Thugs in South Africa on Saturday brutally killed a Malawian man who was living in Cape Town in the country.
The deceased has been identified as Chifundo Abudu, 23.
According to another Malawian living in South Africa M’balaka Zoimbaimba, Abudu was stabbed to death when he was on his way from work to his home.
“Thugs demanded money from him but he didn’t give them because he had no money,” said M’balaka.
The thieves then produced a knife and stabbed the deceased until he died.
“He was badly beaten that is why we have failed to send the corpse to Malawi,” said M’balaka.
The deceased was together with his friend who was also badly injured and has been admitted at Cape Town Hospital.
The remains of late Abudu were laid to rest at Grasspark Cemetery in Cape Town, South Africa. The deceased hailed from Kamange village, Traditional Authority Malengachanzi in Nkhotakota.
Eish very painful
Ndindan ophedwayo and aluchokera chakutikuti m’malawi muja?
MAY HIS SOUL REST IN PEACE!!!! Koma aMalawi omwe akupanga nawo chipongwe ichi, ndithu adzafa imfa yowawa!!
it waz very sad. y this happened to our malawian we must do something us a malawian
koma mzachison tizitelono
chenjelani ndi Akazi aweni apo biii cape town kuli makaladi okwiya
So which man was killed in the picture above
Nawenso chizungucho sukuchimva bwanji? anakalemba chiyawo koma eti
Amene anapeke national anthem ya Malawi anali ndi bvumbulutso lalikulu popeza anapanga include nsanje which is a biggest disease among Malawians, tho zinali choncho kunali kwabwino kuwalora kuti atenge ndalamazo coz maso amulungu amaona zonse. God is not a man u beliv he cld replace and double those everything just like he did with Job.
Kodi mankwala adatha kodi??? Zitsiru izo kungozi funthisa basi…
Rest in peace mbale
Comment Loading…….
Ths story its not new it hpps anyday
Mmm very sad
R i p.
Nde wakufa ndamene alipa pic apa???????
Malawi 24 koma yaaaaas ine kaya!!!!!!!
Inna lillah wa inna ilayhi rajiuun..RIP
Mchiani a Malawi?
Sorry rip may his soul rest in peace
That dude got shot..nt brutally killed dnt gt it twisted..he is my homie,inna lillah wa inna ilyh raj’un
Man zachitika kuno sikuti anaombeledwa mayazi kunali kukhapa mwa nkhaza ku “Over come ” Capricon syd
Really? 3days I go friend frm Nkk there in SA posted..and anati amuombera..nde pot inuso mulikonko ndakuvetsetsan man
South African satana anayenda ndi mmwendo,kupha nzathu ctiona mvuto
These days don’t trust anyone except God and yourself. …
Chikondi cha chibadwidwe ndi umunthu zidatha…
Animals are far behaving well than ife wanthu….Shame!
R.I.P.
chimombo nkhani ukufotokoza iwe inachitika kuhoutbay mandelapark pomwe anthu omwe ali apa wamtaliyo anabayidwa ku capricon end maliro tayika sunday konkuno kucapetown grasspark
The killer they suppose to die with muthi. Every one who touch the body
Malawi national anthem,sanje,kaduka,malawian,people,
SA,is not nice place to stay bilive me
R i p brother amalawi safunila munthu zawo zabwino ufiti ndi sanje basi…ndakwiya nanu munalembela nyambalo kut zi duwise bro amenewa
Mpaka kumaphana guys
Timaphana tokha tokha kuno..
R.I P fundo
Rest in peace brother , we will miss u
I know de story n am also living in Capetown please anyasa muziyamba kaye mwafufuza then kupanga post
Imfa ili paliponse ndipo nthawi ikakwana yoti umwalire umamwaliira ngakhale ndi udzudzu. Tonse tinachokera kwada NAMALENGA Ndipo kwada IYE mkobwerera kwathu tonse.
Mjomba sopano
ohhh my frend why go soon,R.I.P
Kodi Bwana, Tatiuzan Ndiwakuti Amene Waphedwayo?Chonde Tiuzeniko!
nkhotakota ,TA malenga chanzi ,ngomba village, chifundo abudu
Rip. Its just somthing whch cn hapen to anyone anytym anywhere.
