University of Malawi’s Chancellor College has been closed, Malawi24 has the information.
According to a statement the College has been closed indefinitely with students being told to vacate the Campus by 4 pm today, 19 July 2016.
The decision to close the institution has come after the students were involved in running battles with the Police following government decision to hike fees with about 100%.
The students started protesting yesterday and in the process they turned violent and engaged in cat and mouse chase with Police Officers.
Today the students went back to rioting and blocked the way for a convoy that was carrying the US Second lady Jill Biden who is on a three day visit in the country.
As this is a developing news, Malawi24 will keep you updated.
zanyanyadi thogh am not there….
am not a students bu frankly speaking the hike is too much.Lets com together and fight for it
am not a students bu frankly speaking the
Munena apazi chifukwa cha kusaziwa nyengo yomwe ife tili mukadaziwa kut tili nyengo za masku omaliza sibwez mukumalimbana nd Peter Mutharika, ngakhale Mutharika atachoka kubwelapo Postor kapena sheihe musayembekezele ntendele mu dziko lanu kapena mu mabanja anu chifukwa tili thawi yowawisa zed. Muziwe izi Mutharika alibe campany yokhonza mafuta ai, komanso mu dziko mukafika njala si kut nd Presdent ai Presdent sangabwelese mvula kapena kuthesa mavuto anu onse no, pano ndikunenapa ndili ku Gaborun dziko la Botswana komatu tsiku nd siku athu akuchita zioneselo chifukwa cha kukwela kwa zithu Nayo Pula yagwelatu athu akuufula, ndmadabwa nazo amalawi ambili amalimbana nd Boma kuiwala kut nalo Boma nd athu omwe akuyenela kulola kut mau A Yehova akwanilisidwe oti masku akumapeto kuzakhala njala kukwela kwa zithu nd kusowa cikondi nd zina zotele. Sono athuni mukuyembekezela ntendele mmmmmm musaononge thawi yanu muzingofuulila kwa Yehova pa vuto lomwe muli nalo kulimbana nd boma kungotaya thawi yanu, ambili omwe akupeleka ma comments apawa ngosutsa Boma, ndan wabwino? Kapena ndan azakhale wabwino Mutharika akachoka?
Munena apazi chifukwa cha kusaziwa nyengo yomwe ife tili mukadaziwa kut tili nyengo za masku omaliza sibwez mukumalimbana nd Peter Mutharika, ngakhale Mutharika atachoka kubwelapo Postor kapena sheihe musayembekezele ntendele mu dziko lanu kapena mu mabanja anu chifukwa tili thawi yowawisa zed. Muziwe izi Mutharika alibe campany yokhonza mafuta ai, komanso mu dziko mukafika njala si kut nd Presdent ai Presdent sangabwelese mvula kapena kuthesa mavuto anu onse no, pano ndikunenapa ndili ku Gaborun dziko la Botswana komatu tsiku nd siku athu akuchita zioneselo chifukwa cha kukwela kwa zithu Nayo Pula yagwelatu athu akuufula, ndmadabwa nazo amalawi ambili amalimbana nd Boma kuiwala kut nalo Boma nd athu omwe akuyenela kulola kut mau A Yehova akwanilisidwe oti masku akumapeto kuzakhala njala kukwela kwa zithu nd kusowa cikondi nd zina zotele. Sono athuni mukuyembekezela ntendele mmmmmm musaononge thawi yanu muzingofuulila kwa Yehova pa vuto lomwe muli nalo kulimbana nd boma kungotaya thawi yanu, ambili omwe akupeleka ma comments apawa ngosutsa Boma, ndan wabwino? Kapena ndan azakhale wabwino Mutharika akachoka?
