Malawian man brutally murdered in South Africa

Advertisement

Thugs in South Africa on Saturday brutally killed a Malawian man who was living in Cape Town in the country.

Malawians in South Africa
Abudu (in grey top) was murdered while his friend was injured

The deceased has been identified as Chifundo Abudu, 23.

According to another Malawian living in South Africa M’balaka Zoimbaimba, Abudu was stabbed to death when he was on his way from work to his home.

“Thugs demanded money from him but he didn’t give them because he had no money,” said M’balaka.

The thieves then produced a knife and stabbed the deceased until he died.

“He was badly beaten that is why we have failed to send the corpse to Malawi,” said M’balaka.

The deceased was together with his friend who was also badly injured and has been admitted at Cape Town Hospital.

The remains of late Abudu were laid to rest at Grasspark Cemetery in Cape Town, South Africa. The deceased hailed from Kamange village, Traditional Authority Malengachanzi in Nkhotakota.

Advertisement

174 Comments

 1. Amene anapeke national anthem ya Malawi anali ndi bvumbulutso lalikulu popeza anapanga include nsanje which is a biggest disease among Malawians, tho zinali choncho kunali kwabwino kuwalora kuti atenge ndalamazo coz maso amulungu amaona zonse. God is not a man u beliv he cld replace and double those everything just like he did with Job.

 2. These days don’t trust anyone except God and yourself. …
  Chikondi cha chibadwidwe ndi umunthu zidatha…
  Animals are far behaving well than ife wanthu….Shame!
  R.I.P.

 3. chimombo nkhani ukufotokoza iwe inachitika kuhoutbay mandelapark pomwe anthu omwe ali apa wamtaliyo anabayidwa ku capricon end maliro tayika sunday konkuno kucapetown grasspark

 4. R i p brother amalawi safunila munthu zawo zabwino ufiti ndi sanje basi…ndakwiya nanu munalembela nyambalo kut zi duwise bro amenewa

 5. Imfa ili paliponse ndipo nthawi ikakwana yoti umwalire umamwaliira ngakhale ndi udzudzu. Tonse tinachokera kwada NAMALENGA Ndipo kwada IYE mkobwerera kwathu tonse.

 6. Admin bwanji koma mufuna kusuntha makolo anzanu mitima?tamalembani za Chanco apa za joni sizitikhuza tipange zathu kuno asiyeni ajoni apange za joni apa shatapu zako

 7. Nkhanyi sindikuimvetsa mukumva kwanga mwati mwini ndalamayo alikumalawi, wachiwembuyu anatuluka ku police akufunanso adzipita ku Malawi nde anaphedwayo ndindani pakati pa anthu awiriwo?mwini ndalama ndi m’bale wake wachiwembuyo?

 8. Chonchobe nanga titani? Malawi wavuta uyu kuzisaka basi, ena ndi awo ali ku saudi Arabia akulephela kubwelawa mmhhmm.

 9. My condolence goes to de family n friend’s, u may soul rest internal n peace.We all knws dat life is not Permanent,,,but losing young pple, so sad.

 10. Nanga amalawi pamenepo pali chikondi mpaka mzanu kumpangilachiwembu mtimawanjiru sitizatukukampaka kale cz wapadela sangaziwe kuti munthuwakuti ali ndindalama anthu opanda chikond amalawi anthuakuba ambanda acashgate osayamikila zimene wapanga nzathu ufiti sikutamba kokha ufiti uposeapa?why amalawi?MHSRIP AMEN!

 11. South Africa is dangerous place to lieve,people act like animals their don’t have soul .Too much thug and envil people, may he’s soul rest in peace

 12. Nkhani yophedwa munthu panopa siyachilendo popeza ndi kwinakulikonse. Tizikaphana a Malawi tokhatokha, munthu ndi mbale wake ndiye tinene ku maiko a eni. Nkhani ndi kulimba mtima. Atachite tsoka kuphedwa tizingoti pepani osala imfa ili penapaliponse masiku osiliza

 13. Zoonadi nkhaniyi,ineinandipeza kuoffice kwacha,mtundu woyipa osakondana,ndi amalawi,matanzania ndiokondana,kuno malirosanapitebekumuzi,amalawi akumapeleka ,2,rand,amalawikomamabozandiyeawo

