Member of Parliament for Mulanje South, Bon Winiko Kalindo, has finally presented a petition to parliament which highly calls for a death penalty on attackers of people living with albinism in Malawi.
MP Kamlepo Kalua received the petition at parliament.
The protests was joined by hundred of people, most of whom said expected Kalindo and other leaders to be totally naked.
However, government has indicated it will not accept the calls, something which Kalindo says will fight for even to the last drop of his blood.
He has since called on government to consider the lives of albinos in Malawi arguing that without a functioning directive of death penalty on albinos, it equally means government is not concerned.
We have lots of feedback to come.
Koma NDE kwavuta ana kuonela ababo awo,!!
Ngati anthu akuphedwa inu muzingo yang’ana.sichoncho kwanilitsani utsogoleli .God bless u Hon kalindo amalawi awone utsogoleli waluntha ndi chifundo kudzela mwainu tili pamodzi nanu.
We have. to be. Serious about this as Malawian
Zaugalu Munthu wabanja lake kukhumbila misala manyazi agwile akazi ake ndi ana ake
Behind honorable
A gud citizen
I Salut Winiko Pazomwe Mwachita Ndinu Nokha Amene Mwaonetsa Kusakondwa Kwa Nchitidwe Onyasawu Ithink Tigodikila Boma Kuchichitaapo Kanyhu Big Up Bwana Bon Kalindo
Action spks louder than words. muli bho Hon keep it up olo asamve
Bambo a munthu amenewo , shitt anamwa kaye bawaaa ndikuyamba kuyenda malise ,, ugalu
zikuyenela kutelo kuvula basi
uchitsuru basi,nanga m’dala wamkulu ngati ameneyu aziyenda bwamuswe, y? komaaaaaaa! nyasalande wavuta uyu!!
Winiko ndi deal ndinamuonadi pa tv lero aliserious,,,,msamuopeze naneso nzavula njala ikaonjeza
Danny Matungweh
Bon kalindo ndi galu kudvula kukutanthaudza zichani ufiti chani.
Mumaitha bwana kalindo!
Iwe umafuna kumusalila winiko ndikukhulupilila wachita manyazi malo mosalila alubino usalila winiko pepa
Bon,am proud of u
stupit to those peopie who attended stupid demostration
Kkkkkkkk uku ndiye. Kukwiyadi
Shut up if you cannot do what is ‘proper’ to help , let the honourable be, he fights for justice the best way he knows how, peace!
Kuyenda osavala kkkk
Misala sakopera chifukwa ndi matenda a kumutu. Odwala misala sadziwa kuti wavula ndipo matendawa amagwira aliyese kaya mfumu,kapolo,mfulu. Mpofunika apite nao ku Zomba akayesedwe. Mutha kugaliza akupanga zionetsero koma mzanu atapenga.
It takes people with real courage and concern like Hon. Bon Kalindo. You are one of such freedom fighters for your gesture shows selflessness. Critics will always be there but you have achieved the objective. Bravo honourable
Big Man Wankulu
Tili limozi ada
Comment loading…..
Winiko waitha
Munthu osadza mavuto a malawi aletsa bwanji kuphedwa kkwa ma albino amalawi munasankha molakwika winiko wawabadwa ndikukulira mmalawi akudziwa za mavuto amunthu koma bwanawo mmmmmm ndi a ku america adziadziwa bwanji ndangodutsa sindinathyole mnkhwani
Bravo winiko!!!!!govt shud du samtin abt dis…..
guys dziko likufunika timusalile kudya winiko mwina ndi chiyabi chamisala
iz it not tikuferanji episode 2016 kkkkk
Waitha
winiko
bravo winiko!
concerned citizens……thumps up for ur presentation.APHEDWEEE!!!!
zilibwino
Winiko amene ndikumudziwa ine sioonda chonchi pezan nkhan ina yolemba
Do uthink boma lingavomereze kuti munthu ayende maliseche, izi sizingatathauze kanthu pa chitetezo cha alabino koposa kupempha unduna wa za chitetezo kuti akwimitse chitetezo kwa anthuwa. Dont be xtupit m’malo moti mudzikamba za njala ku nyumba ya malamulo mukukamba zovula, cholinga mudzisilirana kuti mudzigonana kufalitsa matenda, STOP THIS POUS.
not bad as we expected
ndikanakhala ku malawiko Winiko ndikanatenga ndodo ndikukwapula ndi2 kuyalusa Malawi basi MP wa Mulanje kkkkkkkkkk mawa muzavoteso a2 aku Mulanje.