Bakili Muluzi mumkapatsilanji #mbeleswa mpando,? taonani pano nyasi zalowa m’mudzi fees kumangokweza ngati akweza #soap! Peter mutharika matako ako wamvaaaaa…… Ungofaso ngati bingu uja basi tivezina
Akuona ngati mtengo wa passport.akuona ngati akukweza mtengo wa mbewa
ghetto youth hold the faith
Mpaka lero a Malawi sanadziwebe kuti mzungu kwake ndi kutilakwitsa basi. Kumutsekera njira mzungu wamba wa ku America college kutsekedwa koma kuitsekera njira Inkosi ya Makhosi Gomani mudzingoseka. A Malawi mpaka lero tidakali mu mkonono tulo tofa nato.
NOLONGER BE CALLED MALAWI MAYBE IT CAN JUST BE NYASALAND WAMOTO
Komatu penapake zithuzi sitikuzitenga bwino amalawife sisawapase mpata anthu akunja kubwezeretsa mbuyo maphunziro athu kut tikhale mbuli 400,000 nkaitenga kutiko mene zithu zuvutilamo sibwinoyi koma think again
K400,000 is just too much for we poor malawians.Government should look into this mess!
Kuno akulipira R15,000 komatu amachita kuyendera zinthu zizikubwerera mbuyo sizachilendo
Increase salaries so that anyone can afford to pay that fuken amount ,idots,
Eee zowawa maphuzilo alowa pansi
Maboma ofoira akunyasalande
Yaaaaa koma mukhauladi simunati bwerani kuno muzizalima komaso zoti profesa afa mukunama munadya omweaja uyu sa afa ndi inu mpaka mwini wake azamutenge,mukunama mpaka twenty 19 wooooooo
Nanu Tasiyanitsani Ndale Ndichitukuko
Ayi zachitabwino zibwelani kuno. Kutheba tionjezele fees o kutibwelera posachedwa kuti tikapitilize maphudzilo paja munati ine ndili kuthebane ndiosaphuzila
Ndie ndikubwelatu ndizapitilize maphudzo anga achitabwino
Kkkkkkkkklkkkkkkkkkk
Akuphani ma proffessor,ndi amenewo,amachita zinthu ngati amwa kabanga
Malawi must expect more of these up until when she will know how to choose and vote wisely
True, I Have Already Meet With Luanar BSU ,President
Hello I’m Samuel Okizou by name, I’m giving a testimony about Dr.Sule the great Herbalist, he has the cure to all manner of diseases, he cured my HIV disease, though I went through different website I saw different testimonies about different herbalists, I was like: “Many people have the HIV cure why are people still suffering from it?” I thought of it, then I contact Dr.Sule via email, I didn’t believe him that much, I just wanted to give him a try, he replied my mail and Needed some Information about me, then I sent them to him, he prepared the CURE and sent it to me via UPS courier service, they told me that it will take 3-4 days before I’ll get the parcel, 3 days later I received the package and I started taking the medicine as prescribed by him, after 7 days of taking the medicine I went for check-up, I was tested HIV NEGATIVE… IF YOU ARE SERIOUS YOU WILL BE CURED!!! contact Dr Sule on whats-app +2348162447651.
Ndichifukwa chake malawi tidadzadzana mbuli zokhazokha chifukwa cha ma fees
That is good idea just to close it rather than giving the chance kwa ana amabwana kuti azipitiliza kuphunzira and everyone has the right to educate. Who don’t want to escape from poverty and yet education is a key for poverty eradication. Bola mngoyisekelatho kuti ana amabwana asatengere mwayi kumeneko
Zoona
U Deserve Better
zayenera kutelo nanga fees kukweza choncho chonsecho malipiro amakolo sanawakweze nde ngati pena imavuta yochepayi bwanji apapa mxiiiiiiiiew ufiti wawo ndithu
CHIBWANA CHIMALANDA,SI IZI?
Vuto sinu ai but ur vote . I hope next tym u wil vote wisely
Adzavotaso,abakha a anthu
Vuto la amalawi kuyiwala ati ophunzira akukuberani who conna manage to pay K400,000 . Eish so bad no money no xool
This government,,,!,,,, ndilosathandiza!!!!!! Matchona ayayayayaaaaaa!!!!!
This government,,,!,,,, ndilosathandiza!!!!!! Matchona ayayayayaaaaaa!!!!!
Muzamuvoteleso adzakumalizitseni
IT IS GOOD THAT IT IS CLOSED. THIS WILL GIVE HEADACHE TO THE PRESIDENT. IF IT OPENS, DEMOSTRATE AGAIN. YOU ARE NOT FIGHTING YOUR OWN WAR. YOU ARE FIGHTING FOR THE NATION. I WAS THERE DURING THE BINGU ADMINSTRATION. I LOST MY COMPUTER DUE TO A SUDDEN CLOSURE. I THOUGHT I WOULD NEVER GRADUATE, BUT HERE I AM. SO FIGHT TO THE VERY END. I THINK YOU HAVE EVER READ ‘THE CASE OF A PRISON MONGER’. A CERTAIN ETHIOPIAN LEADER WAS NOT SATISFIED WITH WHAT HE ALREADY HAD. HE THEREFORE RAISED THE PRICES. IN THE END ETHIOPIANS DEMONSTRATED, AND HE LOST HIS POSITION. CHANCO SIMANAMA AYI. WHAT CHANCO DEEMS VILE, IS INDEED VILE.
Haiboogh
Kodi a polisi akamaponya ma tea gass kuletsa mademo ndiye kuti iwowo akwanitsa kuwalipilira ana awo fees??? Kupepela mapolisi athu instead of joining in aaaah
I’m not a Unima parcel,but honestly speaking, the hike is way too much for an average Malawian whose salary doesn’t even shoot to that figure 3 months combined.A student is forced to demonstrate in an improper way chifukwa atati wapanga demonstrate mu njira yoyenera nothing would pay off.It could be a worse effect, but kudos my brothers and sisters!!!!!!!!
Abale mmmmmmmmmmm
the wife of vp america ? Eeeeeeeeeeh pepani .and washington will torelate this ? Impossible .feel the heat in the records and diplomatic cycles .who to blame ? Ya the savage sudents themselves and most importantly the protocol personal at capital hill who will push the blame to intelligence people and police .sorry malawians u touched a wrong button and secretly washington will punch back .u aare so small to embrass a wife of joe biden .u will kiss yo ass for this
Expt me
Benson hunga liked this
Mukutaya nthawi guys anena anena kkkkk
Zangoyamba apa ma demo akubwerabe zodanda nzambiri
Not new; chanco was also closed wen the current presdent was the minister of education in his brother’s era; poor administration!
ndengati uminister unavuta mbali imeneyi itheka? Malawi màyankho ali untiĺ this regime
That issue was already spoken before 2014,Malawians are more foolish
Malawi where r u going? Moti a mphawi ngat ife tizilipira k400 pin? Shaaaaaaaaa go chanco go!
OK chabwino mwachitanso mwano 700,000 kkkkkkkk kumalawi tinasiya kalekale kusisa zinthu koma timangokweza
Very good chanco am proud of u
The fees was too moch guys, tiwamvereko chisoni kwa makolo anawa,
Frankly speaking the hike is too much. Malawians are not united and even our civil society organisations are very weak. This is the time to join hands and fight at national level . This is a national issue and we have to stand up and fight.
gud idea lets unite
Kodi m’mesa mumafuna ma proffessor,ndi amenewo akukwaneni
Kkkkk. Alipo amene ankawafuna ine ayi.
