The Malawi Blood Transfusion Services (MBTS) has expressed frustration over the low number of people donating blood in the country.
MBTS senior public relations officer assistant Upile Kaivi who was speaking when a Blantyre youth group donated blood said since last year up to date the body has failed to collect the needed quantity of blood.
She then called on people in the country to take part in blood donation with the aim of rescuing lives of people who need blood.
“First of all am asking Malawians to take part in donating blood to save lives and an example is the Malawi club 25, a group of young people who are dedicated to blood donation in the country,” said Kaivi.
She added that donating blood is a matter of helping those who are stranded and struggling for life in hospitals due to loss of blood.
abale tiyen tiziyakhula bwino ngat tonse ndi amalawi, amene ali nd mtima opeleka apele koma ngat xkufuna ungokhala. zotse titsiye manja mwa mulungu,
I cant even donate my blood. what for? The government want more from people, but they dont give anything to people. what a stupid government. They just want to make money out of peoples live’s. How stupid
tasiya kumene mumakagulitsa
this guys they sell our blood to private Hospitals now we tired with that stupid behaviour
Njala is a cause
start buyng pipo wil b coming
I can’t donate my blood.
ma vampire amaliza kupopa ndalama ayamba kufuna magazi….. malawi saakuthekadi
How do u expect more people to donate blood when ndalama za publicity mukawapatsa anyamata anu akumasusanso pompo!kumapeleka fuel wa 5 litres pa tsiku for publicity mungafikire anthu angati? Change the way money is being moved from the central level to the districts for campaigns???????
Kaneneni kupolice yomwe mulinayo pafupi!
tipereka bwanji magazi okwanira pamene ndife ophwanya…..
Zoona kuchipatala kukuchika zachipongwe munthu akumakanizidwa magazi ngakhale mbale wako atampatsa wekha.ndaziona pa DEDZA. D.H.kumakubera magazi opeleka wekha.magazi adzivuta chifukwa chamachitidwe amadokotala omwe akumafuna cholowa pazomwe sanavutikire
Angawa ndikugulisa nothn mahala our days
Tipanga bwanji donate magazi tikugona ndinjala,matupi athu anafooka kale,pofunika mzitipasa chokudya chokwanila osati Sobo ndika Bisiketi Ai Boma Lichitepo kanthu
Magazi achoka kuti tisanadye?ine ndinali opereka magazi each and every time koma vuto ndiloti ambili amafowoka akapereka magazi.
kodi chimene chinasintha ndichani bungwe ili kulibe we were told kuti magazi mzipatala mulibe. Bungweri layamba chimodzizi ndiye kuti blood yomwe mumatenga ija mumapititsa kuti? I see no changes!! Lingokhala bungwe la ulimi muno mmalawi.
Magazi mukufuna anthu apeleke ulele m’bale akadwala mwati magazi ngogulitsa how come? If you really want blood these days it’s for sale as you do finish, mukuzolowera ku dulitsa magazi anthu osaukafe tikumafa nkomwe nkomwe tinachita donate. Hakuna zvakadaro taneta nhekuita donate ropa redu.
#Alick mukanapita Ku transfusion ko anakakuthandizan inexo friend wanga nkulu wake amadwala ndipo amafunika magaz pamenepo nkut ndiri form 4,nditauzidwa ndidapita kuchipatala ndipo adandikanaxo en then ndidapita Ku office kwawo mu dzinda wa BT,Odala centre sadachedwe dzidatheka mpaka munthu adapasidwa magaz ndipo adatulukaxo
Shame on u Lol so u want us to com donate blood with empty stomach?? The government mst find the other way nt us!
The same zitete and mbewa we are told to eat can also make somebody to donate blood? Hehehehehe…..and where do u go with those blood?….because when somebody is lucking blood in the hospital you still ask his or her relatives to donate blood for that person, non is given free blood from you, but you take free blood from us, u people you lucky justice!
it’s unfair kuti ine ndipange donate blood for free koma m’bale wanga mukamugulise the same blood kodi ka low concentrated squash and single glucose mumaona ngati anthu amasangalasidwa nazo?