Admin bwanji koma mufuna kusuntha makolo anzanu mitima?tamalembani za Chanco apa za joni sizitikhuza tipange zathu kuno asiyeni ajoni apange za joni apa shatapu zako
Nkhanyi sindikuimvetsa mukumva kwanga mwati mwini ndalamayo alikumalawi, wachiwembuyu anatuluka ku police akufunanso adzipita ku Malawi nde anaphedwayo ndindani pakati pa anthu awiriwo?mwini ndalama ndi m’bale wake wachiwembuyo?
Nkhaniyi Ikumveka Bwino Baba
Chonchobe nanga titani? Malawi wavuta uyu kuzisaka basi, ena ndi awo ali ku saudi Arabia akulephela kubwelawa mmhhmm.
My condolence goes to de family n friend’s, u may soul rest internal n peace.We all knws dat life is not Permanent,,,but losing young pple, so sad.
ndkupepesa kwa onse agweledwa zovutazi ndikut pepani Yehova Akusamalire NdiKukutonthoza Mizumu Yawo iuse mtendele
Nanga amalawi pamenepo pali chikondi mpaka mzanu kumpangilachiwembu mtimawanjiru sitizatukukampaka kale cz wapadela sangaziwe kuti munthuwakuti ali ndindalama anthu opanda chikond amalawi anthuakuba ambanda acashgate osayamikila zimene wapanga nzathu ufiti sikutamba kokha ufiti uposeapa?why amalawi?MHSRIP AMEN!
South Africa is dangerous place to lieve,people act like animals their don’t have soul .Too much thug and envil people, may he’s soul rest in peace
Y a photo of smiling ppo pa nkhani yomvetsa chisoni ngati imeneyi
Nkhani yophedwa munthu panopa siyachilendo popeza ndi kwinakulikonse. Tizikaphana a Malawi tokhatokha, munthu ndi mbale wake ndiye tinene ku maiko a eni. Nkhani ndi kulimba mtima. Atachite tsoka kuphedwa tizingoti pepani osala imfa ili penapaliponse masiku osiliza
mmmh ur really gone can’t blv it ..may ur soul rest in peace bro..
MHRIP
tili mu masiku oopsya
Zoonadi nkhaniyi,ineinandipeza kuoffice kwacha,mtundu woyipa osakondana,ndi amalawi,matanzania ndiokondana,kuno malirosanapitebekumuzi,amalawi akumapeleka ,2,rand,amalawikomamabozandiyeawo
Koma kunoko ukangomenya mbama mu Bulidi, eeeish umva unyolo uwo. Koma abale athu umm kungophedwa ngati nyerere.
Muzilemba bwinobwino,chifukwadi Ku r,s,a,amalawi akuphedwadi,kumuziko simukunama,ndikulembapa mpakana pano sanapitebe kumudzi
Cape Town si malo
God bless the dead
Kuti kodi ndiziwitseni
Where exactly the decised was come from in Malawi?
Nkhotakota
Pofela salambula Rip
R.IP
Brutal killing is an evryday story here. All over the world. Thx for updating us anyway.
A malawi24 mundfunse ine ndikuwzan ma details onse bwinobwino,coz munthu anaphedwayu ndimakhala naye street imodz,and nyumba yake nd yang tinangosiyan nd nyumba 4.m’banda kucha womwe anaphedwa iyeyu,mfut zinandzutsa,and chiphedwelen munthuy week ino nd yachitatu,nkhope tawona last sat. Ku hall ina yotchedwa izikolobomi kuno ku houtbay,maliro anyamuka sat.likubwelali kamba kot tinali tikusonkhabe ndalama zot tikampase undertaker.munthuy anali nd m’bale ymwe amafna kut azibwel ku malawi,anal nd ndalama zokwana R80000 ndye tsiku lot anyamuka ngat ndinkuja,m’bale wake kingsley anampeza akuwelenga ndalamaz,kotelo anampangila chiwembu kuwawuza ma congoleese kut akamubele.tsikulu analephel chifkwa atakuwa anthu tinatuluka ndikuwasasantha ndipo anathawa and m’modzi anaphedwa.kutacha munthu anaphedway anamuwza m’bale wakeyu kut atngane nd mkaz wake akagone ku nyumba kwake kuopesa kut akuba aja angampezeso.kutada,akuba aja anamulondola munthuy komwe anakagona kuja.analipo 6,and onse anali nd mfut,atatchola nyumba,anaymba kufunsa komwe asiya ndalama,ndipamene anawombela m’mutu mwin nyumba uja,ndikuwombelas myendo iwili yonse ya mkaz wa mwini ndalama uja,pamenepo nkut mkaz wa mwini nyumba uja atatenga mwana ndikuthawa.keneko mwin ndalama uja anawauza kut awalondolela komw wasiy ndalamazo,akupita anawazemba nkuymba kuthaw,kenako anamuwombela ku nkhongo koma chipolopolo sichinafke mkat pot anali patali,anakafka ku police ndkukapnga report.iyeyu,anatulukaso ku chipatala panopa ali ku malawi.munthu wa chiwembuyu anatulukaso ku police and amat afna azibwelaso ku malawi. Kuno makosana amapanga chiwembu kwambili nd anthu wobwel.a malawi,ma congoleese nd ma vwambo.koma ngatiso kuli mtundu wopanda chikond,wosagwilizana, nd wa a #MALAWI