zachibwana basi
Ndizomwe tinavotera za alomwezo mukuluranji nanga amalawi tili ndi vuto ndipo tiziona sitinatiiii bola moyo
Dziko ladzadza ndi nkhumbu nkhono zokhazokha.achule, apumbwa, abakha, achona,agulugufe,akanyimbi, abulu,mfiti, makape a anthu.Akadakhala kuti nawo ma MP sukulu adapita nayo patsogolo akadamakambiranako zolozeka koma ayi ndithu adangodzadzanako ndi ma JCE apo ndi apo kupezekako wa MSCE, no wander timfundo ngati akupanga ndi wa ku mental.Samadziwa momwe kumavutira kuipeza ndalama.nde aziti if you think education is expensive try ignorance, za chamba inuyo ndinu ma role model a ignorant ppo.Carl Marx sadaname kuti its only the rich who can acquire best education in a capitalist society and & Laws are made by and for the interest of the rich, whatever the poor did is labelled as deviant by the rich.when will this come to an end?? tatopa nanu ndi nkhalidwe lanu lonunkhali.Kuuma mtima ngati mfiti yayikazi bwanji??
Polly,Bunda,kamzu nursing n mzuzu pliz follow,work up.This is undermining us,stop reporting for classes
Its Truf I Have Oredy Told Luanar Bsu President
Fuck the system
A police akumalawi muli mvuto nkhanza to much anthu apange ziwonetselo they end up matear gas Malawi kulibe ufulu ,
Apolice a std8
college kapena shop? kumangotseka momwe afunira.what is wrong that it takes so long for Malawians to solve issues amicably? Oooooooosh!!!!!
enanu mukusangalala kut atseka xul mpaka kumati asatsekulenso. i understand u muli mgulu la anthu omwe mmaifira unima koma inakukanikani ndiyeno nsanje thooo. mukanakhala muli kuno sibwenzi muyankhula mopusa choncho. timadana nzopusa
selfshness imeneyo madam
selfshness imeneyo madam
Kuyankhula kumeneku ofunika fees ifike 2 meter mukuona ngat kukhala kumeneko nd nzeru ana opusa inu zedi
kkkkk enanu osamazipopa….
mmm so u say kuyfira UNIMA ? haha “Va te faire foutre!”
komanso umangochinditsako iwe…. wina akupanga arts humanity ntchito akaipeza kti.. u pay less than that. dont act as if u will pay the whole amount of money…. .. even if u r at unima but I will still be ur boss one day…. ngti kuli prog..yabho ndi law n public adm… koma zinazo matenda
Educated? No, not yet & that’s why they failed to reason on what to & not do.
Ambuye mulungu pangani zomwe munapanga ndi bingu afe uyu basi watikwana mulopwana uyu
Kkkkkkk
Tomse tudikila man mukati afe nanga inu poti asikana munawakanila mimba ajanso akukhumba inu mutafa ndiye tizimpempha mulungu kuti amuyambe ndani inu kapena peter
Alomwe mwaitola kwabasi dzikoli ngati yanu mudzaona polekera.Ndikungofuna kuti demo imeneyo isathe mwachangu mpaka mulomwe ameneyo atsitseko mtengo Wakewo cholinga akufuna aziba pakulu eti
kumalawi…kk,i remember fees hike issue happened n south africa,Zuma came openly to reverse the decision after demonstration done by the students,it reached the extent th@ the state house fence was shaken violently bt here some of u are speaking as if u ll manage to pay fees 4 u r kids,mudzafa imfa yowawa!!!!!
Very true. Malawians are taken 4 granted as if we are in one party rule.
Ku m’fire amene Pitalayo, nanga Polytechnic mukutani kodi? tiyeni mu Highway mo, ku Lilongwe konso Luanar tiyeni tiyeni #feehikemustfall…We nah tolerate dis ting.
Koma peter usamale nayo nkhaniyi ukumbukile kuti unalephera nkhani ya acadermic freedom uli nduna ya maphunziro pano ndiwe nsogoleri anawa afuna aone ngati mutu wako ukudoza.
Hahaha akagalauze kumudzi basi nyengo yamvula yasintha iyi,
great..
