Ken Msonda dumps PP

72

Opposition People’s Party (PP) spokesperson Ken Msonda has announced that he has ceased to be a member of the party.

Confirming on the local press, Msonda said he will now be an independent politician in the country.

Ken Msonda People's Party

Msonda: no longer PP member

“I can confirm but no further comment… I owe Malawians an explanation but it will be later not now,” said Msonda.

Meanwhile, PP acting president Uladi Mussa has claimed that he has not received official communication from Msonda.

“Officially I have not received any communication, I have my three phone numbers working and we have also a PP forum but he hasn’t communicated yet,” said Mussa.

Msonda’s resignation follows reports that he is on the move to join the ruling Democratic Progressive Party (DPP).

Share.

72 Comments

 1. Zosadabwitsa this guy is too poor! A briefcase, illegal,unregistered Estate Agent without any academic qualification. Always chasing Miracle Money no wonder shortly you hear he has joined DPP!

 2. Akulu amenewa ndi nkhawa tsopano akuopa kuikidwamo mu cashgate nanga si aMayi akumatchulidwa pafupipafupi ndiye ali mmmmh ! ndithawemo osati azinama zina ndizina

 3. Amalawi mumaziwa kutukwana koma tiyeni tiyike 0 budget mumalephera sopano ulowera kuti galu iwe zimene unadya zakukwana basi chonde zipani zina musamulore galu uyu abwera ku zawaluma .

 4. Am just being realistic guys people like ken musonda are not politicians they are just parasites and we don’t need him in pp moreover he is not publicity he is just stupid as he is.. Am warning all parties that don’t give him any position if wanna join your party coz is not type of holding position in a party just accept hip as a member of a party..

 5. Let me help you guys.Choyamba ndiyamikire mr Nsonda poganizira mozama kugwira ntchito limodzi ndi boma.ngati boma lolamula lamuchotsa kotsutsa,apo ndiye kuti fundo zakupsya zomwe zinali ku PP zikaphatikizana ndiza chipani cholamulachi,aaa!! apo basi chitukuko patsogolo.kodi inu !!akati boma nditose anthu wokhala Mdzikomo,posaganizira chipembedzo,chipani,kukula mtima,matama,tsankho,umbombo,umfiti,nsanje,kusowa chikondi chachibadwidwe kudziko lako,ndizina zotelo zomwe zakhala zikubwezeletsa chitukuko chadziko pambuyo.Malawi is a small country,we really don’t need too expensive politics,we are too poor we need to accept it,the only way to defeat the poverty in Malawi,is to work together as one nation.Congratulations Mr Nsonda,u r a great leader indeed.

  • Boma silingaende bwino popanda anthu olimba mtima nkususa ngati nsonda,koma chifukwa cha umphawi malawi alibe oppostion leaders olamula akungopanga zomwe afuna,nzabwino kwa nsonda koma ku dziko its a loss.

  • #Moyo,Ndizoona boma silingayende bwino popanda anthu olimba mtima ngati Nsonda.Kutsutsatu nkofunikadi,koma mutati muwone katsutsidwe kamene kamachitika mundale zathu zachiMalawi,sizikhudzana kwenikweni ndizofuna zanzika maka anthu wosaukafe.Kutsutsa komwe kumachitika kumangokhala kolimbilana maudindo,popeza aliyese akufuna kukhala wotsogolera dziko.Pachifukwa ichi ndichifikwa chake tawona mazangazime akuvuta kwazachuma chiyambileni ndale zazipani zambiri.atsogoleri ena wotsutsa akhala akuthamanga nalo bodza kumakauza maiko akunja kuti asathandize boma lolamulira panthawiyo,koma chifukwa chake cheni cheni nkukhala chakuti,anthu amve kuwawa ndibomali,kenako pachisankho adzavotere ife.Zinthu zaziii!! zosapindulira nzika zadziko.tsutsanani pazifukwa zokwanila kenako gwilizanani pafundo imodzi yomwe iliyothandiza dziko kupita patsogolo.

 6. Your impact has been low so try other avenues the only time I heard you make noise was when you had a brawl with a truck driver and when you ordered the killing of gays I quote “gays are worse than dogs”otherwise go ye well

 7. Nde akuti achita join kuti??? DPP, MCP AND UDF musamulandile uyu. Bola akapume wakula asatinyase ife anthu osakhazikikawa. Only shows they don’t know what they want, komanso kumbukilani kuti ndiyemweyu ankakunyozani uja. Njoka siingasinthe manga chifukwa choti yalowa mnyumba.

  • Basi takusankhani mukhala mneneri wa PP, muyamba ndikutiyankha funso ili: “Kodi amayi ali dziko liti? Nanga akutani ndipo zikugwilizana bwanji ndi chipani chathu? Nanga abwela liti, head gear ija taisowa kikikikikikikii odi uko kodi anatha?” Tiwasowa a msonda pawailesi analowa mmalo mwa malemu Izeki RIP Mr Msonda

 8. Mmm akulu awa ndi adyera,atamangidwa nthawi ija,anaima pachulu kunena kuti wasiya ndale kenaka anabwereanso ndiye apa akuti wachoka pp alibe kopita uyu akungofuta amayi atutumuke kenako amupase banzi.wandikwana odi ukoooooo!!

 9. Kkkkkkkkkk some pipo were born 2 b comedians seriously. what was it that he was waiting all this time. Dear Lord when r these pipo gng 2 rizan? we need new blood in de system.

 10. Akanatani Nsonda,have fought a good fight for PP.Where is it going to be the next destination for this talkative and arrogant man?

 11. koma Ken ndakumbuka akufusidwa mafuso ndi Brian Banda last yr mene amatumbwila..chimodzi amachita kuonjezelamo mawu amulungu mundale poyankha..zomwe ine simagwilizana nazo zoti wandale azinamizilaso kwamulungu..ndale is dirty game anthu aku USA amatelo ndipo tandauzo laku social kwathu kumalawi amati its force manfesto/promise nde awa agwa nayo ayiwala mawu omwe amatumbwa tym imeneyo…ine wandale sizamukhulupilila 4ever.

%d bloggers like this: