Malawians not donating enough blood

129

Malawi Blood TransfusionThe Malawi Blood Transfusion Services (MBTS) has expressed frustration over the low number of people donating blood in the country.

MBTS senior public relations officer assistant Upile Kaivi who was speaking when a Blantyre youth group donated blood said since last year up to date the body has failed to collect the needed quantity of blood.

She then called on people in the country to take part in blood donation with the aim of rescuing lives of people who need blood.

“First of all am asking Malawians to take part in donating blood to save lives and an example is the Malawi club 25, a group of young people who are dedicated to blood donation in the country,” said Kaivi.

She added that donating blood is a matter of helping those who are stranded and struggling for life in hospitals due to loss of blood.

Share.

129 Comments

 1. abale tiyen tiziyakhula bwino ngat tonse ndi amalawi, amene ali nd mtima opeleka apele koma ngat xkufuna ungokhala. zotse titsiye manja mwa mulungu,

 2. I cant even donate my blood. what for? The government want more from people, but they dont give anything to people. what a stupid government. They just want to make money out of peoples live’s. How stupid

 3. How do u expect more people to donate blood when ndalama za publicity mukawapatsa anyamata anu akumasusanso pompo!kumapeleka fuel wa 5 litres pa tsiku for publicity mungafikire anthu angati? Change the way money is being moved from the central level to the districts for campaigns???????

 4. Zoona kuchipatala kukuchika zachipongwe munthu akumakanizidwa magazi ngakhale mbale wako atampatsa wekha.ndaziona pa DEDZA. D.H.kumakubera magazi opeleka wekha.magazi adzivuta chifukwa chamachitidwe amadokotala omwe akumafuna cholowa pazomwe sanavutikire

 5. Tipanga bwanji donate magazi tikugona ndinjala,matupi athu anafooka kale,pofunika mzitipasa chokudya chokwanila osati Sobo ndika Bisiketi Ai Boma Lichitepo kanthu

 6. kodi chimene chinasintha ndichani bungwe ili kulibe we were told kuti magazi mzipatala mulibe. Bungweri layamba chimodzizi ndiye kuti blood yomwe mumatenga ija mumapititsa kuti? I see no changes!! Lingokhala bungwe la ulimi muno mmalawi.

 7. Magazi mukufuna anthu apeleke ulele m’bale akadwala mwati magazi ngogulitsa how come? If you really want blood these days it’s for sale as you do finish, mukuzolowera ku dulitsa magazi anthu osaukafe tikumafa nkomwe nkomwe tinachita donate. Hakuna zvakadaro taneta nhekuita donate ropa redu.

 8. #Alick mukanapita Ku transfusion ko anakakuthandizan inexo friend wanga nkulu wake amadwala ndipo amafunika magaz pamenepo nkut ndiri form 4,nditauzidwa ndidapita kuchipatala ndipo adandikanaxo en then ndidapita Ku office kwawo mu dzinda wa BT,Odala centre sadachedwe dzidatheka mpaka munthu adapasidwa magaz ndipo adatulukaxo

 9. The same zitete and mbewa we are told to eat can also make somebody to donate blood? Hehehehehe…..and where do u go with those blood?….because when somebody is lucking blood in the hospital you still ask his or her relatives to donate blood for that person, non is given free blood from you, but you take free blood from us, u people you lucky justice!

 10. it’s unfair kuti ine ndipange donate blood for free koma m’bale wanga mukamugulise the same blood kodi ka low concentrated squash and single glucose mumaona ngati anthu amasangalasidwa nazo?

 11. Athu wofuna kupeleka magazi alipo bt sangabwele kudzapeleka magazi pamene sakudya mokwanila,mapetoake angodziputilapo matenda komanso muthu wotchedwa blood doner makolo ake kapena mwanawake akasowa magazi alim’chipatala zimavuta kutialandile chithandizo,ndiye mukuyenela kupeza njiraina yotipangila encourage bcoz am the one ndapelekapoka 16,dziwaninsokuti kunjaku kulinjala Ka transport so mumapereka kongogulira mzimbe basi,Ganizani mofatsa bcoz Magazidi asowa sizidawoneke ndithu.

 12. NDIPELEKE MAGAZI MWAULELE NDIKAPITA KUCHIPATALA MUKANDIGULISE MAGAZI ANGA OMWE KOMANSO CHODABWISA NDI CHAKUTI MAGAZI TIMAPELEKA KUZIPATALA ZA BOMA KOMA KUPITAKO UMVA KULIBE .MUFUNA MUZILEMELA NDI MAGAZI ATHUWA APO MPAKA BLOOD GATE ZOMWEZI MUKAFUNA TIZIGULISANA KUPANDA APO MUZITENGANA NOKHANOKHA KUMENEKO

 13. Ine sindizaperekanso magazi ndithu..ndinayamba kupereka ndiri Ku secondery ..masten kudwara kenako ndinauzidwa kuti kukufunika magazi ine kupita ndi card ya umembala kupezeka zoti achipatala kundiyankha mwano..amvekele zimenezo sitikuziziwa

 14. NO BLOOD FOR FREE! 300 ml of blood = k300,000. Mukangotero, ngakhale agogo anga amene ali ndi zaka 90 athamanga kuti nawo apereke magazi. Apo bii, mmmm

 15. We are just luck that pple are still donating blood,,,,with this hunger crisis we r facing its very difficult 4 someone to have enough blood and also dont 4 get there is HIV which is also growing rampant hence reducing a number of blood donors lets just thank God for what we are getting.

 16. Pamenepa ndie kuti ogwira tchito yopopa magaziwa akulandira malipiro? Nanga poti magaziwa akapopa akumawatumiza kunja kukathandiza iwo amene ali ndi ndalama opopedwawa mkumadwala anemiya kaya kuti kusowa kwa magazi nthupi ndie mukudabwapo chani? Sangaperekeso basi akwiya.

 17. MUKAFUNA KULEMBA NTCHITO MUMAKATENGA AZIBALE ANU NDIYE POTI NDI MAGAZI MWAFUNA MUNTHU WAMBA ANTHU OYIPA INU PAKALOWA MBEWA OKUMBA NDINU KOMA PAKALOWA NJOKA

 18. Hw can u donate blood while it’s a week without food in the house?Ask ur president n his idiotic fools they will give u blood. Stupid idiots! !!!

 19. Kuyangana amene akugwira kumenekowo ndarama zolandira mphwamwamwa,opeleka magazi k250 basi akafika nayo kuti olo chiwalo ndi chips osakwana,anga 15000 tube olo usiku ndikhonza kubwera

 20. Malo monena za njala ya vuta kunoyi mukukamba zopusa pitani kwa aja a cash gate muka Pope km ngati mukufuna kumpha athu pitani mizimu cz athuwa sakudya ndiye mukuyembekezera kt akupaseni magazi chaka chino chokha mwapase chimanga athuwa magazi mukatenge ku parliament

 21. People are sleeping on an empty [email protected] the point of death due to starvation.lnsofar,you expect them to danate blood?? Tell lbu and his hyena to donate blood to MBTS,these are the ones who enjoy the fruits Malawi is offering

 22. Basi tsekani bungwe mbava inu mwalowetsa maphunziro pansi ana onse anatha nzeru kamba kowatenga magazi. Ndikut tsekani bungwe upanda apo mukatenge achebalewanu

 23. Ine ndinasiya amenewa amagulisa magazi anthu nzipatala za privete, nzipatala za boma magazi amasowa pomwe zinazo amapezeka, ife tikamapeleka magazi cholinga chathu nchoti amalawi ovutika azithandizika, akafunika magazi, koma ayesa ngati bussinesss, zopusa akhale choncho

 24. KULISO CHAULELE PANO? POPEZA MUNTHU NGAKHALE APITE KUCHIPATALA MPAKA MUMAFUNA PAPEZEKE M’BALE WAKE APELEKE MAGAZI INE CHIBADWILENI, M’BALE WANGA AKAKHALA NDI VUTO LOCHEPA MAGAZI SINDINAMVEKO KUTI MAGAZI ALIPO TIMUTHILA AI.

 25. Magazi kupeleka koma akngofika mzipatala nkhani yasintha ali akugulisa demeti!!!!! Donate blood save lives ….so how come for bustards to blood yet ppoh donate for free?? U must also buy from ppoh ….. Munya muona!!!!!!!!!

 26. munthu kudwala mumati abwere mubale wake akapereke magazi koma magazi omwe mukutenga anthu mukongogulisa kunja bas anaanjoka inu.business imeneyo muziwapasaso ndalama anthu nawoso osat sobo yekha.inu kumagulisa ma million ku zipatala za private

 27. mukufuna magazi aulere koma munthu kusowa magazzi kuchipatala potulu discharge pali bilo pa botolo lamagazi. muzingolemerera magazi athuwa?

 28. kupeleka magazi nkulinga utakhuta!

  apeze mphatso za padera zopeleka kwa omwe amapelekawo kuti azikopa anzao nanga zoona ka tambula kamodzi ka sobo akuchotse 2ltz ukachokanso panemepo uzikafunafuna maganyu mKanengomu…?

 29. why don’t ask those thieves in parliament to donate coz they are healthier than poor citizens the cashgaters will donates blood ask them including Mr ibu

 30. nanga azingokamidwa ngati ng’ombe, apeze njira zina zopangira convice anthu,ndi responsibility ya Boma kupeza njira ndi ndondomeko zopelekera magazi, amene akumaba ndalamawo samafuna kumapelekako magaziwo, u r expecting munthu oti akuvutika kukagawa magazi aulerere ndikukamwa glass imodzi ya sobo, mmalo moti nthawi imeneyo asake ndalama yokadyetsera mbumba yake kunyumba, tizipeleka magazi kwa m’bale amene wasowa magazi nthawi imeneyo osati kungopeleka chisawawa, boma lichiteposo kanthu

%d bloggers like this: