White tobacco buyer mercilessly beat farmer: Government backs the buyer

A white tobacco buyer on Thursday roughed up a farmer during a fracas that happened at Kanengo Auction floors in Lilongwe.

farmer
The farmer who was roughed up

According to reports, when sales began for the day, the farmers demanded that they should be offered higher prices and also expressed worry at the high rejection rate which had shot up to 70 percent.

At the same time, the farmers were also incensed after noticing that sales were going on well in the contract section of the floors where tobacco was being bought at $200 per Kg and the leaf was not being rejected.

The angry farmers then went to the contract section and disrupted sales.

The growers’ demands and conduct exasperated the white man who beat up one of the famers. In reaction, the farmers mobilised themselves and chased away the buyers from the floors.

The fracas led to the suspension of tobacco sales at the auction floors.

Meanwhile, government has vowed to review security at the floors in order to protect white buyers from being attacked by irate farmers.

Yesterday, officials from Tobacco Control Commission, Tobacco Association of Malawi and AHL Group met to discuss the way forward on the matter.

 

Advertisement

149 Comments

 1. It doesn’t matter wat he dd yu white in my country then yu beat up my people it doesn’t go well with mi. ….i will hurt Him idont care who the hell he is

 2. Whether a european or an african but z there any room 4 boxing? A buyer beating a farmer! Munthu amulinireni hona mbwenu mukubomontholaso na fayiti. Nayo alichetee no kuwezgela. chikuwa ngati chidole. Akulu chifundo chidapha msema mitondo, nawe nga ukaponyako nochimbira. Panji ukukhumba kulwa nayo yakabisalira ya Mau Mau movement?? Ka nadi waka chetee ukagomezga vichi???

 3. Osati kuzikonda kokha …komanso kupusa atumbuka And we are planning nonse tikuthamangisan muzipita Kwanu

 4. Ife amalawi ndichoncho makamaka tikawona mzungu timakhala ngati tawona Mulungu nanga tawonani boma mpaka kumakhaliranso Mzungu chonsecho ndiwobwera maiko anzathu kulibe zimenezo ukakhala wobwera olo ulakwe kaya usalakwe mulandu umakugwera basi, kungoti malawi tulo kwambiri tatiyeni amalawi tidzichenjera dziko ndilathu ili

 5. Baba osalira dziko ndi lokondera ili likomera opata nanga kuvutika ndi kulima tokha kumenyedwanso tokha tigwira mtengo wanji nanga inunso a JUSTIN mukunena zitinso atumbuka mumapenga ndi akazi okongola akwathu kuno inu kwanu kuli akasemasema okha okha ndinapita pa kalonga boma nkazi okongola amene ndinamuona kwawo kunali ku zomba meaning kuti mpoto ndi mpotodi black black osaonako owezuka kkk

 6. atleast, kumenyedwa ndi mzungu?? ndi chinthu cha mtengo wapatali zeeedi, olo kunyumbako ndikhulupilila kuti alamu ndi osangalala, olo powauza odzazonda akumanyadila kuti iwowo oli mnyumbamu adawapanda mzungu ku msika

 7. Uku ndiye timati ‘kutsotsobetsedwa’ mpakana mutu wonse kutupa! chonde gulani fodya wakeyo kuti azikagula PANADO ndi INDOSIN chifkwa thupi lake lonse likungophwanya.

 8. Iwe Justin ndwe galu wava,kupusaa,pali nkhani zonyozana mitundu apaa kwanuko simulima fodyaa??????chitsiru iwe etii,ngatii ulibe chonena osangokhala bwanjiiii,pa chakuti pakoooo,panyooo,nyoooooo

 9. Amenewo ndwo amalawi kumangoyang’ana, ena kumavulala chonch pofuna kutchedwa aulemu. Make up my country! Get wel soon

 10. Amenewo ndwo amalawi kumangoyang’ana, ena kumavulala chonch pofuna kutchedwa aulemu. Make up my country! Get wel soon

 11. Amenewo ndwo amalawi kumangoyang’ana, ena kumavulala chonch pofuna kutchedwa aulemu. Make up my country! Get wel soon

 12. Amenewo ndwo amalawi kumangoyang’ana, ena kumavulala chonch pofuna kutchedwa aulemu. Make up my country! Get wel soon

 13. Amenewo ndwo amalawi kumangoyang’ana, ena kumavulala chonch pofuna kutchedwa aulemu. Make up my country! Get wel soon

 14. Amenewo ndwo amalawi kumangoyang’ana, ena kumavulala chonch pofuna kutchedwa aulemu. Make up my country! Get wel soon

 15. Wakeup Malawi muzadzuka liti zoona munthu kumakumenya dziko lili lako ndichikana Tanzania akufuna kukulanda nyanja iam on the way coming there bt if yo still sleeping you will b in hot soup Malawi

 16. Monday ndubwera konko ndizakukhazulani nonse ma buas inu, mesa ma buno inu ndinu ma peasant farmers kwanuko nde poti ndife amphawi basiiii, shaaaa odala alozedwe onthuwa

 17. shaaaaaaaaaaaa!!!…babawa avulala zeditu awa!!!!!..mawonekedwe ake amenewa??

