Naked parade: Winiko to be arrested

Advertisement
Bon Kalindo

He should not only prepare to display his nakedness, he should also be planning to be in the cell in the cold month and maybe even naked.

Mulanje South lawmaker, Bon Kalindo, better know by his stage name Winiko will on 23rd June lead an all nude protest against the abductions and brutal murders of people with albinism.

Bon Kalindo
Bon Kalindo risks arrest.

Kalindo wants the use of death penalty for albino killers and maintained that he will go ahead with his naked protest.

But the Member of Parliament could be in fresh trouble as Malawi laws go against exposing nakedness in public.

‘’The offence of being an idle and disorderly person is divided into sub-categories listing various acts bringing a person within the ambit of the statute. If found to be an idle and disorderly person, a person is liable for a fine of K20 and may be sentenced to three months’ imprisonment if a first-time offender, and for a subsequent offence to a fine of K50 and six months’ imprisonment.’’ Reads Idle and Disorderly Persons (section 180) of the Malawi penal code.

However in one of his trending media interviews, Kalindo says he is not even afraid to be arrested or killed so ‘long as people with albinism live just as another person’.

‘’I can be arrested or killed, but I will not relent in fighting against theses barbaric acts.’’ He indicated.

Over 18 murder cases have been reported and 14 cases involving kidnapping of albinos are in the records and that three people with albinism are still missing while 28 graveyards of people with albinism have been tampered with in different circumstances, government has indicated.

Advertisement

258 Comments

 1. paja wina uja anaulula kuti bzness ya allubino ena aboma Ama tengapo mbali ndepalibe choti tidabwe or mutamumanga #winiko zikukhalila umboni

 2. Those who are against kalindo are the ones that take part in killing albinos

 3. Kuyenda maliseche kuonetsa mbolo kapena nyini kwa anthu ndi mulandu. Ayelekeze kuzaonetsa mbolo yakeyo azamangidwa

 4. Kkkkkk maliseche maliseche basi moti inenso panopa ndikupopana ndi fanz pa den pano kuti tilowe mntaunimu tili maliseche chifukwa zokupha albino zatikwana komanso winikoyo ndi ufulu wake kumenya nkhondo yovulayi kuti malo mwa albino mutenge maliseche akewa mwina mtima ukuphweni chifukwa nayenso waona kuti zanyanya kodi mesa paja kuli maufulu nanga ma hule amayenda bwaji akuonetsa maliseche simuwagwila tamusiyeni winiko bwanji mukumuseweletsa iwenso wa police usamapange zimenezi monga sukudziwa kuti kuli ufulu opanga zomwe tikufuna chabwino inunso apolice osavula bwanji muone m’ma offece mwanumo m’mene mungakongolere manyazi mayazi maliseche maliseche basi kwambiri amafuna muone local motiev yake kuti ili khenge nanga albino walakwa chani kuti aphedwe ineyo ndi winiko tililimodzi basi go konko konko konko high mulalo

 5. Keep it up munnaka.kuvula munayamba kale nthawi ya suport kumpila pa Muloza DEC.even America kills people.remember Sadam he was killed by hunging.yet the head Quar of HUMAN RIGHT WATCH is there.

 6. Mukulephela kumanga anthu omwe akupha azawo,koma kufuna kumanga muntu amene akuteteza anthu Boma la kumalawi Agalu opanda chifundo inu ,okonda anthu nthawi ya vot,matizolowera ,opusa ndi ife timavotela anthu omweomwewo kuchoka chipani ichi kulowa ichi,mwatikwakwaza nthawi yaitali ena ndi inu a police osauka inu oyenda pansi opanda Nyumba kumuzi ati muli pa Ntchio ?boma lake liti machende anu munatitopesa otsogolela inu ofuna zonse zikhale zanu pa kunya panu okuba inu tizikuopani inu Ziko lili lathu zaku nkholo eti timadya zanu ife tikamakuvotelan mukuona ngati timakupembezani timapindula chani kwanu za manyi eti

 7. Ndikakhala ine ndanola kale chikwanje kukonzekera mariseche parade .yemwe akayerekeze kumanga Winiko patsikiro ndikamudula khosi. Mr .M.P, ife tikudikira tsiku limeneri .

 8. Ndikakhala ine ndanola kale chikwanje kukonzekera mariseche parade .yemwe akayerekeze kumanga Winiko patsikiro ndikamudula khosi. Mr .M.P, ife tikudikira tsiku limeneri .

