku tanzania pa radio ya magic fm.
nonsense’ not nonsece @bless
I can smell disaster with dpp, even hav doubts if it’s Mr president electing these pipo in these positions. Something is fishy here. I’m counting hrs now 4 his arrival 2 sort this mess happening.
Dnt get this thing clearly, why he z appointing high rank positions while he z away? Cnt this wait until he come home? I smell somthng fishy goin on
He can manage to appoint any one by using a remote,its easy.
how could that happen??..where is he?..why is he appointing the Mec chairperson while he is nowhere to be seen?..do you take Malawians for granted?…something is wrong with this so called the president….we will be shocked come Sunday am telling you Brethren.
Komaditu zatamba kupereka cithunzithunzi chinachake apa
Kunali madolo udolo unatha
Tizingosiilana mwamtendele osati tidziphanapo apa amalawi we all one
what goes up always comes down,something will surface one day.
pakadakhala kuti padali kubera mavoti sibwezi atasitha chair ya Board ya MEC.apa ndipamene zaziwikiratu kt mm ee muthuyu adawinira phamvu ya mulungu not kubera,ndani angamusiye pazuwa muthu yemwe adakupasapo mazi okumwa?mwina prediction ikhale yotere:pali kukaikirika kwa moyo wake Apm ndeno wakambirana chochita ndi jane ndicholinga choti akamwalira peter chachiziwikire chilima atenga udindo,poonesesa kt chilima ndi central region apa Peter azaphwanya mawu a Muluzi amene adamusiyira Bingu onena kt”asapereke udindo m’manja mwa zigawo zina”so ngati Apm wasitha apa chachiziwikire 2019 sourthen region ikupezaso president,Atupere Muluzi kod mungandiuze kt panopa ali pati?Nanga akutani?mupeza kt adasiyira lucious Banda kukhala president osusa wa UDF.Atupere ali ku DPP.eee pali kathu apa,pali kubisala kotheratu.#MALAWI DZUKA malawi.ndikunenesa Jane akupanga zozawinwsa Atupere ngati kususane nane nazoni tizaona,and palibe kumwera ndikumuona than iye basi.mbite
mmmm the bwana ,,,,no more this is propaganda
Kumbukilani Mr Mbendera inu mwasankhidwa
Malawi dziko langa lija, akusankha ma udindo amenewa ndindani kweni kweni, koma zimenezi izi izizi izi, Mulungu wathu invani kulira kwathu chonde chonde, gonjetsani satana amene akuzunza zolengedwa zanu
Za nsomba nsomba zikuchitika apa(something fishy is going on here)
Muthalika akumasankha anthu mumaudindo chosencho ali kunja why no sense
Complecated issue, is not APM pointing these people into power but Rotten Cabnet and seems like there is aim behind these pointing, let us wait and see. DPP also known as CRIMINALS PARTY (CP)
He is apointment when? Bcz our leader iz there at USA hey government tell ours truth about our presdent
How did he do that? His last seen is last month. Something fishy is happenning
Why all these appointments comes while he is not in the country stop kidding us anyone responsible for these new appointment will answer to the Malawians after burial ceremony
lol…ati after burial ceremony
Mwaiwala A 24 Kuti, Muzafuna Anthu Monga Amipingo Yosianasiana Kuti Anzapange Mwambo Uja Mukudziwa,komanso Akubanja Adzakufunsan Mafunso Ozama,ndipo Ife Anthu Tikufuna Kudziwa Chilungamofe Tidzakhala Pambuyo Pa Banja La Amunthalika, chifukwa Pano Mukudziwapo Kanthu ok, Adzukulufe Muzatidziwa Khalani Choncho, Musaome Ngati Munthu Okhala Phe Ndiop usa.