Tathokoza zamveka bwino
why amalawi doing like this
Tamva blaza
Timagulitsana tokhatokha amalawi and timaphananso tokhatokha ena ntchito saifuna amangokhalira kuba komweko
And the sad thing is,amadusaso pa maliropo,akakhala ku mowa anthu nkumamufusa kut unapangilanji zimenez amayankhula mozithemba kut amene akufna apange ziiyeyo.koma chosecho munthuy anali m’bale wake weni weni,bambo ake ang’ono mwana wawo
I hate Malawians in Cape Town,anthu a nsanje koopsya! Zitsanzo ndilinazo
Malawi mmmmm
Poor Malawian
But why a Malawi sitikondana??mulowelerepo mbuye
mzimu wake upume mwamtendere.
Too bad, here in SA anything can happen to u anytym just like anywhere on this planet, what matters is just giving them whatever u have if its 10rand produce it and give them or even a fon. All what they want is ur total surrender of every little thing u have don’t try to fuss with them coz they don’t care even akomkunonso amabayidwa ndi kuphedwa kumene, be alert guys life is irreplaceable.
That’s true bro
Good advise,be alert and bahave responsbly kuno nkwaeni kuno kupha munthu ndi ngati mene amaphera nkhuku
RIP Chifundo he was ma real friend yeah its true story en we was same place shelter
so sad,amene wamvala top ya grey
RIP.
What’s de name of de man? And where he comes from? Coz there many Malawians over there and they have got freinds and relatives around and over de contnent so u must give us full details of aperson ok. Coz he is not atree he is aman.
Wel.
Too bad! May his soul Rest In Peace!
There is no safe place in the world these days.
Last dayz! So sory
Rest in peace
Ooooo Allah
R I P
Zoti paliponse pali manda ayi anyamulidwe apite ku malawi. RIP bro dzikoli tikukhalila phamvu ya mulungu. Ndi uphawi kwanthu si ziko lokhalisa ili.
True story this happened in allocation called Capricorn
Sorry guys from that side
Brother they killed him like achicken
Chifukwa
Guys what happen? tell me plz,ndinakhalako mu church cicle 5yrs ago.
Dzina lake ndani.
ku USA,UK,Malawi ndingoti dziko lonse kuphana kosayamba dzikoli lili manja mwa oipa yemwe ndisatana,zimawawa kwachibale,pepani ofedwa Mulungu akutonthozeni ndipo Mulungu akufunisisa kuzathesa ifa panzikoli,ine ndikuyembekezela anthu akukhala mwamtendere atasiya kuphana.pepani.
But SA is too much
SA ndiziko lalikulu compair to Malawi ndesizingafanane koma ndimayiko ena SA akuchepela heavy.panga search uwone komwe kuli high crime rate panzikoli,uona achina America lyk south American countries,USA.dziko lonse kuli achina Boko halam uko.kungoti south Africa imatchuka kwambiri kwathuko coz ambiri akumeneko tili kuno nde ndifeso timakumana ndimavuto ngati amenewa.
Mbola….warning for the rest lvng n jozi take care above all ‘GOD’…may hs soul rest n peace.
Ndizomvetsa chisoni koma kwa omwe mukumudziwa mnyamatayo ndiuti kapena ndi mmodzi mwa anyamata ali pa chinth
Cape town yake iti
capricon
ok’zachisoni
Ndizomvetsa ch
Rlp
Not gud
Bad news and so sad..
May his soul rest in peace
These south African animals are a problem to our region
Ghosh!so sadd men.RIP
Kodi dzinalake ndani,side yake
Which,location in Capetown,man killied
capricon but I have forgottern the road
church circle
Sorry guys,.iwas there 5yrs ago,Ndimankhala plot ya Anitta mu church circle for 3yrs.