 9. zonsezi zikuonetsa kuti akuluakulu ena M’bomamo ali behind albino killings. Bwanji osamanga Wandale waku Thyolo uja ofuna kuti Mulanje ndi Thyolo likhale dziko loima pa lokha?

 10. Im truly behind Winiko but not up to that point of being naked in public..a Malawi are you serious ur busy kuikila kumbuyo zoyenda malisechezo???? My Malawi is gone forsure!

 11. Kumanga winiko it will mean that anthu amene ukupha azathuwa boma likuziwapo kanthu nde amalawi alino ndi ufulu opanga react against this nde mumangeni ife tili mbuyo mwakemo kaya ikhala civil war tiyeni nazoni ife nde kudya kwathu kumeneko

 12. Mungoyerekeza kummanga tigumula ndende zonse chifukwa alubino ndi munthu ngati wina aliyense nde mmalo momanga okupha alubino mukamange owamenyera nkhondo tiimilira tsopano

 13. Don’t worry too much about Mr Kalindo but worry about the dying alibinos. Arrest the killers, the buyers and the beneficially. Leave Kalindo alone, he is dying for a csuse!! Feel ashamed of your actions, you heartless murders!!

 14. human rights activists,where are you?..amayi oyendayenda(mahule) mumanena kuti ali ndi ufulu woyenda mbulanda nde winiko alibe ufulu woyenda mbulanda?..musiyeni ayende basi.

 15. Dont brame to kalindo awo ndimaganizo ake ndie mukufuna wina abwele ndikumati awuluka masana? Why malawian? Where r we goin nkhan yonsei we need action from gvt. Awikho tiyeni nazo!

 16. Kalindo palibe angamumange ,walakwa chani?koma zinazi tamasatirani chilungamo muzayankha walira ndi albino koma bon wamva mfuwu boma lalephera.

 17. tidzakhala anthu 2 tizavula kuwaziwitsa antthu oyipa moyo potipha anthu ifeyo opanda kuyambana nawo becouse of we dot have brown pigment think twice we are one people please pakufunika mulungu akuyendereni mwapadeladela

 18. Winiko is right he dont provock him leave him alone the goverment is doing nothing on th abinolisms they are killed like snake but the goverment jxt watching like drama i wish winiko can continue untile goverment bring nic protecton about killngs of abinolism winniko well done we will hold u untill the truth move naked anout abinolisms

 19. We are solidly behind you Mr! But zovulazi Iiiiiii kkkkkk iyayi mbwiyache! As honorable sizinayenera kutero! A police bwanawa atuluke before 24hrs otherwise muona agalu amichombo! Zikukukanikani kuchitapo kanthu pa Nkhaniyi ya alubinowa then mukukamanga munthu wosalakwa iye wangozivulira sadaphe! Uyu yekha atuluke please tisanayambe kupha a police nafe

 20. Nkhani yokupha ma albino anthu sakukondwera nayo, chifukwa aliyense amafuna moyo. Koma zoenda malisechezo ndiye che Winiko mukuonetsanso ku foira osati kukwiya. The best way ndikugwilizana ndi omwe akuti pakufunika kuchita match basi. Zizofoira zanu zoenda mbulandazo. Kumeneko sikukwiya mbwiyache koma ndikumbwambwana chabe.

 21. Ine ndavula kale, dzandimangeni. Chamba eti. Mity yanu apolisi

 22. This govt is childish indeed,they can’t foresee that arresting Winiko will bring a grave consequence chiefly because this guy is doing all these barely for the good of the nation,meaning that who ever attempts to tamper with him is also tampering with the entire nation,period.

 23. Nkhani yomvesa chisoni Chifukwa anthu akuphedwawo nawonso alindi ufulu wawo,apa zikuwoneseratu kuti A Polisi athu akulephela udindo woteteza anthu,komanso Boma lopanda Chisoni ndi anthu ake,Zoona munthu aziphedwa osalakwa.Mungamve bwanji ali mwana wanu? Mr Kalindo, Sakulakwisa Umunthu omwe alinawo ndichifukwa Maganizo ake afika potero,Kumeneko Sikukondwa koma kuwawidwa mtima