 18. koma mmene akuonekera pachithumzipa ndi mlimi ofoyiradi ndinthu fodya wako mphamvu zako kukutibulanso hahahahaha amalawi tulo ku jon sangawayelekeze

 19. Ine ndinali komko simzungu amene wamenya mulimi ndizoona kt mulimiyu wamenyedwa ndimmodzi mwa ogula fodya waalliance one dzina lake ndi Peter koma kungoti munthu wamenyedwayu izi sizimamukhudza

 20. Ine ndinali komko simzungu amene wamenya mulimi ndizoona kt mulimiyu wamenyedwa ndimmodzi mwa ogula fodya waalliance one dzina lake ndi Peter koma kungoti munthu wamenyedwayu izi sizimamukhudza

  1. How can you say such a thing? I pray to God to honour your family with birth of an albino.

 21. Ingosiyani kulima fodya baxxxx,

  Azanu akulima soya, chimanga, mtedza akapita pa msika mtengo ogulitsila amanena okha, sikelo yopimila amachokaso nayo kwawo…. & amakhala ndi confidence pa ulimi wawo, coz amadziwa kut no matter wat a day wil come they will sell their item since everyone depends on food….

 22. Sopano nayeso mlimi anaonjeza. Iye akumukulila mtima nzungu mmalo moti azimunyengelela kuti amuguleko fodya wakeyo? Anzake fodya wawo wapangidwa rejected abwelela naye kunyumba, iyeyu azidandaula mitengo??? Dont blame nzungu ogula here, rather blame the kwacha which has not been fixed during this tobacco auction. Myviews.com

  1. I support Ramona. Read and understand what he has said. Sometimes we Malawians are pompous and very rude without considering the situations we are in at hand. Muzungu cannot beat u without a good reason. You see now? He will never buy your fodya anymore. Uzikasuta Chingambwe!!

 23. How can I explain this testimony to the public about a great man who help me out in serious illness I have HIV AID for good 3year and I was almost going to the end of my life due to the way my skin look like all I have in my mind is let me just give up because life is not interesting to me any longer but I just pray for God every day to accept my soul when ever I’m gone lucky to me my kids brother run to me that he found a doctor in the internet who can cure HIV online he help me out on everything, the doctor ask for my details, so he can prepare the herbal medicine for me from his temple after all he ask is done one week later I started getting more stronger my blood start flow normally for 4 to 5 days I start getting Wight before 6 days my body start developing my skin start coming up after 8 days which he told me that i will be completely healed, I went for HIV test and I was tested negative I’m so happy that I can say I’m not a HIV patient if you have HIV/AID or any sickness he can still help you in getting your ex-back to you please contact him via his email: [email protected], or whatsapp him on +2348143143878.

 24. Anamenyana,komanso anayiyamba ndi munthuyo ndiye mzungu anangomuonetsa kuti ndalama ndi zake,komanso mamenyedwe ali nawo…….chonde alimi tiyeni tigulitse chingambwe chathu mwa mtendere,ogulawa akanyanyala sitingagaitse ufa nkumadya ndi ana zima barley zanuzo,ndimanyowa basi ndiye tikapeza otigula zinyalalazo tiyeni timulemekeze osati kumamugendanso ndi zafodya zanuzo,mutimenyetsa.

 25. Anamenyana,komanso anayiyamba ndi munthuyo ndiye mzungu anangomuonetsa kuti ndalama ndi zake,komanso mamenyedwe ali nawo…….chonde alimi tiyeni tigulitse chingambwe chathu mwa mtendere,ogulawa akanyanyala sitingagaitse ufa nkumadya ndi ana zima barley zanuzo,ndimanyowa basi ndiye tikapeza otigula zinyalalazo tiyeni timulemekeze osati kumamugendanso ndi zafodya zanuzo,mutimenyetsa.

 26. ndiye mmlimi wachitapo chiyani?osakasuma ku court bwanji?

 27. kkkkkk Ada amenyedwawo ndi awa! ali pachithuzipa!? hhhhh!! koma nawoso awonjezatu kusinjilila kkkkkk mpaka kugwesa khope pansi chochi kkkkk chochobe zache zayenda Alandila Compasation yoti ndiii!!kkkkkk.

 28. mmmm ine ndinali konko,sanali mzungu,alina munthu wakuda dzina lake jack amagula ku allaince anamenya fight kwa mlimi mutu uku akumugenda ndi ndindi za fodya mmaso.kungoti tsitsi lake analiyeretsa ngati general kanene.

 29. mmmm ine ndinali konko,sanali mzungu,alina munthu wakuda dzina lake jack amagula ku allaince anamenya fight kwa mlimi mutu uku akumugenda ndi ndindi za fodya mmaso.kungoti tsitsi lake analiyeretsa ngati general kanene.

 30. White tobacco buyer?? Buyer ndi buyer basi whether black or white. Grammaticay if we substitute white with black then how does it sound?

 31. In Malawi, a foreigner is always treated like a king, and a white man is always a boss.
  Wake Up Malawi !!!

 32. Inu musatinamizepoyapa muzungu weniweni wamakono sangapande/kumenya munthu, koma muziti INDIAN/CHINESE buyer chifukwa ndiamene mumawatchula kuti “azungu” aku Malawi ko azungu enieni sumawadziwa.

  1. Ha-ha-ha….. which article? As 4 me, I don’t have to go 4 the whole thing headline is enough, I don’t not have huge time, OK?

  2. Apa zikuchita kuonetseratu kuti nkhani ndi ya racism (kudana ndi azungu) nkuona kwathuko sikuzatukuka muzungu ndi dhilu osati zomangolimbana ndi ma technology anyanga (ufiti) kulimbana ndi myoyo ya anthu isalakwa ma albino, no mzungu umphawi mpaka nakalekale, nanga Malawi yonseyo osakhala ndi mseu fili wee? Ufiti, ma polofeti onyenye ndi zina zotere zoipa basi….. Kumalimbana popanda chifukwa??

Comments are closed.