Iwe ukuona ngat kupha munthu osalakwa pofuna ndalama ndikumangidwa kwa zaka zowelengeka sikuyalutsa dziko?
ndiye choyendera maliseche ndichiani? shortage of ———- .
Am behind Winiko well done guys for showing your concern upon the killing of innocent people
that is not naked
Kuyalusana basi zanyasi
Bravo Winiko
kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk
Zinayenera kutero.
Wawonetsa kulimba mtima pa chikondi winiko
kalindo has done his part. what about other mps?
Better than home sexual rights freedom fight
We have to stand as One and Stops the act of kiling and abduction of people with abnism
Bwana nyoookkkkkk
Ooooodi uuuukoooo!!!!!!
Mbuzi za wanthu
Ndiye kuti uthenga umapita patali ukakhala maliseche? Kungoyalutsa dziko lathu labwino bwino uku, nanga pamawa anyamatanso akazafuna uthenga ndiye akazavula muzati kutha Kwa dziko shame malawi
Come on the man just want u and the nation to c how serious this is
Serious kuonetsa zimimba , zimapants azibambo azizukulu zawo, ndiye ana awo akamaona zimenezo mawa akamavula nawonso azatha kuwalangiza?
It’s true that it’s unfair to see our relatives being illtreated. But Protesting while naked (uwunso siumunthu). Ngati boma silimamva, silingamve coz a honourable avula. Just as it is that an albino is just like any other person, how many have been found guilty of committing murder and have been charged with a death sentence? Ine ndangodana ndi kuvulako, umenewunso siukhwiri?
Bola anzakowa awonetsa kukhudzika pazomwe zikuchitikazi sanavule munthu ayi, iwe wapangapo chani? Kusamapweke ndikudzudzula m’malo mothandiza
Keep It Up Winiko
braval Mr nyoo!
A winiko anangoda nkhope koma mtima aonetsa apawu ndi woyenera kukhala woyera. Tipemphe a papa wathu atipatse winiko ngati woyera walero kuno kwathu!
komaaaa
komaaaa inu
Kkkk serious man
Mr s s s woye!!!!
KKKKKKK WiNIKO
KkKkk zilibwno fire wambili
That’s what Mr Kalindo have done, showing great concerns to the victims. U n me what have we done? I afford to stay behind u Mr Kalindo. Well done. We want these evil acts to STOP.
Winiko Ndi Wa Drama Zoona. Last Minute Nkunzasintha Akuti Tivale Boxer Nanga Uyo Sadamve Nawo Uthenga Wa Boxerwo Sindiye Kuti Wayenda Bwamuswe. Kkkk
Tiyen nazo bas
zkatele tmat zavuta, munthu wankulu kukhudzka. mukunveka!!!
Oh yah, freedom fighter
Winiko Ndi Nyoo!!
I salute honourable kalindo althought the government will not accept but u have showed that ur concerned and big up bwana ndi Mp yekhayo yemwe akukhunzidwa ndi zonyasa zomwe zuchitika Mmalawi not ma Mp enawa busy kubangulira ma allowances ndima loans God is watching for u
Sopano ku Malawi kuli mphongo ziwiri.zobwe tizizidalira winiko and Mr soldier l banda ili mbuyomuuuuu
koma kumeneko
kkkkkk koma ziliko
Winiko tionetse zida za America’zo tione. Nanga akuopa chani olemekezekawa?
Winiko wavula2 naye kkkkkk tamuona
Honourable Kalindoh; am proud of U always…kkkkkkkk!!! Mumaitha….. Odalah.
Men of character#1Malawi1People
nanga bwanji Winikoyo sadavule?
Kodi guys sibhoo! Kut tizilimbana ndi ndalama ngat chimchi
Mwaitha
zooona zake keep it up
Yako ija kk
Lyk u kalindo
In his wi trust