 24. How can I explain this testimony to the public about a great man who help me outin serious illness I have HIV AID for good 3year and I was almost going to the end ofmy life due to the way my skin look like all I have in my mind is let me just give up because life is not interesting to me any longer but I just pray for God every day to accept my soul when ever I’m gone lucky to me my kids brother run to me that he found a doctor in the internet who can cure HIV online he help me out on everything, the doctor ask for my details, so he can prepare the herbal medicine for me from his temple after all he ask is doneone week later I started getting more stronger my blood start flow normally for 4to 5 days I start getting Wight before 6 days my body start developing my skin start coming up after 8 days which he told me that i will be completely healed, I went for HIV test and I was tested negative I’m so happy that I can say I’m not a HIV patient if you have HIV/AID or any sickness he can still help you in getting your ex-back to you please contact him viahis email: [email protected], or whatsapp him on+2348143143878.

 25. mukamva utsilu nde umenewo.mummange tionesana zakuda zenzeni.ngati mwasowa nzeru kuthana ndi anthu akuphawa mwati mutiphere winiko.nazoni naked naked naked pamsewu mpaka albino apexe mtendere.apolice nanu muzitha kuona zithu zoti mpaka kummanga muthu..mmangeni ngat mukufuna musowe mmalawi muno

 26. Chamba chimenecho munthu akuwonesa mukwiyo wake pazopusa zikuchitika muziko ndiye amangidwe? Mulungu ndiwaphavu zimenezo mupanganazo manyazi anthu shem.

 27. Ine ndidzamatcha nawo, koma sindidzakhala gulu la anthu ovula; chifukwa ndidzavala Jombo, chipewa ndi neck tie. mudzandimanga nawonso?

 28. Peter ndi president odziwa kumanga anthu bwanji mulomwe amadana ndichilungamo amafuna kumuyamikira ngakhale angachite zopusa asiye anthu akumalawi apange zovuna zawo

 29. Who wants to see Most famous man naked ness that’s, mad ness,his Sisters to see his naked ness,all relatives He has gone too far, that’s in sanity, all we’re against killings but not in such adispeakable attempt.

 30. If the government will allow mr Kalindo to be arrested thats means the killing and abduction of our friends (albino) is allowed.Why arresting some one who is against the act of killing.I think anthu ena kundundako akuziwapo kanthu.

 31. Ine ndawonapo mwezi wa feburuary pa 20 chaka chino azungu kuphatikizapo anthu akuda akupalasa njinga ali bwa muswe kuchokela ku center point cape town kupita ku pilats casino apolice ali pompo nde sindiziwa k….??

 32. Mmene ndimamukondera winiko nde amangidwe eeeeee tayesani .bwanji osamanga njara irikumarawiko zitsilu zawanthu inu umburi basi

 33. Arrest those involved in cashghate, not someone who is crying for betterment of others,ziku peleka mafutso ambiri only God knows

 34. Hahahahahahahahaha paja mumadana ndi chilungamo agalu inu ?walakwa chani munthuyo osamanga akupha alubino WO bwanji?iwowo nde sianthu kusowa zochita etiiiiii tamumangeni tikuoneleni ngati mukufuna kutchuka mupeza polekela

 35. Inenso ndapeza kuti anthu akuluakulu ena am’boma akukhudzika ndizimenezi, pple lets all please stand at winikos back pliz pliz pliz, we might take t as drama as usual bt the guy z very right

  1. Ndipo apo biiii! akagwidwa okuphawa a police asamagwile nawo ntchitoyi tigwila tokha iyaaa tatopa nalo boza lawo loti kuli nsika sakuziwako mpaka pano, investgation yao yotani ,akuziwana anthuwa asatiphimbe mmaso ife mmxewww

 36. Apa zikusonyeza kuti akulu akulu aBoma akuziwapo kanthu coz sangamange munthu amene akufunira zabwino anzathu achi albino komanso ndingoti akumenyera ufulu mmalawi aliyense.It will be very very shame!

 37. Apa zikusonyeza kuti akulu akulu aBoma akuziwapo kanthu coz sangamange munthu amene akufunira zabwino anzathu achi albino komanso ndingoti akumenyera ufulu mmalawi aliyense.It will be very very shame

 38. Why are they going to arrest him? For expressing his views? Remember you. Lazy police officers Kalindo is representing the mases,u are failing to arrest the albino killers yet you are planning to arrest an innocent person

 39. Anthu amene mukuti Kalindo amangidwa chifukwa choyenda mbulanda mukunama. Kalindo ndi wa DPP. Akanakhala otsutsa pano atamumanga kale ngakhale kuvula asnavule koma kungolankhula. You remember certain Wandale who declared Thyolo and Mulanje sovereign state what happened to him? Nothing. You remember what happened to individuals who had a whatsup chat on how to topple government? They were arrested pompopompo. So do not cheat yourself that Kalindo can be arrested because of matching nude. Malawi justice is selective.