THE PRESIDENT IS NOT SEEN 4 THREE WEEKS BUT HE IS BUSY MAKING SOMES APPOINTMENTS IF HE IS FIT THE PRESIDENT SHOULD COME ADAY TIME SO THAT EVERY CITIZEN SHOULD SEE ON TVI NEWS
What happened to the information bill!
iiii inu musadabwe amene akusankha anthu kuwapasa maudindo ndi a president adziko lino asaulos chilima amasankhilathu bfore opuma aja asanabwele pavuta apa kkkk
Very lies, mmmmh unofficially result Tb jushua was Right.
kicks of a dying horse!
ZOVETSA CHISONI,AMALAWIFE MUMATITENGA ATULOZEDI KODI DZIKOLI MUZILAMULARA KUJAKO
munthu okumfa akusakhaso munthu wamoyo.
Who is doing this job of appointments? l believe someone is doing it on his behalf and inform him on how we are trying to make things work in his absence.
Kodi Chikuchitika Mchani?
How does he appoint such people? He is nowhere to b seen! online?????
yeah man,these niggas are up to something
Coach amasankha bwanji osewela mpila oti ali kunja? Wafuna kuonesa mphavu zake komaso kuonesa kuti adakali moyo
Amene Anaganiza Kuti President Azisankha Wankulu Wa MEC Anali Wa Tulo Ndani Angazimange Yekha Akuba Inu Kumoto Kale Njoyani Ndi Dziko Lapansi,577 Billion Of Poor People Is Waiting
An advice to the new appointees. Mzako akaphunthwa iwe podutsa umadumphapo. Pamene mukulowapo panaphunthwa mzanu. And from past experience, whosoever helps this government fulfill its evi intentions either does not last long or he is chewed and spat like chewing gum. One living example in Chilima and a non living one in Mbendera.
Kod news zatha ku Mw tatopa ndikuva za munthu modzimodzi ife( don’t under mind us please)
nde mwati dont under mind???? ok.
they are underminding u indeed kkkkkkkk but this is a hit. ngakhale BBC imabeereza nkhani 6 to 6
Kumec Simalo omakalirako zosokoneza malamulo sitikuzifuna anthu otele mulungu adzawalanga
Akanawasakha atabwerakomkuno abwanawo.akusakha alikunja?why?ife tidikira tizave okha bwanawo akulengeza ndipakamwa pawo wakudyesani bazi ndani?mwayamba kukoza kapasi kuti kamwamba ka 2019 katsike?
u guys from news24 you are crazy . the same person who is dead how can he apoint some one in other position? tell people the trueth ? stupid don’t confuse us
Tiudzeni zoona a Malawi! timamva kut Peter mtharika anasowa, is it true o perhaps they are kidding?
lol akut last seen yake it was 20th september,koma abwera sundy koma usiku and no media allowed,(zinveka)
And others were saying that he is capacitated n what do u sy about that?
Nosence,munthu wamwalra uyo,osamatipusitsa nthawi ino siya asamunda.
congratulations mama Malawi
Mmmmmmm
I don’t understand this,ghost is pointing people as leaders?anyway we are all ghosts.
Operating from where??? Why so fast??? Judges and now MEC officials, lets start guessing…
I guess may be APM is dead
50-50 Real gender selection so kip it up prof APM being truly visional, progresive leader plus africa statesman bravo
Hahaha hahaha….joke of the year.
I can fore see that these appointments are up for a hidden agenda,but mind u GOD is there,u will not succeed. When u want to cover a sin u end up commiting another sin. Be careful.
Nde zoti wamwalira dzoona mwina akupanga ma judge ndi ma mec comm. ndi ma dpp guruz afuna apange manipulate who will succeed peter
Kodi Kamulepo atilankhulirepo kkkkkk
Something is not right i can feel it
This is madness, why and how can he appoint people while his whereabouts is not clear known.
This is madness, why and how can he appoint people while his whereabouts is not clear known.