Athu wofuna kupeleka magazi alipo bt sangabwele kudzapeleka magazi pamene sakudya mokwanila,mapetoake angodziputilapo matenda komanso muthu wotchedwa blood doner makolo ake kapena mwanawake akasowa magazi alim’chipatala zimavuta kutialandile chithandizo,ndiye mukuyenela kupeza njiraina yotipangila encourage bcoz am the one ndapelekapoka 16,dziwaninsokuti kunjaku kulinjala Ka transport so mumapereka kongogulira mzimbe basi,Ganizani mofatsa bcoz Magazidi asowa sizidawoneke ndithu.
Fu……k malawi
Nobody in Malawi they all in S.A. maybe u need to collect blood when they cross the borders
umapanga donate blood uli ndinjala
Let well to do Malawians who are having meals donate
Anthu ali ndi njala magaz achoka kuti?shame on you..
Osawuka anzanga ngati mukupereka magazi anu ndinu dzisilu azikapereka ama cash get wo aliii
No one will danate blood for a glass of Sobo
Ndani angapeleke magazi ali ndi njala??..gawani kae zakudya kenako tikupatseni magazi zachamba eti mwaesa ife zitsime?
Iwish i could but am living wth HIV.sorry
Magazi mulatenge kwa amene akumaba ndalama zanga za cash get
NDIPELEKE MAGAZI MWAULELE NDIKAPITA KUCHIPATALA MUKANDIGULISE MAGAZI ANGA OMWE KOMANSO CHODABWISA NDI CHAKUTI MAGAZI TIMAPELEKA KUZIPATALA ZA BOMA KOMA KUPITAKO UMVA KULIBE .MUFUNA MUZILEMELA NDI MAGAZI ATHUWA APO MPAKA BLOOD GATE ZOMWEZI MUKAFUNA TIZIGULISANA KUPANDA APO MUZITENGANA NOKHANOKHA KUMENEKO
Ine sindizaperekanso magazi ndithu..ndinayamba kupereka ndiri Ku secondery ..masten kudwara kenako ndinauzidwa kuti kukufunika magazi ine kupita ndi card ya umembala kupezeka zoti achipatala kundiyankha mwano..amvekele zimenezo sitikuziziwa
NO BLOOD FOR FREE! 300 ml of blood = k300,000. Mukangotero, ngakhale agogo anga amene ali ndi zaka 90 athamanga kuti nawo apereke magazi. Apo bii, mmmm
Kkkkkkk, koma a bro.
Kuli njala,,
Mzikatigulisaso magazi aliathu omwe
Mzikatigulisaso magazi aliathu omwe
iiiiiiiii zoona sindimaziwa eti . ndie zatha bwanji ?
Malawi blood transfusion service should be buying drugs
Munthu angokhalira kutafuna mango zosakhwima daily, magazi achokera kwaani? Chosanani nokhanokha okula mimbanu.
ife magazi athu ali ndi tizirombo toyambitsa kaodzera ife! kodi nduna ndi ma Ps bwanji akapere nawonso
ife magazi athu ali ndi tizirombo toyambitsa kaodzera ife! kodi nduna ndi ma Ps bwanji akapere nawonso
ma mp ndiamene amadya bwino,,ndiye ayenera kumapeleka magazi
We are just luck that pple are still donating blood,,,,with this hunger crisis we r facing its very difficult 4 someone to have enough blood and also dont 4 get there is HIV which is also growing rampant hence reducing a number of blood donors lets just thank God for what we are getting.
Pamenepa ndie kuti ogwira tchito yopopa magaziwa akulandira malipiro? Nanga poti magaziwa akapopa akumawatumiza kunja kukathandiza iwo amene ali ndi ndalama opopedwawa mkumadwala anemiya kaya kuti kusowa kwa magazi nthupi ndie mukudabwapo chani? Sangaperekeso basi akwiya.
Magazi achokera kuti ndinjarayo ndiye kanthu azikafera konkotu!!!
Magazi omwewo anthu apeleke ulere mukugulitsa mzipatala za private ndalama zambiri koma munthu opeleka magazi mukumupatsa orange squash is that fair
Kodi mmesa bungwelo linapangidwa ndi anthu? Dzipopanani ogwila ku Bungweli.
eee
Munthu Wadoneta Magazi Monday Kubwela Tuesday Magazi Kulibe Kodi Munthuyu Azabwelanso?Ganizilani
Anthu apanga bwanji donate blood pomwe akudya zitchetche mufuna afe?