 40. Paja akapokola aku malawi ndichoncho munabgozolowera kumanga anthu opanda milandu, ngati mumaidziwa ntchito yanu bwanji osakamanga okupha ma albino, mulungu akukuonani ndipo akuyankhani ndithu

 41. Nkhani yophedwa kwa abale athu achialubino boma likuchita zozizira kaya chifukwa chani kaya???? koma anthu atayamba kupha ma CHINA omwe amatithandizawa eeeeeee mukhonza kuona boma litapeleka wa police mmodzimodzi kwa M’CHINA aliyense,,,,chonde a PITALA ku state house ko tagwira chikhadabo chanu chitanipo kanthu choooondeeee

 42. yelekezani kummanga ifeso tidzavula nawo Kodi abomawa akukhuzidwa ndi kuphedwa kwa ma albino eti? nanga zikuwapweteka bwanji blatful zanu

 43. yelekezani kummanga ifeso tidzavula nawo Kodi abomawa akukhuzidwa ndi kuphedwa kwa ma albino eti? nanga zikuwapweteka bwanji blatful zanu

 44. Peter Ali mugulu lija lochedwa miracle money kma ndingoti mulungu akuona kodi iye sangazifutse kut brz ili kut kma mulungu Ali ndi mphavu yonse osat za Madzizo ai

 45. we’re with u winiko,ngati akufuna awone mkwiyo wathu azakumangeni inuyo.zachamba mukuteteza anzathu ndiye akumangeni?akamange azimayi ndi asikana akumayenda osavalawa.zausiru eti.

 46. But mkango ukathawa ku reserve umaphedwa even if usanaphe munthu winiko is right those killer must face kwizingation

 47. Winiko is standing for our brothers n sisters, arresting him will call for civil war. I support him n who ever thinks if arresting him ndi mbuzi. Ndalama mumaba kale y killing innocent people???

 48. Ana anjoka y arrest Kalindo?? Mukufuna anthu aziopa kumenyela ufulu anzao?? Mukangomumanga expect very strong n united MOBJUSTICE with all abilities of burning as well as breaking policestions just to kill albino killers.

 49. Where is the human rights activist in malawi now? I know we hear then talk alot on other issues, I guess this one doesn’t need much attention, does it?

 50. asaaa!!zaz!!!!! asanammange winiko ayambe apha kaye Oooooose! amene akumapha anzanthu albino basi pamenepo tathana(NAWONSO ndi ANTHU)

 51. Apa zachita kuziwikiratu kut peter akumawatuma anthu kut azipha abale anthuwa tatsegulani maso guyz.kusayina akukana kupanga zionesero akukana. Tisachedwepo ndi iye akumpha anthuwa

 52. zitheke basi,ngati iwo anali ndi malingaliro okutha mtundu wachi albino posowesa mmodzimmozi takana ku malawi kuno,go ahead winiko aziwe ukanakhala wa oposition akanati ndiwe oukira.2019 uyambe chipani chako tikujoina,ndiwe otchuka kale uzawina basi pa upresident ndiwe olimba mtima ngati futi yophera patali.

 53. Team Bon mwana wa Kalindo Winiko!! Go mbwiyache !go& me with all youth cadates of Mj will support you, more over ka fine komwe akufunako its very cheap nanga k20 /50 manyazi alibe r

 54. Hope the government knows something.Is winiko protesting for salary increase????.Some pple are interested with this killings.The government cld hv to bring the right solution at the right time

 55. kuyenda maliseche sikuthandiza we just need our government to do something to stop this killing of innocrnt people

 56. Bale winiko nkhani ukunenayo ndiyoonadi kwa wina aliyense okonda dziko lathu lino,tingomatch osati zanaked zo,apapa mmene zikuonekera bomamu akudziwapo kanthu,chifukwa serious siikuoneka

 57. Akamange ache ambuyanu amene wayambatsa zoti amangidwe ndiamene akulimbikitsa kuti alibino aziphedwa osamanga anthu amene akuyenda osavalawa bwanji zopusa.