Ngat sungakwanitse siya wakukakamiza ndani?mafana aku chanco mumazfra ngat kusukulu uko mukapta ngat m’manyamula matoilet ndi nyumba zanu
Zopusazo Cndingaseke Ukudziwa Kt They Have Done A Proper Ting
peace,one love. zinthu zimatha kukambira. not in this way. Let’s pray before things get worse. Bigboy Gaspar Lawrence Jeck Çrint Nsona Kalaka Neviee Mnyemorankìng Nakimay Tapatapa Shooter Peter Che-nguni Kachikuni Osman Dzimbiri
Who is she after all? even in US they have their problems. She must this corrupt president to think before he does things. This president is stealing from the poor
Poly is comin soon! Pitala ameneyu asova!! Ikatja Poly Nao Mafumu akufuna apange ka demo ka Malo… Tiona kut athawira kuti bwampini ameneyu
shame!!
mukalambila ku Chanco konko . . .
afta all this, who wins? Mayb students? Maybe
Mwachta bwno kuitseka nthaw yolima. Mumanyenya alukhu inu. N musatsekule msanga mpaka kukolola next year.
Boma silopikisana nalo agalu inu a mcp
I Thought boma ndinu nomwe??? i dnt see any problem da pblm our leader….shame on him
Zoba iwe boma boma chani
Wachibwana Iwe, Wosawonaso
Kodi mukamati chabwino ndikukambilana…pamene amkakweza fees po anabwela kuzakambilana ndiife .?kumenyana basi kukamnbilana pambuyo
Azipitadi Ana amenewa azayesa zophweka akhaule
This is exactly how it started during the time of his brother..Demostrations everywhere,Escom and Water Boards strikes are next!!!
It’s Peter’s weakness. Uyu bwampini dziko lamukanika
Amene Mukumalalata Kut Ana Alakwitsa Its Just Becoz U R Not The 1 Akukwezeran Fees Ndpo Ku College Simumakudziwa.Imakanika 250 Ndye Mukati 400 Tikaitenga Kuti? Khalani Chete Amene Sizikukukhudzan Kom Ife Ngat Ana Asukulu Zikutiwawa Heavy.Go Chanco Go.
palibe cha nzeru chomwe akupanga ana a xul.kwa ine ndimaona ngati chabwino ndikukambilana bac.asasegule mwachangu abweleko tizawamwese mowa kuno.atsikanao abweleko tizawapase zimimba.nankha ndizomwe akufuna bac
#feesmustFall
Yah yachita bwino makape mukalime enainumunakaphedwepo kaye
Azikalima makape atopa ndikuphunzira
Makape mubakilanu.forus sitingakwanise kulipira K400,000.To be quite zikadatanthauza kuti our parents can afford to pay for that.Kwaife no problem njee! Timadana ndizankutu kupatula ma headphone! Mxiiiiiiiiiiiii
kkkkkk
kkkkkkkkkkkkkkk
Hahahaha!
Kkkkk koma yaaa
Kkkkk koma yaaa
Kkkkkkkk umakwana bwezi
morefire guyz osasuntha kudeni fenural kwawoxo de same.adafa chilembwe ife ndi ndanixo.
No winner no loser
Alomwe kukweza fees ngati kuti ndalamazo anthu amachita kukumba
akukweza poti iwo zawo zidayenda ndi dollar za cashgate
bad ting
Osawa chokera pa xul,,,fees shud indeed reduce
Achita bwino ndiye tione ngati apangenso matawo. Ma lecturer za zikulowa
Kape Iwe
Kkkkkkkk koma guys
Apolisi mkuzagwira atsikana okhaokha akuti amayambitsa ma demo! Ulenje wa zitete ndi mbewa by Malawi Police…..
Kupusa manyasa.