MUKAFUNA KULEMBA NTCHITO MUMAKATENGA AZIBALE ANU NDIYE POTI NDI MAGAZI MWAFUNA MUNTHU WAMBA ANTHU OYIPA INU PAKALOWA MBEWA OKUMBA NDINU KOMA PAKALOWA NJOKA
Awuzeni mayi akumationa kupusa amenewa
Azidoneta mabwanawo mumene mukuti ng’ambira custom nkumaka pereka magazi awulele chamba eti
Mufuna mutiphe chani?
Tikuzunzika ndi njala pano nde nanunso mutenge timagazi tathuti?
Ana anjoka inu?
Palinso njira ya ma tablets. Bwanji mumango kakamira yokhayo?
You can’t donate blood with an empty stomach, people are starving out there
Hw can u donate blood while it’s a week without food in the house?Ask ur president n his idiotic fools they will give u blood. Stupid idiots! !!!
Ndi njala iyi afe?
Anthu achifundo tilipo ambiri koma vuto liripo tachuluka ndife a gulu Q athu ndi a green ngati a chiwala ndiye mmatibweza
tiDoneta bwanji blood njala yonseyi?? osamayankhula mopusa
Mhahahaha koma A Herb. Kkkkk
Sinda hehehe aise anthuwa sali serious, tadya zitete tiDonetanso bwanji
Kikiki awuze aaaaa
Joy u know ryt, food first
True that,,asamalankhuledi mopusa lol
Kuyangana amene akugwira kumenekowo ndarama zolandira mphwamwamwa,opeleka magazi k250 basi akafika nayo kuti olo chiwalo ndi chips osakwana,anga 15000 tube olo usiku ndikhonza kubwera
Malo monena za njala ya vuta kunoyi mukukamba zopusa pitani kwa aja a cash gate muka Pope km ngati mukufuna kumpha athu pitani mizimu cz athuwa sakudya ndiye mukuyembekezera kt akupaseni magazi chaka chino chokha mwapase chimanga athuwa magazi mukatenge ku parliament
Try to buy from us,muzasowa powaika 5hnz per pint ife tikatelo wakunkalabongo.
the same blood which we donate kukafika kuchipatala akut ndgule for whatttttt it’s time to suffer now in all hospitals
People are sleeping on an empty stomach@ the point of death due to starvation.lnsofar,you expect them to danate blood?? Tell lbu and his hyena to donate blood to MBTS,these are the ones who enjoy the fruits Malawi is offering
Za ulele zinatha azitigula
Anthu kukhalila zitete ndi mbewa angakhale ndi magazi okwanila?
Basi tsekani bungwe mbava inu mwalowetsa maphunziro pansi ana onse anatha nzeru kamba kowatenga magazi. Ndikut tsekani bungwe upanda apo mukatenge achebalewanu
munayambira muja?abale athu akasowa magazi kumakana kuwapatsa zaziii,mukatipopa magaziwo kutimwetsa katambula ka squash,amene ndinaperekawo akwana
mpofunika boma ligwire oxe cashgate lizkawapopa magaziwo lisanazenge milandu kkkkkkkk
Ine ndinasiya amenewa amagulisa magazi anthu nzipatala za privete, nzipatala za boma magazi amasowa pomwe zinazo amapezeka, ife tikamapeleka magazi cholinga chathu nchoti amalawi ovutika azithandizika, akafunika magazi, koma ayesa ngati bussinesss, zopusa akhale choncho
KULISO CHAULELE PANO? POPEZA MUNTHU NGAKHALE APITE KUCHIPATALA MPAKA MUMAFUNA PAPEZEKE M’BALE WAKE APELEKE MAGAZI INE CHIBADWILENI, M’BALE WANGA AKAKHALA NDI VUTO LOCHEPA MAGAZI SINDINAMVEKO KUTI MAGAZI ALIPO TIMUTHILA AI.
My blood is not for business.
eya magazi kusapeza kumene tachuluka ndi postive okhaokha mwazzwa
eya magazi kusapeza kumene tachuluka ndi postive okhaokha mwazzwa
eya magazi kusapeza kumene tachuluka ndi postive okhaokha mwazzwa
Magazi kupeleka koma akngofika mzipatala nkhani yasintha ali akugulisa demeti!!!!! Donate blood save lives ….so how come for bustards to blood yet ppoh donate for free?? U must also buy from ppoh ….. Munya muona!!!!!!!!!
muyambe kugula ngati mbewu muone mmene atapezekere magaziwo because munthu opelekayo akuyenera akagule chakudya kuti abwezeretse
Basi thesani bungwero…nanga inu mumapereka magaziwo ulele ngat?
pay us for it. nothing for free these days just like how patients pay for the same blood we donate
Musolva…palibe akupereka maganizo pano..!! Afe ndi njala kapena bwanjiii..!!