President anachoka bwinobwino kusazika ntundu wa amalawi ndipo sananene kuti abwelako liti inu lelo nkumaima pachulu nkumati his whereabout is not clear known. mumamvela kuti makamaka kapena mukufuna aziyenda one- by one mmakomo azikuuzani kuti mumvesese komwe ali?
Ayi ife tinamva zoti anapita kunsonkhano koma osati ku holiday and nsonkhano unatha azinzake anabwerako kale.
inu nanu a sobilika musamangobakira zilizose anthu sakudana ndi kuchoka kwa president but they want to know kuti msonkhano unatha what is he doing and where? period, ngati inu mukudziwa fine awuzeni anthu zoona chifukwa ndalama zikuonekazi ndi misonkho yathu bear that in mind.
Always negative mind eeeeeee
He has kicked the bucket lolll
Owk
Why is he appointing people while he is in another country, his last seen is on 20th September hence electing people. Wake up My fellow Malawians and make sure no one takes the laws of Malawi in his hands.
Lol mpakana last seen?kkkkk
Kkkkkk lol ndazitenga pompa pa Malawi24 kkk
True…last time he updated a status on his fb page was on 24 sept.mmmm something somewhere is not ok
Akanatiuza zoona because he is our president and we deserve to know the truth. If he is not well we can wish him well and pray for him
Even u can pray for him but if God says his days are over we can’t say no,let’s just put in hands of God for this matter one day we gonna see de truth
Ngati ndikale Ayanda Gama Wosinthika Duncan? finals iliko sunday game idzamenyedwa pa KIA at 12 midnight.No media allowed….watch this space
Kkkkk koma Elias ndiwe wanthabwala bwanji uli bho
Stop it guys.
The president operates while he is outside kodi bwanji guys kukhalangati simukudziwa maiko amzanthu azichita kutiseka zomwezi?????
Kkkkkk last seen yemweo
bt God not allow that stupid news
I dnt kno kut amene amapanga malamulo panthawiyo ankaganiza chani..amaganiza ngati anthu osaphunzira cos sangapatse mphanv president kut azisankha akuluakulu a MEC…mwachidziwikire apa Dpp izabaso
Thats true I suggest may be it has to be elected in parliament
yeh…We hv educated pple bt dey dnt make use of der educatin…
Sunday if not tiiware or holideyo zinachitikapo muno M’Malawi
REST in Peace Mr President amenewo ndi ma udindo akumidima tsopano komwe mwafikako
Tsokalida komanso tsoka liyenda kufa safelana mwinanso utha kuyamba ndiweyo kapena bambo ako siziziwika
Kkkkkk
Hahhdhahahahahaa anthuwa akusowa chilungamo yawa
Chimene ungadziwetu ndiichi, sikutitu ananenapo kuti sadzafatu ayi adzafa. Koma zomwe mukulengeza apazi iyi ndi misala, kuli aljazeer tv, bbc and cnn tv bwanji sakulengeza? Inu nokha mwa ma tv amenewa angolengeza ku kukhomo kwanuko basi, bwinotu dzenje ili mukukumbayi mutha kutchola mwendo nokha lisanafike lamulungu usiku. Pamene anzanu azidzati tiyeni tikamulandire ku Kia, inu mukubuula ndimwendo wanu dzenje lokumba nokha kaya bvumbwe zako izo.
Mkulu apm wadwala kwambiri oloko wamwalira zimu wake use mutendere
Underground ways,let’s wait n,see
Kkkkkk alikutiko ameneyu mwina ndi last kick?
Mmmmmmmmmm we call it drama zachamba ife ayi inu olemba nkhani tiyeni tidikire sunday thats all
Ili ndilo boza sopano munthu mukuti afika sunday . …….
ok
True
They will implicate Chilima so that fresh elections should be declared within 90 days then current MEC chair supported by those Judges recently appointed will favour DPP into power again
thats true and those are the mathematical calculations which DPP is makin, very clever and cunning people
Okay
Running a country on Auto-pilot