Zili bwino kwambiri,ndipo asaitsekule msanga,enawo amangoumilizidwa nda zinzao mkumapanga zauchitsiru zaozo,apa nde aliyense kwaokwao wina ku Galiva wina kwa Nyezerela, umapulumukira ku xool konko lero siwabwera? uziona.
dumb comment thou
Very
Bola wamva,ana a maPS amene amakuumilizaniwo xool akaitsekula abwelera pamene Mdyerakunthiko ngati iwe zako zada bax.
Kape iwe.xool umaiziwa? osangopisa nkabudula nkumakanda bwanji? 4tsek
Chitsilu galu mbuxi..ulibe nzelu nyanii
Tikudya Ayise Mbuli Yachabechabe,umaidziwa College? Zimawoneka Zopweka Ukakhala Kunjako Kom Ana Ama College Akuvutika Heavy Ndye Azikweza Fees Mwachimidz Chonch.Khala Chete Ayise Timavutika Ndife.
Kapumene kwa achamanu nonse
Harry u r ryt,
Mbeta or what ever your name is ngati mukuvutika pitani kwanu…akukukakamizani ndani.?
Vincent tell dem.
Development needs Education!
U vote for the change on 19 May 2014, so Ironically this is the change we wanted, DPP in action, come to 2019 u will still vote for them, u aren’t only u crying, ask poor malawian people, land tax bill is also there to punish our parents at the village, hehehehehe malawi will never listen, u thought DPP will change the things, u had hope with APM, I hope JB is remembered nw!
Anakisiya UNIMA iwe eti? Ndadabwa nawe
nanga #Idyani mkukhala dzina lamunthu wot ali ndi ubongo?
munkavota nokha anyani inu musadandaule ife school inativuta koma penapake zimatikhudza becoz ana athu azavutika kwambiri komaso nanu simudatsate ndondomeko yabwino akumangeni basi iyaaaa zachamba basi
stop being jelousy coz u never went thru the university of Malawi,do u know what 400,000 is?
iwe ndi galu idyani
U Dont Know Hw Public University Students Are Suffering, So Stupid
Kklkkkkkkl akulumatu anthuwa iwe
If ur suffering,withdraw and go where u won’t suffer,full stop!
Ya adziwe kuti mmene akupanga za girl child educationizo mwana wankaziyo kwawo sadzakwanitsa k400,000 ndiye azaisiya.
mukhale momo
iam not standing neither on chanco folks nor the gvt bt…the blockage that has happened is a big sin and the closure has come on time.
Osachoka guyz pa compus nawoni
uziadyesa iweyo
Mesa aziyamba dala okha amalizise nanga nde akangozisiya zitanthauza chani? kapena apindulapo chani.Iweyo Joe Mc Joe ukuona ngati ndangolembapo osaika komenti yako ku main story uko bwanji chamba eti
These kids need to be heard.They dont have money to pay on highly priced education.Fees must fall!
Man mukunena zoona bt sana tsate njira ya bho..imagine kumalanda mandasi poor pipo kuswa magalimoto a fans yosalakwa nawoso they are victims coz ali ndi ana..osapita ku ptc bwanji or kuswa galimoto za boma …as for me mademo samaononga za munthu…..
Thats what happens when people are demonstrating,if they damages cars thats police problem coz they would suppose to close the road leading to where demonstrations are taking place,Thats normal!
Owen# mukunena ngati munaliko waswa galimoto ndani was there and haven’t observed any bad act you assuming, please find a reliable source for valid information
#BabylonMustFall
Fanuel u are right. If the gap that’s existing between the rich and the poor is to be narrowed, then there is no point kumakweza fees like this coz one may think that it’s a way of denying higher and quality education to the poor Malawians knowing that they won’t afford to pay for their edu instead olemelawo ndi omwe azilipila ma fees okwelawo. Gap ilipoyo mkumangokulilabe. Go students go, kwatsala kwathu ku tipange zimenezi.
its too much guyz
nyasaland,,,,,52 years !
very bad….
Apanga chenene,,,
how come??????