Satanic has alot of blood, what more government? Please borrow from them and refund later.
muzitipasa kaye ndalama ngat mukufuna kut tizipeleka.
Uzani Peter ndi azizake akupatsani
Mmmmm nawonso atani kodi?? Njala yake imeneyi munthu magazi achokera kuti?? Aaaah zibwana ait!!
Tatsekani kaye zibowo zomwe magazi omwe timaperekawo akumatulukira nkumapedzeka muzipatala zopita anthu achuma okhaokha.
Muyixova.
Mbuzi zikatere zikagulise kwa mwa bwana osapatsa magazi
I was one of the peoples who used to donate blood but when a patient needs blood they don’t give him/her for free
i totally agree. that’s why i stopped as well
That’s totally wrong to the government because they get blood for free but why they sell it to the people. It could be understandable to sale if they were buying from the people
yea imagine. the government is just using us for their benefit. i wonder if that’s what happens in other countries
Malawi is now awake simungatibereso makape a MBTS
Njala yake imei
Hahahaha thazi lake limenelo kumanamizira njala
munthu kudwala mumati abwere mubale wake akapereke magazi koma magazi omwe mukutenga anthu mukongogulisa kunja bas anaanjoka inu.business imeneyo muziwapasaso ndalama anthu nawoso osat sobo yekha.inu kumagulisa ma million ku zipatala za private
azayambe kumatipatsa ndalama it’s whn tizizapanga donate blood
mukufuna magazi aulere koma munthu kusowa magazzi kuchipatala potulu discharge pali bilo pa botolo lamagazi. muzingolemerera magazi athuwa?
with this hunger situation mmmm im afraid of starving
azayambe kumatipatsa ndalama it’s whn tizizapanga donate blood
Ndili ndi 2 litres yamagazi, inunso mukufuna 2 litres, mufuna ndiume kapena chani amangwetu?
Kawatengeni ma mp aka cash gate akupaseni magazi zopusa basi
Mmagazimu tizilombo tili thooo ndiye tipeleka bwanji? Mufuna tipulure miyandamiyanda et? Lol
kupeleka magazi nkulinga utakhuta!
apeze mphatso za padera zopeleka kwa omwe amapelekawo kuti azikopa anzao nanga zoona ka tambula kamodzi ka sobo akuchotse 2ltz ukachokanso panemepo uzikafunafuna maganyu mKanengomu…?
why don’t ask those thieves in parliament to donate coz they are healthier than poor citizens the cashgaters will donates blood ask them including Mr ibu
hahahah ndikaonetsetsa ku Malawi kuno boma siife anthu boma ndiamene akudya ndalamawo ndiameneso akuyenera kupeleka magaziwo
Aaaaa nde mpaka ukhale mulandu kodi mumapita nawo kuti ?
2 litre yamagazi malipiro ake kapu ya sobo basi,pezani nzeru ina nanga sobo.
Bushiri amagulisa magazi mufunse akutenga kuti
spending 3 day without eating,and you want my blood,Fools.
Kkkkkk uakwana kkkk auze kkkkkkkkkkkkkkk ndakomokaaaa
eeh koma ada
Adzatenge mikodzo ngati akufuna.
Kkkkkk ndakunva
Osamatenga kwa peter bwanji?
This has nothing to do with govt kodi who z the government mesa ndife anthu tomwe.
nanga azingokamidwa ngati ng’ombe, apeze njira zina zopangira convice anthu,ndi responsibility ya Boma kupeza njira ndi ndondomeko zopelekera magazi, amene akumaba ndalamawo samafuna kumapelekako magaziwo, u r expecting munthu oti akuvutika kukagawa magazi aulerere ndikukamwa glass imodzi ya sobo, mmalo moti nthawi imeneyo asake ndalama yokadyetsera mbumba yake kunyumba, tizipeleka magazi kwa m’bale amene wasowa magazi nthawi imeneyo osati kungopeleka chisawawa, boma lichiteposo kanthu
Atsogoleri ma anzelu
apereka bwanji magazi alindi njala!
njala yake imeneyi magazi apungukakamo nthupimu
Why ????