 58. Inenso wakonko katundu yense panja, azibale wathu azingosowa mosaziwika bwino, kaya kundende tikakhala bola abale athu apeze ntendele. Malawi ndi dziko la wina aliense kaya albino , light skin black skin, olemera, osauka nde umphawi wako usakupangise kuti ntundu wina wa anthu ukhale opanda ntendele. Tiyeni tikondane wina ndi nzake……..!!!!

 59. Nsaname nkhan zina nkamamva zimandipsetsa mtima! !! Nssaa!! Tsono kuteroku tinene kuti apolisi mukudziwa kanthu pa mchitidwe umenewuuu??
  Eshh….

 60. The capacity of this demo is uncalled for. Am not a politician and never will. But nudity? I bet the police to come out quickly and scarf their hands not even a meter from the building they will start. How can Malawi be blessed by God if we publicise our private parts in the name of demo? MPs must lead by good examples unlike Winiko. Only crazy people do walk on streets enjoying their nakedness hence organisers of this demo

 61. Mukozekele kuzamangaso ine, pamodzi ndi banja langa, poti tose tikukayenda basi kufikila tsiku lomwe azathu achi alubino adzakhale otetezedwa ndi malamulo adziko lino,,, kwa omwe simunaluzepo m’bale wanu kapena kuona ifa zowawa zomwe azathu ma alubino akukumana nawo mukutengela nkhani yoseweletsa koma chaona mzako chapita mwawa chili pa iwe,,,,

 62. You also need to arrest most of these women in town, we dont like their nakedness either. They got no reason to be naked but Kalindo has a good reason!

 63. You also need to arrest most of these women in town, we dont like their nakedness either. They got no reason to be naked but Kalindo has a good reason!

 64. Aaaaaah!fokofuuuuu!! atam’mange ndindani ndipo chifukwa chachani?? ineyo mpakana ambuyanga zikutiwawa ndipo tizavula kumene,arrest us too za ziiii basi.

 65. Boma ndilo pusa kwambili la Bwapini bwanji osamagulitsa minyanga ya njobvu zina mukulimba ndikupha albino chomwe muziwe bwapini nayeso Ali gululimozi lopha anthu chifukwa chiyani Mr Kalindo mukuwamanga chifukwa khani anayambisa anthu awili kunyumba yamalamuro ndi Mr Lucius Banda mukumuwopa chani soja inu apolice apa Malawi mutiyakhulisa pambali mwava agalu wosaka inu ngati bwapini wakukutumani wakupwetekesani

 66. eeeee mukamanga ambiri ineso I will be there Boma likuziwapo kathu whay sakulola poti lamuloli lilipo kale malamulo wathu,

 67. ….. if i put on my under wear and walks no one can arrests me of nakedness, once you arrest then you have to compensate me in court……..

 68. Prostitutes are walking naked in public places and you just ignore them instead of arrest them you say they express their freedom so let Winiko express his freedom too.

 69. kkkkk koma zoonetsana maliseche zo ndie ayi akañasankha njira ina mufuña anthu akaona katundu ali bii aziona ngati amakhala ndi zakuda ndi alomwe okha osadziwa kuti ndi wina àli yense ndi choñcho

 70. Kuteloko boma likuziwapo kanthu ndi lomwe likutuma anthu kumapha anthu amtundu umenewu, but remember one thing God is watching you no matter what you skin is black or white we are all chifanuziro chamulungu , aliyense azakayankha mafunso pazintchito zomwe iye anachita

  1. ndipo kumangidwa winiko ndichachiziwikile Peter akuziwa kathu kuti aziphedwa albino angofuna kutitseka mmanso basi.

 71. arrest me too am also concerned with the killing of people with albinism.tikayenda chinochino ndi winiko akatundu athu atakwiyilatu.akuloza pansi ndikuloza kumwamba kkkk komanso mukaona tchire kkk

 72. koma abale AAA chisakho chako iwe winiko bwanji? waziyalusa wekhatu apa + ukarowanso. phindu ra iwe ndi chani? basi malamuro agwire ntchito waziyamba dara uyu!!

 73. arrest me too am also concerned with the killing of people with albinism.tikayenda chinochino ndi winiko akatundu athu atakwiyilatu.akuloza pansi ndikuloza kumwamba kkkk komanso mukaona tchire kkk

Comments are closed.