R I P
Dzina lake ndindani timudziwe
Open the link
His name is Chifundo Abudu from Kamange village TA Malengachanzi nkhotakota
Moto umapita komwe kuli tchire R.I.P pofera salambula
R.I.P
May her soul rest in peace
kunalembedwa kt adzafela ku joni.pali pose pali manda ndipo mzimu wake uuse mum’tendere NDIPO APELEKE MONI KWA ISAA NJOUJU,ROBART CHASOWA
R,I,P
Rip! Tithawira kuti kodi?
Eeeeeesh capetown ndima coloured opanda mano patsogolo too much kuvuta… #RSA_LAND_OF_HEARTLESS_PPOH
CPt is not for ma Cloloured wena… DEad by ma Coloured… :v 3:)
Kkkkkkkk hahahahahahaha hayi mara kkkkkk ma coloured wakhona that side kkkkkkkkkkkkkkkk
kkkkk ma keke eeee
Kkkkkkkkkkkk Kkkkkkkkkkkk Kkkkkkkkkkkk
Kkkkkkkkkkkk mara kkkkkkkkkkkk v>>>
RIP
How many people killed in Chilimba Blantyre from April to July ??? .. Kumenekoso ndi RSA???? Kulikose anthu akuphedwa.RIP
Man musathe mawu ndi chipongwe…anzanu analimutchire….mhsrip
#Ankala , chipongwecho ndiye chiticho apapa?? Ndikutanthauza kuti ku RSA anthu amaphana chimodzimodzi ngati kunoso ku malawi.. Uyu sikuti waphedwa chifukwa ali ku RSA.. Mwandimva????!??????!
SA is just too much. Pitani panet mufufuze anthu amend akuphedwa daily then come back to us.
Bwana #Vic population ya SA ndiyambiri kusiyana ndi kuno kwathu….
wina mpaka like, ufit upose pamenepo?
They are liking the post not the content….The post by Malawi24…that they hv informed us….
Si ufiti…
oky
R.I,P
Eish… he came to SA in search for green pasture now that he’s no more its very painful.RIP
Winaso wadzipha ku Hillbrow podziponya kuchoka pamwamba
Why?????
Ati chifuwa cha nkazi wake
RIP
MHSRIP
Very pityful story n may his soul R.I.P
Who is that man died?
too bad
May his soul rest in internal peace
His name pliz ?????
Forget the full name but he’s Abdul from nkhotakota
So sad
Bwerera Kunyumba
ngati mukunva pa Malawi pa kukoma sitonse a bwana
olo kwanu umatha kumwalila wat r u tryn to mean EJ ,,?rest n peace bro
wamwalilayo ndindani kodi? nanga amakhala cpt mbali yake iti? nanga kumuzi kwawo ndichakutiko
ali mu grey jezyyo amakhala ku Capetown koma kwao ndiku nkhotakota
IWE OSAWERENGA NKHANIYO BWANJI KAPENA KUCHURCH SIMUDAPITE ETI THUS WHY MUKUFUNSA CHONCHO SIMUKUNVAPO MWINA ZOMWE AKUNENAZO KAPENA SINANGA CHURCH SIMUNADUSEMO.
mmm malawians pali nkhani ya mpikisano apa? mmm@Elias behave urself
Pali ena amakhala aku user free data ndiye link singatsekule kungomuuza ndikuona ngat there is nothing to loose
Koma abale, dzina lake Chifundo Abudu ku malawi kwawo ndiku nkhotakota mudzi wa kamange TA Malengachanzi
MHSRP
So sad
Sad. R I P
kwanu ndi kwanu !
Hello I’m Samuel Okizou by name, I’m giving a testimony about Dr.Sule the great Herbalist, he has the cure to all manner of diseases, he cured my HIV disease, though I went through different website I saw different testimonies about different herbalists, I was like: “Many people have the HIV cure why are people still suffering from it?” I thought of it, then I contact Dr.Sule via email, I didn’t believe him that much, I just wanted to give him a try, he replied my mail and Needed some Information about me, then I sent them to him, he prepared the CURE and sent it to me via UPS courier service, they told me that it will take 3-4 days before I’ll get the parcel, 3 days later I received the package and I started taking the medicine as prescribed by him, after 7 days of taking the medicine I went for check-up, I was tested HIV NEGATIVE… IF YOU ARE SERIOUS YOU WILL BE CURED!!! contact Dr Sule on whats-app +2348162447651.
You davil fuck you
Ithink u drank!
Idiot….