Senior Deputy Commissioner of police for the Central Region Hennings Mlotha has asked police heads from the region to be serious in fighting crime and to work together with community policing members.
Mlotha brought forward the statement in Mchinji when he opened a two day workshop on championing community policing for police officers from central region districts.
He said that as law enforcers they have a major role to play in addressing emerging issues such as albino killings.
“As a law enforcing agency we need to take keen interest in addressing issues to do with albino killings and take all necessary measures to sensitise communities,” Mlotha explained.
He however said that since the officers are in charge of resources in the district there is a need for them to come up with strategies.
Mlotha explained that officers working in borders districts need to be alert to prevent cases of transnational crimes such as theft.
The workshop was organised by Malawi Human Rights Resource Centre (MHRRC) and targeted police officers in-charge working in central region districts.
makamaka mbuzi zapalikhubula police unit
Ma officers a mu area 30 ndiye madolo odziwa ku soda(sleep on duty. or SOD). akamapita kuka guuarda ku area 43, 10, 11 ndi 12, amanyamura mkeka, blanket ndi small pillow. tsiku lina officer wina ma guard G4s anamubisira mfuti iye mtulo toferatu. mamembawa nthawi yogona amakhala nayo koma basi busy ma private ati kuzisaka mapeto ndi kuthyolera basi. musinthe tatopa nanu ndi kukudzudzulani.
kungona ndi konsayamba agalu awa
Kuwayimbira phone usiku kuti kwavuta amayankha kuti galimoto yathu ilibe mafuta tikupezani mawa ,basino iwo nkubwerela mu bulangete . Ndinthawi yokha ya Bingu chitetezo chimaoneka . Ikango kwana 800 pm ma vakabu paliponse .
Anapatsidwa ntchito zambiri omwewanso ndi a MRA ndiye akumatopa kwambiri azigona basi ndiufulu wao
Komaso Asiye Kutigwila Vakabu Masana Agalu Osakawa Atikwana Tukhala Ngat Kumalawi Kuno Sikwathu Bwanj?
Mmmmm ! Ngat akulephera kugwira mbava kma kulandira ndalama bas.
Ndiameneso akuyambitsa kuba ndiye pakufunika kuwapatsa malipilo 0chepa
…kkkkkkkkkkkkkkmmmm
A komishonala auzeni kwambiri za katangale amene atchuluka ku polisi kusiyana ndi kugona.
Azigona aphunga kunyumba yamalamulo asiye apolice chamba basi.
Zowona amagonadi dziwani izi mulungu analenga usiku ndi usana.Usiku ndi nthawi yoti tizigona kupumisa ubongo wathu.Masana tizigwira ntchito koma poti malingana ndizintchito zosiyanasiyana timagwira ndizimene zimapangisa tizigwira usiki.Koma ku usikuko kogwira nchito imafika nthawi yoti usinze basi ndipo umasinzadi
Komanso asiye kupepha ngati salipidwa
Manyumba amangileni a bwino abalewa satha kugona bwino usiku nchifukwa akugona ku ntchito
Koma adzilipilidwa bwino abalewa plz.
Big mam
and kachatso asiye kumwa akakhala pa duty
km ziko rakwathu ndimarikonda kwambiri chifukwa ndirachitetezo kwambiri ngankhara ndarama ririmbe km ndimasiyanisa ndikuno guy’s
Thats true even pa phwezi immigration officers half two amagona yabandakucha it was pa 4march this year
Mumaziwa zoti amagona mamembawa eti.? Kugona nkosayamba amachita kunyamula ma Blanket