 14. A malawi24 mundfunse ine ndikuwzan ma details onse bwinobwino,coz munthu anaphedwayu ndimakhala naye street imodz,and nyumba yake nd yang tinangosiyan nd nyumba 4.m’banda kucha womwe anaphedwa iyeyu,mfut zinandzutsa,and chiphedwelen munthuy week ino nd yachitatu,nkhope tawona last sat. Ku hall ina yotchedwa izikolobomi kuno ku houtbay,maliro anyamuka sat.likubwelali kamba kot tinali tikusonkhabe ndalama zot tikampase undertaker.munthuy anali nd m’bale ymwe amafna kut azibwel ku malawi,anal nd ndalama zokwana R80000 ndye tsiku lot anyamuka ngat ndinkuja,m’bale wake kingsley anampeza akuwelenga ndalamaz,kotelo anampangila chiwembu kuwawuza ma congoleese kut akamubele.tsikulu analephel chifkwa atakuwa anthu tinatuluka ndikuwasasantha ndipo anathawa and m’modzi anaphedwa.kutacha munthu anaphedway anamuwza m’bale wakeyu kut atngane nd mkaz wake akagone ku nyumba kwake kuopesa kut akuba aja angampezeso.kutada,akuba aja anamulondola munthuy komwe anakagona kuja.analipo 6,and onse anali nd mfut,atatchola nyumba,anaymba kufunsa komwe asiya ndalama,ndipamene anawombela m’mutu mwin nyumba uja,ndikuwombelas myendo iwili yonse ya mkaz wa mwini ndalama uja,pamenepo nkut mkaz wa mwini nyumba uja atatenga mwana ndikuthawa.keneko mwin ndalama uja anawauza kut awalondolela komw wasiy ndalamazo,akupita anawazemba nkuymba kuthaw,kenako anamuwombela ku nkhongo koma chipolopolo sichinafke mkat pot anali patali,anakafka ku police ndkukapnga report.iyeyu,anatulukaso ku chipatala panopa ali ku malawi.munthu wa chiwembuyu anatulukaso ku police and amat afna azibwelaso ku malawi. Kuno makosana amapanga chiwembu kwambili nd anthu wobwel.a malawi,ma congoleese nd ma vwambo.koma ngatiso kuli mtundu wopanda chikond,wosagwilizana, nd wa a #MALAWI

  1. And the sad thing is,amadusaso pa maliropo,akakhala ku mowa anthu nkumamufusa kut unapangilanji zimenez amayankhula mozithemba kut amene akufna apange ziiyeyo.koma chosecho munthuy anali m’bale wake weni weni,bambo ake ang’ono mwana wawo

 15. Too bad, here in SA anything can happen to u anytym just like anywhere on this planet, what matters is just giving them whatever u have if its 10rand produce it and give them or even a fon. All what they want is ur total surrender of every little thing u have don’t try to fuss with them coz they don’t care even akomkunonso amabayidwa ndi kuphedwa kumene, be alert guys life is irreplaceable.

 16. What’s de name of de man? And where he comes from? Coz there many Malawians over there and they have got freinds and relatives around and over de contnent so u must give us full details of aperson ok. Coz he is not atree he is aman.

 17. Zoti paliponse pali manda ayi anyamulidwe apite ku malawi. RIP bro dzikoli tikukhalila phamvu ya mulungu. Ndi uphawi kwanthu si ziko lokhalisa ili.

 18. ku USA,UK,Malawi ndingoti dziko lonse kuphana kosayamba dzikoli lili manja mwa oipa yemwe ndisatana,zimawawa kwachibale,pepani ofedwa Mulungu akutonthozeni ndipo Mulungu akufunisisa kuzathesa ifa panzikoli,ine ndikuyembekezela anthu akukhala mwamtendere atasiya kuphana.pepani.

  1. SA ndiziko lalikulu compair to Malawi ndesizingafanane koma ndimayiko ena SA akuchepela heavy.panga search uwone komwe kuli high crime rate panzikoli,uona achina America lyk south American countries,USA.dziko lonse kuli achina Boko halam uko.kungoti south Africa imatchuka kwambiri kwathuko coz ambiri akumeneko tili kuno nde ndifeso timakumana ndimavuto ngati amenewa.

 19. kunalembedwa kt adzafela ku joni.pali pose pali manda ndipo mzimu wake uuse mum’tendere NDIPO APELEKE MONI KWA ISAA NJOUJU,ROBART CHASOWA

  1. #Ankala , chipongwecho ndiye chiticho apapa?? Ndikutanthauza kuti ku RSA anthu amaphana chimodzimodzi ngati kunoso ku malawi.. Uyu sikuti waphedwa chifukwa ali ku RSA.. Mwandimva????!??????!

  1. IWE OSAWERENGA NKHANIYO BWANJI KAPENA KUCHURCH SIMUDAPITE ETI THUS WHY MUKUFUNSA CHONCHO SIMUKUNVAPO MWINA ZOMWE AKUNENAZO KAPENA SINANGA CHURCH SIMUNADUSEMO.

 20. Hello I’m Samuel Okizou by name, I’m giving a testimony about Dr.Sule the great Herbalist, he has the cure to all manner of diseases, he cured my HIV disease, though I went through different website I saw different testimonies about different herbalists, I was like: “Many people have the HIV cure why are people still suffering from it?” I thought of it, then I contact Dr.Sule via email, I didn’t believe him that much, I just wanted to give him a try, he replied my mail and Needed some Information about me, then I sent them to him, he prepared the CURE and sent it to me via UPS courier service, they told me that it will take 3-4 days before I’ll get the parcel, 3 days later I received the package and I started taking the medicine as prescribed by him, after 7 days of taking the medicine I went for check-up, I was tested HIV NEGATIVE… IF YOU ARE SERIOUS YOU WILL BE CURED!!! contact Dr Sule on whats-app +2348162447651.

Comments are closed.